Limpopo Chakwera wakhaula ku Lingazi CCAP dzulo lija Ntanyiwa waphedula yonse timve bwino bwino

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 10 жов 2024

КОМЕНТАРІ • 196

  • @ThandiMbewe
    @ThandiMbewe 2 місяці тому +10

    Atanyiwa ndinali pa Malo ena ake dela lomwe ndimakhala koma koma seriously anthu akumvela Limpopo ndimangomva nyimbo ya Limpopo ija program ikamayamba, wooozaaaa chikangawa ndinu number 1🎉🎉

  • @WarriorKB-u3k
    @WarriorKB-u3k Місяць тому

    Zoona,zoona mr chikangawa ndi satana mumakwana ampingo ife tikufuna yesu ❤ it

  • @WarriorKB-u3k
    @WarriorKB-u3k Місяць тому

    Salute comrade Ntanyiwa mwambo wa ma candle sitisiya mo fire mpaka chakwera atanyeledwa

  • @TyawanisoHala
    @TyawanisoHala 2 місяці тому

    Number one Radio station

  • @PreciousHenderson-qc1hq
    @PreciousHenderson-qc1hq 2 місяці тому +1

    Mumakwana comrade❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤

  • @watsonmhango8794
    @watsonmhango8794 2 місяці тому +7

    Powerful message from comrades Ntanyiwa❤❤❤

  • @AnthonyPhiri-e3g
    @AnthonyPhiri-e3g 26 днів тому

    Power Limpopo 🙌🙌🙌

  • @AlexKaunda-ny2eg
    @AlexKaunda-ny2eg 2 місяці тому +14

    😢😢😢 achakwera muona dzosaona ndi mwazi munathila

  • @mthawisakaunda
    @mthawisakaunda 2 місяці тому +13

    Akonzekere next year kumangdwa chakwera . Galu okupha

  • @StiveKantiki
    @StiveKantiki 2 місяці тому +1

    Km akuluakulu ndikupempha nyimboyi amene alinayo chonde tigaileni

  • @TyawanisoHala
    @TyawanisoHala 2 місяці тому

    Wonderful

  • @AjibuTwalibu
    @AjibuTwalibu 2 місяці тому +7

    Mukundifika mumtima
    Bwanji❤I ❤u❤😂😂

    • @RiteRoderick
      @RiteRoderick 2 місяці тому +1

      😂😂😂😂Inenso bro 😂😂

  • @harrisbanda5891
    @harrisbanda5891 2 місяці тому +2

    Eish!, mtima wanga unagunda nditayamba kuwelenga title ya lero ya nkhanga zawona ndipo nditafika poti " NTANYIWA WAPHEDULA ", ndimawona ngati akuti NTANYIWA WAPHEDWA, eish!, nditawelenganso ndapeza kuti pali mawu oti NTANYIWA WAPHEDULA😂😂, may ALLAH guide and protect all the freedom fighters in Malawi Ameen 🤲🤲🤲

  • @AiameAdamo-su1nt
    @AiameAdamo-su1nt 2 місяці тому

    Welcome back Limpopo fm. We listen your channel everyday from Mozambique.

  • @PeterJames-i8y
    @PeterJames-i8y 2 місяці тому +2

    Osaopa mulungu wa abraham, Davite,yakobo,yosef,shadrec, misheki ndi abitinego awatetezera azitsogoleri amenewa.mwachitsanzo kuti mudziwe kuti mulungu alinafe chiwembu chilichose chimene akupanga mulungu akuchiika poyera tiyeni tipephere mokweza mulungu alinafe

  • @Samu-q3z
    @Samu-q3z 2 місяці тому +1

    Limpopo number 1 sirens

  • @Mikekachigamba
    @Mikekachigamba 2 місяці тому

    Ntanyiwa umanivetsa kukoma ndipo nimakonda for ever❤

  • @SonMontieDamiano
    @SonMontieDamiano 2 місяці тому

    🤣🤣Zafika pokuti antha kumukhwimira sikono sopano 😂😂😂

  • @RitaKainga
    @RitaKainga 2 місяці тому +1

    Yomweyoo azibambo mwaimba bwino kwambiri! Salute Comlade

  • @EsnartMalewa
    @EsnartMalewa 2 місяці тому +1

    Eeeeee mpaka kwa nsing'anga😂😂😂

  • @munashemoyo4190
    @munashemoyo4190 2 місяці тому

    Makandulo ayake bas akumva kutentha thupi mwake satana 😂😂😂

  • @BlessingsTembenu
    @BlessingsTembenu 2 місяці тому

    Kkkkkk kumalawi kulibe kupuma,satana chokere yemweyoooo

  • @AhmadumkomaTambala-lr9gp
    @AhmadumkomaTambala-lr9gp 2 місяці тому +1

    🎉🎉kod Abale tizangolusa ndikuwathamangitsa obwelawa

  • @PeterThomas-o9k
    @PeterThomas-o9k 2 місяці тому

    Umakwana ine zayatsa wanga Candle wakuda ndi yellow kumaliza kupempherako aziwe
    Kuti chawera ndi ntembo peter Thomas port Erazabeth we sick & tired because of him chakwera

  • @johnkanyika9465
    @johnkanyika9465 2 місяці тому +1

    More fire Ntanyiwa. Kodi ayamba kale kikhwima hetii

  • @AlgentChilanga
    @AlgentChilanga 2 місяці тому

    Kain kain iwe amalawi awuzeni komwe munamubisa chilima
    Limpopo FM ndi imeneyi ndimaziwa ine with comrade ntanyiwa kp it up Mr God bless wherever you are.
    Koma iwe I
    Kain mwazi wa chilima ukukanthe uziona Chaka chake nchino

  • @FosterChinzimuBanda
    @FosterChinzimuBanda 2 місяці тому

    More fire Ntanyiwa❤❤❤❤❤

  • @augustMag
    @augustMag 2 місяці тому

    Inu ndi mtunda akatundu oyankhula Chilungamo chokha chokha Limpopo FM ndi Ntanyiwa 🔥🔥♥️

  • @KunyengaMoyo
    @KunyengaMoyo 2 місяці тому +4

    Mukamva ndafa mmudzimu, Chakwera wandipha. Uyu ndiye andipha

  • @kennethkaunda3636
    @kennethkaunda3636 2 місяці тому

    Ndipo ndikuweruka ❤❤

  • @Jessica-pg6ep
    @Jessica-pg6ep 2 місяці тому +1

    Zoona ma candle aziyatsidwa masana tizitha kumaona chikubwela mfundo yabwino.

  • @AdamLano-sj1gv
    @AdamLano-sj1gv 2 місяці тому +4

    Osamasowa Mtanyuwa ❤ u masiku akupitatu awa hot hot tsopano

  • @AbudulJohn
    @AbudulJohn 2 місяці тому

    Koma mukazawombela Atupele ziwani kuti tsiku lomwelo muzasamuka ku state house kukhala ku Chile ndinena ndi inu

  • @PatrickAnusa
    @PatrickAnusa 2 місяці тому +6

    Zikavuta toyasa khuni 😂😂😂😂aonaso

  • @Mikekachigamba
    @Mikekachigamba 2 місяці тому

    Koma ntanyiwa umanivetsa kukoma ❤😂😂😂😂😂

  • @DicksonChibisa-w1v
    @DicksonChibisa-w1v 2 місяці тому +1

    Mavuto kuwaputadala Anthony osalakwa vuto nimagazi adawalowelela alandila zolowazawo mulungu adaona zone amen

  • @StiveKantiki
    @StiveKantiki 2 місяці тому

    Nkhani ndi kaini chilima alikuti iwe😭😭😭🔥🔥🔥

  • @eunicesaiti
    @eunicesaiti 2 місяці тому +3

    Welcome bwana, following.

  • @Francismitengo-w6s
    @Francismitengo-w6s 2 місяці тому +3

    AYEREKEZE KUOMBERA ALIYENSE MWA ASOGOLERI AMENEWA TIKAGUMULAPO STATE HOUSE TRY IT SITIKUOPA AYI🎉🎉🎉🎉

  • @AlgentChilanga
    @AlgentChilanga 2 місяці тому

    Manganya wauyasa ulendo ndi Richard chilundi Banda wakwasing'anga kkkkk

  • @clementchatepa
    @clementchatepa 2 місяці тому

    Waimba ndani tipange download...ndaikonda

  • @ChifundoGalusa
    @ChifundoGalusa 2 місяці тому

    Following from Armageddon

  • @FelixMachika
    @FelixMachika 2 місяці тому +4

    Mukapha ena, muphenso tonse, mutsalepo nokha pano. 😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭👀👀👀👀👀👀😎😎😎😎😎😎

  • @RuthMushauri-ck5qr
    @RuthMushauri-ck5qr 2 місяці тому

    Mthanyiwa more fire

  • @JowasiMasina-fy8ji
    @JowasiMasina-fy8ji 2 місяці тому +2

    Nthnyiwa iweyo mulungu akupatse moyo wautali aboma ndi zisilu

  • @JackieJamson
    @JackieJamson 2 місяці тому

    kma Limpopo ndayikonda

  • @CHIWSABINYAMBOSE
    @CHIWSABINYAMBOSE 2 місяці тому

    Moore fireeee😊

  • @shanlaljith5389
    @shanlaljith5389 2 місяці тому

    Akadulitsa kandulo tiyatsa nyani using paraffin akakwezanso tizikadzula udzu kutchire kumayasa till the truth come out and face consequences kaini gwenembe🙄

  • @Jamesmwale-iz4ri
    @Jamesmwale-iz4ri 2 місяці тому +8

    Mwaswela bwaji anthanyiwa

    • @AlgentChilanga
      @AlgentChilanga 2 місяці тому

      Kumupasa moni mnthu wankulu kp it up kkkk😊😊

  • @MerryMphande
    @MerryMphande 2 місяці тому

    Ndipo ndiyatsadi masana ma candle

  • @THOCCOChimbali
    @THOCCOChimbali 2 місяці тому

    Chakwela unya manyi 2025 nyau party out forever

  • @benjaminjobo3525
    @benjaminjobo3525 2 місяці тому

    Nyimboi Antanyiwa tikuifuna zedi tipatsen link

  • @AlexKaunda-ny2eg
    @AlexKaunda-ny2eg 2 місяці тому +1

    Kodi chakwera unasiya kuyenda kunja pomakatha 4years kuchoka Lero pa July 15 ndidzakhala ndi takupedza man iwe udzisaka enao ine (I'm looking for u 😢😢😢

  • @gladyschisomo4324
    @gladyschisomo4324 2 місяці тому

    Kodi mwati amakatani kwenikweni ku lingadziko apulezidentiwo komatu akumana nazo ulaliki opposite nyimbo opposite madzimadzitu

  • @JosephWeruzani-o9h
    @JosephWeruzani-o9h 2 місяці тому

    Kkkkkkkk comrade umakwana

  • @GRACEKHOLOWA
    @GRACEKHOLOWA 2 місяці тому

    Koma nyimboyi sidayimbidwe ku Lingadzi ndiyachigwirizano chabambo

  • @mikellzaithwa8602
    @mikellzaithwa8602 2 місяці тому

    Mtanyiwa akumva nae kuwawa

  • @AlexKaunda-ny2eg
    @AlexKaunda-ny2eg 2 місяці тому +3

    😂😂😂 chakwera ndi opusa size

  • @AlgentChilanga
    @AlgentChilanga 2 місяці тому

    Nyimboyo osazayiwara pa kampeni ikubwera Mutu wake Kain Kain kapena iwe chifunga

  • @ThokozaniMaulana-oi5hz
    @ThokozaniMaulana-oi5hz 2 місяці тому +1

    Ntanyuwa mulungu adzikusunga ndi kukuteteza chifukwa zambili popanda iweyo zikanachitika..koma chilungamo cha nkhaniyi ya kuchikangawa chidzadziwika boma likasintha

  • @Margaret-t7m
    @Margaret-t7m 2 місяці тому +2

    😂😂😂😂😂😂😂😂 mwazi wa munthu simasewela ayi sanati

  • @SafariBvumbwe
    @SafariBvumbwe 2 місяці тому

    Ndipo mcp yalozedwa ndinthu

  • @StanleyMayenda
    @StanleyMayenda 2 місяці тому

    Ife tikupeohereea Malawi wathu..

  • @staindulamanja1218
    @staindulamanja1218 2 місяці тому

    Yomweyo mtanyiwa

  • @matembomkhalipi870
    @matembomkhalipi870 2 місяці тому +3

    Visambwazeni viwanthu vakupha ivi

  • @ChristopherKalumbu
    @ChristopherKalumbu 2 місяці тому

    Abwana masiku 4 osafika mmmm koma takunyadilan

  • @DevisonHala
    @DevisonHala 2 місяці тому

    ❤❤❤❤

  • @austintonnymauricemlolowa1050
    @austintonnymauricemlolowa1050 2 місяці тому

    🤣🤣🤣🤣🤣 tiziyatsadi masana ma kandulowo

  • @ThokohPrescotKalonga
    @ThokohPrescotKalonga 2 місяці тому

    Nice song 👍💪💪🇲🇼

  • @louismagongwa
    @louismagongwa 2 місяці тому

    😂😂😂😂😂😂😂😂 abhiyeni munawaphelanji

  • @romanandrewmusic3989
    @romanandrewmusic3989 2 місяці тому +1

    Akhawura chakwera 2025 kupha athu asarakwa ineso pomwepa pazambia ndikuyatsa makendo😢😢😢😂😂😂😂❤❤❤ ndimakuva tanyiwa

  • @AjibuTwalibu
    @AjibuTwalibu 2 місяці тому +3

    Mmm koma mtanyiwa

  • @ClaraChimwaza-u8f
    @ClaraChimwaza-u8f 2 місяці тому

    Koma sanathe apitanso kwa yaya sanathe

  • @REXCHARLESKAJAWO
    @REXCHARLESKAJAWO 2 місяці тому

    😂😂😂😂 zafika pomapita Kwa asimg'angaso? 😂😂😂 A vice president 😂😂

  • @EdwinPhiri-ee4sn
    @EdwinPhiri-ee4sn 2 місяці тому

    Malawians must work up Malawi is not is not a company of Chakwela

  • @HoseKatsekera
    @HoseKatsekera 2 місяці тому

    wina apenga misala kkkkk

  • @SaidiAdamu-c6i
    @SaidiAdamu-c6i 2 місяці тому

    Real nkhanga zaona

  • @DavieMasowo
    @DavieMasowo 2 місяці тому

    zowooona kumayatsadi masana ambuye ali kumbali yanthu llv limpompo

  • @jamessheki4293
    @jamessheki4293 2 місяці тому

    Aaaa nzeru palibe man,koma ku DRC akayiwerenga kkkkk

  • @lyiemax
    @lyiemax 2 місяці тому

    Powerful 💪💪💪

  • @IssaBwanali-v6r
    @IssaBwanali-v6r 2 місяці тому

    Next year yatalika alamula bwanji ma percentage atatsika achoke pompano

  • @MaxWell-d7o
    @MaxWell-d7o 2 місяці тому

    Ntanyiwa woyeeeee🎉

  • @CharityChirwa-t1e
    @CharityChirwa-t1e 2 місяці тому

    Tidikila inu antanyiwa azayasidwe basi

  • @kennethkaunda3636
    @kennethkaunda3636 2 місяці тому

    Pafupi ndi mount view lomwe ndimaphunzira kkkkk Kwa agogo Ake athoko😂😂😂😂 Kwa gulumba

  • @rennieyoublessmewiththisso4981
    @rennieyoublessmewiththisso4981 2 місяці тому

    Komaaaaa

  • @MarkGonda-qr4vm
    @MarkGonda-qr4vm 2 місяці тому

    Mpaka kwa ng'anga

  • @MillicaBanda
    @MillicaBanda 2 місяці тому

    Makwana matimilira

  • @IsmaelBilal-lh1pi
    @IsmaelBilal-lh1pi 2 місяці тому +1

    Osatiyiwala ku Durban kuno tilipo ambiri. Tisayaze makandulo 😊

  • @YusuJames
    @YusuJames 2 місяці тому

    Ntanyiwa sangamupeze ndipo tilimbali yake Ntanyiwa bwerani muzasake muzionela nokha kmwe kuno kut aphedwe ndani tikudikila inuyo kuno

  • @dondamissonchdziwe3958
    @dondamissonchdziwe3958 2 місяці тому

    What profit if, some one kill some body, the results is chilango Chifukwa chilango Chima yambira pansi pomwe pano, Chakwera amaganiza zoti wabisala Osaziwa Kuti pa maso pa Yehova palibe chinsinsi, Yudas ada zipha yekha Chakwera azipha Chifukwa choipa chisata mwini,wa Chipani chaMcp ayembe keze kuona mazanga zime

  • @CathrineRamseyJafaal
    @CathrineRamseyJafaal 2 місяці тому

    Ndiye mukuti bambo asikono anali kokhwima yoooooo!!!!????

  • @EllenNgoon-nc8vg
    @EllenNgoon-nc8vg 2 місяці тому

    Amutanyiwa makenduro tiyasedi kuno koma nafeso kuno tikufuna ti voter nawoooooooooo🎉🎉🎉

  • @bensonmughandira
    @bensonmughandira 2 місяці тому

    MDF ,ngati ndizoona kut mdzko muno muli zigawenga methane nazo

  • @janemanyamba7201
    @janemanyamba7201 2 місяці тому

    Udindo wamasiye omwewo mpaka kunkhwimila koma akuyendadi ndi nzimu wa ma drama basi

  • @RuthChilobwe
    @RuthChilobwe 2 місяці тому

    Eyadi makandulowa muziyatsadi masana kuti oipawa adzioneka .kuli koyera..zoonadi Antanyiwa

  • @PeterMaulana-qk5uq
    @PeterMaulana-qk5uq 2 місяці тому

    Nae mosesi kunkuyu kungosiya kuonesa video show kwamanase anvekere mcp yomweo,!!! Wanya

  • @mbzoonly298
    @mbzoonly298 2 місяці тому

    Nyimbo imeneyi title yake ndi chani

  • @chimwemwenkute3839
    @chimwemwenkute3839 2 місяці тому +3

    Wachikulire timakunyadirani

  • @ClaudiaarmandoMafunga
    @ClaudiaarmandoMafunga 2 місяці тому

    Koma yah ntanyiwa umatha

  • @MiddayDeleza
    @MiddayDeleza 2 місяці тому

    More fire ntanyiwa mumatiyimilira ngakhale ena amaona ngt mukunama
    Asilikani changa ukani chonde, candle boladi masana