LEAH WAPHAPHALISA MKULU WA PAC BISHOP MATONGA NDI MAFUNSO OKWIYA~ NANGA PAC INYOZA BWANJI CHAKWERA?

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 31 січ 2025

КОМЕНТАРІ • 32

  • @JoelTchuma-g3s
    @JoelTchuma-g3s 10 днів тому +1

    PAC says, "Proverbs 27:5,6, Open rebuke is better than secret love.(A love that says and does nothing is not as valuable as an affection that rebukes.)vs 6.Faithful are the wounds of a friend;but the kisses of an enemy are deceitful.(A "friend" who will kindly tell you of your mistakes or faults is not destructive,but rather helpful [faithful].Conversely,one who flatters and kisses proclaiming everything to be wonderful and well,when in reality,it is not,is said by God to be "deceitful" and therefore ,an "enemy. ")

  • @CharlesMlenga-k4m
    @CharlesMlenga-k4m 15 днів тому +5

    Sitikusintha❤❤❤

  • @ReadsonChisaga
    @ReadsonChisaga 14 днів тому +2

    Ndi omwewa afiti opemphela anatiika m'mavuto azawoneni, zaka 4 zonsezi amati Chakwera akuyendesa dziko bwino, ife a Malawi tikuvutika.

  • @BakhePaliso-h8h
    @BakhePaliso-h8h 11 днів тому +2

    Boma ndilomweri la Malawi koma utsogoreri tisintha

  • @TonyMhone
    @TonyMhone 12 днів тому +1

    Apule Koma chidodo pochita zinthu ziwapangitsa Kuti September ziwavute motsakaikitsa. Akonda anthu akuba mu BOMA kusiya kukonda ife anthu wobvutika

  • @SydneyNyasuli
    @SydneyNyasuli 15 днів тому +3

    Leah umakwana

  • @SolomonMumba-i5n
    @SolomonMumba-i5n 14 днів тому

    Honestly speaking, their intervening has come at an extra time that is almost towards the end of the game.

  • @Dickies-mk8cd
    @Dickies-mk8cd 14 днів тому +2

    Leah you're such a talented journalists, recieve your flowers🎉

  • @victorbanda9039
    @victorbanda9039 10 днів тому

    Inuyo a pac mykupindereza mamember ena Kuti atenge mipando yanuyo kuleperera kupanga convetion cholinga muzingokhalabe inuyo nde mphanvu zodzudzula azanu mukuzitenga Kuti aneneri onyenga inu

  • @DanielChipasula
    @DanielChipasula 14 днів тому

    RATING YA MALAWI WA LERO MALINGANA NDI IZO TAKUMANA NAZO [MUZOBVUTA & ZABWINO ] 🇲🇼✍️TILI PA 82 % VIVA MALAWI.. Mmmm UKIMI NDI BUSINESS... OSANKHALA DZAKAKA/ UDZAKWAYE / ALENSI... TIYENI TIKHALE TONSE NDI CHIDWI CHITUKULA MA BANJA ATHU NDI DZIKO LATHU.. mosasudala NEEF: AIP!: ZAMANJA LENDE... AYI !! Just work extra harder in our Fields k o m n s o KUKONDA WOTILAMULURA POPEZA ENA CHITUKUKO Chao Mmmm MCHAPAKAMWA... KOMA Mgosatha pa Ground 😅🗣️ PRAYERS 🎉🖐️👉👍🇲🇼

  • @CharlieChirwa
    @CharlieChirwa 9 днів тому

    Pac yopoyira komaso yokondera

  • @smartjilamu8026
    @smartjilamu8026 12 днів тому

    Vuto mukusitama koma mafuso mukumakana kuyankha pac inatha imamufuna Peter

  • @JamesChiphazi
    @JamesChiphazi 11 днів тому

    Kumwela palibe chimanga cholandila Ife timaona ngati kwaoko ndekomwe akupeleka mwakathiti

  • @AmbiaTrust
    @AmbiaTrust 14 днів тому

    akugawa chimanga kumwela koha pakati sakugawa mchifukwaxchake aluzire kmaso kuchedwa kuthandiza

  • @GiftFrancesco
    @GiftFrancesco 14 днів тому

    Akubwela tikuyandkila Ku vota bwanj akanangokhala chete bas ndpo Boma Lina likalowa azakhaleso chete bas

  • @AbdulJohn-t7l
    @AbdulJohn-t7l 12 днів тому

    A pac atutumuka akuwona kuti zindu zitha kuwavuta ku sogolo kuno chifukwa akhala akubeleka bomali ndiye pali awasina khutu kuti achenjele chochi😅

  • @wetheinkosiyamakosi
    @wetheinkosiyamakosi 15 днів тому +1

    😂😂😂😂😂😂 cadet walila

    • @symoldicky
      @symoldicky 12 днів тому

      komatu siyense angatsekule pakamwa motsutsa or kuzuzula boma kut ndi cadet cuz at the end of all Malawi ngwatose so ndale zili apo tose tili ndi udindo kumpanga Malawi okoma

  • @Brockbaby143
    @Brockbaby143 15 днів тому

    Awa amatengeka ndi mphepo,akaona anthu akutukwana boma nawonso amapita konko,pamene boma lachitako amayamikira koma mopanda nako chilimbikitso,saona m'mene zinthu zikuye dera pa dziko lonse lapansi ndikuyelekeza kwao kuno,komano kwakulu amaona zoipa Basi.

  • @JosterLeman
    @JosterLeman 10 днів тому

    A pac ndiokondera inu

  • @BakhePaliso-h8h
    @BakhePaliso-h8h 11 днів тому

    Leah umaitha

  • @JohnLatigoNyirenda
    @JohnLatigoNyirenda 14 днів тому

    Zoona a PAC ndi okondera

  • @FisherAction
    @FisherAction 13 днів тому

    Mkulu wa pAc wabwera mochedwa

  • @KananjiMtchera-x8n
    @KananjiMtchera-x8n 14 днів тому

    Malikisio tipaleka tokha 0.7%

  • @StevenDastan-f5y
    @StevenDastan-f5y 15 днів тому

    Chimenechi ndicho chilungamo chinenedwe

  • @KondwaniDabwani-vi5cm
    @KondwaniDabwani-vi5cm 14 днів тому

    Atakhuta bwinotu kwambiri

  • @DanielChipasula
    @DanielChipasula 14 днів тому

    💺🙏A PAC AMATIYIMIRIRA TONSE AMALAWI !! A PRESIDENT DR LAZARUS M CHAKWERA VIVA AMAYIMIRIRA AMALAWI TONSE MONGA PRESIDENT WA DZIKOLI 👍🇲🇼ZOBVUTA IZO TAKUMANA NAZO MDZIKO MUNO ZATIKHUDZA TONSE KUPHATIKIZA MKUZIPANI ZONSE . MABVUTO ENA TILINAWO MDZIKO MUNO MKUSAKHULUPIRIKA KWA ENA PAKATI PATHU Maka NGATI PAKUBVEKA ZA KATANGALE, KUSADZIKHUTHULA PA KAGWIRIDSE KA NTCHITO ZATHU, ULESI , KUBA, UMANJA LENDE, UNYOZA UTSOGOLERI MCHOLINGA CHOGWERSA CHUMA CHA DZIKO LINO. PAMENE A PAC ATENGA MADANDU ATHU KUPEREKA KWA A PRESIDENT MKOYENERA IWO A PRESIDENT ATAYESETSA KUKONZA ZINA MZINA KUTI ACHITE BWINO KUTI U PRESIDENT WA U MCP UPITILIRE. MONGA BWENZI , A PAC AKUTIWUNIKIRA KUTI TICHITE BWINO MDZIKO MUNO NDIYE KUTI PALI CHIBALE ! UMODZI POPEZA ZABWINO ZOBWERA, A MALAWI TONSE TIPINDULA. ✍️🎧,NDIPO UMPHAWI WA NJARA ; MAFUTA! MAGETSI! ULIMI! MISEU ! NJANJI ! CHITETENZO CHA MA ALLUBINOH ! UMODZI PAKATI PATHU ! KUTHETSA KATANGALE / KUBA ... ZONSENZI MKOYENERA KUCHITAPO MPHAMVU KUTI ULAMULIRO WA UTSOGOLERI WA A PRESIDENT DR LAZARUS M CHAKWERA 💞 UPITILIRE KUPANGA ZAKUPYSA ZOPINDULIRA BOMA LONSE IFE TONSE . POPENZA AZATHU AMATI * WAKUTSINA KHUTU NDI MNANSI .. !! * NDIPO AZIPANI ZOTSUTSA MGOSAYENERA KUSANGALALA NDI MA > SAKOLINE! ZINKHONDO ZA KU RUSSA/ UKRAINE!! KU MOZAMBIQUE!! KU ISRAEL/ MA PALATINA! KUPHEDWA KWA MA ALLUBINOH!! KUSOWA KWA FOREX !! NDI ZINA ZOTERO !! TIYENI TIYAMIKANE PAMENE BDIKOLI LILINKUYENDA BWINO!!. NB UKAKHALA WA NKHAZA PA UCHIPANI ! MDZIKO ZIMADZIWIKA... !! TIYENERA KUMAKONDANA NDI KUMAPEPHERERA DZIKO LATHU KUTI TONSEFE MULUNGU APITILIZE AKUTIKONDERA . PRAYERS 👍🙏

  • @GeorgePhiri-ub2of
    @GeorgePhiri-ub2of 15 днів тому

    Ndizoona boma ndilomweli tikumanena mobweleza bweleza kuti boma ndilomweli basi

    • @symoldicky
      @symoldicky 12 днів тому

      yeah koma tizitelo for the better future as a country not mmene zukhalilamu , tinene zoona Malawi sakuyenda mosonyeza tsogolo labwino nde Pena ndibwino wena akamatsutsa or kuzuzula kumanvera otherwise boma ndilomwelidi koma ntsogoleri nde anthu adzasintha