Anzanu my maiko amu Africa yonse salimbana Ndi munthu Oti anamwalira chifukwa sangabwererenso pa ziko la pansi koma ndale za kumalawi amalimbana Ndi nkhani imozi mozi ena zawatopesa Anthu akumwalira siku Ndi siku thandizani anthu ovuyika mumamuzi mwanu kuti apulumuke Ndi njala apaseni dzakudya ngatidi muli asogoleri awanthiu osawuka
Chomvetsa chisoni chakuti azitsogoleri a Mpingo amene anatumidwa ndi Mulungu kudyetsa Nkhosa za Mulungu ,zachisoni kwambiri ndi kumavomeleza umboni Obama.
Am from SA 🇿🇦 and I don’t understand the language but i think A malawi ndinu anthu otopetsa eeh 🙌
Wadziwa bwanji kulemba kuti amalawi ndinu otopetsa uli waku South Africa zaziii
Mtima wanga umati usa comment km mmm chi handsome ichi anakonza samamva km chosangalasa amatha kulemba wow
Iweyo wakut sopano kuno ku south Africa amalankhura chichewa, wasowa zolankhura iweyo srs kuno sikwathu chimatiberesa kuno ndi mavuto sizomanyoza kwanu kuno anagwiratu paja usaiwale ukumbukira kwanu akakubopha
@@HappyAbyssinianCat-xt2bm Guys ingokhulukani enatu amangozionetsela uchinsiru wawo
Sangamuphe uyu ndi oopsa kwambiri,, anamulephera kale,, more 🔥🔥🔥🔥🔥 mpaka 16 September wooooo
Koma awa ndi machine
Bon kalindo! The pangolin
Malawi tikulira koma otilirisa kwambiri ndinu anthu amenewo mukuti mukutiyankhulira zoyankhula zanu mwaife tikuona mufuna kutchuka kuziko osati zimene mukunenazi mukafuna kusintha boma pangani zeru anthu akukondeni zonsezo mukufuna azikunyengerani mukuthamawu ndipo mukuti nyasa
Zipani za ndale pakatipa zinali ziiiiiliii lelo kungofya chilima nkhani imodzimodzi musiyeni mzimu wake upume sangabwere amene amaweruza Ndi mwini wake mulunhu
Speaking loud and clear
Kkkkkkk the DC Born Kalindo u r standing for us luv u
Anzanu my maiko amu Africa yonse salimbana Ndi munthu Oti anamwalira chifukwa sangabwererenso pa ziko la pansi koma ndale za kumalawi amalimbana Ndi nkhani imozi mozi ena zawatopesa Anthu akumwalira siku Ndi siku thandizani anthu ovuyika mumamuzi mwanu kuti apulumuke Ndi njala apaseni dzakudya ngatidi muli asogoleri awanthiu osawuka
Bon kalindo alibe vuto Koma asongoleri ndi amene Ali ndi vuto.nanga zimene akunena ndizonama nanga
Lero loka ndie mwandigwetsa misonzi!!!!
Eish 😭😭😭 boma ili ayi ndithu
Truth and clear.
DC has no fear ❤❤❤❤
Odana ndi chilungamo Adana naye koma mulumgu amuteteza
Boma loyendetsedwa ndi m'busa 😂😂😂😂😂. Koma ubusa wa akulu amenewa unali mtchalichidi koma kapena unali ubusa wang'ombe????? Mau ndilibe ine guys 😢😢😢
The DC freedom fighter 💪
Tiyeni nazo zimenezo tili pa chulu mukuwona i
Ndakuvani kwambiri , dziko ili palibe mvusa palibe kuti uyu justice, palibe ndindani MCP inaononga ziko
DC ndi makina palibenso, umakwana
Namayenda
Mawa likazafika Boni kalindo ndiamene azatembenukenso Boma munalicjosa nosa la DPP ndipo Dpp ikanati isapange nkhaza chilima sibwenzi lelo Ali mmanda zonsezi linali dyera la DPP Ndi msogoleri wake lero siyani kubwebweta anthu a DPP akhala akumudandawula chisale nthawi zambiri mukuwona ngati lelo wasintha muzamkhawula tiyeni nazo mwana WA njoka Ndi wanjoka sakhala msomba
Agalu amenewa
Chomvetsa chisoni chakuti azitsogoleri a Mpingo amene anatumidwa ndi Mulungu kudyetsa Nkhosa za Mulungu ,zachisoni kwambiri ndi kumavomeleza umboni Obama.
Kkkkkkkk akut kunyindula kkkk Kom ndaseka
Kkkkkk this dc
Mmmmm nde ifeyoo tiinve ziti bwana?ingopitan mukafufuzetu inuwo😢
Namayenda😂
😂😂😂😂
Amene..walemba title ya PROFILE IYIYI UMUWUZE PANTUMBo PAKE ET...thank U
Iwe pita Kaye kusukulu izizi wachepa nawo akutuma et
Tili ku Holiday 🥱
Zimatipweteka heavy
Its a pity thingz 😢😢😢
🎉🎉🎉🎉🎉🎉
IWEYO UKATI BON AMWALIRA UKUTANTHAUZA CHANI ZOPUSA BASI MUKASOWA MITU YANKHANI BILA OSAMALEMBA MUZINGOPONYA ANGAMUPHE KALINDO NDANI ? NDINU A MCP ETI
Chilungamo
Born kalindo atamwalira kumaona thupi Lake anthu mutha kumaseka kumati akupanga sewelo, chifukwa chilichonse amanena kalindo amalawi mumati drama
Km boni zakumasewelo zinja ndizoyamwila kd
Kuyakhula kukhala kopanda mphindu bola ndewo ndiyomwe ndikuiona ikhala solution yabwino
Khani kuyambira ku report ya ndege yakathera ku NRB nde ifeyooo mumafuna mutiiuze ziti kweni kweni
The DCs ndi one ndipo umatiimilira ndipo iwe uli pachilungamo ndipo zowona anthu ambiri sanalembetse
Kodi kuophanaku mwakutenga ngati mkophweka ? Kodi mumadana ndichilumo bwanji?
masiku ano sikuti munthu azikhalila mantha ano simasiku achipani chimodzi ichi musamaliwale aliyese Ali ndi ufulu kaya kutukwana puresdent palibe cholakwikka chifukwa ndi ufulu wake otukwana osati kuopsezana
Amalawidi koma commission yatilephera
Atakupheni ndani Inu,kuti apindule chani
Zimatipwetekadi
Kkkkkkkkk pamenepo chitsiru mesa ndiweyo
Lipoti limene ukufuna iweyo ndilakuti chani kapena ukufuna anene kuti chiluma sanamwalire? Zopusa basi wafa wafa nasi zaziiii