A Dpp adzadzana Ku Police Ya Area 3 Komwe Alfred Gangata wamangidwako.

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 10 січ 2025

КОМЕНТАРІ •

  • @MaxonKambazithe
    @MaxonKambazithe 4 години тому +7

    Ntambo trapence mwaona zomwe munachitira ifeee amalawi tooonse ambiri munasiya mmavavuta

  • @rashidadan2533
    @rashidadan2533 3 години тому +5

    His exllence professor Peter muthalika
    The president of the republic of MALAWl 🇲🇼🇲🇼🇲🇼
    🌹 The winner of 2025 general election 🌹
    Ofooka , osatopa ndipo osaopa ,
    No sweet without sweting

  • @osmanmdala-uh7xw
    @osmanmdala-uh7xw 3 години тому +2

    Chakwera ali ndi tsoka lalikulu iye mwini ndi mamina okha-okha tiyeni omuthandizira madzi okha-okha. Kkkkkkk ataya bomwetamweta

  • @MarkElia-i7q
    @MarkElia-i7q 3 години тому +1

    Anthu mwatopa mpaka tambala uja wagwidwa chitopa 😂😂😂😂

  • @CharlesKapalamula
    @CharlesKapalamula Годину тому

    AAA dziko lasintha Ili katundu anakwera Zambia, Mozambique, Tanzania,kose mbola

  • @MzikaPhiri
    @MzikaPhiri 2 години тому

    Viva Malawi Viva....Dpp woyeeeeeeee Gangata woyeeeeeeeeeee..APM my vote

  • @HaroonSaidi-jv3ek
    @HaroonSaidi-jv3ek 4 години тому +2

    Keep on my dear brothers and sisters osaopa osatopa osafooka

  • @IsaqueFernandoAntônioAntônio
    @IsaqueFernandoAntônioAntônio Годину тому

    Ntambo ndiwausilu anagulitsa dziko ndiiyeyo

  • @SolomonNjolomole
    @SolomonNjolomole 3 години тому

    Chakwera ndi mfiti adapha chilima mmm adadzitemberera Chakwera mtendere sadzaupeza viva dpp❤❤

  • @AbdulJohn-t7l
    @AbdulJohn-t7l 3 години тому +1

    A MCP ziwani kuti a police kuwatumawo akukupangani de campeni kuti akugweseni bas coz anthu omwe mukumangawo ali ndi anthu awo komaso madela omwe akuchokela ziwani kuti madela amenewo mukuluzako mavote chifukwa choziwonesela nkhaza kwa anthu

  • @dondamissonchdziwe3958
    @dondamissonchdziwe3958 3 години тому

    Viva aa, A luta continua aa, povo no poder, Muzi imba muziti povo no poder, povo no poder, battle goes on

  • @AchinaKellz
    @AchinaKellz 2 години тому

    Apa ndiye tikutenga ma members ambiri a mcp ena samayiziwa pano ayiziwa I hope so apanga decision yoyenera😂more vibe dpp Chithupsya azifinyana okha 😂

  • @DavidKanyemba-n2s
    @DavidKanyemba-n2s 2 години тому

    My Malawi 😭

  • @MillieMalakam
    @MillieMalakam 3 години тому +1

    Chakwela sakupanga nawo guy's koma mvuto ndi nduna zake zamusokoneza mutu. Tawonani guy's mfundo imene anapatsa ija kuti akuwongola mafupa ndi pule watundu wanji sangabwelese ndi mfundo ngati imeneyo ija kuwawuza athu chakwela anali wabwino kwambili koma mistake yovomeleza kupha chilima is a big mistake mulungu wamukwiyila chakwela

  • @LeyvanSamuel-pe5tc
    @LeyvanSamuel-pe5tc 4 години тому +1

    Koma guys paka chakwera ndi mfiti😂😂😂😂

  • @dondamissonchdziwe3958
    @dondamissonchdziwe3958 3 години тому +1

    Taotchaponi, muwapheponso apólice wo mugumule ponso nyumba yonseyo,akuzolowera tawa chiteni Za Ku Mozambique,. bwanji adapha Chilima pamodzi Ndi Wanthu wena aja, koma osamangana Musamamu sekerere Chakwera ndi Chitsiruu komanso MCP yonseyo Chikangawa matumbo amawo wonsewo, Chakwera Ndi mfiti adapha Chilima yomweyo Galu iweee ee

  • @NoliaGama
    @NoliaGama 4 години тому +1

    Apm my vote

  • @GeraldChilundu-e3v
    @GeraldChilundu-e3v 3 години тому

    They can't kill us all. Koma boma lapita basi Ku DPP

  • @HanifaMambo
    @HanifaMambo 2 години тому

    Ndinapanga mistake wosakalembetsa mukaundula kuti dzavotere DPP nsamene chakwera akundipweteketsa m,mimba ndizochitika zake dzodzadza mamina m,mutu akadzalamuliranso chakwera anthu akufa aja adzauka izizi sidzoona koma any way tiye tasiyeni amange momwe angafunire kapan October uno ndiiwo akumangidwa ndye chiyambira sichipwetek koma chobweza adzalira

  • @AchinaKellz
    @AchinaKellz 2 години тому

    Zowona mr president chihana

  • @KennedyPhiri-h9h
    @KennedyPhiri-h9h 2 години тому

    Wosawopa wosafoka wosatopa malawi 🇲🇼 ndi wathu uyu

  • @IsaqueFernandoAntônioAntônio
    @IsaqueFernandoAntônioAntônio 2 години тому

    Koma mcp chitani manyazi.

  • @jacklinenkhata
    @jacklinenkhata 3 години тому

    Yoooooooooooo koma mcp 😢😢😢😢😢😢😢 yafikapo

  • @YusufMaulidi-b2c
    @YusufMaulidi-b2c 3 години тому

    Ngati mukunena kuti achakwera sakupanga nawo, muzifunse kuti president ndindani ku Malawi kuno iyeyo sakuona, ngati sakuziona izizi ndiye kuti tilibe president

  • @YoungMwacho
    @YoungMwacho 3 години тому

    Chakwela leadership ndi MCP akuyaluka tsiku ndi tsiku. Vinyo wawathela.

  • @EllahChikwatu
    @EllahChikwatu 3 години тому

    Cihana ndamene akuwa funira a mw zabwino kt chakwera acoke

  • @WallyMsiska
    @WallyMsiska 3 години тому

    Dr wazithupsa mmmm ndimanyaka

  • @BrianJoe-z7u
    @BrianJoe-z7u 2 години тому

    Koma mcp yaonjeza geyezi ayi ayi

  • @WilsonFelix-j9n
    @WilsonFelix-j9n 3 години тому +1

    Panyini paamake chakwera tchende lake

  • @malisawakabanga9856
    @malisawakabanga9856 2 години тому

    Kodi ku MCP wina aliyense akupanga zolungama, kulibeko amene akuchimwa? Ochimwa ndi a DPP okhaokha?

  • @YusufMaulidi-b2c
    @YusufMaulidi-b2c 2 години тому

    Achinyamata ndi awa ali ndi ma lodge angapo muzaka zochepa kuba kwabiri, experience yawo sakuigwiritsa ntchito potukula dziko koma kubela amalawi ndikumapanga ma tactics kuti asaziwike kuti akuba shame on them

  • @YusufMaulidi-b2c
    @YusufMaulidi-b2c 3 години тому

    Ndikanakhala ine achakwera ndikanangozisiya zafika pauchitsilu komanso ziposa pamenepa

  • @BerthaKasambala-y5k
    @BerthaKasambala-y5k 2 години тому

    Nkhani ndiyoti chakwera akawona peter sakupuma bwino akatero amangaso chisare km akuiwira kt atha kumanga ariyense km voti sangaimange chakwera maprani atha sure

  • @ruthkasiya
    @ruthkasiya 4 години тому

    APM my vote ❤😂😂😂

  • @AchinaKellz
    @AchinaKellz 2 години тому

    Apatu ndi russia mwava ma guy's, afrobometer ya baya ikagiwina dpp onse alowe muzafufuza ali mkati kuopa athawa akapukuwa

  • @WhyteSmart
    @WhyteSmart 3 години тому

    Kupitiliza kuzipisira mbiri basi MCP

  • @RoseThindwa
    @RoseThindwa 3 години тому

    Aaaaaaaaa chikangawa chilombo chopanda chisoni alephera kukonza zinthu chitukuko chikhale chomanga anthu what a shame.

  • @NikolasNanawe
    @NikolasNanawe 3 години тому +1

    Madwa limozi ndalama

  • @YusufMaulidi-b2c
    @YusufMaulidi-b2c 3 години тому

    Achakwera pano tinene zoona ali pakati pa bridge yoonongeka,kapena tinene kuti anakwera mu mtengo iye kuitanitsa nkhwankhwa mkumadula pansi iye ali chammwamba pano sakudziwa kuti apange bwanji koma adziwe ichi mphamvu zimene akugwirisa ntchitozo tinachita kum'bweleka iye waiwala akuganiza kuti ndi zake

  • @FundoNdeketeya
    @FundoNdeketeya 3 години тому

    Kodi Malawi anzanga palibe muti tithane ndi chakwera mmene timaziwila makhwala amawi koma chakwera osathana naye

  • @SiliAmanu
    @SiliAmanu 4 години тому +1

    Akanatula pansi udindo..

  • @ChuzyBoy-u1c
    @ChuzyBoy-u1c 3 години тому

    Mcp iku ndikuzionongela mbiri yoyipa Malo momumanga 2017 yomweyo Manali kt izi ndizachisiwikile kuti chaka chino mukuluza bpp woyeeee

  • @WilliamMisoya-g3z
    @WilliamMisoya-g3z 2 години тому

    Mwatiyimilila akulu

  • @PeterKainga-e3h
    @PeterKainga-e3h 4 години тому

    More fire opusa Mr chithuphya

  • @HopefulCoralReef-tx4vx
    @HopefulCoralReef-tx4vx 4 години тому

    MCP Malo mothana ndi njala komanso kusowa Kwa mafuta bas buys kumapanga anthu apposition Ali pee!!! Koma tsiku ndiiwawo ili ndidziko

  • @lifredchikumba420
    @lifredchikumba420 3 години тому

    Anthu andale ndiwo yipa ofunika kuwa tuluka bola Kuma kango lima

  • @MsondaBanda
    @MsondaBanda 3 години тому

    Va ziii kalimeninge

  • @GayKaliati
    @GayKaliati 3 години тому

    Tatenga boma bas chakwela Ali ndimatha,

  • @DONNEXKhama-bk1gy
    @DONNEXKhama-bk1gy 3 години тому

    Sakuziwa MCP zomwe akuchita mapeto Ake mbiri ikuipilabe you see athu akuimba chakwera ndi mfiti anapha chilima

  • @ephraimmulo
    @ephraimmulo 2 години тому

    🔥🔥✔️

  • @RiteRoderick
    @RiteRoderick 4 години тому

    Dpp anakoza ❤❤❤

  • @HandEllah
    @HandEllah 4 години тому

    😮Nyimbo yo akuti Chakwera ndi mfiti anapha Chilima? 😮

  • @fosternyirenda-wo4eb
    @fosternyirenda-wo4eb 3 години тому

    God is watching

  • @StuwartKaunda
    @StuwartKaunda 4 години тому +1

    Koma malawi inu achinyamata muzaphuzila liti ukuyika agogo pasogolo wakalamba tu uyo asiyeni achinyamata

  • @macdonaldkainga
    @macdonaldkainga 2 години тому

    Mcp what a shame

  • @CassimMeleka
    @CassimMeleka 3 години тому

    Mcp manyi

  • @AdamuKasimu-x5o
    @AdamuKasimu-x5o 3 години тому

    Km amanga anthu angat

  • @ChiefJustin-l5p
    @ChiefJustin-l5p 3 години тому

    Kudya katatu kwasandukano kumanga wanthu eti

  • @BORNFACESIMBOTA
    @BORNFACESIMBOTA 4 години тому +1

    Chakwera ndikumanda

  • @ZelifaMwale
    @ZelifaMwale 4 години тому +1

    DPP BOMA

  • @HamiltonSachokeraKamende
    @HamiltonSachokeraKamende 3 години тому

    Inu aboma siyanie kumanga

  • @AnaJakson
    @AnaJakson 4 години тому

    Chakwera mukupangisa manyadzi mcp

  • @LawrenceBelson
    @LawrenceBelson 4 години тому

    Chakwera magazi amuzaza ku machende kwake

  • @JessieMbewe
    @JessieMbewe 4 години тому

    Kunja kuli mulungu tiwona pa mathero

  • @RobertElias-g3p
    @RobertElias-g3p 3 години тому

    Km yaaa

  • @Alfanmoseka
    @Alfanmoseka 4 години тому +1

  • @RaheemMoosaraheem
    @RaheemMoosaraheem 4 години тому

    Nyau Party ndi agalu ndithu

  • @davidchapomba
    @davidchapomba 2 години тому

    😂❤❤😂❤❤

  • @FrancisStima-sc7zs
    @FrancisStima-sc7zs 4 години тому

    Nyimbozeke izi anyamata azikwanje akuphanitu

    • @TrizaMbesa
      @TrizaMbesa 3 години тому

      Apha achakwera osati adpp akunama angovomeleza kuti alephela basi

  • @CharityChikomo-hl1gz
    @CharityChikomo-hl1gz 4 години тому

    Koma mcp this is nonsense too much komaaaa

  • @GayKaliati
    @GayKaliati 3 години тому

    Boma iloooo

  • @FrancisStima-sc7zs
    @FrancisStima-sc7zs 4 години тому +1

    Eeeee

  • @AlephaManganjira
    @AlephaManganjira 4 години тому +1

    Dpp my vote❤❤❤

  • @GeshoMwakitwile
    @GeshoMwakitwile 4 години тому

    Kkkkkkkkk atengera kut boma nkhalamba yanuyo kulibe kusintha boma ndilomweri

    • @RachealHarawa-xc9gs
      @RachealHarawa-xc9gs 4 години тому

      Mukhaula smartmatic yafufuta mavoti anu onse aja Pano chukanika kuyaka chomachine chani chija musova simunati ngati simufa ndima bp ndimwayi

    • @MaxwellChiwaya-i8q
      @MaxwellChiwaya-i8q 4 години тому

      Boma lake litiro chimanga 70000 fertilizer 130000

    • @GibsonMithi-n4y
      @GibsonMithi-n4y 4 години тому

      Kaya ndiwe wantundu wanji koma ndikutukwana mchitumbuka muchaza wako

    • @ruthkasiya
      @ruthkasiya 4 години тому

      Mukhaula. Mfuti yanuyo yomwe mumaulukira limodzi yo yauponda. Mulungu akukuonani agalu Inu ndikuipa mtima kwanuko. Chonsecho ukuvutika akukuzunza nawo galu iwe.

    • @ruthkasiya
      @ruthkasiya 4 години тому

      APM my vote 🎉

  • @WallyMsiska
    @WallyMsiska 3 години тому

    Dr wazithupsa mmmm ndimanyaka

  • @MaggieCement
    @MaggieCement 2 години тому

    End mp wa tsiliza anali bus kutenga anthu ku 25 kupita nawo kwatsiliza kukagula ma vote ATI azamuvotere munyera tuvi ankhongeletsi munya muona

  • @AdamuKasimu-x5o
    @AdamuKasimu-x5o 3 години тому

    Km amanga anthu angat