Mai chokochoko more 🔥😂 Queen wapeza chotanira ndi chemwali ako anadwalapo misala eti😂😂😂😂me here Annie,Ayi A name kulibwino muwakakamire achiphwanya basi😁
To be honesty with you i love your comedies , my request please make your comedies a bit longer and try to show everyone , because i didn't see Mulelemba , Mercy , mwana wa M'kango , Chipwanya , Sindy including zhyo-zhyo .
Queen paka mayi shokoshoko ufuna uwarande shokoshoko wawo komano giya wayikhoma apita kumuzi
Mai Shoko shoko aaaaa pano iiii 🙌🏻🙌🏻🙌🏻 nanu Pena mtendere ukukanikani chifukwa zambili zikukudutsani nditu. Akazi aGani nawo afika ndimbebe kkkkkk
Mrs Zambia amakwana mai shokoshoko becareful
Queen mwayisolola pat imeneyo 😝😝😝 mayi shokoshoko muyaluka ndithu kameneko ndka queen kamfiti 🤣🤣🤣🤣
Munyanyiwa wafika mwa coming, uli bho 🔥🔥
Me here Annie here annie house 😃🤣kkkk koma guy's
Flora ndi crew yanu yonse mukuyitha...This is great! We have great talent ndithu ku Malawi kuno. Just needs this kind of exposure
Kkkkkkk my Karaka ndi farayi mumakwana
Ati inenso andigaire ndalamazo😀😀😀 koma kwachema.
Queen 🥳🥳my fav
Yatha ikukoma😂 Munyanyiwa uli bho heavy💪Keep up the good work,tikuphunziramo zambiri.
Alamwawo a Munyanyiwa sanalandile bwino, Eeeee Queen 👸 ♥️ ✨️ kikiki zayambiranso tipitenso kwa A Sing'anga?Queen waulura zisinsi za Achemwali ake Hahaha 😆 😂 ♥️ Tsikana wa ku Zambia 🇿🇲 😆 wabwera ndi Nkhondo,
Zili mushe Guy's.
Mkaz shokoshoko eeeee saugwila mtima azaluza banja 😂😂😂😂
Kom Mai shoko shoko kkkkkkkkkkkkkkk masaya phwamwamwa
Kkkkkkkk Chiphwanya alikuti guys mnyanyiwa sanabwere bwino
Amunyanyiwa mwabwela ndi fire ❤
Anne here house kkkkk keep it tap
Ipha basii tidzadyepo
mai shokoshoko eeeeee more fire kikikikiki
Kkkkkk anapengapo ndithu koma Queen mpaka wayidziwa
Koma Munyanyiwa wafika ndi moto guys, komaso Shoko Shoko ukuitha ❤
for sure kuiwala nkwa munthu koma kukumbuka nkwa ambuye
Mai chokochoko more 🔥😂 Queen wapeza chotanira ndi chemwali ako anadwalapo misala eti😂😂😂😂me here Annie,Ayi A name kulibwino muwakakamire achiphwanya basi😁
Akuti kuteroku amayi anamuuza kwini za nkhani ija
Nde sidzinayendetu🤣🤣🤣
To be honesty with you i love your comedies , my request please make your comedies a bit longer and try to show everyone , because i didn't see Mulelemba , Mercy , mwana wa M'kango , Chipwanya , Sindy including zhyo-zhyo .
munyanyiwa naye wabwera ndi moto,,, i like him
We have good talent. Proud of you guys
Sasoka ndiye wayamba kutchenatu😍, ukufuna kupikisana ndi mwanawamnkango😂💥❤
Kkkkkkkkkk ashokoshoko chonkhalila mumakwana
😂😂😂😂😂😂😂😂 am here Annie here in house
Koma ndiye yes
Annie here Annie house 😂😂😂😂😂😂Munyanyiwa 😂😂😂😂Gan ndiye wazikwatilira mavuto
Mai shoko shoko ndi actor mbambande 🔥🔥🔥 🔥
Mwagenda kalulu masana kalulu madzulo kalulu
Sindi mulelemba mercy mulikt mwasowa
Annie here here, kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk ai zikomo!
Enawa are not dancing!
😀😀😀😀😀amunyanyiwa tsopano Anne house hire
Kkkkkkkk misala sagawana koma iyiyi nde sikudziwika odwala wenwen😅
Kkkkkk mukuveka guys .....mix Anne here here 😀😀
Akuti inetu Misala ndinadwala ndili wamng'onioo🤣🤣🤣🤣🤣
Munyenyiwa sipano
Mai shokohsoko 😂😂
I really dream to join the team..@💥
Sasoka good advice to your wife
Awa aphana kkkk
Opanda chiphwanya ndi mlelemba zizinakome
Amunyanyiwa kkkkk
Ati ndiphapo munthu pano😂😂😂😂
Banja lachimwemwemwe sasoka mwaitha
😂😂😂😂Koma mudzi uwu iiii
Kkkkk koma munyanyiwa
Mumativesa kukoma guys
Banja laSasoka layamba kuyenda
Munyanyiwa wabwela ndi moto kkkk
🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣 Queen♥️♥️♥️
I appreciate you guys you really showing us good work honestly work hard flora will vote for you as best comedy writer
Munyanyiwa more fire 🔥
Queen ❤❤🎉
Kmnde kusaka maganyu mumakutsatatu azimayi inu
😂😂😂😂 koma ziliumu
Mumatimvesa kukoma guys
Munyanyiwa kulankhulu chizungu 🤣🤣🤣🤣
Queen mukutumiza sister anu kumuz
Munyanyiwa kkk
Munyanyiwa wabwela ndi mkokomo, nanga Achiphwanya alikuti?
Miss Zambia 😂😂😂
Vizingu vavutatu apa
Tifana mmankondadi sasoka
Queen don't make me 😂😂
Koma queen 😂😂😂
Koma abale Juu tikadamuona kuti akufanana ndi sasoka?
Chokhalira chimaonesa mwana alindiuthenga😅😅😅😅
Ati samadziwa kuti ndiinu a bp?😂😂😂😂
😂😂😂😂😂 chokhalira
Kkk queen 😂
Anne here here
Gan kunja ndi Zina lokha basi kkkk
Kkkkkk yalowa Rasha
Sasoka in love ❤
Yalowa russia😂😂😂
ha ha ha ha
Im here for qeen❤❤
Tipite kumudzi chifukwa zikuoneka kuti zaysmbiranso
Owoo kodi maiwa ndi misala eti
Kd chipwanya alikt zakuoneka
😂😂😂
🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣
Or mukanangot mayi rapper 😂😁😂😂😂
Mayi dyangu
Kkkkkk koma nde sex trillion eeee
Kodi @liki-liki simungatimapadire inside dairies chondechonde
😂😂😂😂😂😂
Missing chiphwanya and mulelemba km anambewe abwere tawasowa
So great
😂😂😂😂😂