May God continue bless and protect you adad only hopeful of all Malawians, to say true I love this guy not to be only candidate but great patriotic and humble guy ❤❤❤
Long live a DAD ulemu wanu Mulungu akuphimbeni ndipo ayende nanu ndi kukutetezerani kwina kulikonse mutapiteko we love you our fatther Mr Peter muntharika even God knows ❤😂
Ine sindmalota zovota km apa pokha ndkuvoteran adad wamkulu nd wamkulu bas ndaonera pa inu ndale zopanda kutukwana wina osat enawa zokamba mbweeeee za mzawo
Am sorry to say this.Adad akungoyenera kukapuma for good so that he stays praised and honored.Guys mkuluyu wakalamba to be honest ndipo ngat ndikunama ineyo ndie kut inuyo nenani kut ali bho koma ngat mukunama ndinu... Akapume 😊
A president mulungu akudalitseni inuyo ndinu chiyembekezo cha Malawi pulumutsani Malawi 🇲🇼 Ali pa moto oops wa kuphedwa, kumangidwa opanda zifukwa,njala kudya chitedze kusowa kwa mafuta,kukwela kwa zinthu zonse kusowa kwa ndalama, kusowa kwa mankhwala nzipatala ndi Zina zambili.koma inuyo a president a munthalika pulumutsani amalawi ku nkhalamu izi za mcp
Aaaaaaa za ziiiii!!!!! Mesa munali mu boma momwemu koma anthu anachita kukuchotsani atanyasidwa nanu apa mufuna kumanimizaso anthu ! Ndiye bola akanakhala wina oti sanaloweko mu bomamo!!!!!
Chikuni chachikulu kusunga moto Big up prof peter mthalika❤❤❤
Adadi number one bsi my vote 🗳❤❤❤
Munthu wamkulu born to be a leader.
May God continue bless and protect you adad only hopeful of all Malawians, to say true I love this guy not to be only candidate but great patriotic and humble guy ❤❤❤
Amen 🙏
For sure this is government we want as Malawian,APM boma iyooooo❤❤❤❤❤❤❤
Kudos.Excellent speech my President APM
Beauty is he does what he says. God Bless APM.God Bless Malawi
Long live a DAD ulemu wanu Mulungu akuphimbeni ndipo ayende nanu ndi kukutetezerani kwina kulikonse mutapiteko we love you our fatther Mr Peter muntharika even God knows ❤😂
I love this party Dpp because the staff was better that time and the food was every where💙💙
I love you dad you're the best leader
chiyembekezo cha amalawi ❤❤❤❤🎉 DPP my vote more fire
Chitsime Chakuya Chimadziwika madzi Akaphwa, respect Mr Apm
God in heaven guide and protect APM
Amen 🙏
Ndinu adad athu tikuzakuvoterani ndithu ❤❤❤❤❤❤❤
Most of the malawias now are complaining but we don't do it again please make sure that everything is ok for you to lead this country.
May GOD continue protect and bless you our leader APM❤️💙💙💙💙💙💙🙏🙏
Ndiye mfondo adad mumatha Ndipo mwandiuankhulira bwino kwambiri vote yanga ndinuy adad ❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤
Timakondani adad mumayankhura osanyoza muthu ndare zabwino❤❤❤❤
President wathu wa chitukuko komanso opanga zofuna za anthu good bless you
God bless Peter ❤❤❤
The democratic and humane soul. Leader ndiyemweyu. Long live my man
Kuyakhula kwabwino mr Peter ❤ my vote
Peter Mutharika mean well for Malawi people
Ndiweeee wankulu yeeeees....koma unayetsetsa kulamula bwino....❤❤❤
God bless this man ❤
We are behind you our president, please Malawi let support him.
Good leaders, everyone smiling
The man is good leader and he got good heart... The heart of peace and democracy
Apm my vote , nice speech
Ma vote ndi anu adad mtima mmalo❤
He is intelligent man He knows what he is speaking and truly people have learnt something
Chikangawa sangamake bola kwa Apm wachepa mr chikangawa
Mumatiimilira bwana❤❤ vote ndiyanu bas
God Chosen u APM to Lead this country
2025 I kuchedwa long life my APM my vote ndi family yanga 🎉🎉
Ana achepa,long live APM
Wathuwathu peter❤
DPP my vote
APM my vote mo🔥🔥
Peter muthalika my vote
Tate wa fuko la Malawi mulungu adzikusungani ndi moyo wa thanzi
Kukhala wachikulire si chifukwa koma nzeru zidakali zonse adadi awawa
Live
Long live APM 🔥🔥🔥💙💙💙💙
Utm and Dpp ❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤my vote
Ine sindmalota zovota km apa pokha ndkuvoteran adad wamkulu nd wamkulu bas ndaonera pa inu ndale zopanda kutukwana wina osat enawa zokamba mbweeeee za mzawo
Instead of humbling himself,, he should stop that and starting kupepesa,, he is the one lead us into this mess
APM my vote ❤
Am sorry to say this.Adad akungoyenera kukapuma for good so that he stays praised and honored.Guys mkuluyu wakalamba to be honest ndipo ngat ndikunama ineyo ndie kut inuyo nenani kut ali bho koma ngat mukunama ndinu... Akapume 😊
I'm even proud of him ❤❤❤❤❤❤
APM my vote
APM MY VOTE
My vote APM❤
federal system of government is good for Malawi we don't hv good leadership in this country people are suffering the poorest country in the world
Owina wina uyu chikangawa umve ulipo ndiwe galu kwabasi
Apm my vote
𝐈𝐳𝐨𝐨𝐨𝐨𝐨𝐨𝐨𝐨𝐨💙💙💙💙💙💙💙💙💙
He is right president
Love you apm always❤❤❤❤🎉🎉
Dpp hoyeeee ulem wanu adad
Adad Prof rather Peter muthalika 2025 boma illo athu alapa fitiyi itazuza mokwanira
Federal system is the way forward.
Adad my vote
Mawu andiwadza kwambiri akut tikabwerezanso adzatimvera chisoni kwambiri Iwo akupanga retire
Mawu amphavu ndipo wayenjedzela aKuti ndikufuna kamadzapanga retire ndili boma,what a beautiful hope Malawi ❤
Good speech dad
A president mulungu akudalitseni inuyo ndinu chiyembekezo cha Malawi pulumutsani Malawi 🇲🇼 Ali pa moto oops wa kuphedwa, kumangidwa opanda zifukwa,njala kudya chitedze kusowa kwa mafuta,kukwela kwa zinthu zonse kusowa kwa ndalama, kusowa kwa mankhwala nzipatala ndi Zina zambili.koma inuyo a president a munthalika pulumutsani amalawi ku nkhalamu izi za mcp
Respect APM
God bless you Dad
Goo luck adadi
Tinavota kale iffe DPP kulibe China kuno ku Malawi
This is very amazing
Machine appointments based on merit not just because you all elders ku dambwe ai😂😂😂😂😂😂
Ine kunva kukoma
Likukumwe la athu.mmmmm
We need you Apm
Boma tikupenge kare iseee tambala wakuda tizamukoma pa 2025 uyo
Pm nimuwemi chifukwa wakutuka yayi, kweni mwamasapotazi kutuka
Nice Apm
Adadi mmakwana kwambiri ndipo palibeso president ngati inu kumalawi kuno
Congratulations apm
bravo peter wamutharika
❤❤adad apm
People's asset ❤
Boma ili Adad number one,ulemu wanu ndi makukondani
Boma kma ili🤩🤩🤩
God fearing Man
Sitidzabwelelaso ku nkhaza za dpp kumaotcha manyumba
APM 4 ever
Mwayiwala nkhani ya njara abwana ndiyokhayo izabweretse inu Boma mukamaikamba
Munthu wa nzeru sakhulupilira munthu amene anamukhululukira.
The true bro peter
A constitution maker
Poti, Mwanena Nokha kuti muli Chibwana Too Much M' DPP, Basi Boma Ndlomweri, kulibe kusintha!! Eeeya!!
Big up Peter
Iwe phalibeso peter mutalika umakwana
God bless you
Amene akudana ndi adad Mutu waku sumagwira ndi chikangawa ll
Adadii mwarandiridwaso mu boma
❤❤Muthalika
My vote
Kumphuzila sikumatha amalawi aphuzilapo kathu after challenges
APM MY PANGOLIN❤❤
15 in government now you are going devep Malawi kkkk
Ilike you dad
Aaaaaaa za ziiiii!!!!! Mesa munali mu boma momwemu koma anthu anachita kukuchotsani atanyasidwa nanu apa mufuna kumanimizaso anthu ! Ndiye bola akanakhala wina oti sanaloweko mu bomamo!!!!!
Inu yamikilani inu manyazi bwa chikhamu chimasatilaunthu oti siwabwino?mumva m,bebe awa ndi akatundu omanga ndi mawaya klkkkk