Розмір відео: 1280 X 720853 X 480640 X 360
Показувати елементи керування програвачем
Автоматичне відтворення
Автоповтор
Komatu Mai Padela ndikamakuonelani pa play imeneyi ndimaiwala kuti ndi play, seems it is true
Ndipo Mai padera deserve something 🙏👌
Tiwonele kaye izi basi ,zinazo tayima kale
Namoyo ndiwozungulira Mutu from pretoria
Namoyo wagwa nayo mboni yamukana pa bwalo
I feel good here S.A kempton park more fire padela
Padela man of the match 🔥🔥🔥🔥🔥
I feel good here S.A, Kimberly
Me too oh !! ❤ SA grass park capetown
A padera ati ayenda ndi mpeni
Kub progress? @@JeffreyKambwemba-zs7wy
Kodi chabwalo afumukazi adya kangati Anamoyo posuma anapereka komaso nkhani yafika pabwalo akufunaso yina mwambo utiwo
Kodi Mercy basi iweyo waganiza zomangokakamira azimuna 😂😂😂
Komatu flora suya ndiwe wanzelu umatimvesa kukoma
Big up pa ntchito ukuyigwira timanyadila plus kuseka ndi series imeneyi..kuno ku Bagamoyo
Fantastic from RSA Zomba boy
Ine amandiimilra nd abwenz lao a amfumukaz amandsangslatsa kobas. Namoyo keep it up
Mwezi wanthu Mr shopulaiti munawaona fumu KAZI Ali ndi maiwa Ku patsana hagi koma Mr shopulaiti simunapange chilichonse komatu munalusa mmm tamamalizani bwinobwino maiwatu mukumupatsa mpata ochulukatu
Tsekani mmaso azimai ndalama ili mkati mwa kabudula wa mkati😂😂
Agili mwatchenatu lelo kkkkk mpaka red tie zilibwino kkkkk
Kkkkk km mwati ikokele nthawiyo
Kkkkkkkkkk Mr pandera mumakwanatu
Komatu mumatha agiring,ande inuyo ndi ufumu chinayamba ndi chani kkkkkkk
Koma Padera ati Namoyo ayikokere nthawi yomwe yataika😅😅😅😅😅😅
Pagolini Nate kufuna kusokoneza
Nkazi amakawonekela
Great Team! Guys mumatha kuchita mix bho: great minds you are
HAAAA JOSHUA IS THE BEST OOOH 😂😂😅😅😅 IYEEEEEE
Achitsime kuyankhila zaeni
Timayamika kwambili koma anuwake ashupulaiti amayeneleka kufusa masamba Kwa fumukazi chifukwa wakatenga Kwa maiwa koma akudyabe
Apadela ndi mbambande
Padera ndi Moore above all good work team ❤
Padera anakhoza
Nginde comment ndee amaiziwa eeehhAti muikokere nthawiyo km ma Comment ake eeeeh
Watching from South Africa namoyo wagwila padela
Padera man of the match 😅😅😅
Padera umatambaaa😂😂😂😂😂😂
Nice
Lululuuuuu ngakhale ndikululutira koma ndiine okhumudwa chigamulo sichinayende bwino padera akuyenereka kupitilidza banja ndi namoyo apo ayi apange mitala ndiye momwe zilirimu chidwi changa chiri kwa song'anga Kodi namoyo ayendako bwanji ?
Pachoka nzako Pali Maro nyimbo ya khwini mishuuuu wafaaaa nayo ndiimodzi Namoyo 😂😂😂😂😂😂
Mfumukazi nd 🔥 mmatha gyz simupala ❤
Mai Padela job well done 👍 Namoyo keep up your good work , Mfumukazi comedy you're number 😂😂😂😂
Mwana ndizimu
Mfumukazi yalalatira mfumumuna kuno😂😂😂😂😂😂
😢padera amaitha more fire
Usaope ndayenda ndi mpeni ineyo😂😂😂😂
Mai Padera mumandisangalasa ❤❤❤koma padera eeeeeeh anakonza 😂😂😂😂
Ndikamawonera ma video anu ndimaona ngati ndii ku mudzi ndimakunyadirani nonse pitilizani ndithu
Tiwerengabe ..tionera Kaye...ili bhooo😊
Kkkkkk kom padera umakwana iwey tikuwonera kuno ku south Africa cape Town
Mfumukazi, mwakongolatu
padera wadabwa mwana wapereka moni kwa dad
Morefire guyz
Nanyoni akukongola mmene akukulamutu
😂😂😂koma ndikusekerera!😂..ati my daughter
Ati sitepeyo ndi nyumba muno amaliro kkkkkķ😂😂😂😂koma mfumukazi
Maphunziro alipo ambiri mu nkhani izi
Watching from RSA in upington
Watching from Cape town
Watching from cape Town
Nice acting I lyk this comedy so much
Koma padera😂😂
Tiupange aquit😅😅😅😅 All the best guys
Joshua akalowa nae umfumu wakumwanba😂😂😂😂
Ma Joshua mwanenepatu
Watching from S A mpumalanga
Namoyo umatha. Koma Mfumukazi ulionse washout?
Km mene amfumukanzi amaweluzila mulandu mmmmm ine yanga sazanzenga antaaaaa ndikaipititsa kupolice ndithu 😂😂😂😂😂
Kkkkkkk weshauti yemweyo 🤣🤣🙌
Padera are you related to Winiko?😂😂😂😂😂😂
He speaks exactly like Winiko😅😅
😂😂😂😂😂
Yes tupangedi akwiti bas hahahh
Watching from Dubai what do you mean when you say mfumukazi mukuchisa nsima
This is massive eeeee anthu mumatha now mkuphanaphana ndi tikufelanji
Good morning I like that
Family ya padera mmmm onse ndiogwirizana😂😂
Amfumu anji owakalipila amunawo pa gulu la anthu😂😂Koma padela ndi nkhan zina😅
Namoyo dzina lako ndwe banja lisowa😂
Paderasopano
Pamela ndi winiko kale😂😂😂
Very great nice
Nkhani yi ndiyomvetsa chisoni
Mboni ikhala bwanj mfumukazi
Joshua nawe sukula bwino....misala yamdala wako waitengera basi😂😂
Komatu sing'angayo alibwino kkkkk
Padela ndi ndi Mbambande ngati Jetu. 😂 😂 😂
Mwabwelatu maguys
Best from Malawi
Komasoo mfumukazii😂😂😂😂😂
Padela you wa the man❤❤❤
Afumukazi mirando yose wachauti 😀😀😀😀😀😀
Good work F suya
You're number one 😂😂😂
Munthu wadera lanu asakupengereni mukuona iyayi🤣🤣🤣🤣
😂😂😂😂 kma josha
Afuna amenye mzimu Namoyo 😂😂😂😂
Koma apadera kudabwa kwake kkkkkkkk
Padera bwera ku Capetown asaaa umatha😂😂😂😂😂
Joshua umatha iyeyo ndiwe Akita wava
Eliya phiri from Zambia
Waching from India which country is this mumakwana guys
😂😂😂😂 koma Joshua kuyikila umboni 😂😂😂
So sweet Mai pafera
Apadera pena mwafika pobowa
Ndipo my daughter waine sanganame pandela 😂😂😂😂😂

Nginde comment ndee amaiziwa eeehh
Ati muikokere nthawiyo km ma Comment ake eeeeh

Amfumu anji owakalipila amunawo pa gulu la anthu😂😂
Koma padela ndi nkhan zina😅