ambuye akudalitseni nonse pa choir yanu ndipo apitilize kukuunikilani nyimbo zambwino za tanthauzo . since ndaona nyimboy ndangoi ika pa repeat yandikumbusa zambiri . grace of God upon you guys ikatha ntchito mziko lino muzandikumbukile mu ufumu wanu
Ana inu mayimbidwe awa ndioliritsa zedi maka kwa Ife osamvera mau a Chauta Eee Khristu.
Rest in peace my father and grandfather 😭😭
Pitirizani kuimbai kokomaku. Mulungu akudalisen.
Kuyimba kwabwino kothandizila anthu kt adziwe zaufumu wamlungu .umbuye akuonjezeren mzeru munkuyimba
I like it 👍
Ndipo nyimbo ndikumvela daily cos muli uthenga wamphamvu mulungu akudaliseni choir yanu
I love this song imanikumbusa patali mupilize maimbidwe abwino amen 🙏🙏🙏🙏
I like this one 😂
ambuye akudalitseni nonse pa choir yanu ndipo apitilize kukuunikilani nyimbo zambwino za tanthauzo . since ndaona nyimboy ndangoi ika pa repeat yandikumbusa zambiri . grace of God upon you guys ikatha ntchito mziko lino muzandikumbukile mu ufumu wanu
Touching song🎉 keep it up guys
I love this song keep it up guys
ilove ❤
Amen ❤
Nice song Good burs you
Amen
What awonderful song great
amen
Nice track
God bless us
What a nice song keep it up guys
Nice song n powerful message
Yandidalitsa Ambuye akudaliseni
Too emotional
❤❤my favorite song
I have been looking for your songs and finally I got it❤❤❤❤❤❤❤
Nyimbo niyabwino 🙏🙏
My best of this year mulungu mutikumbukile
Nyimbo yotsitsimutsa
Zili bwino ndithu
Nice song
❤❤❤ This song
This choir mmmm, beautiful music ..... Where can we buy their DVD
Great
Glory be to God
🙏✋
MULUNGU ADALITSE CHOIR YANU.NYIMBO ZONGWILA MITIMA YA ANTHU AMBILI .MULUNGU AKUDALITSENI.
Zikomo kwambiri
@@brianphiri1397 chiovol
nyimbo yabwino
❤ my lovely 🌹 song lyrics God bless you
Amen
Amen
Amen