Vuto ndi kagulu kochepa ka anthu kakumupusitsa president Sakumuuza zoona zenizeni, Lero ndi izizi wazionera yekha, Ma advisor anu sakukuthandizani Mr President, achotseni
Video pena ioneke ngati inajambilidwa 1973😂😂😂😂😂....anthu saakusamba....kaya ndi vuto la sopo kaya angodzipatsa busy ndi nyau...mmmm ai koma anyamata dzisamalireni tili mu 2024😂😂😂😂😂😂😂
Kkkkkkkk chakwela akuziwonela komatu kunoko ndikwawo
Zimene zikusonyeza kuti anthu chilungamo akuchiziwa ... Koma akumangofuna ndalama chabeeeee
Zabodza izi good editing mwaphuzila
😂😂😂😂😂tanenani ndege inagwa bwanji...zandisangalatsa bwanjiiiiii😂😂😂😂😂😂
pamenepa ndipomwe adziwe Kuti amalawi siwogona
Mwazionera nokha anyawu inu chakwera sakuziwa chilichonse uyu muthu oyipa kwambili ngati idya amin wasakho
Same on you chikangawa ❤❤ u don't have peace chakwera
Heeeeee izoooo pilato anati iwe sukuyankha anthu atundu wako omwe ndi omwe azakupereka Kwa ine? Kumufusa Ambuye Yesu muziwa nonkha zimene ndikuthauza 🙌🙌🙌🙌
Kkkkk 😂😂😂😂😂koma ndaseka zilombo mademo? 😂😂😂😂
Ndege inagwa bwanji ku Chikangawa😂😂😂 ndiye mwati ku Dowa uku ayi zikomo
chilima sanarimuthu wamasewera nkhulupilan
Kkkkkk 😂😂😂😂😂😂 chikangawa chakwela wazionela Mmmm
A president ndi pomwe akuyenera kudziwa kuti pemphero limathera ndi Amen
President ameneyu anthu sakumufuna ngakhale pang'ono, akungokakamiza.
Chakwera sadziwa chirima chose ananena ekha nimburi chikangawa kuyankhura sadziwa timuonera poti 2019 amamuyankhurira nichirima pano Uzi uzanyau zakozo
😂😂😂😂😂😂😂😂😂 Koma Chikangawa mtendere sadzaupeza
Kukhala ngat akupita kumalirotu kkkkk😂😂😂
😂😂😂😂😂 chikangawa oyeeeeeeee
Utsogoleri uwuwu ulibe madalitso
Akile kumeme tikufa ndi njala,osanyengerera boma lilipoli.Anthu akunva kuwawa..
😅😅😅😅😅 km galu ameneyu azionadi 😅😅😅
Kkkkkkk kuyalukatu arsenal pakwawo kukuwidwa
Shalom Malawi shalom kkkkkk anene ameneyo
Kkkkkkk kwawo kwemwe 😂😂😂
😂anthu amafika potopa
Mwana waukila Bambo wake kkkk ndale zakuno kwinthu Ku Malawi za u chisilu ,razarus ngwabozatu kkkk
yomweyo chikangawa tiyeni nazo agwa nayo 😂😂😂
Speechless 🙊 😶 🙊 😶 Chomwe mukuwazuzirra anthu ndi chiyani huuuuuuuuuuuuuuuuuuuuuuuuuu.
😂😂😂😂 Chikangawa ndege inagwa bwanji 😂😂😂😂😂
Iii kma kumalawi athu sachedwa kuukilana😂😂😂
Tipemphe anzathu akwa Nsundwe atiyankhule😅😅😅😅😅😅😅😅
Asakupusitseni uyu nyimboyi wangoiyikapo, adayimba ndi ma kadet m'mbuyomu pa msonkhano wa DPP.
P
President wathu ndiye Eeeeeee zachititsa manyazi zedi
Yomweyo chikangidoo!! Airport
Zamanyazi ochakwera
Chikangawa wazimvera yekha
Anthu Oli mnjala😂😂😂
Boma la bodza ndi kupha basi
😂😂😂😂😂 koma kuchedwa kufaku tiona zinthu
Choipa chisata mwinii
Muthu waMulungu ndinyau paliubale wanjinso ???
Komaso zinthu zake ine ndilibe mawu
Kkkkkk a nthu atopa
Malawi yakana zopusa❤this is down of barbulo
Vuto ndi kagulu kochepa ka anthu kakumupusitsa president
Sakumuuza zoona zenizeni,
Lero ndi izizi wazionera yekha,
Ma advisor anu sakukuthandizani Mr President, achotseni
Nyau zinakwiya eeee 😂😂😂😂 koma ndalama abale
😂😂😂😂 kwawo konko, uziona 2025
wawa chikangawa😂😂😅
Umfumu wakuba ndichomcho umaona ngat themberero
Nyau
Mpaka
Zafika
Spa,,,,,ndipase I
Madzi
Ndikomoke
🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣koma Malawi 🙌
😂😂😂😂 dambwe pa home
Nkhani yabodza😂😂
😂😂😂😂😂🎉 koma anthu akhuza kunena kuti anthu akumalawi sasamba ndi video iyi
Mzimu wa chilima uwu ukulowa mitima yawanthu, komaso zilombo
😂😂😂😂 this is hilarious
Khaaa
Wadzivela yekha kut ndi Chikangawa osat Chakwera , shem on him kkkkkkk
SIUNATI CHAKWERA .UZIONA ZA NYOO..!! INAGWA BWANJI KUCHIKANGAWA NDEGE !! CHAKWERA .ACHEWA AMTUNDU WAKO UMENE AKUDABWA NAWE KUTI IWE NDIOIPA MTIMA NDIPO NDIWE WAKUPHA UNAMUPHA CHILIMA
😂😂😂😂😂😂😂koma zolilisa mwava😢😢😢😢😢😢 paka apa
Zachisoni
Zamanyazi kkkkkkkk tangotulani pansi udindowo inu
zadalaaaaa🤸🤸
Gureyo anamuwuza ndani kuti ndege inagwa mizimuyo😅😅😅😅😅😅😅😅😅
😂😂
Nayesotu amavala suit nkukavota
Mukunama dowa ndi ya MCP mukhawula
Very shame aaaa
Kodi kumaliru😂😂😂😂
Mmmmm nyimboyo nanu mwachita kuyikapo
Ntundu wawo wa Mr President watopa😂😂😂
😂😂😂😂😂😂warapa
Shame!! Chakwera just resign please
😂😂😂😂😂😂😂 yomwe namachende iwe
GOOD NOT ALL CHEWAS ARE WIVKED LIKE CHAKWERA AND HIS MCP..AMEN @ INAGWA BWANJI CHIKANGAWA NDEGE !! UTIUZE IFE NYAU LERO !
😂😂😂 kom ndaseka
Kkkkkk koma nyau zapanga mademo
Kkkk pitani ku nkhata bay mkaone atonga gule wawo kuti amavala bwanji mwinaso a chakwera anavalanso nyauyo for few minutes kkk
Video pena ioneke ngati inajambilidwa 1973😂😂😂😂😂....anthu saakusamba....kaya ndi vuto la sopo kaya angodzipatsa busy ndi nyau...mmmm ai koma anyamata dzisamalireni tili mu 2024😂😂😂😂😂😂😂
Kkkkkkk
😂😂😂😂 koma chonchi nkumati tizawina Richard mbuzi yamuthu
Kkkkk koma ma guys simukuchezana bwino kkkk
Penaso kumakhalako serious kungova kuti 5000 bas nyau mpaka kuposera anthu? be serious guys tiyen tiphuzile kulingalila bwino🤦
Ndale sitipanga pa social media mongokumbutsana,
ndegeyo koma ,nyau zikufuna kuziwa
I don't believe 🥺🥺🥺🤣🤣🤣🤣
😂😂😂😂😂😂😂 so shameless chikangawa
Kkk ayankhe funso chakwela
No comment
Anzathu mafuta alinawo
Osalola Smartmàtic
Boma loyendesedwa ndi zitsilu ndi choncho
Nyimboyo nde ikukomatu kkkkk,inagwa bwanji
Nyauzo basi kusowa zochita moti akalime koma achewa kuvetsa chisoni😂😂😂😂
Kkkkkkkk koma achewa ndi anthu onvetsa chisoni kwambiri mbuli za anthu
Kkkk kom abare kkkmmmm phakhana photero
Cadet on duty, paja ndi Bakili Muluzi TV bodza
Azikalima asamadalire zolandila kkkkkk😂😂😂😂
Ndipamene angadziweno zoti anthu pa msonkhano wake amangobwera kuzaona ma gamlimoto koma vote akudziwa kopita nayo Amalawi
Nyau dzomwedzo Kuti WA WA WA 🤣🤣🤣🤸🤸
Kkkkkkk wabodza uyooo uli ku dzuwaa tikudziwa a
Kupitiliza kudzionongela mbiri mmm zamanyazi
Galu aluma mbuyache
Shame on him😢😢😢
Chakwera manyazi bwanji
Kkkkk anthu afika potopa
Mukulondola anthu olakwika