Komatu a Mdyangunmutionetsa. A Nepman mwalepheratu kuyankha funso. Akuti Kodi ku Phanzi lanulo kulibe Chala chachifupi? 😂😂😂😂😂😂😂 Keep it up Guys mukutiimilira
Kkkkk koma Nepman ai ndthu 😂 aMdyangu nde ana akungobwera mututumukatu atadzadza bus 😂 Gani nde ya Junior Mdyangu yamukwana 😂 Mlelemba nd best actor off course koma kulongolora too much akumafika pobowesa coz akumatenga nthawi yaitali nde pls konzaponi ndthu pamenepa
Mlelemba it's too much...he is good acting koma he makes it beyond and boring..he needs azipereka mpata kuti ena azilankhulako otherwise it brings interest down
Kkkkk mulelemba kulongolola kwambili umatidyela nthawi
😂😂😂 mlelemba akti Zakeyo amadziwatu wammutengo kma lero amuwona akuyenda ndi miyendo
Kkkkkkkkk
Kkkk
Mlelemba amabhowetsa sometimes he always takes too much time
Zoona
Inetu pa mulelemba ndimapanga forward, amangokamba zokhazokhazo
Mzingodusisa pa Mlelembapo amene amatisangalasa tizionera ...... Keep it up Mlelemba
That's true brother
Zoonad
Big man Mdyangu munasowa2 kwambiri koma apa ndawaona a Mdyangu
Ndudikirabe yankho from Nepman ndi Gani, dzala zanu palibepo chachifupi😂😂 3stop kkkkk
Mndyangu woyeeeee koma mlelemba akuonjeza kulongolora
Kkkkkkk mumakomesa big up
Mulelemba my favourite
Koma abambo amdyangu? Chulukanani ngati mchenga 😊
😂😂😂 MLELEMBA THE GOAT
Mulelemba ndi dolo amandiwaza kwambiri
Mr Mdyangu is here now with his sweet talk❤😂😂😂
Mulelemba adzikhala ndimalire plz akuwonjedzatu aaaaa
Koma Nepman umatha kungofika ndikusokoneza😂😂😂
Pati ya mulelemba muiganizile ikuononga sewelo akuchulutsa zonena koma zosakometsa sewero
Ndipo zotopetsa zokhazokha
Mulelemba is too much kulongolola aaaaa
Bambo a joh make a jo and chipwanya 🔥 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥☄
Km naye mulelembaso akufuna kusokoneza zinthu bs
Mdyangu ndi mwanawo gani kkkkk ataphane
Koma mulelemba mapasa thawi yochuluka y aaah
mulelemba umakwana.ati kaya mamuna wa ndale 😅😅😅😅
We are here from new York
iwe shatapu!!! Mdyangu ali pheee
Nice one
Mdyangu ndi number 1 😂😂😂😂 kwabwera ka short sindikudziwa MG 1 mayi mkulu akava zitha bwanji 😅😅😅
Kom yeah
Mulelemba ndiwe katundu gyz mumatha
Mulelemba ndi 1
Muleremba amatha kwambiri
Junior wayitha ndiwe dyangu basi
A Mdyangu tsopano 😅😅
Hodi hodi ❤❤❤
Gani kulakwa
Love you all ❤
Mulelemba kkkkkkk
Kwaipa
My best actor ever since" Muleremba"😅😅😅
Koma che Junior mdyangu azigona pat
Ndipo live
Komatu a Mdyangunmutionetsa.
A Nepman mwalepheratu kuyankha funso.
Akuti Kodi ku Phanzi lanulo kulibe Chala chachifupi? 😂😂😂😂😂😂😂
Keep it up Guys mukutiimilira
I think I'm addicted to this comedy..😢 I'm not missing any episode 😅😅
Mulelemba ai ndithu😂😂😂😂😂
Same here mdyangu ndimaikonda 😂😂😂😂
Same to me ........ikakwana Friday mtima dyokodyoko😅😅😅😅😅ndisamise
Mdyangu woyeeeee😂😂😂😂😂😂😂😂 ana akungobwera. Naye Mlelemba 😂😂😂 akatelo adziti Mulungu wandionetsela😅😅😅
Mpongozi opanda khalidwe ndi mwana wawo onse alibe khalidwe
Ana ofoila kulepheretsa mission😂😂😂
Kkkkk koma Nepman ai ndthu 😂 aMdyangu nde ana akungobwera mututumukatu atadzadza bus 😂 Gani nde ya Junior Mdyangu yamukwana 😂 Mlelemba nd best actor off course koma kulongolora too much akumafika pobowesa coz akumatenga nthawi yaitali nde pls konzaponi ndthu pamenepa
❤❤❤❤😂😂😂😂😂
Mlelemba it's too much...he is good acting koma he makes it beyond and boring..he needs azipereka mpata kuti ena azilankhulako otherwise it brings interest down
Interesting. Watching from Mozambique
mulelemba ukusokoneza kwabas ungotulukq ndiulaliki wakowo wa bozawo
Mlelemba Mr bigy we love
Kusavinidwako Eunice 😂😂😂😂😂 jane yamukwana kkkkkkkk
Mulelemba akubhowetsa
Ndipo ine amandi bowa bwanji mulelemba
Ndipo akuwonjedza kwambili akudya nthaw kwambili iyeyo aaaaah
Kom gani bambo mdyangu ari buzy ndikugubuduzana 😂😂😂😂😂
😂😂😂😂 kugubuduza basi kuzizire ntchito ndiyo mweyo kkkkkkk
Kkkkk palirangwe chimzy topola mwana wamdyanguyu ukumziwa
Kma mercy kunyalurano iweyo suzatheka basi😂😂😂😂
I like mdyangu comedy for 🇶🇦🇶🇦🇶🇦🇶🇦🇶🇦🫶🏿🫶🏿🫶🏿🫶🏿
Am Aaron Njobvu from chipata Zambia I like and love this comedy i watch this every week
Amulelemba amatidyera thawi aaa. Mayi Shokoshoko ndawasowa kkk
😂😂😂 Gani mulibe ulemu kuuza Bambo wanu zakuchipinda zoona 😂😂
Koma a mulelemba kusokoneza kwambili
Chonde samalirani nthawe
Welcome back Mr mdyangu😊
Malangizo apite kwa mulelemba asamatenge nthawi yayitali
Mulelemba ati walosela kkkkkk abusa woyeeeeee
Koma bwana Mdyangu tinti ameneyi mumampeza kutiiko
Amreremba mumatangwaniska sewelo ni ubusa waboza
Kkkkkkk anawa sanapange zabwino dala amafuna afewe
Mdyangu Moto moto😂😂😂😂😂😂😂😂
Nepman abudula m'memo 😂😂😂
❤❤❤❤❤
Fire burning
Mulelemba phokotso kwambiri achepetse mmmmmm
first to comment keep it up guys
Amabowadi mlelemba aaah zoyankhula zake zake za zii
Ati,'ma hater'😂😂🔥
Mulelemba oyeeee oyeeee oyeeee oyeeee oyeeee
Ine mlelemba ayi amatchulutsa kulongolola
CDM TOUR and TRAVEL 🇲🇼
Mdyangu umandiwaza
Akuti inu mulibe chala chachifupi 😂😂😂😂😂
Am single am single again 😂😂😂
Iyiyi nde mwapala kuposa zonse
Mdyangu more fire 🔥
Koma mulelemba muma mpatsa nthawi yambiri
Kkkkkkkk km gani kwayakhula abambo ake chocho
Ati mundipase holy water
Banja la sasoka ndilokhalo likusangalala bas
Amulelemba mukumawapasa mpata ochuluka mmm
Km guni mpaka mwina ndizibale kwinakwake
Mlelembayo aaaa akumazizilitsa sometimes
Mulelemba akumalongolora zambirimbiri
Mlelemba kkkkk😅
Mdyangu koma pilizi mukamete
kkkkkkkkkkk koma lero
Chipini wake wakwathu emweyi😂😂😂
Koma ganizan ndimwana opusa kwambri
Mlelemba akutithera nthawi 😢😢
Koma amdyangu mukula liti inu😅😅😅
Kkkkkkkkk km Gani
Give mulelelemba small clips pilizi
Mmmm km mulelemba akulakhula kwambili
Kkk km mulelemba zakeyu wabaibulo
Mlelemna koma aiaia😅😅