- 405
- 1 186 445
Morton Baghaya
United Kingdom
Приєднався 15 лис 2007
Protests, Politics and Culture
Відео
Mbuzi Zisamavote - Demokalase Imafunika Anthu Odziwa
Переглядів 1,4 тис.4 години тому
Opanda MSCE sakuyenera Kuvota
Nthenda Ya 'Bola Mchewa Mzathu' Ndiyoopsa
Переглядів 2,2 тис.4 години тому
Chirombo Cha Tsidya Lina Chimavuta Kuchipezera Nyimbo
Ndinapita ku Tcalitchi Cha Apuse-Apuse Mulungu Afuna Ana
Переглядів 3,2 тис.12 годин тому
Ndinakadyako nyama ya njobvu yokoma ngati nkhuku
Azungu Abwerenso - Dziko Talikanika
Переглядів 7 тис.16 годин тому
Anthu akuda ufulu tikungombwambwana nawo
A Triephornia ku Equitorial Guinea Ankataniko?
Переглядів 69 тис.14 днів тому
Kodi a bwana awo anali ndani? Ndipo ndi munthu oopsa bwanji?
Do Nothing for 8 Minutes as I Descend the Shaolin Temple Mountain
Переглядів 40621 день тому
Cool Stuff
Tsogolo la America pansi pa Ulamuliro wa Trump
Переглядів 2,1 тис.21 день тому
Aononga, avuta ndipo ayamba pa day 1.
Surrogacy Itha Kubweretsa Forex Kuposa Fodya
Переглядів 1 тис.Місяць тому
Surrogacy Itha Kubweretsa Forex Kuposa Fodya
Exploring the Grand View Mall In Guangzhou China.
Переглядів 154Місяць тому
Exploring the Grand View Mall In Guangzhou China.
Bushiri Wawinanso Award Yokayikisa- Ndili ndi Mafunso
Переглядів 862Місяць тому
Bushiri Wawinanso Award Yokayikisa- Ndili ndi Mafunso
Ndalowa mu Ndirande kuti Ndione Ghetto Life
Переглядів 185Місяць тому
Ndalowa mu Ndirande kuti Ndione Ghetto Life
Ndithokeni ndikupangireni Kompyuta Yoopsa
Переглядів 2242 місяці тому
Ndithokeni ndikupangireni Kompyuta Yoopsa
kodi Shipping Zinthu Kuchoka Ku China imayenda Bwanji?
Переглядів 2532 місяці тому
kodi Shipping Zinthu Kuchoka Ku China imayenda Bwanji?
Ma Yoh Kuwatere ndekuti basi akuvotera
Переглядів 1672 місяці тому
Ma Yoh Kuwatere ndekuti basi akuvotera
Akuti osadyera mpeni ungadwale chibayo😅
@@osygmultimedia9854 hahaha za ziiiiii
Zaziii
Umakwana🎉
Koma ndie umaendaendatu
Anthu akuda kukula mbolo
Nde iweyo mkaz wako uja unapeleka zngt
@@Booxystrong free
Sono awo akumenyedwawo bwanji iiiiiiiiii
Mbuzi izizi 😂😂😂😂
😂😂🥴 Morton ndi chitsiru koma chothandiza
You mean this is for what yet it's water under the bridge. Somehow it's foolish
Kkkkkk dzitchwapi kkk
Panado waku Uk amachiza chindoko
Aaaaa ndangowononga bandle yanga
Mbuzi iwe ndinakupempha kut ukambe za system ya education ya ku china komanso usiyaninse ndi ya ku Malawi ena amati timaphunzira parts of the grasshopper or birds ndiye tafufuza zikusiyana bwanji and zikufanana bwanji?
Do you recommend that someone should work and live there?
Zaziii
Hy
Koma ku china sikophweka kubwerakotu et??
@@MorganBanda-oc2jx sikophweka...unless ndiwe businessman
Umakwana
Lawyer ndiribe ine
For example south Africa, it was admired country go and see today only high hackers thy urine any where, killings robber's shaa ,is dangerous to be in south Africa than to be in the national park, where there's lions and other dangerous animals
I a gree with u 100% brother man zoona zimenezo, ma resources Ali pweee but let's go and see development nothing. Only stupid of leadership
Ukutiimilila fada, keep up the good work. We get to know China as if we're there😅
Good explanation
PHWALA NDIWEYO GALU IWE
Choka iwe azungu achiyami
Koma Pena Morton umapulumusa anthu woti amafuna kuzimangilira😂😂😂
ndi kape Dhala ameneyo
She is a gold digger.
Anthu akujon amakhala busy kunchito alive nthawi yopanga type wanva mbuzi iwe ndi fun wakoyo
Amene ujadi ndi kapolo
Inuso ndachisilu bingu anali dolo ndipo osati zanuzo aaaaa
Mbuli now days zimaganiza bhooo kuposa wa MSCE, nkhan Nd civic education kwa anthu onse
Real talk men❤🎉
Chilungamo 😂😂😂❤
Imagine a very successful business person, big time taxpayer opanda MSCE.. kenako kape wina wake wa MSCE yapa Good Maganizo ongokanda.. nde mwati who is supposed to have a say on choice of leaders? Civics can be taught to illiterate villagers and educated elites (Phds) can still and do vote on tribal basis.. My point being it's not that simple Dada Mhango.
@zamadulasimango6972 no need to spend more time and civics is not about money...nor is democracy about money. To pass MSCE you know enough about the world...biology, agriculture, politi, history, history, English and so on
zoonadi
😅😅kumangowaza ma leftover wo
Wapala fundo iyiyi
Aise umanena chilungamo upitilize kutiziwisa zambili timakunyadilani kwambili amwene mot
Ndiwe Dolo!
Komaso minster azikhala waku university osati akangqnyawa
Ukawone amene ali muma udindo akuluakulu ndi mbuliso achina manganya
You are not serious are you?
ASE manganya Ali ndi doctorate musiye amene uja sungamake ASE ndiophuxla amene uja
@siwedmataya7429 maphunziro ake siokwanila poyendesa boma ali ngati lazalo
@siwedmataya7429 manganya ndi namwino azikagwira kobelekesa
Exactly Morton malawi.ambiri ndi mbuli
😂😂😂 Amalawi ndi mbuzi man a president akeso mbolo. yinatota kale pano akungobaya nyini
😂😂😂😂😂😂
Mbuzi iwe, ndinakupempha kut ukambe za system ya education ya ku china komanso yaku Malawi pajatu amati timaphunzira parts of grasshopper or birds ya ku china ndiyotan
Uli ndi ndalama zingati iwe sasamba ngati iwe
Can you make a video on why exactly the Malawian population is so uneducated?
Mfundo Ili bhoo