NZIMAYI UYU MARY NAVITCHA NDIOLIMBA MTIMA NDIPO WANG’ALURA CHAKWERA LIVE LERO KU MZUZU PANSONKHANO

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 20 вер 2024

КОМЕНТАРІ • 64

  • @GeorgeBanda-x6l
    @GeorgeBanda-x6l 7 годин тому +1

    amayi mumangofatsa koma muli ndi nzeru koposa chikangawa mwayankhula zaoona zokhazokha Mulungu ati chitile chifundo ❤❤❤ DPP bomaa

  • @ziwani3682
    @ziwani3682 7 годин тому +7

    Navicha ndikatundu guys.... dziko likufunika anthu ngt awa

  • @lameckmphande-yt4ou
    @lameckmphande-yt4ou 5 годин тому

    Good bless you mom washing form part Elizabeth South Africa I love you DPP kuyambilakale ❤❤❤

  • @Creslevison-vj2sl
    @Creslevison-vj2sl 4 години тому

    Brave woman ❤ good speech madam

  • @HendrickBanda
    @HendrickBanda 8 годин тому +2

    🔥🔥🔥

  • @EmsAdam-c1i
    @EmsAdam-c1i 3 години тому

    Amene zikumuwawa zomwe akuyakhula amaiwa azimangilire ndichingwe chafilizes

  • @MarcosDjussa
    @MarcosDjussa 4 години тому

    Apm my vote 🗳

  • @NEBRA-lm7ji
    @NEBRA-lm7ji 2 години тому

    Apm my vote❤

  • @LytonGalison
    @LytonGalison 7 годин тому

    Ulemu wanu mai Apm my vote

  • @ThandieChris
    @ThandieChris 2 години тому

    Apm my vote

  • @henrymedeliko8727
    @henrymedeliko8727 2 години тому

    ❤❤❤ my vote 💙

  • @SherifaG.Mlelemba
    @SherifaG.Mlelemba 5 годин тому

    Kuyankhula kwa anthu ama Lawyer uku....🎉🤔2025 kuli ntchitoo!😊

  • @Randy-er2xo
    @Randy-er2xo 7 годин тому +1

    Zoona mai adazakuthamangitsani mpaliamenti muja

  • @WisikiBlack-gj4gu
    @WisikiBlack-gj4gu 3 години тому

    Mai navicha more fire 🔥

  • @munashemoyo4190
    @munashemoyo4190 6 годин тому

    Mau mau ndthu mai wathu ❤

  • @FrynessMoyo-to2du
    @FrynessMoyo-to2du 6 годин тому

    God bless you mom

  • @AlickJam
    @AlickJam 7 годин тому +1

    Eeew ndi panza uwone nkono 0:47

  • @JohnJohn-og8rt
    @JohnJohn-og8rt 7 годин тому

    GOOD nice Apm

  • @Biath-m4b
    @Biath-m4b 7 годин тому +2

    APM my vote navitcha more fire

  • @LiahRestoration
    @LiahRestoration 5 годин тому

    Mai wanzeru uyu 🥰

  • @BrightZionga
    @BrightZionga 2 години тому

    Navicha ❤❤❤

  • @ROSEKATHYOLA
    @ROSEKATHYOLA 7 годин тому +1

    Zoona zake mayi wopanda mantha

  • @0wenNkhambule
    @0wenNkhambule 7 годин тому +2

    Good message Mayi❤

  • @ellensambo6323
    @ellensambo6323 7 годин тому +1

    Eish 😢

  • @BlessingsGogoda
    @BlessingsGogoda 2 години тому

    Love you ❤❤❤❤❤❤

  • @YasinSabili-dj9xe
    @YasinSabili-dj9xe 7 годин тому

    Apm fire❤❤❤

  • @patrickmacheso-m4m
    @patrickmacheso-m4m 23 хвилини тому

    Munaitha ku parliament kuja mayi

  • @Yoxym
    @Yoxym 3 години тому

    APM 💙💙💙💙💙🇲🇼

  • @moureenmolesi
    @moureenmolesi 6 годин тому

    yes mam simukunama dpp ndi moto chikangawa sakumaka

  • @PatrickMtira
    @PatrickMtira 7 годин тому +1

    Km ndilibe mawu

  • @paulnyondo7572
    @paulnyondo7572 7 годин тому

    Uyu simayi wamba .kungalura kuwauza chilungamo a chipani chakupha

  • @LenardJames-j1n
    @LenardJames-j1n 7 годин тому +1

    Zandikhuza 😢

  • @JohnJohn-og8rt
    @JohnJohn-og8rt 7 годин тому

    Ameen

  • @omarajibu860
    @omarajibu860 7 годин тому

    Ife anthu akumuzi tili nganganga ndi APM, tichotse manyiwa

  • @MaxWell-d7o
    @MaxWell-d7o 6 годин тому

    Navitcha 😂😂😂 adad omweo 🎉🎉🎉🎉

  • @MiracleDamiano
    @MiracleDamiano 7 годин тому

    💙💙💙💙💙🔥🔥🔥

  • @JasonMailos
    @JasonMailos 3 години тому

    ❤❤❤

  • @Halima-i4x
    @Halima-i4x 7 годин тому

    ❤❤❤❤🎉🎉🎉🎉

  • @Paul-q2p
    @Paul-q2p 7 годин тому

    Chimanga Chija akuti akunama chisilu chikangawa

  • @ChrisyMbewe
    @ChrisyMbewe 5 годин тому

    Zoona.mam

  • @PatricaTchuwa
    @PatricaTchuwa 6 годин тому

    Mtengetu wadya nkhumbo ukuu kkkkkkk ipatse moto mama

  • @VincentManyenje
    @VincentManyenje 6 годин тому

    Ife tilinacho chimanga zatengeni.

  • @kumbukanikafwafwa
    @kumbukanikafwafwa 7 годин тому

    Kkkk i think i rather go for mai jb. Amapeleka ma solutions . A person who focuses on problem has no solutions. Same way tonse was doing during campaign

    • @FosterKalinde-b2p
      @FosterKalinde-b2p 4 години тому

      Dpp sikuyeneranso kulongosola,timaziziwa kale.its a massive party and so wise economically

  • @AlexKaunda-ny2eg
    @AlexKaunda-ny2eg 7 годин тому +1

    Zikhale ng'oma wadya Mai gotani Hala Ku ekwendeni Ku room 😢😢

  • @user-lw4hw9ce4w
    @user-lw4hw9ce4w 7 годин тому

    Mai ndinu makani mumakwana

  • @VincentManyenje
    @VincentManyenje 6 годин тому

    Apm wayima ngati president wa MCP .chakwera woyeeeeeeeee 2025 bomaaaa.

  • @VincentManyenje
    @VincentManyenje 6 годин тому

    Inu wosawapasa chakudyacho bwanji.

  • @ShilatonCosmas-y6s
    @ShilatonCosmas-y6s 5 годин тому

    Ok dpp Ili bwino ,vuto peter wakula pakanakhala wina oti ayimire it's ok.tonse tikupititsa ana ku xool ukawafunsa akut akufuna kudzakhala president. Ndye......

    • @AngellaAnge-p7x
      @AngellaAnge-p7x 4 години тому +1

      Kukula kulibe kanthu nkhani ndi chitukuko osati izi zomadya chitedze

  • @AlexKaunda-ny2eg
    @AlexKaunda-ny2eg 7 годин тому +1

    More fire ma'am

  • @NgwexWhite
    @NgwexWhite 2 години тому

    Mai mkulu

  • @LevisonMalemba
    @LevisonMalemba 7 годин тому

    Mai inu ndi katundu osafooka

  • @SydneyNyasuli
    @SydneyNyasuli 6 годин тому

    Musiyeko zakudya uko kumupoto mukukhula bwino tuu kumeneko

  • @KENETHMAJASA-ud5ee
    @KENETHMAJASA-ud5ee 6 годин тому

    Mbambande

  • @MayesoBikefa
    @MayesoBikefa 7 годин тому

    Mau abwino

  • @ChiukuseIbrahimJNapoloMakungan
    @ChiukuseIbrahimJNapoloMakungan 5 годин тому

    Zoonadi mayi

  • @HerbartKaphamthengo
    @HerbartKaphamthengo 7 годин тому

    Koma anthu inu ndiye Kuti fundo zoti anthu akukondeni mulibe bwanji osauza anthu zoti mukazalowa M,boma muzawapangila izi ndi izi .Koma ndale zomango nyozana basi.vuto mumangoyamba ndale osapanga maphuzilo ake andale . Ndiye Kuti Chakwera simukugona naye Tulo eti AAAA guys tayesaniko ndale Za mfundo kuti anthu akukondeni please

  • @Halima-i4x
    @Halima-i4x 7 годин тому

    Koma anthu aliko zuzu

  • @EsnartGirivin
    @EsnartGirivin 6 годин тому

    ApM my vote❤