I like the fact that samalimbana ndi anthu akanakhala wina akanayankhula zambirimbiri za anthu but he was more centered on himself. That's the spirit that we need
Makawa nd goat n he is so funny 😂 Waiting patiently for another badger n shout out to u Kev the way umachezera nd guest akabwera ur such an amazing person, keep the fire burning my guy, Madness inte10ment 4 life ❤❤
Nnali ndisanaonere pg imeneyi but Mbwiyacheyu ndi wambo Munthu oziwa macheza osalombana ndi anthu ena... Bwana Jah Kev inuyo i salute mumacheza bhooo ndima guest and can't wait for the next episode in the TRUTH or DRINK🎉 Akuti munatambako, mumatamba, nanga munapangako za ufiti, panopa ndiinu nfitibe?? Mafusowa anachema ka refreshment question yankho lake ndi Nyashi nzibambo anakondwatu apa lol😂😂😂😂😂
I like the fact that samalimbana ndi anthu akanakhala wina akanayankhula zambirimbiri za anthu but he was more centered on himself. That's the spirit that we need
ndipooo moyo uno ufunika anthu ngat amenewoo
I enjoyed this one😂 nsaname he is original he is him sakuchita zoti ine izi ine izi wangokhala mene aliri munthuyi🔥
Way he got excited when he was asked about the type of girl he likes 🤣🤣🤣
Been waiting for this video😂😂 the whole of this week
Makawa simunamufuse mowa omwe amayenela kumwa zikuonetsa kuti mwamumwetsa mowa wosiyana🤣🤣🤣🤣
😂😂😂😂😂 I have laughed like a mad person 😂😂😂 I like the show from Zambia 😊
15 minutes into the game and this guy is drunk already😂😂
6 shots, dude is drunk
"Akuti blezzer"🤣🤣🤣💔😭
Makawa nd goat n he is so funny 😂
Waiting patiently for another badger n shout out to u Kev the way umachezera nd guest akabwera ur such an amazing person, keep the fire burning my guy, Madness inte10ment 4 life ❤❤
The guy is drunk 😅
Ndavala from the bottom of my heart 😅😅 (Makawa 2024)
So the guy is now looking like this.... This is nice
Nnali ndisanaonere pg imeneyi but Mbwiyacheyu ndi wambo Munthu oziwa macheza osalombana ndi anthu ena... Bwana Jah Kev inuyo i salute mumacheza bhooo ndima guest and can't wait for the next episode in the TRUTH or DRINK🎉
Akuti munatambako, mumatamba, nanga munapangako za ufiti, panopa ndiinu nfitibe??
Mafusowa anachema ka refreshment question yankho lake ndi Nyashi nzibambo anakondwatu apa lol😂😂😂😂😂
Ha ha ha iiiih koma mbwiyacheee lithepo banjali 🤣🤣🤣🤣 munthu wamkulu kwambiri
Shot number 2 the guy is already in the mood, katundu uyuyu ngolemetsa.
Winatu adzasanzira pa table ukuku 🤣🤣🤣🤣🤣
Mwina zimachitika koma amangodula thru editing
@@nokuthulalenong mwinadi zikhoza kutheka.. chifukwatu a Makawawo ndiye anayaka kuposa aliyese 🤣🤣🤣
This guy 😂😂😂😂zikafika apa timati macheza asintha😂😂😂
Who's watching it right now
Chizungu chayambika!😂😂😂
At least he's putting that alcohol to good use😂
😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂koma ndaseka mpaka misozi iiiiiii makawa ndi chi vibe
When the interviewer is interviewed 🥰
More 🔥🔥🔥 makawa komano uyitaneso gwaladi pls
Next gwaladi Mr jaa Kev❤
Kani Moses Makawa analowamònso mkalasi? Nice to hear this
Komatu ku CCAP sitimwa mowa😂😂😂😂 ndiposo Moses 😊mumutumo wasiyana pati ndi Jkelvn
Watching from Moçambique
Makawa Moisés eeeeee akuoneka bomtu
Makawa uja kunooo ndakomoka ndikusek 😅😅😅😅😅😅
Lets do a truth or drink challenge yama fans..... Am in😂
Mowa anakonza..komabe those signs eeeee are something 😊😂😂😂😂
Ndpo sure inetso ndatutumuka naye Kalipo amatathauza eish dziko
Lero nde wayenda Ali m'manja m'manja mbwiyache .big up yourself kkkk
"Iwe tasiya chimowa chakocho", Mbuyache anatheka😂😂😂😂😂
Mwadziwana etiii. Mpaka sign ✌️. Mwadzindikirana eti
Madness yomweyo 🔥🇲🇼
Jaakev mpaka wayamba chibwibwi atangomva zot amatamba😂😂
😂😂😂😂😂
I like this one🎉🎉🎉
😂😂😂😂😂😂 ATI tichenjere mafunsidwe mwina mutha kutipeza nthawi inayake🤣🤣🤣
😂😂😂zasiya kumvekatu makawa
Mbuyache wadwalikatu ndi nkunda wa Gin 🔥🔥🔥🔥🔥
Zikuoneka kuti makawa sanalezele koma ada akumfutsa makawayo ndi amene alezela kkkkkk😂😂😂
Truthfully speaking truth or drink koma iyiyi 😂😂😂😂😂 ndaseka through out 😅😅😅😅😅
Moses was the last part necessary 😂😂😂😂😂😂
That's madness🙌🏾🤣🤣🤣
Mowa ndi chizungu zimayenderana kwabasi😂 ayayaya
Ndipo ukalezela mpamene timabomba stick ward timabwera from no where kkkkkkkk
Makawa mumandivetsa kukoma nyimbo zako ziri ndi matamdauzo
Mafuso ako ofuna mbuyache aredzere et!!!! More 🔥🔥🔥 makawa
Mbuyache akuchita kuyankha mwa confidence ngati akukhonza 😂😂
mukati muziti mano mbe eh mutha muona 😂😂😂
Ngt akuonetsa ma sign amenewo pa camera what more padima kwaoko😅😅
There's a good reason why they call it SPIRITS that kind of drinks 🍷
Kkkkkk sir of the year🎉 koma kev makawa simunthu wamba wav end sungamupusitse kkkkk
Makawa. Sorry si fatar uyu akukomolatu 😂😂😂
Aaaa makawa, ndiosekesatu hevy komn ndi guy wa bhoo otha kuchedza, i like hilm😂😂😂😂😂😂
I didn't know about you guys but you're gud,very very very gud.
Next Joe gwaladi please
Factsss
😂😂kuzabebatu
Iiih uyu azativuta uyu, azizangotukwana
uyu ayi.uyu
Koma kungavutetu
Jaa keV nawenso ukufunika truth or drink 😂😂😂
Love Jakev’s vibes on this show!
😂good interview...koma akuselewesa mowa
Ndungoseka ngati chitsilu😂😂😂 aah Makawa amabeba akaledzera😂😂😂😂
Madness ❤❤❤❤❤❤
Kodi anabwera atayaka kale coz 11minutes waledzera kale😂😂😂😂
Ine interview iyi sindimayevetsa ai mumapangitsa kuti anthu adzidzamwa mowa or kuti chan kwen kwen
Anthu amayenera kuyankha mafuso
Madness I like this program since day one (one love from 🇿🇲🎧)
I like this program
Tinakusiyani kuti muzionera nokha kujaku
Koma tiulawe kaye eeeh..
Tiulawe kaye ..
Tiwulonche eeeh
Tiwulonche..
😂
Aaaah uli bhoo
Jaakev unapilikitsa wama sox obooka apa wachifuwa😂😂🤣
😂😂😂😂😂😂 Akuti zikhale ng'oma kapena ma drums.😂😂😂
Wachibwana, that's why Kev pretended ngat sanamunve
Gin maulemu ake 🙌🙌😂😂
Jaa kev fans let's gather here.
Mwana opepuka wayaka kale kkkkkkkkk any way watinvesa kukoma big up
Anthu enawa amakhala angofuna kumwa mowa... manga kukufusa ndiwe okwatila mpaka kumwa
Munthu nadziwa ine makawa sangamalize Malawi gin ekha.osamayesana.enawa muziwagulira caster
Infact Makawao ndimfana wabhoo salimbana ndi anzake bg up fada
Kod mkhani zogonana zimavuta kuyankha bwanji?
@jaakev, kod nginiyi singamAKHALE LIVE??
Ooooh tayambaso kuyankhula chizungu hahahaha chiyankhuleni mbwiye
English 😂
Kodi apapa akupanga interview nzake ndi ndani??
Akut 😂😂😂 Zonse zimene mukamba apapa nzaboza
Koma Mowa😂🔥👀
Guys munthuyi anayaka😂😂😂
Ase Kev ada awawa akuwonekazosutatu 😂😂
😂😂😂😂Makawa ndi shasha ati blezzer😅😅😅😅
Mukhaulitseni Makawa ayende wa uyouyo.
Mumfusekonso za atsamunda
Guys for your end of interview potambapa pandipeza bwanji 😅😅😅it's like 2 answers the moses umatamba 😂😂😂😂
Umakwana Jah keav ❤️🔥🔥
Kodi wabwela atayaka kale?
Makawa ati chani kod 😂😂😂😂😂
Macheza abwino kwambili 👍🤝👍
Now I know the meaning of legend that ndioimba wa mkulu
Do they eat before they come to live show Bro?😂😂😂😂😂😂🎉🎉
Shot waiona tsopano kuti ndi kamtondo....gin waeletsa mmaso😂😂😂
😂😂 ndisekeretu , simmene kulilitu
Moses mumfusa bwanj za Lucius Banda anali asanabadwetu🤣🤣🤣
Malawi Gin simadzi😂😂😂 school fees imaoneka pomwe inapita
Mowaso ndimankhwala achizungu 😂😂
Koma interview iyi ndiyokoma eeee makawa akukometsa kuno😂
Nonse Church antha kukuthamangitsani 😅😂😂😂😂😂😂
Next please abwere Joe Gwaladi
amoyaeeeh achimwene iiiih alongoawo amayiawo njala nchilombo kkkkk 🤣😁😂🙌
😂😂😂 moses makawa sopano ....
Koma ana mmawaphunzitsa chan 😂
😂😂😂😂 mbuyache fire mabomba trying to invite Lulu next