Ndizona mavuto a ku malawi amawoneka ngati ndi anthu okhala ku malawi km olo anthu amene anatumiza ana awo kunja Ali pa mavuto kopya kwambili chifukwa mavuto akula kwambili mabanja ambili nkhan ndi njala yavuta ngati muziko misonkho sapeleka ku boma mwalo mokoza malawi km kuba ndalama bas
Mbusa uyu dzina lake Chakwera wationongera Mother Malawi.. .Full stop.....Bishop more Fire 🔥...Auzeni amenewo ❤
Agalu awa atitopesa ndipo atibwelesela mavuto..
Chakwera azipita basi ndi mbuzi ya munthu imeneyi
Ichichi sichikuumilatu mau 😂
chakwela ndi president ochitisa manyazi kwambili ndikumuvera chisoni kwambili lazaro kunama abusa aja ai ai kunama chakwela
PAC yachedwa kwambiri
Mwaziona liti aPAC?komatu takhala tikukudandaulilani nthawi yaitali munangoti ziiiiiii .Pano mwabwela bwino.
Ndizona mavuto a ku malawi amawoneka ngati ndi anthu okhala ku malawi km olo anthu amene anatumiza ana awo kunja Ali pa mavuto kopya kwambili chifukwa mavuto akula kwambili mabanja ambili nkhan ndi njala yavuta ngati muziko misonkho sapeleka ku boma mwalo mokoza malawi km kuba ndalama bas
Chakwera alikunamiza mutundu wa a malawi ndipo alikunamiza Mulungu chilipo atuluke muboma basi
Koditu apuresidenti sangayankhule chilichose chonkhuza katangale chifukwa achakwelawo ndinamba Wani wakuba kuposa Wina aliyese
😂 True
Akutitu ndi a price of corruption😂
@@MeliaMichael 🤣🤣🤣 Mcp aaa basi man izipita kkkkk
Chakwera 😂😂😂😂😂😂😂😂
You spoke over the introduction sitinamve
HlS exllence professor Peter muthalika
The president of the republic of MALAWl 🇲🇼🇲🇼🇲🇼 2025 to 2035
Vuto la chakwera sakumva munthu uja olo kumuuza, akukhala ngati ndi nkhutukumve
Kuteroku anthu akakhala ali pa udindo ndye akulakwitsa ndi iwo eni kudzipanga kafukufuku coz amadziwa kut choipacho chikuchokera kwa iwo ndye ndikovuta kuyimbidwa kapena kudzimba mulandu wokha
😂😂😂😂MCP WOYEE ALI PAULENDO! 😂😂😂😂
Ulendo wake utio?
@@kingsleymacheza Opita ku Kasiya 😂
MCP yotopesa September pa ulendo
a PAC si odalilika cuz 4 years anali chete osayankhulapo kanthu pazovuta zomwe amalawi akumana nazo yet maboma mbuyomo ankaonekera patari then lero adzibwela ngat tili limodzi Kumati bwezi lawo aliwunikire zopusa kumatenga anthu kufoila
Chakwera amamva komanso kuona PA social media koma vuto ndiokula mtima that is why amayankha mafutso mowilingula not directly
Mcp mmmmm sidzatheka akanawina mosavuta km mmmm akudzipanga decampain okha
Chakwera ndi chisilu anango kula mtima
M'khulu uyu zakugawa makondomu