He is right he doesn't mean there's no God but religion ikutipeperesa and most of are just religious and not really Godly timabeliever in myth not not real God is supernatural ... whether you like or not religion won't put you anywhere God works supernaturally not zomwe mkuganizazo malawi will never grow because we are too religious on things that are myth
Nduona ngati mamvetsedwe a yesuwo ndi omwe anthu sanamutenge bwino oolo sanamumvetse. Cz ndiye yesu yemweyo anati gwilani ntchito kuti mupezee zofunika zanu za tsiku tsiku. So we cnt blame jesus. Vuto ndiife osaiwalansotu. sikuti yese akuti yesu yesu ndee akalowe kumwamba. Ndiye kuti we cn see kuti ambiri yesuyo timangokamba pakamwapa koma ntchito sizayesuyo tilibee mapeto ake tikumutukwanitsa. Don't blame yesu cz even jesus hates ulesi makatangale ndi zina.
@@mutafire eeeh udzamuona ukadzayamba kumugwilitsa ntchito. He's there jus that pipo chose nt to recognize him. They choose to brush him off bt use his name to steal n brain wash pipo.its all devilish. His teachings wud give us all riches by working hard. Unfortunately we choose to be lazy n steal n corrupt.
@@mutafire ndiponso wen u talk Abt wat jesus has done kumalawi think also wat the devil has done kumalawi. So u cn HV balanced views. Don't be bias unless u tell us u already on devil's side.
Unaganizapo utapeperapo ndi satana! Ever thot of wat devil do to people. Yesuyo sitingamukanee koma tingolimbikira akugwila ntchito bAsi. Cz behind malawis poverty there's devil. Ulesi ndi katangalee zomwe yesu amaletsazo. Nde osaiwala kuti moyo wanuwo wakupatsani ndi yesu koma muyankhula ngati kuti munadzilenga nokha or devil created u. Nduona ngati pena pakee muonjeza tadekhani bhobho. I feel bad honestly
Ambiri wa akupanga mixing a fixing mixing devil n Jesus koma dzina limatukwanidwa ndi la jesus n I hate that. Munthu u cn work as well as pray I don't see any vuto. Bt aneneri a devil apanga brain wash pipo with miracle money zomwwe khalidwe limenelo silayesu. That's devilish. I HV seen pipo working hard as well as praying n it works. Ndee pena pakee osaiwalanso kuti devil. Trying to create paradise on earth so u cn forget jesus. Ineyo I don't believe kuti kuti jesus watipepeletsa chabe sitinamutenge bwino. If u truly follow he's teachings u.ll see kuti he's ndi power.
I court ur point by say wherever there is development there is no Jesus Christ and the same where there are poor people there is Jesus Christ so meaning that Jesus came for pour ppl coz as God says tsoka mtunda nd nyanja oipa watsikira komweko broh ukusocheletsa anthu ulakwitsa I wish this channel ikanakhala yopindulira amalawi but unfortunately anyway its okhy continue with ur buda
uyu uyu wakunena zoona koma
A Malawi tikufunika "eating bitterness" osati Jesus wa ma miracles.
Mulungu sanyozeka
He is right he doesn't mean there's no God but religion ikutipeperesa and most of are just religious and not really Godly timabeliever in myth not not real God is supernatural ... whether you like or not religion won't put you anywhere God works supernaturally not zomwe mkuganizazo malawi will never grow because we are too religious on things that are myth
Nduona ngati mamvetsedwe a yesuwo ndi omwe anthu sanamutenge bwino oolo sanamumvetse. Cz ndiye yesu yemweyo anati gwilani ntchito kuti mupezee zofunika zanu za tsiku tsiku. So we cnt blame jesus. Vuto ndiife osaiwalansotu. sikuti yese akuti yesu yesu ndee akalowe kumwamba. Ndiye kuti we cn see kuti ambiri yesuyo timangokamba pakamwapa koma ntchito sizayesuyo tilibee mapeto ake tikumutukwanitsa. Don't blame yesu cz even jesus hates ulesi makatangale ndi zina.
Fair point...koma yesu munenayo sinamuonepo Ku Malawi.
@@mutafire eeeh udzamuona ukadzayamba kumugwilitsa ntchito. He's there jus that pipo chose nt to recognize him. They choose to brush him off bt use his name to steal n brain wash pipo.its all devilish. His teachings wud give us all riches by working hard. Unfortunately we choose to be lazy n steal n corrupt.
@@mutafire ndiponso wen u talk Abt wat jesus has done kumalawi think also wat the devil has done kumalawi. So u cn HV balanced views. Don't be bias unless u tell us u already on devil's side.
@@SarahMusama-eu7wt komatu there is no devil outside Christianity and Islam...
@@mutafire so u don't believe there's devil bt u believe there's jesus who confuses malawians?
Abale
I am the one am not believe in jesus name am just a african name
Unaganizapo utapeperapo ndi satana! Ever thot of wat devil do to people. Yesuyo sitingamukanee koma tingolimbikira akugwila ntchito bAsi. Cz behind malawis poverty there's devil. Ulesi ndi katangalee zomwe yesu amaletsazo. Nde osaiwala kuti moyo wanuwo wakupatsani ndi yesu koma muyankhula ngati kuti munadzilenga nokha or devil created u. Nduona ngati pena pakee muonjeza tadekhani bhobho. I feel bad honestly
Ambiri wa akupanga mixing a fixing mixing devil n Jesus koma dzina limatukwanidwa ndi la jesus n I hate that. Munthu u cn work as well as pray I don't see any vuto. Bt aneneri a devil apanga brain wash pipo with miracle money zomwwe khalidwe limenelo silayesu. That's devilish. I HV seen pipo working hard as well as praying n it works. Ndee pena pakee osaiwalanso kuti devil. Trying to create paradise on earth so u cn forget jesus. Ineyo I don't believe kuti kuti jesus watipepeletsa chabe sitinamutenge bwino. If u truly follow he's teachings u.ll see kuti he's ndi power.
Kod akupemphanipo angat ,mukunyoza dzina layesu inu,mulungu akuyendere ukanali moyo,