Mwinadi a Triephornia Mpinganjira adakwatiwa mcholinga chongofuna kusakaza chuma cha Bwanawa kapena.

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 8 жов 2024
  • Kuchoka pamene Mayi Triephornia Benda adakwatiwa ndi Chikhwaya cha M'dziko La Malawi a Thomson Mpinganjira zaambiri zakhala zikukambidwa, ena mkumati mayiwa ndi Gold-digger chabe. kodi izi ndizoona? zambiri ziri mu video iyi.
    yakonzedwa ku : 265entmag.live/
    Mukafuna kugula katundu wa origina okongoletsa khungu ochokera ku UK ma products monga body lotions, Serums, Body Creams, Deodorants ndi zina zambiri, ayankhuleni a Mastoura Cosmetics..
    Tsamba lawo la Facebook lili apa web.facebook.c...
    Iwowanso ali pa TikTok / mastouracosmetic

КОМЕНТАРІ •