Розмір відео: 1280 X 720853 X 480640 X 360
Показувати елементи керування програвачем
Автоматичне відтворення
Автоповтор
Chimbo kuchita kuveka bwino uyu ndi oimba amene saguga ndipo sadzaguga Respect 🫡
Sir Evans Meleka, uyuyu saizi yake ndiyeyo mwiniwakeyo, uyu sound amakuntha sizachibwana ndipo alibe mantha ndi akalungusese!!! brilliant song!!!
Size mulibe kunkhan yoimba bro ulemu wanu 🙏🙋 nyimbo iyi mwaswaaa
I saw some years ago performing in Stellenbosch (kayamand) Capetown, I like his songs
Oyimba yekhayo ndimamusatira bwino lomwe ,,, keep it up bredah
Mistake ndi kamodzi ndithu Beautiful song ulemu Wanu 🙏🙏
Mbali yako wanena ndasala ndiineyo big up Mr meleka love kuno cape town
Keep the fire burning Nthumwi ya Amphawi...May the good Lord Our savior Jesus Christ bless your talent
He never disappoint Malawian we really appreciate meleka ur song ❤ tisankha mwanzelu 2025 oyimba koma awa osati manyaka apita ku mcp kutsatila ndalama
Mwapanga mbariyanu bro kwatsala kwaife kuchitamwazeru
Kumbali yake wamenya nkhondo
Evans wapangadi kumbali yake kwasala kwaife a Malawi kuti titenga mbali yanji.
Koma chiinyimbo ichi aii🙌👏👏❤🔥🔥✅ my brother 🎉
Bola Dpp timawolesa chimanga zoti chiteze chakudya taziwa pano km Mulungu watipasaso mwayi
Uku ndiye kuyimba osati zakumidima zija😅😅😅😅😂😂😂yomweyo Chikangawa
😅😅😅😅eeet
😂😂😂😂😂😂😂
😀😀😀😀😀
Stellenbosch Cape town,l need you again here please, nyimbo mwamphaa,ndipo basi tingobwerera ku DPP
Nyimbo ilibho it needs to understand deep mwaphuma sungaimvetse Ai ❤
Dolo ka million, mawu amamveka bwino kwambiri
Nyimbo yabwino kumbali yanu mwachita bro kwasala kwa ife
Uthenga suposa apa aliye aziganizile yekha pazomwetaziwona komaso pazomwe tudutsamo nice one song 🎉🎉🎉❤
My favorite artist in Malawi Evance Watsopano Meleka.Ndimakunyadirani
Oimba ozozedwa uyu respect Mr Meleka nice song agonthi tikhalenso ife tisakamve
Moto moto moto ! Keep it up mumatha inuyo
Mwatipanikiza ndi nyimbo zokomatu bwana keep it up
Awawa ndi big man🔥🔥🔥
Watching from Johannesburg lets support this
LEGEND ❤❤❤❤ LOVE YOU I WILL NEVER MAKE MISTAKE AGAIN
Mbambande 🔥🔥🔥 simungagule oimba onse
Evance meleka ndimamuziwq ndi uyu keep up.bro nice song 🎵
Uyu ndie waimatsula MCP koopsa mmmmmmm munthu owopsa uyu zedi osakomedwa ndi ndalama koma Chilungamo ❤❤
Malawi as a country, we are proud to have a talented man like you brother evance keep it up
utm may vot
Tikamati dziko tili ndi madolo ndi awa❤
inuyo mulibe size yanu ku malawi kuno pa nkhani zoimba eish am short of words
Mistake ndi kamodzi ,onse ndi akuba koma ena sikukhala kuba koma kupakula😢😢😢
Machine Evance Mereka waimba iweyoo
Meleka umatha iweyo
Dolo kwmbri, sitireti to the point mwee My fellow Malawians uthenga nd umenewu 👏
I like your song malume keep it up osati oimba adyela achina Dan lu mkasa mlaka anthu awa ndi ma kape
Nyimbo yatathauzo, you are blessed brother💯💯
Legend never bore,, umakwanaaa Evah,, that's why I love you and I will forever ❤
Panopa oimba mmalawi muno ndi awiri basi Evance ndi mlaka nyimbo zao ndi za mzeru
Zoona evas mistenk nkamodzi wanenatu muthuyi
Namandwa wa oimba kwa oipa onse usazafe E, Meleka kulibe kuvota kwa mistake the blues
❤❤❤❤❤❤❤ Kom mau awa ndikapanga chibwana kachikena ndizamukumbukaka Evance
Eeeeeee koma yaaaah 😂😂😂😂😂 wa MCP akunva pain 😂😂
The true son of the soil, Evance Watsopano Meleka🫂🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Indeed ndiwe osakhika mmaimbidwe brother machesi alindife tiona mmene tiyasile,enawa anangozapakula basi
God bless you Evanc mmmm kulirila tuntu wa amalawi
Mtengeni Dan yo Ife Tasala ndi Evans meleka
😂😂😂😂 Amtenge Danyeleyo😂
😅@@SamKaposa-i5c
Koma guys kkkkkkkkk
Brother😘🗣🗣 god bless you😍😍sound yaveka iyi💃💃💃💃
Amati agula oyimba mmmm awa ndi mashin bambo amakamba😂mbali zonse kut tipange chisankho tokha thanks God bless you evance 🙏
Big man what a great message Malawi tisegule maso
Nyimbo yabwino kwambili zonad watipasa Mwai ambuye Kut tisankhenso😅😅😅😅😅😅
Ku Ndirande Kuja musazakudelele.... Makina opangila Makina anzake... Iyiy ndi capital hill payokha #Meleka on fire
Ndipo safalawoyo😂😂😂
UTM my vote❤❤❤❤❤
Ndipo inuyo ndi daliso wanu bas umenewu bwana ❤❤❤❤❤
This guy heshi!ambuye azikutetezani
Iiii😮! Koma nkulu ameneyu na kuzoimba za mfundo zogwilika ndi dolo, waposa skeffa ndi dan lu , big up
Ndikuti uyuyu Amatha ndipo zaiye Tikambe ndifeyo 🔥🔥💪
Koma ichichi chili ndi mzeru🎉🎉 mistake ndikamodzi kachiwiri zimakhala zadala sure 🔥🔥
Uyu nde evance meleka ndikudziwa ine amayisiya ndalama apo wadzeru wadziwa akutathauza
Nyimbo mbambande, I salute you Evance Meleka
Ulemu wanu brother Eva's ndinunokha olimba mtima we support you my brother
Real Malawian ❤❤❤❤ you evance osamakhala ndi dyela 🔥🔥🔥🔥
Uyu ndiye amavomereza zomwe alinazo yehova akupambanise kuposa pomwe unari
As an upcoming gospel artist, I learn a lot from Meleka's song composition. God bless you brother.
Sizachibwana bwanawa amatha kuimba aaaaa eeeee AMATHA BWANAWA
True legend,iyi yokha wabaya msomali pa liwombo ,umatha aise
Mumaitimirira Mr mpeleka I am proud of you
Ndizoonadi ifeyo tichite mwadzelu ndayikonda nice song
Salute powerful message God bless you evans
Ansaaaa 💜💜 Amalawinu iveleni bwino nyimboyi ikuthandizani!
U good for everything this is deep true
Iweyo ndi fire 🔥
Bravo evance powerful massage i❤ this song
Keep it up man Marika, from jons
More 🔥🔥🔥🔥 Mr Meleka
Powerful song mr Mereka 🔥 🔥
Kuswakuswa,,,,,,Amen and Amen again 🙏 🙌
Powerful! Maintain the hype Evans!
What a powerful massage is!!
Emeniiii nice one
Ulemu wanu mr meleka .timenyeleni ufulu kuzela mmaimbidwe bwana .
Nice song bro kuimba kuzitero osati nyasi zinazi DPP my vote 🔥🔥🔥🔥🔥
Amen❤❤❤❤❤ watipasaso mwai wina ambuye
From oyimba uyu anabadwa oimba osati za patsi panyanja good songs guys iiiiii
😮mumakwana wakulu 😊
Blessed Guy your very handsome u never change ur mind🎉🎉
Nice one bro keep it fire
Nice so song
Keep it up brother
Mmmmmmm bro iyi mwapha kwa basi ❤❤❤❤❤❤❤❤
You have a lovely heart Eva. God bless.
Uyu apweteka gulu ❤❤❤❤
This is nice song Mr Meleka
Nice song brother inuyu ndi nkhani zina
Powerful message Mr Evans Meleka🎉🎉
Powerful message meleka keep it up
😂😂😂😂 This one is outstanding 🥳🥳🥳
Uthenga waveka kaka mulungu akudalitseni kwambiri ❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤
❤❤❤❤❤it deserves to be on repeat
Wabwinoko ndani aaa Inuo big man mwanena basi
❤❤ great composition bro
Chimbo kuchita kuveka bwino uyu ndi oimba amene saguga ndipo sadzaguga Respect 🫡
Sir Evans Meleka, uyuyu saizi yake ndiyeyo mwiniwakeyo, uyu sound amakuntha sizachibwana ndipo alibe mantha ndi akalungusese!!! brilliant song!!!
Size mulibe kunkhan yoimba bro ulemu wanu 🙏🙋 nyimbo iyi mwaswaaa
I saw some years ago performing in Stellenbosch (kayamand) Capetown, I like his songs
Oyimba yekhayo ndimamusatira bwino lomwe ,,, keep it up bredah
Mistake ndi kamodzi ndithu
Beautiful song ulemu Wanu 🙏🙏