Mkangano wa Kamuzu Banda ndi Samora Machel.

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 18 жов 2020
  • Udani komanso chimkulirano pakati pa Kamuzu Banda ndi Samora Machel.

КОМЕНТАРІ • 253

  • @chifundoveluwa1184
    @chifundoveluwa1184 3 роки тому +18

    Samora machel was a hero that's why his statue can be found in many parts of the world.

  • @mr98556
    @mr98556 2 роки тому +9

    Imagine learning the history of Kamuzu from Bakili Muluzi News Channel...This is ridiculous

  • @MaryKana-vt3hc
    @MaryKana-vt3hc Рік тому +2

    One great. Statement by Kamuzu was: I don't mix politics with economics. Hence Capital Hill and many other developments!

  • @djmakedzana9917
    @djmakedzana9917 3 роки тому +5

    Brown Mpingangira anali Chief Informaion Officer, atapita ku Zimbabwe anakumana ndi anthu matchona kumufunsa kuti ku Malawi kuli bwanji ? anati ku Malawi kuli njala , chimanga akungopasa a RENAMO. sanadziwe kuti anthuwa anali ma spy a kamuzu. Pobwera kufika pa Chileka anafikira unyolo

  • @aidaomicaia2430
    @aidaomicaia2430 3 роки тому +6

    Good history, so amazing .

  • @osamabinraden9391
    @osamabinraden9391 3 роки тому +4

    🙋🙋🙋 👏👏 mbili ilibwino👍👍👍👍👍👏👏👍👍👍👍

  • @francismsowoya278
    @francismsowoya278 3 роки тому +6

    To tell the truth, K. Banda did great things in Malawi. Most infrastructures which use today were done by him. We usually remember bad things someone did to us and not good ones. Even now people are killed because of political motivation in all states of Africa and the entire world.

    • @charlesmuyaya8839
      @charlesmuyaya8839 3 роки тому +4

      Which infrastructures Kamuzu build? Ma infrastructure ambiri adamanga anali atsamunda koma umbuli ndi omwe ukukuchititsa kuti uziganiza mopusa choncho. Queen Elizabeth central hospital, Blantyre high court, Zomba central hospital, dedza secondary school, malosa secondary school, Blantyre secondary school, natural resources college, domasi TTC, Soche TTC, polytechnic college, ma community day secondary schools around Malawi, maofesi a agriculture Ku Lilongwe, nsanje, mulanje, thyolo, Zomba,mangochi, mzimba and so fourth. Zonsezi adamanga anali atsamunda not kamuzu. So don't be a fool

    • @duncanchizizi6543
      @duncanchizizi6543 Рік тому +1

      Kamuzu anali munthu woyipa basi

    • @lucaswhite4279
      @lucaswhite4279 Рік тому

      @@charlesmuyaya8839 P

    • @ahmadjamahiryajuma6456
      @ahmadjamahiryajuma6456 Рік тому

      Kamuzu adapanga adopt zomwe a Zungu adapanga.
      Komaso zomwe a Zungu Adayamba Iye kumati wapanga ndiiye.
      Kamuzu adali oipa

    • @dhaoudhiabedinegomaseko2363
      @dhaoudhiabedinegomaseko2363 Рік тому

      You know nothing

  • @sidickbadat1086
    @sidickbadat1086 2 роки тому +3

    If Kamuzu was still alive and ruling Malawi 🇲🇼 all these corrupted politicians and Indians wouldn’t stand a chance.

    • @juliusnkhoma755
      @juliusnkhoma755 Місяць тому

      Mwinaso anakakudyeserani ku ng'ona inuyo

  • @aubs4321
    @aubs4321 3 роки тому +8

    Kamuzu anali oipa koma pa nkhani iyiyi he was right, do you think Malawi would be as it is without RSA providing the grant to build Lilongwe?
    Kamuzu was not backing the whites but
    1. he believed dialogue was the best remedy to sort out the apartheid issue osati violence.
    2 he was advancing his own interests for the sake of developing Malawi.
    3. Those years after independence Malawians lacked skills to run the govt that is why Europeans were still employed.
    Documentary iyi wapala aise try not to take sides

    • @africulturetv6498
      @africulturetv6498 2 роки тому +3

      Man bodza inu what was the point of getting independence while not knowing how to deal with it
      How can you get independence kenako nkuma sapota chitaganya cha mayiko ena zazi

    • @khodotech6481
      @khodotech6481 2 роки тому

      Good

    • @elliotchisalanga12
      @elliotchisalanga12 2 роки тому

      Wapala uyu Zina angolankhulapo

    • @duncanchizizi6543
      @duncanchizizi6543 Рік тому

      You are the one not making sense. We wanted to remove white rule in order to run government on our own ...we fought whites. Why did kamuzu support white rule in another country?

    • @juliusnkhoma755
      @juliusnkhoma755 Місяць тому

      Point number......it requires two parties to do dialogue....south Africa inaona ndipo idakaona khaza za azungu....what dialogue would you do pamene ukupandidwa ndikuphedwa chifukwa ukushala pakwana and you want you person space??
      2. Point yachiwiri....kod what was the fight those days ?? Ngati mukuziwa the Zina zoyenera kusapota azungu?? Kod inu mukafuna kutukuka zimatathauza kuti enafe tifinyidwe ?? Mwina munatero kwanuko zikhale choncho....
      3. Kod Angwazi ankaxiwa chomwe amafuna kapena ai.....John chilembwe ndia mazana mazana achikuda anaphedwa ndi kuzizika ndi white regime.....mumaiziwa slave trade?? Mukazavesesa zomwe a2 anaona kuli azungu muzavesesa kuti mzungu sanali m'bale koma yes it's ok to use two or three abwinowo koma azungu akamuzu ubwino palibe chifukwa amamugeirisa ntchito ngat puppet.....u can Google meaning ya puppet kuti mumvesese

  • @bkelly3053
    @bkelly3053 3 роки тому +6

    kamuzu he was not malawian

  • @user-ll7hz7uy3q
    @user-ll7hz7uy3q 9 місяців тому +1

    Komatu Mozambique inatengadi malo ambiri ku Malawi

  • @chimmukono7102
    @chimmukono7102 3 роки тому +11

    Kamuzu was genius
    He was choosing them just to make things work in Malawi
    He knew how we think and how we can easily destroy

    • @juliusnkhoma755
      @juliusnkhoma755 Місяць тому

      Ng'ona ku Stella Maris, Young Pioneers, gwirizano ndi apartheid.....ma card, kupha omuzuzula, kusokoneza ku Mozambique......kupondereza ufulu wa2..... education system yovutikira ....nzeru mukuzitama ndiziti ??? Most of chitukuko anachipeza and he stayed unchallenged for 31 years ...

  • @mrmustdeDj
    @mrmustdeDj 2 роки тому +1

    Koma the narrator si munthu wamba..🙌🏿😂..white people in public sectors was ideal..that’s why Forex wise tinali nyatwa

  • @oziledambula9107
    @oziledambula9107 3 роки тому +4

    Kamuzu was sellout just imagine nkhaza zonse zinkachitika zija

    • @jonathancox4189
      @jonathancox4189 3 роки тому

      But there was no rapes,murders,uchigawenga ,we were united one Malawi. I am glad the MCP et Al will revive those sweet old days.

    • @juliusnkhoma755
      @juliusnkhoma755 Місяць тому

      ​@@jonathancox4189 pena zimachita kudabwisa kuti history yosabisika ngati iyiyi mu2 ukaime pachulu kubakira kamuzu ati kunalibe murder .....mwatani kodi ???

  • @najereeliya7761
    @najereeliya7761 3 роки тому +3

    This is amazing

  • @patumaabiti2415
    @patumaabiti2415 3 роки тому +5

    Ada awawa mukuti a Kamuzu anali chigawenga

  • @timeyomzumala
    @timeyomzumala Рік тому +1

    Kamuzu anali wa nkhaz.this story is good

  • @adamkaisi6954
    @adamkaisi6954 3 роки тому +3

    Indeed Kamuzu was a doubtful President, not even one day he surprised the Malawians by speaking the vernacular .he gave influential posts to whites in his government
    Good research brother

    • @botaclive5898
      @botaclive5898 3 роки тому +3

      Kamuzu spoke tumbuka fluently

    • @mwai72
      @mwai72 2 роки тому

      There is no research...this is not even history...this is done at a slant AGAINST Ngwazi. From his early days Ngwazi would speak for minutes about how the Bible has been translated poorly into chichewa. He spoke the real chichewa, cha ku central region. This is propaganda...Mandela would later say "Kamuzu was right" look it up!

    • @sydneynyirenda7745
      @sydneynyirenda7745 2 роки тому

      We shall not have as patriotic a president as Kamuzu was. Unlike our neighbours, our country was the least developed at the time of our Independence and it was Kamuzu who kick started development from scràtch.

    • @duncanchizizi6543
      @duncanchizizi6543 Рік тому

      @@botaclive5898 which tumbuka? Tumbuka he banned?

    • @juliusnkhoma755
      @juliusnkhoma755 Місяць тому

      ​@@sydneynyirenda7745aaaaaa koma mavuto tili nawo ndi2

  • @brianmwizagondwe1321
    @brianmwizagondwe1321 3 роки тому +2

    If I was Kamuzu, I kamuzu have allied with SA as well. Samora was a threat to Malawi..

    • @duncanchizizi6543
      @duncanchizizi6543 Рік тому

      Kamuzu was a puppet to the white imperialism. He was a hypocrite

  • @perlinsmhone5472
    @perlinsmhone5472 3 роки тому +3

    He did very well to grow the economy. Forget about those who killed during his term. It is happening even here in S.A. people are killing each other due to politics. There was no hunger in his term.

    • @duncanchizizi6543
      @duncanchizizi6543 Рік тому

      My friend kamuzu was a dangerous killer and dictator. That can't be taken away. Malawi was not free

    • @juliusnkhoma755
      @juliusnkhoma755 Місяць тому

      Pilizi tamafufuzani bwino mbiri ya dziko lanu

    • @ManuelKhefasi
      @ManuelKhefasi 15 днів тому

      If we could need development we could leave the whites to govern but we fight for peace osati zitukukozo pambuyo zimenezo koma kupulumusa miyoyo

  • @brianmwizagondwe1321
    @brianmwizagondwe1321 3 роки тому +3

    So kamuzu knew that the dude was dying in 2 weeks time. Dzikoli chinachilichonse ndi ndale

  • @mrmustdeDj
    @mrmustdeDj 2 роки тому +3

    Ati kamuzutu anali chigawenga 😂🙌🏿

  • @isaacbanda2973
    @isaacbanda2973 3 роки тому +4

    Kamuzu Banda just wasted our time and inali mbava cause when amkamwalila Anali 22 billion kwacha just imagine

    • @yobembewe7078
      @yobembewe7078 3 роки тому +1

      You don't what you are talking about.

    • @jaffarzacharia9011
      @jaffarzacharia9011 3 роки тому

      kamuzu anali ofoira

    • @kwangujaidi1020
      @kwangujaidi1020 2 роки тому

      I would agree, this guy was very rich and his people still have it komaso kunalibe omufufuza chuma chake ndiye anali mfulu wathe!!!!

    • @joebrown1158
      @joebrown1158 Рік тому

      Kamuzu was wealthy of 422billion chakwa you people you need to do more research

  • @charlesmbale7739
    @charlesmbale7739 2 роки тому +1

    Kamuzu Banda is the one who was supporting Mugabe financially.... Mugabe once mentioned this even KK mentioned the same at SADC summit in Namibia which former head of states attended. ...

  • @modiejonathan8547
    @modiejonathan8547 3 роки тому +5

    Your enemies are not my enemies.

  • @jaffarzacharia9011
    @jaffarzacharia9011 3 роки тому +3

    Kamuzu was a sellout

  • @ernestmkanthama7329
    @ernestmkanthama7329 2 роки тому +1

    Kamuzu amakatukwana azungu man

  • @user-rf4br1fv2z
    @user-rf4br1fv2z 3 місяці тому +2

    Pena a big ma history anuwa muziwatenga bwino zina zomwe mumanena za ku Mozambique atati adzikuvelani kuti kamuzu adapha samora kodi mumadziwa tikhoza kukhala pa mavuto akulu zina zimafunika kuziona bwino koma mumadziwa zithu zambiri timalandilila ku Mozambique ifeyo tilibe port yolandilila please think b4

    • @ManuelKhefasi
      @ManuelKhefasi 15 днів тому

      Mmmm sananenepo kuti kamuzu anapha samora ayi koma he sayed he was support Portuguese instead of samora and this is well known in Mozambique ndipo Amadana kwambiri ndi Malawi especially Mcp , , , , amangobwexa moto pang'ono pozindikira kuti kamuzu amazunza ngakhare amalawi anzake komanso sadari Mmalawi , , , apo biiii ukanaona bwezi ataiyambisa kale

    • @user-jc7uw8sh5i
      @user-jc7uw8sh5i 6 днів тому

      Who doesn't know in Mozambique kuti kamuzu had a hand in samoras death,,, history simuyisata inu

  • @djmakedzana9917
    @djmakedzana9917 3 роки тому +1

    1986--1988 Kamuzu appointed Hans Joachim Lesshaft as governor of the reserve bank to replace Chakakala Chaziya. Chaziya anamangidwa koma boma linalengeza kuti wapita ku school

  • @user-xj2mt8dj6t
    @user-xj2mt8dj6t 8 годин тому

    abale mcp yomwe ija zikuonetsa kuti ilipobe siizi zikuchitika panozi chipani chakupha anthu komanso chili ndi zigawenga zoopya zomwe zinagwetsa ndege muchikangawa

  • @asiyatumilera7349
    @asiyatumilera7349 3 роки тому +5

    Kamuzu Banda was a traitor

  • @innocentmpoto
    @innocentmpoto 2 місяці тому

    Great job Mr

  • @StanleyWachazaBanda
    @StanleyWachazaBanda 9 місяців тому

    Africans, let alone Malawians, are adventurous they have and still continue to travel to South Africa even before Africa started to gain independence and Dr Banda knew that Malawian being landlocked country we needed South Africa to access their ports. He believed in contact and dialogue and not boycott and isolation. When he went to South Africa, he challenged them that you white people you were under Roman Empire for ages and do you think these Africans will want to be under you forever. He even advised
    UNGA that you can not be talking about South Africa when there was no delegation from RSA. For your information Dr Banda supported ANC that the more reason when .Mandela was released he came to Malawi and other countries to acknowledged the support. Mugabe sought refuge in Malawi when he was fighting with Smith.Dr Banda was a freedom fighter. Malawi Zambia Zimbabwe when they were fighting for independence and went to England with Kaunda Joshua Nkomo Dr Banda was their spokesperson. Mozambique Zambia and Zimbabwe opted for boycott and isolation during the day while at night they were eating food from RSA Dr Banda didn't subscribe to this way of thinking

  • @edwardnsapato8840
    @edwardnsapato8840 3 роки тому +2

    Aluta Continua!!

  • @gesusgegangphray7689
    @gesusgegangphray7689 3 роки тому

    Mwambetani, kanyama chiume was helped with my own father in njombe Tanzania. Bishop aipa was kamudzu agent i know all the secret meeting.. but bishop aipa dint betray kanyama chiume,

  • @duncanosman10
    @duncanosman10 3 роки тому +1

    Mwatitsukula mmaso maka za Samora ndi Kamuzu

  • @mosesgeorge9016
    @mosesgeorge9016 3 роки тому +1

    During Kamuzu Photocopiers were not in Malawi. Tamanenani zoona. I think narrator was not even born.

  • @abdulrafiquekalembo469
    @abdulrafiquekalembo469 3 роки тому +3

    The story could be true at some point but my advice to the narrator is that are some stories that are so sensitive,secretive for the safety of the nation.ngati izi za ubale wa Mozambique ndi Malawi.that story is sensitive

  • @motomoto5588
    @motomoto5588 3 роки тому +2

    Koma kuno kumbali Kamuzu Banda ndi Galu

  • @ishmaelhero6160
    @ishmaelhero6160 3 роки тому +2

    kamuzu anali wakupha basi
    mzungu wausilu...

  • @alexanderkaunda9554
    @alexanderkaunda9554 3 роки тому +3

    Kamuzu amadya chamba moipa ndikumidziwa

  • @promisekwenda4556
    @promisekwenda4556 3 роки тому +5

    Kamuzu wachamba bas

  • @kingstonephiri5495
    @kingstonephiri5495 2 роки тому

    Please try to take out the background sound most sound like this comes from our country video only it’s making noise

  • @danielkhinguirossejuliasse6106

    Malawi ndi Mozambique sadzamwerana madzi mpaka kare
    Komasso tidzangolanda dziko lamalawi kukhara provincia ya 11 kuno kumozambique

  • @charliepoulaliecky5687
    @charliepoulaliecky5687 3 роки тому +1

    Kamuzu banda sadali Mmalawi ayi ndi chifukwa chake anthu ambiri akumalawi adalikuzuzidwa

  • @snathan99
    @snathan99 Рік тому +2

    Kamuzu, the father figure of Malawi, you will never erase this history whether you like it or not...

  • @joebrown1158
    @joebrown1158 2 роки тому +3

    Just in short Kamuzu was not Kamuzu from kasungu that one was from Ghana his real name was Richard Armstrong his father was an American, his mother was a Ghanaian.

    • @adam6kazembe642
      @adam6kazembe642 Рік тому

      A theif

    • @mcandrewsmaunda7921
      @mcandrewsmaunda7921 Рік тому +1

      We care less about that.We care more about the fact that he did a lot for Malawi

    • @joebrown1158
      @joebrown1158 Рік тому

      @@mcandrewsmaunda7921 What really more Kamuzu did that time by keeping people in captivity making people so much suffering is what you tell people that he did alot? How I old are you during the reign of Kamuzu?

    • @mcandrewsmaunda7921
      @mcandrewsmaunda7921 Рік тому

      @@joebrown1158 Yes.During his time, there were both good and bad things.We must acknowledge both sets of things.We must not be selective.You will find someone seating on a bus travelling on M1 that Kamuzu built but denying the fact that Kamuzu developed Malawi.I wonder what we should call that.

    • @mcandrewsmaunda7921
      @mcandrewsmaunda7921 Рік тому

      @@adam6kazembe642 Whatever!

  • @frankcassim
    @frankcassim 3 місяці тому

    Kmaso anachita bwino amozambeque kutilanda Malo ambiri

  • @zachariahlungu3577
    @zachariahlungu3577 2 роки тому +2

    Zikomo bwana

  • @madalitsomachira7477
    @madalitsomachira7477 2 роки тому

    Leaned where Malawi was and now is.

  • @basiliochiueteca6239
    @basiliochiueteca6239 3 роки тому +5

    Kamuzu Banda was a traitor and a liar, in a poor country being able to deceive his people and humiliate him like nothing would happen if his people lived together.

  • @isaacchipatala9143
    @isaacchipatala9143 3 роки тому +1

    Ndizoona zikachitika

  • @Lemankais
    @Lemankais 10 днів тому

    Kamuzu sanali wakumalawi

  • @AlexKaunda-ny2eg
    @AlexKaunda-ny2eg Місяць тому

    Kamuzu anali opusa ngati chakwera

  • @madakumanga4395
    @madakumanga4395 3 роки тому

    Mmmmm koma yah

  • @user-dn8pt4uz3q
    @user-dn8pt4uz3q Місяць тому

    Kamuzu anali wakupha🙌pano ali ku moto😅

  • @kuziririzaisabatosiitegeko7088

    Malawi idagali mumanja ya atsamunda!

  • @user-cl5pi4nb1e
    @user-cl5pi4nb1e 4 місяці тому

    Pano chipani cha MCP chasitha chikupha powapasa njala amalawi, kusapezeka makhwala muzipatala, kuba ndalama za boma katangale

  • @JamesChaponda-em7op
    @JamesChaponda-em7op 28 днів тому

    1971 Gaddafi was not president by then

    • @kingsleyhopematchaya5184
      @kingsleyhopematchaya5184 16 днів тому

      Akulu awa bodza mmmm ndiye afuna kt Mozambique itani pano chakwera ndi nyusi akugwrizana ndiye choyambitsa khani imeneye ufuna chiyani umuthu uyu alibe

  • @FutureBeatzStudioz
    @FutureBeatzStudioz Місяць тому

    He went their for the benefit of Malawi...

  • @simonchilala4138
    @simonchilala4138 Рік тому

    Like it

  • @chimwemwenkute3839
    @chimwemwenkute3839 Рік тому

    Aluta continuea

  • @johnkaitano5081
    @johnkaitano5081 3 роки тому +6

    ZIKUONETSA, KAMUZU SANALI MMALAWI
    analibe chikondi ndi Amalawi
    Satana anamugwiritsa ntchito kuika, amalawi mu mdima
    Inu mukunena, mbiri zotere PITIRIZANI Mulungu akusunge ndi moyo wautali kwambiri 👌👌👌👌

  • @siyaninansolo1375
    @siyaninansolo1375 3 роки тому +1

    But also I hear that Samora was targeted by Kamudzu banda & Nelson Mandela bicoz here in south africa there's a place called Samora where that airplane that was with Samora was attacked by those two president so can I get help on this so that I can over stand

    • @brianmwizagondwe1321
      @brianmwizagondwe1321 3 роки тому +1

      I think this was before mandela. I understand Kamuzu allied with the arpatheid government.

    • @kennethmagombo6934
      @kennethmagombo6934 10 днів тому

      Survival of the fittest is one factor that can keep you in a field of play for long.
      Ndale zimadalira kuganiza mwa ukadaulo. Sungachite ndale zopusa ndikumayesa Utah kutsogolera dziko.
      Kudziwa anthu akwanu ndi anthu okuzungulira umatha kusova zothekera mundale. Kamuzu ankadziwa bat an I lodinya kuti athe kutumiza uthenga mundale.
      Samabisala pachulu. Pachulu ukabisala ambiri amakuona. So, Kamuzu amalowa pa galaundi ambiri akuona... Dialogue and contact!!!!!

  • @josephmaster4367
    @josephmaster4367 Рік тому

    Continue

  • @catherinemtunga2259
    @catherinemtunga2259 3 роки тому +3

    Still Malawi was a better country to live in. We had all the good living standards. Kamuzu wa still a genius.

    • @charlesmuyaya8839
      @charlesmuyaya8839 3 роки тому +1

      Which living standards are you talking about? During Kamuzu azimayi ambiri ankaberekera kwa azamba, ana ankanyentchera chifukwa cha kusowa zakudya, there was kwashiorkor, marasmus in the villages. Anthu ankadalira ma missionary schools,Kamuzu failed to build schools and hospitals in Malawi. Ma secondary school a boma amene analipo were built by colonial govt. Look at domasi college, natural resources college, polytechnic college, malosa secondary school, soche technical college, mpemba administration college, dedza secondary school, Blantyre secondary school, Zomba central hospital, queen Elizabeth central hospital, chichiri stadium zonse ndi zitukuko za atsamunda. Ndi chani chimene Kamuzu anamanga for 31 years? Ambiri mmanena zitukuko za atsamunda because you know nothing about it.

    • @danielmaluwa7896
      @danielmaluwa7896 3 роки тому +1

      Kamuzu was very cruel and bad. He didnt nothing in this country except stealing 250 billion kwacha

    • @kannandhanukkodi8548
      @kannandhanukkodi8548 3 роки тому +1

      Very sad that malawi was ruled by a foreigner who was more cruel than a wild animal

    • @duncanchizizi6543
      @duncanchizizi6543 Рік тому

      There is nothing like good living standards. Kamuzu was a dictator and killer . He was selfish too!

  • @NJELEKA
    @NJELEKA Рік тому

    Kamuzu was a destroyer and he made most of Malawian not to have freedom in other countries

  • @jackson866
    @jackson866 Місяць тому

    You don't know the politics of Kamuzu Banda very well he was ahead of his time. While Kamuzu was working with the white South African government for economic reasons openly in the day he was helping the ANC privately at night. Many of the ANC soldiers used Malawi passports to go to Russia where they were trained to fight the Apartheid government. That's why when he went to SOWETO in RSA he was received like a hero, they knew how he was helping them with the mabhunu's money. I know this because I was in the system. Ndale za Kamuzu simungazimvetsetse mwachepa nazo bambo musanamize wanthu. Kamuzu ananthandizana ndi Kenneth Kaunda wa ku Zambia ndi Joshua Nkomo wa ku Zimbabwe kulimbana ndi a tsamunda kuti maiko amenewa alandire ufulu, Mugabe mukutchulayu asanabwere. Zina mukulondola koma zambiri simukuzidziwa. I remain.

  • @FidelisNthenda-qq5sg
    @FidelisNthenda-qq5sg 6 місяців тому

    Zaubwekabweka 😂😂😂

  • @patrickphiri5334
    @patrickphiri5334 3 роки тому +1

    Very sad history indeed

    • @princemanda2642
      @princemanda2642 Рік тому

      Fake story

    • @duncanchizizi6543
      @duncanchizizi6543 Рік тому

      @@princemanda2642 nothing is fake here chief . Kamuzu and mcp killed so many people in malawi. We can't forget

  • @rodglae6657
    @rodglae6657 5 місяців тому

  • @cphiri8035
    @cphiri8035 3 роки тому +3

    Wa khuta mgayiwa uko nkumakamba zopusa pa media tandi tchulile present anachitachitukuko kuposa kamuzu

  • @gesusgegangphray7689
    @gesusgegangphray7689 3 роки тому

    I cant give u my name .. but i schooled in malamulo benson ligenda time... Malawianí get ready of me. I will save u from man-made poverty. And musiye kulozana and truating asing'anga.. we will change first this.. i know I every 2 malawian 1 trust nyanga ...how many mukufuna chitukuko

  • @JamesMuhango-yd3ie
    @JamesMuhango-yd3ie Рік тому

    Yes kamuzu anali wawupandu

  • @BornwellNurd
    @BornwellNurd Місяць тому

    Sharp

  • @user-jf8zt3pe8p
    @user-jf8zt3pe8p 4 місяці тому

    Mmmmmmmmm

  • @chancyshaba3664
    @chancyshaba3664 3 роки тому +3

    Nice one

  • @modiejonathan8547
    @modiejonathan8547 3 роки тому

    Kamuzu amalankhula chichewa

  • @donaldj.kufankomwe1254
    @donaldj.kufankomwe1254 Рік тому

    My dear, ideology difers. Never think that the way you think others will think in the same way. Appreciate differences.

    • @duncanchizizi6543
      @duncanchizizi6543 Рік тому

      Zomwe akunena apapa sikuti ndi opinion kma ma facts. Ndi zomwe kamuzu amapanga. Records are there. Kamuzu was a serial killer and dictator

  • @user-pg9yl8jq8p
    @user-pg9yl8jq8p 9 місяців тому

    Thats it

  • @AnishaMoosa-ej7yr
    @AnishaMoosa-ej7yr 7 місяців тому

    Chipan choipa

  • @AnishaMoosa-ej7yr
    @AnishaMoosa-ej7yr 7 місяців тому

    Is not Malawian

  • @user-yt9gc5ur8b
    @user-yt9gc5ur8b 9 місяців тому

    Kamuzu was a hero

  • @mikewilzmphundi4927
    @mikewilzmphundi4927 3 місяці тому

    iwe ndiwe wabodza. besides Dr Banda being friends with RSA white gov. On the other side he was helping ANC. that guy was a genius. why are you giving out only negative info? za zii

  • @humbleyuzyx7150
    @humbleyuzyx7150 Рік тому

    May God gives him severe punishment where ever he is , Jonathan Smith was a bad person

  • @nyobomba
    @nyobomba 3 роки тому

    muluzi news indeed ... tell history non partisanly pilizi

    • @charlesmuyaya8839
      @charlesmuyaya8839 3 роки тому

      Zonse wafotokoza apa is a true story. The problem is you who thinks otherwise.

  • @laitonkamanga7679
    @laitonkamanga7679 Рік тому +1

    Samora Machel

  • @enwoodmlotha6318
    @enwoodmlotha6318 3 роки тому

    Kamudzu Banda was a British man his real name was Richard amstraw

    • @pachalojailoskincaidphiri4545
      @pachalojailoskincaidphiri4545 3 роки тому +1

      There has never been such a name as Richard Amstraw since....please do your search properly before u commit ur stories to platforms such as this.

    • @abdulmalikissah6979
      @abdulmalikissah6979 2 роки тому

      @@pachalojailoskincaidphiri4545 kamudzu was not real we are not Children, that guy was rechard and he hard British citizenship including the United States

    • @joebrown1158
      @joebrown1158 Рік тому

      @@abdulmalikissah6979 Richard Armstrong that was his real name all the way from America to Ghana his father was American and his mother was the Ghanaian people need to understand the biography of that man so called Richard Armstrong/ Kamuzu Banda the imposter

  • @alexanderkaunda9554
    @alexanderkaunda9554 3 роки тому +3

    Kamuzu sizinali zinthu

    • @smithsaidi9237
      @smithsaidi9237 3 роки тому

      Kunena zoona kamudzu Banda sanali was kumalawi

  • @lazaruskamangira8730
    @lazaruskamangira8730 Рік тому +2

    Three if not four positive things about Kamuzu's visit to RSA then 1, FREEDOM TO CHOOSE. He wanted a loan to build Capital Hill. He refused the IMF loan which comes with conditions and interest to devalue our currency and enslave Malawians 2, AGAINST APARTHEID. He was the 1st Black president who told Black South Africans to go with him into white-only shops and toilets. 3, POLITICAL SUPPORT, On kamuzu's death, Nelson Mandela personally said " Kamuzu was a good man because he used to send me money when I was in prison at Robin Island. 4, GREAT ECONOMIST. It is documented in the Book " Who Is Who" that Kamuzu Banda and John Tembo as ministers of finance managed to Hold Malawi Kwacha 1to1 with British pounds. Look today at 1:1226.09 and it's still in free falling into the next hyperinflation like Zimbabwe. 5, CORRUPTION. Most of his leadership was less corruptive than it is today. These are my perspectives. This was world politics and not religion. Kamuzu was as bad as any other leader that followed him. Let's talk about The good and the bad of Kamuzu, just like everyone else in a position of Power.

  • @felixmasamba4657
    @felixmasamba4657 Рік тому

    Is this man, is he a Historian or he wants to support someone?

    • @juliusnkhoma755
      @juliusnkhoma755 Місяць тому

      Ngati akukupangani point kusayenera mutsikeni .....koma ngati mukuona ngati ndi ngamo akothakayi pangani chiganizo chabwino basi

  • @joshuamusaa
    @joshuamusaa Рік тому

    Why many stories are coming after the death of a person

    • @hi-profileltd
      @hi-profileltd Рік тому

      Munthu mku mbuyo...the beggining has nothing but the end...how wil you finish your journey thas wht matters heaves and hello..depends on your ending lets finish good so that we enter heaven

  • @kalimawandale7161
    @kalimawandale7161 Рік тому +1

    In conclusion this is a clear cooked history of Kamuzu cooked up by his haters, Kamuzu remains our hero no one can change that

  • @bestonjoseph2193
    @bestonjoseph2193 3 роки тому +2

    Nchifukwa Malawi inali yolemera azungu ankayendatsa ndalama

  • @jonathancox4189
    @jonathancox4189 3 роки тому +10

    I miss PRESIDENT DR BANDA, I have been here in UK for 33years 2 years ago I visited home for the first in 31 years I decided to visit His Mosleum, I couldn't hold myself, I cried and cried to a point that the Gentleman who is stationed there asked people to leave for 30 minutes and told me that I can take pictures. I was so distressed that couldn't hold my camera and I ended up leaving empty handed . I was shaking and wailing on top of my voice . I must admit that I never knew that would be my reaction. I took me totally by surprise. MY name is Mrs Chrissie Spencer-Cox ( née CHRISSIE KUNKAPUNDA) from Chikwewo Village ) Ntaja

  • @aubreywallo1987
    @aubreywallo1987 3 роки тому +5

    Kamuzu was the greatest!

  • @lastonekaponya7675
    @lastonekaponya7675 3 роки тому +3

    Muluzi zidankanika bola achingopitiriza azunguwo now south African pano yikusauka

    • @pachalojailoskincaidphiri4545
      @pachalojailoskincaidphiri4545 3 роки тому +1

      Very true Lastone...awa zawo ndi ma propaganda basi....Kaya akudziwa kuti ndale ku Malawi zinasintha kaya...Anthu tikumawerenga ndikumadziwa chenicheni....Sizoti poti mwalemba apa nde tikukhulupilirani ayi. Bring your sources here, no propaganda apumbwa inu

    • @amoshepson66
      @amoshepson66 3 роки тому

      Wabanda uyu zampweteka

    • @yobembewe7078
      @yobembewe7078 3 роки тому

      Samola is dead

    • @catherinemtunga2259
      @catherinemtunga2259 3 роки тому

      😂😂😂😂😂

    • @catherinemtunga2259
      @catherinemtunga2259 3 роки тому

      Pano mwana ky primary akulephera kuyankha How are you? Weni weni yu

  • @mayesokulea2445
    @mayesokulea2445 3 роки тому +3

    Kamuzu was good ,ada awa ngofoila maboza awowa they think angabuleke good news of kamuzu Banda njeeee!! Akunamiza this kamuzu we know sungasinthe history yake , everything you say is bad of kamuzu what a fake history?? Akupusisa akuuza kuti ulimbane ndi mzimu wakamuzu iweyo sudzatchukapo nchabwa😜😜😜

    • @beketemoyo9279
      @beketemoyo9279 3 роки тому +1

      Kamuzu ubwino wake unali pati munthu wakupha ngati ameneyu. Mwina kwanuko sikunaphedwe anthu nchifukwa chake ukulankhula zopusa apa. Kamuzu anali galu wakuba, wakupha, he is rotting in hell now

    • @bolakunthazi589
      @bolakunthazi589 3 роки тому +1

      Iweyo ndie ofoira. Zoona mpaka kumasapota chigawenga ngati kamuzu? Ukuoneka mutu ndiwe mwana palibe chomwe ukudziwa chokhudza kamuzu banda. The guy was evil.

    • @mayesokulea2445
      @mayesokulea2445 3 роки тому

      @@bolakunthazi589 kamuzu was good only adzigogozi ndadzibambo akwanuko adakuuzani zoipa zakamuzu ,ndipo to everybody ali ozindikila though ntapange ma Cv anu mukuipisa mbili yakeyo mungochedwa , that man alrdy created good Cv the whole world, mudzingodya deya kwanuko

    • @mayesokulea2445
      @mayesokulea2445 3 роки тому +1

      @@beketemoyo9279 umafuna akapangile chitukuko pakhomo pakwanu?? Everything you see mu malawimo mesa that's dzitchito dza kamuzu Banda?? U are too late nkulu , that man created nice Cv alrdy ,inu dzikandani ndiuphawi adzandale akupusisaniwo mukungodya machenjewo

    • @charlesmuyaya8839
      @charlesmuyaya8839 3 роки тому

      @@mayesokulea2445 you are just a bunch of nonentity. How can you say everything we see is for Kamuzu? For 31 years analephera kumanga zitukuko. Ndi misewu ingati imene Kamuzu anamanga ? For 31 years analephera kumanga zipatala. Look at Queen Elizabeth central hospital and Zomba central hospital zomwe anthu ankadalira; zonse zija anamanga ndi atsamunda. Look at secondary schools, ndi angati amene anamanga? Poti ma Secondary masukulu ngati malosa secondary, Blantyre secondary or even dedza secondary schools anamanga analinso atsamunda. Kamuzu wakoyo anapanga chani pa 31 years choposa kudzilemeretsa yekha?

  • @kondwanitembo386
    @kondwanitembo386 3 роки тому +4

    Zaziiii

  • @donaldj.kufankomwe1254
    @donaldj.kufankomwe1254 Рік тому

    Not in support of what you are talking. Your discussion or points seems to be based by on political basis