BAKILI MULUZI TV 2 JULY 2024

Поділитися
Вставка

КОМЕНТАРІ • 336

  • @IbrahndemangaIbrahndemanga
    @IbrahndemangaIbrahndemanga 3 дні тому +2

    Best of the best bakili muluzi tv

  • @muhmmadsarwer9527
    @muhmmadsarwer9527 2 дні тому +3

    Anthu Andale ndiabodza koma awawa eeeeeee awonjeza kwambiri

  • @FrancisKazembe-og4vh
    @FrancisKazembe-og4vh 2 дні тому +1

    Watching from Zimbabwe

  • @oneriaChiwaula
    @oneriaChiwaula День тому

    I like this TV keep the fire burning dude

  • @harrisbanda5891
    @harrisbanda5891 2 дні тому +2

    Akutivutisadi ng'azi ameneyu 🐬🐊🐊🐊🐬

  • @VinsentMwapabwe
    @VinsentMwapabwe 2 дні тому +1

    Yes mwamuza zona ZIKOMO kwambili potiziwisa chikhalidwe chake

  • @user-xr3ty6qq5o
    @user-xr3ty6qq5o 2 дні тому +3

    Ine n'saname Chakwera amandinyasa

  • @user-ww9rj2wx8d
    @user-ww9rj2wx8d 3 дні тому +3

    Chakwela ndi mfiti kwabasi

  • @SymonNamalomba-sh3fu
    @SymonNamalomba-sh3fu 2 дні тому +1

    Olo chimodzi palibe chomwe wapanga iye, 30minutes olo itakhara non stop sizingatheke ayi ,

  • @JeanKambala-gm1zr
    @JeanKambala-gm1zr 3 дні тому +2

    Akwanilitsa bwanji kupanga zonsezo ndalama akupatsa anthu akunja kumalemba anthu aganyu Kuti azimpha anthu ndalama zake zomphela anthu

  • @Concerned320
    @Concerned320 3 дні тому

    Best TV ever..may God continue protecting you Bakili Muluzi TV

  • @user-ep6ro8uk6e
    @user-ep6ro8uk6e 2 дні тому +2

    😅😅😅😅koma anthu.inu musandisekese akut akaziwo mimba nguuu ngat mbuzi yakhuta mphale yokuba

  • @user-ec4jo9cu4d
    @user-ec4jo9cu4d 2 дні тому +2

    😂😂😂😂😂ati kagowero kkk km naseka bwanji

  • @user-uc1pd1tc2x
    @user-uc1pd1tc2x 3 дні тому +2

    Boss mwaiwalatu chitukuko China chomwe MCP yapanga kupha Ralph ndi Chilima

  • @BishopMaxwell
    @BishopMaxwell 2 дні тому +2

    Afune asafune 2025 azaluza akumkuyu akumpusitsa kape wawoyo

    • @user-hm9nc7lz6e
      @user-hm9nc7lz6e 2 дні тому

      Onse ndi amagazi mmanja kumkuyu sakudziwa comwe akuyakhula

  • @raytavares2256
    @raytavares2256 2 дні тому +1

    Ifee nga ngaa nga nga pambuyo pa ngwazi yamuyaya Dr LAZURUS CHAKWERA wathu wokendedwa 🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉❤❤❤❤❤

    • @ChristopherMakamo-ky4pq
      @ChristopherMakamo-ky4pq 2 дні тому

      Galu wachabechabe iwe

    • @harrisbanda5891
      @harrisbanda5891 2 дні тому

      Chokani apaa mwana wang'ona iwee, mwapha chilima asatana inuu 👹👺👿☻ , kunali ng'azi ina mdzaka zammbuyozo mumkaitchulanso kuti ngwazi, , lero alikuti?

  • @ZenusKabwili
    @ZenusKabwili 3 дні тому +3

    Aaaaa koma kunena zowona kutengela mmene analonjezela zambiri szinatheke 😢

  • @DelamoBalacho
    @DelamoBalacho 3 дні тому +2

    Best tv bakili muluzi

  • @georgechikonje4904
    @georgechikonje4904 3 дні тому +1

    Best TV station in Malawi so far.

  • @vinceynyone6693
    @vinceynyone6693 2 дні тому +2

    Ndaonadi nkhope yamfitidi

  • @user-dh1oi8mb4v
    @user-dh1oi8mb4v День тому

    Akunamizana akuti awina ndipo sawina anthu ameneyo ndipo azafa ndi mtima ndithuu my vote for Dpp hoyee

  • @user-fd1tu6ku1r
    @user-fd1tu6ku1r 2 дні тому +1

    Mr Kamwendonjira okudya Matako agaluwa sangawine Chisankho in the Next Polls

  • @user-zr5oc3rg2c
    @user-zr5oc3rg2c 2 дні тому +1

    Kkkkkkkkkkkk koma brother mumatha Inu mudzangokhala president ndinuyo chaka chikubwerachi

  • @JafaliAkimu-ll1bf
    @JafaliAkimu-ll1bf 3 дні тому +2

    kumkuyu ma chende abambo ake chakwera ndi mcp ndizigawenga za kupha anamupha chilima mcp ndi chipani chazigawenga zitsiru zokha zokha

    • @WittinessBeza-cp5kf
      @WittinessBeza-cp5kf 3 дні тому

      Chakwela mumuone khope yakeyo chigawenga cheni cheni akakhaka mkaka ngati wagwa kotamba

  • @user-mi3fw1zg8b
    @user-mi3fw1zg8b 2 дні тому +1

    Ali Maso rwaa! Ngati Nazikambe kkkkkkk koma Manganya😂😂😂

  • @JjhdshkKfdsahk
    @JjhdshkKfdsahk 2 дні тому

    I trust bakili muluzi TV always because is talking true

  • @user-pi8mz3bx9n
    @user-pi8mz3bx9n 2 дні тому

    We really appreciate for this channel

  • @user-qx3dd7xt9c
    @user-qx3dd7xt9c 2 дні тому +1

    😂😂😂 bon voyage kkk da gama emweyo wa gowelo

  • @Aisha-db6ds
    @Aisha-db6ds 3 дні тому +2

    Kunkuyu mapwala ake ndithu

  • @user-qq1uj7ct6n
    @user-qq1uj7ct6n 3 дні тому +1

    Kunkuyu umve zimene ndikunenazi,, iweyo ndi amene akumuuza zabodza chakwera wakoyo. Achakwera mumve Mau angawa,, kunkuyu akukunamizan ndi mfundo zake zopeperazi. Chifukwa iyeyu akukulimbikisan kukuuzan zabodza zomwe amalawi Eni ake sakukondwera. Muzafa ifa yowawa.

  • @user-nf3ik3ff6y
    @user-nf3ik3ff6y День тому

    Bakili TV number one ❤

  • @stainmujiwa3617
    @stainmujiwa3617 2 дні тому +1

    Kkkk ati kamuyenda njila anadya matako agalu.nde ndi nkazake ngt otupa mutu uja😂

  • @Kelvin-hj5qv
    @Kelvin-hj5qv 2 дні тому +1

    Kkkk 😂😂 khaniyo ndiyowona amange gowelo bs zachamba bs

  • @user-hq6dq7zr1e
    @user-hq6dq7zr1e 14 годин тому +1

    Zomwe wakwanitsa ndi kupha ndikumanga osalakwa

  • @Moses51
    @Moses51 3 дні тому +1

    Best TV in Malawi keep

  • @harrisbanda5891
    @harrisbanda5891 2 дні тому +1

    Koma ada awa amatha kwambiri, kuwelenga mwachifase ndimodekha

  • @sharlifcassim6591
    @sharlifcassim6591 День тому

    Tamulimbikiseni nkhani yomanga gowelo Ku airport komwekoyo😂😂😂

  • @BlessingMbule-m4d
    @BlessingMbule-m4d 17 годин тому

    Iwe ndi one❤

  • @AubreySymon
    @AubreySymon 2 дні тому +1

    Ndiana sakuziwa kathu auze mwina aiwala. 😅😅😅

  • @ORTONPHIRI-i1z
    @ORTONPHIRI-i1z 2 дні тому +1

    Chakwera chomwe wa kwanitsa ndi Mabokosi AMALIRO osati chitukuko Chitsiru cha munthu .

  • @DanMwatchipitsa
    @DanMwatchipitsa 2 дні тому +2

    Chitumbili chingwile pangali mbwaa in 2025😂

  • @user-xe1so5xj2w
    @user-xe1so5xj2w 2 дні тому +1

    Chakwera tatopa nayo bolani afe basi anthufe tatopa naye kwambiri

  • @ChriKezi
    @ChriKezi 2 дні тому +1

    Mcp izalila maliro onyamula wina azathawa malawi akufuna

  • @harrisbanda5891
    @harrisbanda5891 2 дні тому +2

    Chilichonse chamoyo chikàmaphedwa sichilephela kuphupha chikamafa , umu ndimomwe chikuphuphila chipani cha magazi cha mcp killing party

  • @user-cj2bo4lf7c
    @user-cj2bo4lf7c 3 дні тому +1

    Chakwera waononga dziko la Malawi .angongwetsa kwacha mosanganizira anthu osauka

  • @user-vb1iq5un5p
    @user-vb1iq5un5p 2 дні тому +1

    Koma pa udindo wa upulezidenti uja umafunika kukhala okhwima nzeru.😂😂😂akt amakajambulitsa zithunzi ku china akazawo Ali pompo ..

  • @GreenMwachande
    @GreenMwachande 2 дні тому +1

    Kkkkk akuti umange gowero Garu iwe

  • @rashidlamos3403
    @rashidlamos3403 3 дні тому

    Thanks brother for news

  • @thomasbodo4099
    @thomasbodo4099 2 дні тому +1

    President uyu ndi pa nja penipeni munthu osadziwa chimene akuchita ndi munthu wanji

    • @AbdulmajeedJbanda-oz3jv
      @AbdulmajeedJbanda-oz3jv 2 дні тому

      Sindikudziwanso Kuti ndiophunziladi uyuuu
      Kunachita kuyiwala zomwe alankhula dzulo zimayenda Koma mkalasi munthu ameneyu

  • @kubengovender6996
    @kubengovender6996 2 дні тому

    Keep it up brother man!!

  • @allamalbertbeza2679
    @allamalbertbeza2679 19 годин тому

    They ,MCP are playing too much with lives of Malawians ,but God is watching

  • @omarjustin5518
    @omarjustin5518 3 дні тому +2

    Chakwera Kodi sigaru ameneyu

  • @PhillipMtonga-g7o
    @PhillipMtonga-g7o День тому +1

    Yakwia ndi mizimu

  • @user-xe5lb4uf3n
    @user-xe5lb4uf3n День тому +1

    Zoonadi amange Gowero ku Airport komweko.

  • @user-dx4zu1wv4q
    @user-dx4zu1wv4q 2 дні тому

    ❤❤❤timakunyadila man kwambiri tione ku lsrael ndi ku Russia zikuti bwanji kumeneku

  • @CatherineDesire
    @CatherineDesire 2 дні тому +1

    Komanso Mzuzu airport Ngati airport ya witchcraft kkkkkk

  • @JuliusAndrea-iq6xc
    @JuliusAndrea-iq6xc 15 годин тому

    Kkkkk chitukuko chake ndi kuba 😅😂😂

  • @nationsmpweti8088
    @nationsmpweti8088 2 дні тому

    Abwana bwanji mzakhale president zikuwoneka kut muli ndi nzeru zoti mngasinthire znthu

  • @LysonMtalika-tb6fk
    @LysonMtalika-tb6fk 2 дні тому

    Powerful long live bakili muluzi TV

  • @shafiemalobvu
    @shafiemalobvu 2 дні тому +1

    tafufuzani za ku Burkina Faso kuli president wazeru kwambili mutibweletse mbili yake bg man

  • @user-es4jt6ds8m
    @user-es4jt6ds8m 2 дні тому +1

    Chakwera zimene wakwanitsa kupha chilima basi palibepo chimene akupanga komaso nanga asikali Aja Amati azapanga ma video ya momwe chilima alikuti anthu Aja chonde asawaphesotu

  • @CatherineDesire
    @CatherineDesire 2 дні тому +1

    Akadzi Ake kamimba ngu Ngati mbudzi yakhuta mphare yakuba 🤣🤣🤣

  • @user-is5dl7np9g
    @user-is5dl7np9g 3 дні тому

    Zoonad MCP singawineyi, thanks bro for informing us

  • @TimothyNkhutembaChirwa
    @TimothyNkhutembaChirwa 2 дні тому +1

    Kumukuyu alibe ku immigration anthu akuvutika kwambiri komaso kuba passport amati yikhala k50,000,pano ndi k500,000

  • @MichealDPhiri
    @MichealDPhiri День тому +2

    😅😅😅 at bola Vasco da gama 😅😅

  • @user-nm1jj5qv8i
    @user-nm1jj5qv8i 3 дні тому

    Welcome bwana for today again
    Amen ❤

  • @RhodneyBwa3
    @RhodneyBwa3 3 дні тому +1

    Kunkuyu ndi mfiti otheratu

  • @user-mw8dq4is6k
    @user-mw8dq4is6k 2 дні тому +2

    😂😂.😂 Chilichonse chakwera ndichakwera adatelo APM

    • @fxmw
      @fxmw 2 дні тому +1

      😅

  • @MosesPhiri-l6e
    @MosesPhiri-l6e 2 дні тому +1

    Let me correct you in Mzimba sugar ndi k 2495 in big mart shop ya fair price
    Chakwera dziko lamukanik passport anasiy kupang ndet only in lilongwe zoona zak achinyamat ntcht njee
    Achoke I will support that

  • @ishmaelmkuluma2013
    @ishmaelmkuluma2013 2 дні тому +1

    Iwe aise video iyi ndiyakale wamva galuso iwe eti uzingoponya ma videos akale kale

  • @ElonBlack1999
    @ElonBlack1999 2 дні тому

    Iwe osamaba za bakili muluzi tv

  • @JamesChiphwanya-tb3tq
    @JamesChiphwanya-tb3tq 2 дні тому

    Abwana president chakwela Ali ngati chidole kapena kuti katuni ena amagomungwila ntchito zaumunthu uyu mulibemo ndipo ndi khutukumve chakwela wa mwazi uyu

  • @user-wd9yd1bg9n
    @user-wd9yd1bg9n 16 годин тому

    Ķķkkk chitukuko chake ndi kuba😅😅

  • @thomluckson4557
    @thomluckson4557 2 дні тому +1

    In fact chakwera nd mbuzi

  • @PatrickTchuma
    @PatrickTchuma 3 дні тому +1

    Dziko la Malawi silidzasithaso ngt atsogoleli anthu sadzasintha

  • @msatisi.reangfordphiri
    @msatisi.reangfordphiri 2 дні тому

    Kkk koma ndaseka yandibaya yomanga kagowero ku ku airport

  • @rashidadan2533
    @rashidadan2533 3 дні тому +2

    Kumkuyu ndi Mr nonsense

  • @user-sk1wj9bw6l
    @user-sk1wj9bw6l День тому +1

    Ndipo Mcp sizalowaso mu boma

  • @abe9104
    @abe9104 2 дні тому

    l,m watching from .am angry with Britain .mcp never win

  • @BrightPhiri-bt6ev
    @BrightPhiri-bt6ev 3 дні тому

    Ine ndikanakhala peter ndikanangozitaya kuti apume kutukwanidwa.mwina iweyo nkuzakhala minister galu iwe.

  • @LastenWesele-wq8jh
    @LastenWesele-wq8jh 3 дні тому +1

    Video iyi ndiyakale tinayiwonela kale

  • @Pangolinimw
    @Pangolinimw 2 дні тому +1

    Bakili mulizi❤❤❤❤

  • @VeronicaYohane
    @VeronicaYohane 3 дні тому

    Amangilen pofikiladi abusawo nkhosa zikudandaula busa amanthawa😄😃😄😃😄😃

  • @JacksonMoyo-tm8dv
    @JacksonMoyo-tm8dv 2 дні тому

    Inu ndinu heroe bwana ,MCP isazabwelere muboma kufikila titafa chifukwa muwaru,gadama,solobala ,chilima,chisiza anaphedwa ndi MCP komanso amatenje

  • @BrightPhiri-bt6ev
    @BrightPhiri-bt6ev 3 дні тому +2

    Iwe galu iwe watikwana sopano wamva tadikila next year kuti peter mthalika wakoyo azatenge boma ngati angazalongosole zithu.mesa peter yo akuzimvela ma propaganda anuwo.

    • @goodsonmw
      @goodsonmw 3 дні тому

      Kodi anthu ngati inu Mmakonda kulowa mma page ndikumapanga ma comment opusa fukwa chani? Za usilu basi ngati mwabwerela pano ma comment awusilu Manyi anuso

    • @user-cn3gi2vf5n
      @user-cn3gi2vf5n 3 дні тому +2

      Onse akumapanga ma comment opusa si dzika za ku Malawi palibe munthu amene angakondwe ndi dziko la Malawi mmene likuyendela pano tiyenela tikonze dziko osati kumangopanga ma comment opusa ayi zautsilu basi

    • @BrightPhiri-bt6ev
      @BrightPhiri-bt6ev 3 дні тому

      Choka galu iwe chikukupangisa iweyo kukhala dzika kwambili ndichan? Kunziva u malawi kwambili? I will counter attack thy way i want iam also a malawian citizen stupid cadet.achipeleke chizikocho kwa mlomwe nzanuyo ngati iyeyo azakupaseni zinthu zaulele fotsek

  • @TerryNac
    @TerryNac 3 дні тому

    Good good continue

  • @user-tu8yx2on1r
    @user-tu8yx2on1r 3 дні тому

    Following 😊

  • @user-nl4so8ox3t
    @user-nl4so8ox3t День тому

    Nice one

  • @AngellachifundoMwale
    @AngellachifundoMwale 2 дні тому

    He has forgotten about the boolet train your just reminding him now poor Malawi that used to be a milky and honey country shame on us 😂😂😂😂

  • @user-kr8bn1bb8c
    @user-kr8bn1bb8c День тому

    99 percent ya anthu ma comments section atopa ndi amcp adzawina bwanji mavote

  • @RasheedMaster-md2vz
    @RasheedMaster-md2vz 3 дні тому +1

    Apanga post not bakili muluzi page yake ai nokha simukuona inuyo

  • @kondwanlackson8319
    @kondwanlackson8319 День тому

    Kkkkkkkk koma amangedi ka gowero ku airport azigonela komweko

  • @GoodwellRaphael
    @GoodwellRaphael 3 дні тому +1

    Akapume atisautsa mokwana agalu amenewa

  • @user-hk1kj9bk7b
    @user-hk1kj9bk7b 2 дні тому

    Kkkkk khani ndiyomanga gowero ,

  • @danielmuriya8675
    @danielmuriya8675 3 дні тому +1

    Mosses ndi mmodzi mwa afiti mmalawi muno.

  • @user-zr7wk4oq2x
    @user-zr7wk4oq2x День тому +1

    Bwana kumanena kuti mwamaliza 🙄😫

  • @jameschibisa1433
    @jameschibisa1433 3 дні тому +1

    Ichichi Cha bakilichi ndi amdala mitunda isanu

  • @amoschataika7440
    @amoschataika7440 3 дні тому

    Kkkkk Anyamata tilipo ife timanga ka Gowero Bro 😂😂😂😂

  • @MercykanchureJohnson
    @MercykanchureJohnson 2 дні тому

    Tikhara kuti tikungotukwana bas pa social media sizitithandiza
    Ife tingopanga zoti Mulungu atione ndikutivera chisoni basi
    Tizizivera chisoni kuti Mulungu atikhululukire

  • @user-re7fo3be2z
    @user-re7fo3be2z 2 дні тому

    Palibe chimene akuchitawa awa