MZIMAYI UYU WAUKA KWA AKUFA

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 4 жов 2024
  • Mzimayi wauka kwa akufa

КОМЕНТАРІ • 133

  • @renardgift4023
    @renardgift4023 6 місяців тому +6

    Ine ndimaona ngati omwalirawo ndi awawa ...
    Heading mumayika akufuna ma viewers et?

  • @TheLeezo
    @TheLeezo 6 місяців тому +1

    This lady councillor isa good story teller,I like her her narration.

    • @fuzimoyo
      @fuzimoyo 6 місяців тому

      Zaziii basi

  • @FysonElliot
    @FysonElliot 7 місяців тому +9

    Osati wauka koma wapezeka nthawi yodzuka anthu akufa sinakwane ameneyo anangozembetsedwa mumasenga

  • @IssahAluba
    @IssahAluba 2 місяці тому

    Wakufa samadzuka mayiwa Ali okwima aaaaa

  • @ranswellngwira2102
    @ranswellngwira2102 6 місяців тому +1

    Mamuna openera ameneyo, munthu akafa sadzukanso. Amapemperowo angomunamiza pomupasa mkazi wina.

  • @hudsonkawinga685
    @hudsonkawinga685 6 місяців тому

    Watching from Mfuwe Zambia

  • @SiphokuhlePitar
    @SiphokuhlePitar 7 місяців тому +3

    Thankyou hainifa pondifikisa mmuzi mwathu

  • @VictoriaTanthole
    @VictoriaTanthole 7 місяців тому +1

    Mwina anangosowesedwa m'masenga nkumakagwirisidwa ntchito eeh mulungu atipase chidziwiso

  • @AllanMtambalika
    @AllanMtambalika 2 місяці тому

    Aaaaaa zimenezo zikuchuluka hvy

  • @GreciphiriGaute
    @GreciphiriGaute 2 місяці тому

    EEE ayi uyuso atiopsa

  • @ElinaBanda-gh7ye
    @ElinaBanda-gh7ye 2 місяці тому

    Nanga zadress lomwe anavala akumwalira anaziwa bwanji😅

  • @rashidsaid2232
    @rashidsaid2232 7 місяців тому +1

    Chamba munthu adzafa ndi kuuka mmanda tsiku la chiweluso/kiyama ndiye izi zikuchitikazi zopanda umboni chifukwa ndiza ufiti owoneka ndi maso zomvera anthu opanda chipembezo chenicheni 😢

  • @LindaChithumba
    @LindaChithumba 4 місяці тому

    Amene sanaziwone amayankhul kwambil kt sizoona. Km apropheti alipo kunj kuno akupanga zodabwitsa zimenez taziwona ife

  • @BerthaChitsulo-ti2mz
    @BerthaChitsulo-ti2mz 6 місяців тому

    Iiii izi nde ndizoopsa asaaa sizoona ayi😢😢nde ndingathawe mmmm

  • @ZephaniaPhiri-ro3lw
    @ZephaniaPhiri-ro3lw 5 місяців тому

    Zephania from Zambia show the person ti s boza

  • @ZakeyoCjere-bd1gj
    @ZakeyoCjere-bd1gj 7 місяців тому

    Khani yopatsa chidwi zikomo man of god

  • @HamuzaNyahoda
    @HamuzaNyahoda 7 місяців тому

    Aaaa sanali akufa kom anangotekedwa mpweya

  • @ConfusedBabyTurtles-gi4hb
    @ConfusedBabyTurtles-gi4hb 3 місяці тому

    Izizi zimakhala Zabodza , Zimangokhala zauchiwanda basi pena amakhala kt Wabwelayo wangokhala openga Chabe. It also happened ku Migowi zabodzazi but it ended up kt sanali m'bale wawo

  • @ElizabetieMailosi
    @ElizabetieMailosi 7 місяців тому +1

    Sidziwanda koma asakhaletu opephelawo atumiza chiwanda chofananako ndimuthuyo

  • @mercyphiri6867
    @mercyphiri6867 7 місяців тому +1

    Amakhala kut sanafe,anangosungidwa kumagwilisidwa ntcito nde amathawako kosungidwako

    • @joyedward45
      @joyedward45 6 місяців тому

      Pena kumakhala kuti mwini wake amene amawasunga matsengayo wamwalira ndi palibenso owasamalira basi awatsegulira kuti adzipita zoopsatu eee

  • @ChikondiBJosaya-pr1zu
    @ChikondiBJosaya-pr1zu Місяць тому

    Mmmmm izi ndizidabwisandi

  • @EdinaKaonjola
    @EdinaKaonjola 6 місяців тому

    Next waiting

  • @jamesmakonyola4096
    @jamesmakonyola4096 7 місяців тому +1

    nkhani iyi ndiyabodza ...munthu yemwe akunenedwayo amapanga ngaiti mmmutu simmayenda bwino anangosochererako coz munthuyo ndiwakwa Chinakanaka ..

  • @HendersonChikanaulanga
    @HendersonChikanaulanga 7 місяців тому

    Watching from ntchisi

  • @PaulKumwendadaire
    @PaulKumwendadaire 3 місяці тому

    It can not happen that's so amazing.

  • @IsaacAraujoMarcelino
    @IsaacAraujoMarcelino 3 місяці тому

    Amati khulupirira ngakhare usanaone brod

  • @MartinChinkhuntha-e6w
    @MartinChinkhuntha-e6w 7 місяців тому +15

    Why don't you show the face of the particular person?

    • @JojiziKatanga
      @JojiziKatanga 6 місяців тому +1

      Exactly

    • @ramiemkwezalamba1905
      @ramiemkwezalamba1905 6 місяців тому

      You don't just post someone's face without his/her consent. You can be sued. I guess thats the reason. Komanso a councilor kufikila Popeleka umboni ndiye kuti ndi zoona..

  • @MercySatumba
    @MercySatumba 2 місяці тому

    Tionetseni wokufayo

  • @GeraldJairos
    @GeraldJairos 3 місяці тому

    Zochitika m'masiku otsiriza machenjera amdyerekezi
    Osakhulupira kwa tonse owerenga tiyeni tikhale mmaso,wakufa sadziwa kanthu bii

    • @GeraldJairos
      @GeraldJairos 3 місяці тому

      Kodi inu bambo osapeza mkazi wina,ndikupemphera ,ngati mutachita bwino nkudzakumana ku ulemerero wa mulungu

  • @NeoSoko-mo2gw
    @NeoSoko-mo2gw 2 місяці тому

    Mayi kd anakupasani zingati moti paka inu muzichimwa chotele

  • @fulggiechilinda809
    @fulggiechilinda809 6 місяців тому

    Muziika bwino ma head line anuwa mwatipu tsitsaka a khansala kukhala so ngati ndiwo muukawoka kkkk

  • @wellingtonmilanzie
    @wellingtonmilanzie 6 місяців тому

    Eeeh komanso mafunso ake ambwelera bwanji😅

  • @LisaMwemba
    @LisaMwemba 3 місяці тому

    We need to see her face why don't you show her face?

  • @janetchinga695
    @janetchinga695 7 місяців тому

    Ndintawi ya mulungu, ndaionanso ku Tanzania munthu wabwela

  • @DicksonLongwe
    @DicksonLongwe 5 місяців тому

    Aaaaa tkufun wakufayo ife

  • @JoneMaquina
    @JoneMaquina 2 місяці тому

    Mas ever Dadi isu

  • @mackgozambia
    @mackgozambia 7 місяців тому +1

    Watching from KATETE Zambia

  • @KimamboPk
    @KimamboPk 3 місяці тому

    Zam'Zam'masiku omaliza no wonder

  • @JudithLaitani
    @JudithLaitani 4 місяці тому

    Izi ndizo opsa asaa 😥😥😥

  • @daltonmoisessimoco
    @daltonmoisessimoco Місяць тому

    Zoyona

  • @jacquelinemagwera155
    @jacquelinemagwera155 3 місяці тому

    Eti osawaonetsa?

  • @GiftMbewe-z4u
    @GiftMbewe-z4u 2 місяці тому

    God is going to judge one by one.

  • @nestolmafosha394
    @nestolmafosha394 7 місяців тому

    It will end in tears. Akamazazindikira kuti Prophet akuwabera it will be too late.
    A similar episode of 2010. Ask me

    • @thokokawaza
      @thokokawaza 7 місяців тому

      Tiuzeni, what happened in 2010?

  • @PaulNkhoma-iu1ny
    @PaulNkhoma-iu1ny 7 місяців тому

    Ndinzukwa ameneyu

  • @HendersonDziwa
    @HendersonDziwa 2 місяці тому

    Km athu tikumuseweletsa mulungu

  • @whitekabird
    @whitekabird 5 місяців тому

    Why don't you show the picture of a person

  • @gladyschisomo4324
    @gladyschisomo4324 7 місяців тому +1

    Part 2 please

  • @mercyphiri6867
    @mercyphiri6867 7 місяців тому +1

    Mundkodole akabwera kulilongweko

  • @IdrissahSadick
    @IdrissahSadick 3 місяці тому

    That's just jiin

  • @bashirumalikiki358
    @bashirumalikiki358 7 місяців тому

    Musamatiwone ngati zitsilu ife ayi khani zikungofanana bwanji ndinu agalu kabasi

  • @MemoryPhiri-i6g
    @MemoryPhiri-i6g 7 місяців тому

    Angofanana

  • @ranswellngwira2102
    @ranswellngwira2102 6 місяців тому

    Amapempere ena akufunika asiyisidwe msanga kumalawiko, akupengetsa anthu kwambiri

    • @JosieShumba-n1t
      @JosieShumba-n1t 6 місяців тому +1

      Kkkkkk mulungu akuulula zisisi zake

  • @Omwale
    @Omwale 6 місяців тому

    mbwerera za channel
    mzimayi uyu?

  • @innocentnkhwazi2331
    @innocentnkhwazi2331 6 місяців тому

    Headline yamtundu wanji iyii Kodi mumangoziyamba osadziwa malembedwe ankhani etiii mxiii

  • @morganchimbaka5843
    @morganchimbaka5843 7 місяців тому

    Chezani ndi waukayo osati akhansala ngat zandele,mafumu kulibe?? Osamatinamizatu

  • @RosaMaritius
    @RosaMaritius 6 місяців тому

    Show us the person pliz

  • @MatthewsNyirongo
    @MatthewsNyirongo 5 місяців тому

    Kumalawi nako

  • @xtinabrown
    @xtinabrown 7 місяців тому

    Mibawa ikafike uku

  • @IshmaelSaidi-f8l
    @IshmaelSaidi-f8l 3 місяці тому

    Chiwanda chimenecho

  • @prettytambala5687
    @prettytambala5687 5 місяців тому

    Amalawi tili busy

  • @storytambala6088
    @storytambala6088 7 місяців тому

    Munthuyo ndiyemweyo, ngati anafika ndikuyitana ana ake komanso kukumbukira munthu woti anamusambitsa panthawi yaima yake. Ndiye choti, anthu mukayikirenso ndi chiyani?

  • @ThokozaniMakwangwala
    @ThokozaniMakwangwala 7 місяців тому

    Kodi anthuwo samamuzindikira meaning kuti anasintha nkhope?

  • @IqrahSikweya-wm5mn
    @IqrahSikweya-wm5mn 3 місяці тому

    Bodza.... Mzosatheka munthu kufa mkuukanso...... Anali asanafe ameneo

  • @GabrielMbaweMbonongo
    @GabrielMbaweMbonongo 6 місяців тому

    Alady didn't die, a devil is a liar

  • @MAFAITI
    @MAFAITI 6 місяців тому

    👿 Demons power😈

  • @charityfphiri
    @charityfphiri Місяць тому

    I wish l would see the face of the specific person who has resurrected

  • @dondamissonchdziwe3958
    @dondamissonchdziwe3958 7 місяців тому +2

    Ayi sanali wakufa, Koma nzamasenga zija amakonza abathwa aja kapena ndondocha zotenga ndalama zija ndima ziwa bwino za kumeneko nkwamasenga panopa Wanthu ambiri mbiri panopa akuma bwerera nzosadabwisa kumene ndiri kuno Wanthu ambiri akufa akuma bwera ati ku Blantyre mkumene amaka gwira Ntchito mwa A mwenye

  • @lindakondowole8021
    @lindakondowole8021 7 місяців тому

    Nde mpaka zovala zamunthu wakufa Sept amasungabe

  • @DicksonKamwendo-s3d
    @DicksonKamwendo-s3d 6 місяців тому

    Mwina ndizoona kuli apulofet kulilongwe nsewu wa kasia

  • @MercyKachingwe-b7l
    @MercyKachingwe-b7l 7 місяців тому

    Ku Lilongwe ayendako bwanji

  • @gabrielmaluwa1038
    @gabrielmaluwa1038 7 місяців тому

    Nzukwa umenewo

  • @Jermah51kennias
    @Jermah51kennias 6 місяців тому

    Nde bwanji mukuti mzimayi uyu??? +

  • @FrancisPhiri-v6j
    @FrancisPhiri-v6j 7 місяців тому

    Mutitumizilekonso akabwela kumapemphelo uthenga umenewu

  • @AgnessMasilika-ti5mn
    @AgnessMasilika-ti5mn 7 місяців тому

    Koma masiku otsiriza timva mkuona zinthu 😮

  • @bettiemgamphula6275
    @bettiemgamphula6275 7 місяців тому

    Tiyamike kumwamba kuti Ambuye akuchita z

  • @sibokawana2358
    @sibokawana2358 7 місяців тому

    Aaaaa osamuona

  • @whitegadama4238
    @whitegadama4238 7 місяців тому

    wonderful

  • @kondwanimwalani
    @kondwanimwalani 7 місяців тому

    Nde simunayitane A police bwanji!?

  • @AgnessMasilika-ti5mn
    @AgnessMasilika-ti5mn 7 місяців тому

    Nanga osationesa mumthuyo bwanji???

  • @ElizabethKazambwe
    @ElizabethKazambwe 7 місяців тому

    Muli mzimayi uyu wauka kwakufa ,mzimai wake uti?

  • @NaduMbewe-zz6iw
    @NaduMbewe-zz6iw 7 місяців тому

    Muzatiuzenso kuti kulilongweko mwaendako bwanji

  • @kondwanimwalani
    @kondwanimwalani 7 місяців тому

    Chikulupililo chani ndi chachabe

  • @RichardKachingwe-p8h
    @RichardKachingwe-p8h 7 місяців тому

    Shaaa

  • @GiftChiumiaMagawa
    @GiftChiumiaMagawa 7 місяців тому

    Show the face of the risen .

  • @StevenKampira
    @StevenKampira 7 місяців тому

    Waoo 😢😢

  • @RhodrickMathewe
    @RhodrickMathewe 6 місяців тому

    Zaziiii

  • @HassanRashid-r1u
    @HassanRashid-r1u Місяць тому

    Comedy

  • @NavyShachele
    @NavyShachele 4 місяці тому

    Tam Navy from Zambia that's total lie

  • @JoshuaAamon
    @JoshuaAamon 5 місяців тому

    That is not true😂😂😂😂😂 wait for God's judgement. The problem is that these people live for a while and then die forever.

  • @JosephKumwenda-zq8ih
    @JosephKumwenda-zq8ih 4 місяці тому

    Is this true

  • @JamesPhiri-g3o
    @JamesPhiri-g3o 7 місяців тому

    timakukondani komanopenapake mukamasakaniza zinthu mumatipatsa peee kuti kodi akutibwanji amenewa

  • @ZioneKananji
    @ZioneKananji 7 місяців тому

    Zozizwitsa sizizatha

  • @felixharry3117
    @felixharry3117 7 місяців тому

    Koma ndi omwewo

  • @SimonKokhwave-yr2mh
    @SimonKokhwave-yr2mh 7 місяців тому

    Za mstsenga munthu samwalira

  • @MartinChinkhuntha-e6w
    @MartinChinkhuntha-e6w 7 місяців тому

    Why don't you she person's face?

  • @BlessingsWakhutamoyo
    @BlessingsWakhutamoyo 4 місяці тому

    Vdormc

  • @kondwanimwalani
    @kondwanimwalani 7 місяців тому

    Bible ndi Colani sanena choncho??????

  • @MarkoNyondo
    @MarkoNyondo 7 місяців тому

    Nkhaniyi isanthere pompho mudzatipasilitso

  • @BerthaChitsulo-ti2mz
    @BerthaChitsulo-ti2mz 6 місяців тому

    Iiiiiiii Inu munawagwilaso? Mmmmmmm zolilisa

  • @thokoJames-gp8mk
    @thokoJames-gp8mk 7 місяців тому

    Zongofuna kuwagunguza mitu anthu basi