Kma maguys awa amanditsangalatsa the only three guys in Times radio timawanyadira kwabac ndipo sanyengelera amanena chowona kwabac krep it up the good work ,you are the followrs of Bakili Muluzi TV ,both of you guys keep malaelwi Shine without you guys no morre true things could be
Brian banda usamakhale ndi mkwiyo nthawii zose ai chifukwa choti adakuchotsa kubomaku ai azakowo akukuuza chilungamo osati kumangotsekula kamwa Yako kumangolubwalubwa chosecho sukudziwa kalikose ai monga momwe akunenera wonder yo wava osati nthawii zose zinthu za against ai
KODI ANTHU INU DO YOU KNOW THE MEANING OF MANGANYA? TANTHAUZOTU LA MANGANYA NDI MUNTHU YEMWE ALI OZETSA CHISOKONEZO PAMALO THATS WHAT THAT "MANGANYA" NAME MEANS INCASE SIMUKUZIWA. YOU CAN SEE ZOMWE AMAPANGA MU TIKUFERANJI DRAMA ZIJA NOW ZINAMULOWA WABWERA NAZO IN REAL LIFE KUMBALI YA NDALE. You can see kamakhala kamunthu koti aliyense amangokadandaula kamba ka zochita zake in the drama. Lero nduyu akuyiwala kuti khalidwe lopusa akupangali si mu tikuferanji ..
Osama tizana ayi iyo ndi public broad cast ndiye munkakhala pa tv mudzikhala sirious idea timakhala tikudikila zokupsa, koma zinazo muchepetse tisamamve zamsima pamenepo ayi
Futso nali, Kodi ku mgwilidzano wa zipani ziwilizi oyenela kunena Kuti tatuluka mmgwilidzano ayenela kunena ndindani pakati pa chipani cha UTM Ndi vice president?
Brian is a Brilliant journalist
Ineyo ndine Wa UTM we are having hope on Dalitso Kabambe please Kabambe live as Dalitso basi kkkk
Pakanakhalaso Bayana chunga. But this was fantastic ❤
Kabambe amgoyemela❤🎉
I understand dziko lino silikuyenda bwino njala m'midz umu zosayamba koma with you three guys mumativesa kukoma
UTM forever more
be your own man,tell us who you are,if you are trying to be Chilima you will fail miserably,,end of quote#Ndebvu za mwai 😅
Brian Banda wayamba kujiyanso ya Kabambe. This guy is UTM big time
I watching from zambia
Watching from South in love with Kabambe
Am watching from lusaka Zambia
Good update keep it up
More fire ❤ vuto kwanguma
Usi azipita ku chipani chake asasokoneze ku UTM
😂😂Guy's inuo mumandiangitsa tsiku langa kukhala lokoma pama program onse Kwagwanji, Hot Current ndipo sindimalora kudutsa osavela onsewa
Azibambo inu simunyengelela
Kma maguys awa amanditsangalatsa the only three guys in Times radio timawanyadira kwabac ndipo sanyengelera amanena chowona kwabac krep it up the good work ,you are the followrs of Bakili Muluzi TV ,both of you guys keep malaelwi Shine without you guys no morre true things could be
Very
Brian always amakhala mbali yotsutsa chifukwa akumamva ululu omwe anamuchotsa ku State House
Owoo ah ah
Ndipotu zoona zake, anthu asankhila fundo zomwe awona mwa Kabambe
Mungobakira zazii
Timawonela ttv flom mozambiki
I love you guys
Mng'aluri can u say that again akakokha kamaBeBetsa🎉😅😅😅😅
Ameneyo ndi Mchuni- Brian Banda
Brian banda usamakhale ndi mkwiyo nthawii zose ai chifukwa choti adakuchotsa kubomaku ai azakowo akukuuza chilungamo osati kumangotsekula kamwa Yako kumangolubwalubwa chosecho sukudziwa kalikose ai monga momwe akunenera wonder yo wava osati nthawii zose zinthu za against ai
Wonder Msiska 😂🤣😂😂😂 anthu Mmang'alura😂🤣
Ulemu Kwa delegate
Brian ur the best
😂😂😂
Delegate, ndilibe naawe mawu
KODI ANTHU INU DO YOU KNOW THE MEANING OF MANGANYA? TANTHAUZOTU LA MANGANYA NDI MUNTHU YEMWE ALI OZETSA CHISOKONEZO PAMALO THATS WHAT THAT "MANGANYA" NAME MEANS INCASE SIMUKUZIWA.
YOU CAN SEE ZOMWE AMAPANGA MU TIKUFERANJI DRAMA ZIJA NOW ZINAMULOWA WABWERA NAZO IN REAL LIFE KUMBALI YA NDALE.
You can see kamakhala kamunthu koti aliyense amangokadandaula kamba ka zochita zake in the drama. Lero nduyu akuyiwala kuti khalidwe lopusa akupangali si mu tikuferanji ..
Machezawo kunyumba kwanu please.
Panalowa statistics
Yes, Brian ukhala Ng'aluri, osadabwa za amapha Ng'ombe. 😂
ine ndimakondwa nanu kwambiri komanso simubisa
Watching from, Lilongwe University of agriculture and natural resources Bunda campus, the big Three guys inuo mumatha
Kod program yi imakhalapo nthawi yanji pa times
AKALIATI MWAONA APA MUMADANA NDI MUNTHU AMENE MALEMU CHILIMA ANAMUKHULUPILIRA KUYANJA ALENDO LERO MWAONA ANATOLA ODUTSA CHIKWAMWA
Dalegate ndi munthu wa nzeru zedi😅😅
DELIGETI .
Ng'aluri Brain Banda, ikuveka bwino kwambiri
Osama tizana ayi iyo ndi public broad cast ndiye munkakhala pa tv mudzikhala sirious idea timakhala tikudikila zokupsa, koma zinazo muchepetse tisamamve zamsima pamenepo ayi
Kabambe live as Dalitso basi
Kodi akwangwanjiwa sanambvere speech ya usi atabwera pa 15 November? Mxiii
Your generous guys
Inuso mzapinda michira aphwanga
Ndevu zamwayi ndamuwona alibe mbali amafuna azimupotoza Brian banda
Kkkkk anyamata inu chipongwetu mpaka NPK ndithu ati Ntumbuka,Patricia,Kambala chipongwe chachikulu ichi
Zikut bwanji
Yes timakunyadilani komano muchepetse. Kumanyozana be serious guys
Mr Banda...
Mukutisewelesa kwambili pamtumbo panu 1:00
Brian, ka word kaThamo, sukanatukutse bwanji?
Anyamata awanso eish 🎉
the power of delegate 😂😂
Ndiyoopsatu 🙌🙌🙌
Koma abanda opangayo anapanga
Tizaonana poweruka kkkkk
Zikayenda bwino,abale zinadzi kumavomeredza
Good analysis
😂😂😂😂kom tisanakalembetsefedi zisatikhudzedi kkkkkk
PA convention ya UTM 5 minutes inapatsidwa kuti candidate aliyense alankhulepo anthu asanayambe Kuvota.Zinachitakuwonekeratu kuti Kabambe analankhu mfundo zogwirika kuposa onse, kenako a kambala, kenako a Kaliati nkumalizira a Mtumbuka
Koma anatenga mpando wawo komaso coffee wawoso xoopsatu
Delegate ndi katundu
Ndale ndichoncho,ukhonza kuzaza anthu pamasintha koma mawa tiyeni tikavote iwe osapeza or imodzi
Koma ifeyo tikanasangalala mukanapita inu ku conversion kuja ngati momwe mumachitila ma convention azipani zonse
Lero pangwanji kulibe kung'alula akukamba za UTM atola nkhani a utm munja mumachila photos mukamanyanzitsa map ndi chakwera lero ziiii ai zikomo
Kwangwanji imandsangalatsa kwambiri, ma guys awawa mulibe mantha, kma DK uja muli zeru
Odya zanga😅😅😅
Lelo mukulakhura mofatsa a Brian coz mukukamba za kuchipani chanu ayi zikomo
Mumakwana Ng'aluli,andevu za mwayi .ndi amtsukuluzi
Namiwa ndi chi tsiru amwene
Amanganya ngati muli munthu wopita Ku school basi musakakamire chipani cha UTM ai yambitsani chipani chanu chanu na ngati mukudziwa ndale ,UTM muyisiye Komanso kuli dzipani dzambiri pitani kumeneko, kodi bwanji mwatani Kodi mukufuna anthu adzikunyodzani?
Usi angobwelaso ku adra tawasowa
Wonder msiska, kod dander head ndi ndani kkkkk
Kaliate anapang mistake kusintha position
Bwana Michael usi adzisiye za ndale si mbali yawo, alimbikire sewero basi kuti adzipasidwa ulemu
Fact aise ndi chilungamo
Words
Mmmmm inu anthu andale ndimene amanenela. Kuyankhula ngati adzapanga bodza.
Kodi abrian mukupindula chian pomunyoza usi ?
Afisi awa eeeeeh amadalila chani😂😂😂😂😂
Futso nali, Kodi ku mgwilidzano wa zipani ziwilizi oyenela kunena Kuti tatuluka mmgwilidzano ayenela kunena ndindani pakati pa chipani cha UTM Ndi vice president?
Anthu inu mumandifikapo
Deligete simunthu konse
Wonder msiska amada ndi namiwa kwambiri
Ineso ndamudabwatu. Do you know why?
@Josephill9vo I don't know why he hates him with so much passion
And this is the second time wonder kupanga zimenezi pa namiwa
Not Wonder Msiska amamuda Namiwa ayi koma sagwirizana ndizambiri zomwe amachita chifukwa iye uja amayankhula ngati wa CIDED koma kumumvetse bwino amatsatira chipani china chake mosabisa DPP. Chifykwa chakuti chiri choose chomwe yanena DPP iye amatenga chimenecho kukapanga amplify ku press briefing . Ngakhale akudziwa kuti zomwe ayankhula a DPP zilibe backing ilionse. Amaoneka kuti kuyankhula amatha koma kuganiza kwake ndikobwerera mmbuyo. Pali anthu atatu awa Boni Kalindo , Namiwayo and Brian Banda zambiri akamayankhula sakhala objective especially akamayankhula zinthu zokhudza chipani chomwe iwo amatsatira. NDIFUKWA CHAKE MUNAMUNVA MSISKA ATANENA KUTI 'DONT RECRUIT ME'. Chifukwa Brian amafuna a program paja anzake aja azimvera zonena ayeyo basi. Ndiye anzakewo amamutsutsa.
@yassinn5634 They know the truth themselves
Ngt fertilizer N PK 21 kkkk km athu muli ndichipogwe
Kabambe alibwino
A usi akungofuna kutukwanidwa apusa nazoo izii kkkkkkk
Moçambique wayiwala?
Koma mwati ngat NPK
Akuterotu 🤣🤣🤣🤣
Ananyanawo nsonkhamo galu uyuuu Brian amangokamba zosemphana komaso zaziiii
Autsi ndimunthu osokoneza kwambili ndikuyipa mtima😈👹
Usi si umakwana
That's the best solution basi visiting president's place
Chakwera akuononga ndalama akuona ngati amalawi awapusisa ndi Dola azaona ngati zomwe aziona ku utm
Autsi amulemekeze kabambe ndi Pulesedent
Usi ndidolo guys simungamake mukapusa usi gwetsa UTM mosavuta
Ena osewa akangopanda kupanga alliance Chakwera samuchotsa achepa awona zachina kaliyati
Koma a Pulesedent akabambe asamaonelele zinthu zikuchitika a Balalisa anthu Utsi akulakwisa