LIMPOPO FM MVELANI NDIKUYANKHA MAFUSO AWA NDI MR DON’T TRUST

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 4 вер 2024

КОМЕНТАРІ • 119

  • @user-wy2tx2cj6v
    @user-wy2tx2cj6v Місяць тому +8

    Manganya ndi wa MCP ndipo ndi mzake wa Chakwera. Komanso mukaona chiyambiyeni ma cabinet Onse apitawo , Manganya sanachotsedwepo mu cabineti.Komanso iye uja magazi ake ndi a MCP, Thanks

    • @NedsonMatia
      @NedsonMatia Місяць тому

      Zoonadi zake ndizimenezo

  • @IssahAluba
    @IssahAluba Місяць тому +4

    Ndipo kuvota kovotera ID pakufunika kwiyo wawukulu kt chakwera asakhaleso ndi mpavu komaso akuna kwambiliiiiiiii

  • @user-ih7li3im4s
    @user-ih7li3im4s Місяць тому +3

    Manganya ndi udasi anapeleka Yesu uja, naye adzafa ngat chilima musiyeni,

  • @MosesTangwe
    @MosesTangwe Місяць тому +3

    Manganya akupanga ija ndi campaign motumidwa ndi chakwera ndipo anthu tisamukhulupilire

  • @chifundobuledi
    @chifundobuledi Місяць тому +4

    Makandulo apitilre
    Ovota adzakhale mmalawi aliyense
    Manganya ndi WA mcp

  • @levisonkaluwa6411
    @levisonkaluwa6411 Місяць тому +3

    Manganyatu akudziwadi kanthu za SKC. Ndipo ameneyu akuyenera achotsedwe ku UTM. Nzoonadi, m candli akamayaka tu anthu wa mtendere sakuupeza choncho anthuwa asasiye kuyatsa kuti anthuwa amve mtedza.

  • @DominicNkosi-iq9fh
    @DominicNkosi-iq9fh Місяць тому +3

    Mayi amaphikira ana ake chakudya kunyumba kwake, osati kunyumba ya munthu wina

  • @YasinMusa-ym8lp
    @YasinMusa-ym8lp Місяць тому +3

    Wachamba ken msonda kauzuzu kowonda kamja ngamti kali ndimatenda mwina matena

  • @gracemkandawire8769
    @gracemkandawire8769 Місяць тому +3

    Manga ya akumupangila campaign a Chakwera

  • @user-wx1jt5fd2j
    @user-wx1jt5fd2j Місяць тому +1

    Amalawi anasukusula ndalamazoo alandire ndi zawo koma asazabvotere ankhanzawo opanda chifundowo

  • @user-zk7jw9up6m
    @user-zk7jw9up6m Місяць тому +1

    Mpaka lelo manganya sadayankhulepo za imfa ya chilima

  • @user-gx5ht9gm3z
    @user-gx5ht9gm3z Місяць тому +2

    MANGANYA NDIOSOKONEZA KWAMBIL NO PAIN NO GAIN

  • @EmilyBanjachikwatula
    @EmilyBanjachikwatula Місяць тому +2

    Thawi yawo yantha amenewo zaka zonsezi Malawi akhala akukanda ndiye lero adziti ngongole ? Samapanga zimenezo skc asanamwalile bwanji?

  • @BwanaGD
    @BwanaGD Місяць тому +1

    Chakwera zake zada ndiye akuyesa yesa kugwilitsa ntchito zitsilu zinazake kuti mwina kapena ziwale zupusa zakezo naye maganya chikagawayo tamutulukira kale kuti ndiwagulu la chikagawa ndipotu chomwe adziwe chakuti chilichose akupanga Malawi yadanawo kunkhosi mcp panu ikuveka mwachifungo chonunkha ndipo Kubota tivota momwe zimayendera mbuyomu zuyenda chimodzimodzi gati akuwona kuti Kubota kulibe ok ubwinoso wanthawi timamupatsa chakwerawo ukuntha timuyendera ndimapazi kukamusuntha gati sitipatsidwa mwayi olembetsa ndi zintupa zosiyana siyana ifetu sitipanha nawo zakudabwe

  • @RuthKaunda-tc5qd
    @RuthKaunda-tc5qd Місяць тому +1

    Palibe kuthetsa kuyatsa candle lo sitilolo

  • @user-zk7jw9up6m
    @user-zk7jw9up6m Місяць тому +1

    Zoona a malawi sitichedwa kuyiwala akatipasa chibanzi

  • @chirwaellace1093
    @chirwaellace1093 Місяць тому +2

    Manganya ndi Yudas. Pano akuchita kusangalala busy kupereka umboni wa umphawi wake wa kale

  • @user-my4gr1pv8h
    @user-my4gr1pv8h Місяць тому +2

    Athu avutika vutika wina azibwela apatsa ndalama fukwa yovota ikubwela...Ajaso ngoouma mutu ndi mpala uja et awagwiritsa ntchito chakwera aja km akunama ife kupoila kwao tadziwa kale

  • @user-hx6jl2jq9j
    @user-hx6jl2jq9j Місяць тому +2

    Manganya galu wamunthu wamchira weni weni komanso fiti yamalaza.
    Msonda machende ake pamodzi nd banja lakelo

  • @user-uk3bz1hr5t
    @user-uk3bz1hr5t Місяць тому

    Nthiko watenga kumakaphikira nsima nyumba mwa eni wake kusiya kumaphikira nyumba mwako ndi ana Ako,,,,manganya asatibowe!
    And manganya adaikapo nkono pa imfa ya chilima 😊

  • @gracemkandawire8769
    @gracemkandawire8769 Місяць тому +2

    Zoona,,koma anthu amuzindikile manga ya alandile ndrama koma osawavotela

  • @dumisanimoyo3152
    @dumisanimoyo3152 Місяць тому

    I think this government has lost its target bcz there's no need of giving Money to the Malawians

  • @esaMoha-dm4kj
    @esaMoha-dm4kj Місяць тому +1

    Shina shillishosnse soshitka nkwa anduamenewa ashankwela ndiomwe ankutumaso ngani yyonse amanganya ndi waw mcp ngani yyankusa abanda amangidwe ngati ashankwela ankufunna kt mulungu awatetese. Live in the sauth ✌️✌️👈👈✌️👌

  • @dumisanimoyo3152
    @dumisanimoyo3152 Місяць тому

    Kumbukirani Michael usi simumalawi ameneyo ndiwakuzimbabwe

  • @user-uk3bz1hr5t
    @user-uk3bz1hr5t Місяць тому

    As long as uli mzika ya Malawi you are ligible to vote even though popanda Cha unzika

  • @MariaWilson-gq8st
    @MariaWilson-gq8st Місяць тому

    Iyeyo awasiye anthuwo ndi ufulu wao bs ngat iyeyo ngat sakusangalatsidwa nazo asiye cipanico ena apitilize

  • @FrezerJangiya
    @FrezerJangiya Місяць тому +2

    Akupanga kampeni ya mcp

  • @ndawonamhango
    @ndawonamhango Місяць тому

    Don't trust manganya he is on MCP ticket

  • @petertaulo8014
    @petertaulo8014 Місяць тому +1

    Manganya akupanga kampeni wa Mcp not kuthandiza Malawi, komaso Ken Nsonda ndi manyi amunthu Ma ARV apeweteka!

  • @thulanimpphiri6873
    @thulanimpphiri6873 Місяць тому +1

    Manganya akupanga campaign Chakwera akuziwa kuti akuwowozedwa ndichifukwa wagwirisa kamanganya. utm imuwu manganya kuti akamapanga musonkhano azipanga za mcp osati za chilima. Manganya better udasi ata zindikira kuti walakwa anabweza ndalama ndikukazikweza mumtengo koma manganya akudya ndalama ndikupangira campaign. Musonda zeru alibe. Kuvota aliyese amene ndizika yamalawi yiyenera kuvoto ukhale ndi ID or ulebe ali ndiufulo kuvota.1994 timavota without ID pano zavuta pati

  • @OssmanGuevarra
    @OssmanGuevarra Місяць тому

    Inetu brother ndine malawi Koma ndilibe ID Koma ndili ndi passport ndipo 2014 ndinaka vota komandinagwirisa ntchito ndi pepala lochokera kwa amfumu akwathu nde zama ID ifeyo zimenezo sitikupanganao

  • @watsonmhango8794
    @watsonmhango8794 Місяць тому

    Ndalama yilibe Neef ,akungonama sanatinamize

  • @SteveChapola
    @SteveChapola Місяць тому

    Ndiyekuti ngati aside akuvomereza kuti anaphadi bwanji akulesa okuphawo

  • @UsenLashid
    @UsenLashid Місяць тому

    Sitikugwilizana nazo onse ndi amalawi

  • @CharlesMaloya
    @CharlesMaloya Місяць тому

    This government is worse in the history of Malawi

  • @user-dn3gp6yi4y
    @user-dn3gp6yi4y Місяць тому

    Ken msonda za ma candles chikumuza ndi chani anthu tiyasa ma candles Malinga ndi chikulupilo chathu komaso Ausi ndi a MCP not UTM.nkhani yo vota pa libe ku gwilisa ntchito chitupa Cha udzika anthu akavote mwa chisawawa ngati momwe timachitila kale pofuna ku vota komaso anthu omwe tingakhale ma centres muzawonesese nkhope za chilendo zisazapezeke

  • @AjibuTwalibu
    @AjibuTwalibu Місяць тому +2

    You are welcome

  • @user-uk3bz1hr5t
    @user-uk3bz1hr5t Місяць тому

    Manganya Palibe angachite chothandiza Amalawi,,,

  • @UsenLashid
    @UsenLashid Місяць тому

    Mwambi umenewo WA kunyumba kwake ndi amake ndi wa MCP athu AMene atsalila kugwilizano ndi amene anampeleka chilima

  • @dumisanimoyo3152
    @dumisanimoyo3152 Місяць тому

    Kodi police yikugwira ntchito ndi mcp or dziko la Malawi

  • @user-do2cs8nf4b
    @user-do2cs8nf4b Місяць тому

    Ndim'mene manganya akupangila zikusonyezetatu kuti chipani cha mcp analowa kale kale, komanso za kuphedwa kwa Chilima amadziwa po kanthu
    Komanso zimene akupanga panozi ndi compain nthawi yonseyi anali kuti anthu m'mene amvutikira muja m'malo moti ndalama zomwe akugawazo zithandizire zosowekera mdziko, palibe chanzeru chimene akuchita amalawi pano tinachenjera tiyeni tilandire ndlamazo tidye ndi misonkho yathu imeneyo mbvoti ili mumtima

  • @RuthKaunda-tc5qd
    @RuthKaunda-tc5qd Місяць тому +1

    Ali part of campaign koma ya MCP
    Ndalamazo akupatsidwa ndi Boma.

  • @user-bi6pb5gc8t
    @user-bi6pb5gc8t Місяць тому

    Manganya akanakhala kuti ndi wa utm bwenzi nsimayo akuphikila kunyumba kwakeko

  • @NedsonMatia
    @NedsonMatia Місяць тому

    Manga siwa utm ayi uyu ndi wa mcp ndipo chakwela ndinzake kmso akuziwapo kanthu

  • @ziwani3682
    @ziwani3682 Місяць тому

    Manganya ndiyemwe anaperekera zida kt skc afe pano tinamutuluka

  • @SteveChapola
    @SteveChapola Місяць тому

    Magenta anachoka kale muutim ali ndi chipanichake choir odyazake alibemuladu kuchiliba

  • @AubreyWilson-j8w
    @AubreyWilson-j8w Місяць тому

    Ndizonvesa chisoni kwa ansonda chilima sanali munthu wamba kuntundu WA AMalawi ife ngati AMalawi chilima tizamukumbukira komanso tizimukumbukirabe

  • @FortyoneHarwa
    @FortyoneHarwa Місяць тому

    A miko usi tsi a. U. T. M ndi a. M. C. P. Chipani chakupa anthu cha magazi

  • @Mervic-vm8eo
    @Mervic-vm8eo Місяць тому +1

    Manganya ndi poison

  • @HendersonJumbe
    @HendersonJumbe Місяць тому

    Akufuna kupusitsa anthu komanso part of cumpian

  • @emilypayesa8391
    @emilypayesa8391 Місяць тому

    Kampeni , ndipo ndalama zikuchoka kwa Chakwera

  • @UsenLashid
    @UsenLashid Місяць тому

    Chintchora pakuti wosewa ndi akuba that's why Ali ndi fulu ndipo Amalawi tisadzayelekezeso kuvotela mbava izi

  • @MrThomas-j9d
    @MrThomas-j9d Місяць тому +1

    Analowa kale MCP amangokuputsisani ziwani kuti
    Udindo omwe alinawo siwamuyaya

  • @user-dn3gp6yi4y
    @user-dn3gp6yi4y Місяць тому

    A ussi ali ndalama ndakalazo akutekutenga kwa anthu okuba a MCP omwe amatibela misonkho yathu

  • @UsenLashid
    @UsenLashid Місяць тому

    Ndekuti Ali mwa modzi amene anapha chilima. Koma a UTM sasiya kuyatsa makendule mpaka chiilungamo chioneke

  • @user-cd4df3vg4y
    @user-cd4df3vg4y Місяць тому

    Manganya akutinamiza ife a amalawi. Ndalama akulandira kuchoka ku Boma kuti adzigawa. Ken akudwara koma sakudziwa ayi. Ayi sitikugwirizana nazo kuti anthu akagwilitse ntchito chophaso cha unzika ayi. Aliyese akavote basi. Manganya ndiwa MCP ankangobisara kumbuyo kwa UTM. Manga anali kumthira kuwiri. Taphunzira kuti Manga ndi Yudas. Anagulitsa moyo wa Chilima. Za imfa ya Chilima zikuonetsa kuti sixikumukhudza za imfayo. Akushashalika kwambiri ndi ndalama za Chakwera. Ndalama zinari za ifeyo a Malawi anaba pogwilizana ndi Pulezident Chakweraa.

  • @user-fm8ed7eo3i
    @user-fm8ed7eo3i Місяць тому +1

    Manganya sakuchita bwino chifukwa anthu avutika ovutika Lero nthawi yawathera akufuna kunyengera anthu ndi sweet cholinga azingomva kusekemera mmilomo pomwe m'mimba mulibe kanthu (2)Keni msonda ndi atimke nawo alibe mphavu ku MCP ndi chifukwa akumalolera ku mwayankhura cholinga azipedza ndalama yogura matemba (3)pa chiyambileni cha ifa ija ine ndapbudzira za kuti MCP ndi chipani chamagadzi

  • @user-do2cs8nf4b
    @user-do2cs8nf4b Місяць тому

    Ken msonda ali mgulu la n, gonna uja palibe chamzeru chimene akupanga kuletsa ma candle cho zikuchita kuwonetseratu kuti akusowa mtendere moto ukwawotcha sakugona tulo mzimu wa Chilima ndi anthu 8 aja uli pamitu pawo mtendere adzawusowa moyo wawo wonse

  • @RiriKamphata
    @RiriKamphata Місяць тому

    Sakuunthandiza manganya akuononga kwambiri

  • @Shelifibraheem
    @Shelifibraheem Місяць тому

    Choyambilila manganya ndiwadyela khalidwelake ndiosiyanila ndi winiko chachiwili mtiko omwe alinaowo aphikile msima yodya mkaziwake ndi ana ake.

  • @RuthKaunda-tc5qd
    @RuthKaunda-tc5qd Місяць тому

    Manganya si WA UTM koma WA MCP

  • @RiriKamphata
    @RiriKamphata Місяць тому

    Manganya ndi wa Mcp musapusitsike and iyeyu ndi modzi yemwe akudziona kuti akhoza kupanga anthu kukonda so Mcp
    Ulutsani kuti asapusisike amalawi Manganya munthu oyipa kwambiri

  • @RuthKaunda-tc5qd
    @RuthKaunda-tc5qd Місяць тому

    Manganya akupanga ndale kumene

  • @EfeloYovita
    @EfeloYovita Місяць тому +1

    akugwilitsidwa ntchito manganya aona kuti nthawi yatha 4years yose palibe chomwe achita kukweza zinthu basi anthu kumudzi akuvutika

  • @Ernestkamvazina
    @Ernestkamvazina Місяць тому +1

    Ken Nsonda kukula naye galu ameneyu akathetsere kwa Make

  • @RiriKamphata
    @RiriKamphata Місяць тому

    Kulira maliro kulibe malire
    Oyipa ameneyo msondayo afuna pongopezeeapo ndalama kuchoka kuboma akagwere uku
    Aliyense akavoti zoyiika malirezo ayi
    Akhale iwowo ndi manganya wawoyo yamakabduulo yatenga mavote ose

  • @MarcosDjussa
    @MarcosDjussa Місяць тому

    Manganya anapeleka chilima komanso ndi wa map

  • @user-fh7sd6gp3f
    @user-fh7sd6gp3f Місяць тому +1

    Manganya ndi tikufelanji weniweni.
    Ngongole it's just the waste of money palibe amene angabwenze

  • @user-ky8eq5ek1p
    @user-ky8eq5ek1p Місяць тому

    Manganyayo ndiwa chipani Chang'ona

  • @MariaWilson-gq8st
    @MariaWilson-gq8st Місяць тому

    Zovotera cimpaso cokha sitikugwirizana nazo ife aliyese akufunika kuti apange njira zoti aliyese azavote mwaufulu wake

  • @user-do2cs8nf4b
    @user-do2cs8nf4b Місяць тому

    Ngati akunena kuti opanda cha uzika asakabvote pamenepo pokha nde akunama chifukwa anthu ena chauzika chawo anayamba kuyendera kale kale mpaka pano sanapatsidwe zonsezo akupangila dala ndicholinga choti adzabere zisankho
    Bola kumbvota opanda chauzika chifukwa kale timambvota opanda chauzika

  • @MISHECKBANDAH-m3h
    @MISHECKBANDAH-m3h Місяць тому +1

    Part of campaign akufuna kugula anthu aziwasatira akubiasalira kumbuyo kwa boma ndi wa MCP ameneyo

  • @user-uk3bz1hr5t
    @user-uk3bz1hr5t Місяць тому

    Ken Msonda alowelera bwanj za nyumba ya mwini ?alibe mphamvu yolesa candle lighting

  • @HajjiSufiyani
    @HajjiSufiyani Місяць тому

    Pepani tiyakha. Lelo. Manga. Alingati. Khoswe. Amati akakuluma. Iyeyo amapepeze. Cholinga. Chakuti. Tisamuve.kulumako. Ndimene Alili manganga. Muthu oyipa

  • @MaggieMuhone-r7m
    @MaggieMuhone-r7m Місяць тому

    Mannganya ndi udasi akupanga kampeni manganya

  • @RuthKaunda-tc5qd
    @RuthKaunda-tc5qd Місяць тому

    Ndipo zenizeni zunenedwa apapa ziii

  • @user-hm9nc7lz6e
    @user-hm9nc7lz6e Місяць тому

    Manganya ndi wa mcp osati utm ndipo imfa ya chilima manganya akudziwapo kanthu

  • @OssmanGuevarra
    @OssmanGuevarra Місяць тому

    Brother manganyatu ndi wa MCP kuyambira kale akupanga masewelo ake nde Ku UTM kujatu anangopitilatu ndiukazitape umtila kuwili. Nde zonse akupanga manganya ndi kampeni ya MCP

  • @user-so7wg6ii5m
    @user-so7wg6ii5m Місяць тому

    Manganya ndi wa mcp aliyense akudziwa amalawi musapusitsidwe

  • @UsenLashid
    @UsenLashid Місяць тому

    Manganya akuyenela kukuthidwa, this is just kampeni

  • @RuthKaunda-tc5qd
    @RuthKaunda-tc5qd Місяць тому

    Adaniathu ndiomwe timakhalanawo pafupi

  • @user-gb2sl1jt4s
    @user-gb2sl1jt4s Місяць тому

    Bwana trust mwasowatu

  • @dumisanimoyo3152
    @dumisanimoyo3152 Місяць тому

    Sitikuvomerezana nazo zimezo

  • @user-zk7jw9up6m
    @user-zk7jw9up6m Місяць тому

    Ndalamazo tizitenge ndizathu

  • @IshmaelJimu
    @IshmaelJimu Місяць тому +1

    Ayi Mesa chipani chake ndixhomwechi cha MCP

  • @IbraheemclassickmahmoodIbrahee
    @IbraheemclassickmahmoodIbrahee Місяць тому

    Imene ija ndi ndale komanso campaign in other way,nde akanawalolanso ena achite nawo campaign yawo coz it's part malamulo

  • @user-nf3ik3ff6y
    @user-nf3ik3ff6y Місяць тому

    Manganya ndiwa MCP

  • @SlindiryLoveness
    @SlindiryLoveness Місяць тому

    Ndinu aboza inu ma properganda anuwo si azakupindulirani muzalira mukhaula mcp yiwinaso tikuziwa munatumidwa inu nd dpp mukufuna abale anthu abwelereso mumavuto azilowa munyumba 6 oclock zako izo

  • @susanmkorongo3585
    @susanmkorongo3585 Місяць тому +1

    Part of campaign

  • @mathewsmbaluko8522
    @mathewsmbaluko8522 Місяць тому

    Mukunena zowona manganya ndi wa mcp komaso akupanga kampen

  • @user-eo2hl9ug1h
    @user-eo2hl9ug1h Місяць тому

    Kanpeni. 2ndlama .za .chakwela. .3ndale

  • @Bonisiwentamo
    @Bonisiwentamo Місяць тому

    Phala akunenalo athu omwalila menemo fiti ameneyo

  • @user-bg7ur1gw1q
    @user-bg7ur1gw1q Місяць тому +1

    Akupanga kampeni ndipo ndi wa mcp

  • @UsenLashid
    @UsenLashid Місяць тому

    Ali part of kampeni

  • @Bonisiwentamo
    @Bonisiwentamo Місяць тому

    Aleselanji makandulo wachabe

  • @user-bg7ur1gw1q
    @user-bg7ur1gw1q Місяць тому +1

    Zovotela lb tisazalole chonde amalaw

  • @user-bg7ur1gw1q
    @user-bg7ur1gw1q Місяць тому +1

    Nsonda alibe mzelu ndipo alekeletu

  • @dumisanimoyo3152
    @dumisanimoyo3152 Місяць тому

    Ken msonda asatiuze zo chita

  • @DafterSam
    @DafterSam Місяць тому

    Ken nsonda adatha

  • @SolomonBewula
    @SolomonBewula Місяць тому +1

    Ndikampeni ndithu