NKHANI ZALERO CHIPANI CHA UDF

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 20 січ 2025

КОМЕНТАРІ • 24

  • @SylvesterSululu
    @SylvesterSululu 16 днів тому +1

    Kkkkkk koma thumba lachimanga kod awa ndipaubale ndi chakwela eti kkkkkkkk koma bomba lachakwela ndi la mafiyad

  • @AdamKay-q1l
    @AdamKay-q1l 16 днів тому

    Atupele ❤❤❤ don't give up

  • @MdokaJames
    @MdokaJames 16 днів тому

    My vote atupele Muluzi 🎉

  • @PrinceChapola
    @PrinceChapola 16 днів тому

    Eeeee komadi osati osankhawo alakwisa akanakhalatu pita munthalika ndiye zamunyasatu pajatu amafuna zabwino zonse zikhale zake kkkkkk koma atupele zabwino zonse

  • @GiftBello-v1i
    @GiftBello-v1i 16 днів тому +1

    Vote for Atupele honestly leader

    • @SliviaJosephy
      @SliviaJosephy 14 днів тому

      Za ziiiiiii mupite,ku machinga,nselema mukafunse kuti 20,, years pa MP anapanga chani ,,mbavayo ine sindingachivotele

  • @NgomaRaheem-k2t
    @NgomaRaheem-k2t 16 днів тому

    Mkulu ameneyu ngopusa ndithu chimanga mkachaniso

  • @HerlbertKaalis
    @HerlbertKaalis 16 днів тому

    Atupele ndi mtsogoleri wa mphavu ndipo ndi bwino ayendele limodzi ndi APM adadi chiyembekezo cha AMALAWI ndi inu.MCP.....Chikangawa ndi yakuphaaaaaaa!!!!!!!

  • @Eric-gb9ms
    @Eric-gb9ms 16 днів тому

    Zoona munthu wathawa kundende ine ndiwulule zoona ndimusiya kundende simalo

  • @MartinsilverChirwa-fv9wn
    @MartinsilverChirwa-fv9wn 16 днів тому

    For Atupere I'm saying congratulations

  • @AndrewChimunzu
    @AndrewChimunzu 16 днів тому

    Zaugalu kugwila akaidi kulipila chimanga

  • @DanielJuwawo-s5n
    @DanielJuwawo-s5n 16 днів тому

    Asowa zonena iwowo akulandira ndalama iwe adzikupatsa chimanga basi kuonana kupusa bwanji

  • @WisemanChima
    @WisemanChima 16 днів тому

    Zopusa bwanji inu ndi agalu

    • @Eric-gb9ms
      @Eric-gb9ms 16 днів тому

      Galuyo akuwoneka ngati iwe amene so it means nawe ndiwe galu

  • @AfyawylessKachepa
    @AfyawylessKachepa 16 днів тому

    Ndachibwana mkaidi at tizimtaniii? Aaaa azipanga onga zmnz akutifunira zabwin km iwoo

  • @AWARIBLACK
    @AWARIBLACK 16 днів тому

    Tikorola bwanji popanda fetereza palibe kutiuza zachibwanazo

  • @YAKOBEMAGANA-oe5hd
    @YAKOBEMAGANA-oe5hd 16 днів тому

    Wathawa wathawa basi anthu akuba m bomamu anivulaze chifuka cha 50kg yachimanga

    • @Eric-gb9ms
      @Eric-gb9ms 16 днів тому

      😂😂😂😂😂😂😂 komatu

  • @ChiefJustin-l5p
    @ChiefJustin-l5p 16 днів тому

    Tumba la chani? 😂

  • @Bashir-s8s
    @Bashir-s8s 16 днів тому

    Kkkkk

  • @AkweniHafule
    @AkweniHafule 16 днів тому

    Tizimuthandizira kuthawa wapurumuka ameneyobas

  • @MartinKapanga
    @MartinKapanga 16 днів тому

    munthu zoona azigwila munthu othawa Ku ndende pomwe azisogolili pomwe akuba ndalama zambili Za chamba zimenezi mugwilise nchito njila ine

  • @AkweniHafule
    @AkweniHafule 16 днів тому

    Zopusa bas