Umu ndi momwe a Prophet Bushiri adapezera ndalama, za dziwika

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 8 жов 2024
  • A Bushiri ndi munthu olemera kwambiri mu dziko la Malawi komanso Africa. Iwowa pamanveka mphekesera zosiyanasiyana zokhudza chuma chawo. mu video iyi tikuona momwe iwowa adapezera chuma chawo.
    Check magazine website: 265entmag.live/
    Radio Website : radio.265entma...
    Company website: agency.265entm...

КОМЕНТАРІ • 22

  • @IbrahimMatola-h4i
    @IbrahimMatola-h4i 3 дні тому +4

    Pastor wasatana ameneyo osati wa mulungu ai komaso mboliyamake munthu oipa ameneyo mukamadya ndalama za ameneyo chifukwa cha umphawi umphawi wanu sudzatha vomelezani kukhala mphawi koma ndalama za bushili musalandire

    • @SiphiweTonnyChidumayo
      @SiphiweTonnyChidumayo 3 дні тому +3

      Makolo ake sizikuwakhuza amakana anything from him akuvutika kwaoku fukwa akuziwa kt mwana wao sali straight

  • @VanessaThomas-jm6eq
    @VanessaThomas-jm6eq 10 годин тому

    Mmmmmmmmmh no comment only God knows

  • @alicembetewa5151
    @alicembetewa5151 10 годин тому

    akufuna attention ku channel yake,😮😮😮

    • @265ENTMAG
      @265ENTMAG  10 годин тому

      @@alicembetewa5151 ndichifukwa timatulutsa content

  • @Jessica-tc7rf
    @Jessica-tc7rf 3 дні тому +1

    Mukudziwa ndinu mukunenanu😂😂😂😂

  • @VitumbikoKaunga
    @VitumbikoKaunga День тому

    Simunthu wa mulungu Uyo

  • @patrickphwete
    @patrickphwete 4 дні тому +1

    The truth is with him and God we have no idea 🙌

  • @ElisaMkandawire
    @ElisaMkandawire 3 дні тому

    Only GOD knows

  • @ChimwemweSauka
    @ChimwemweSauka 3 дні тому

    Bushiri akufuna kuno ku South Africa waba kwambiri ziko lino.

  • @SirpromiseMatabwa
    @SirpromiseMatabwa День тому

    Ndi njoka iiii inu simunthu akudikilira moto awa jahena

  • @FWhite-w3l
    @FWhite-w3l 7 годин тому

    Akulu inu ngabonza

  • @VitumbikoKaunga
    @VitumbikoKaunga День тому

    Machende ako kulimbikisa usatanc

  • @PeterBanda-dw6yf
    @PeterBanda-dw6yf 3 дні тому

    Only God knows

  • @HusseinBinali-z1s
    @HusseinBinali-z1s День тому

    iwee uyu ndi wa satanic not izoo ukunama akupasa zingati kodi uzindifunsa ine bwino uwoneka anakupasa ndalama

  • @ThandohThembieJuly
    @ThandohThembieJuly 3 дні тому

    Mmodzi mwa anthu osaziyanganirani pansi kuno kumalawi.

  • @kondwanivyalema9449
    @kondwanivyalema9449 4 дні тому

    WAKUBA ALIBE MALEMB MBA PROGRAM YOU SO 😢

  • @patriciajangaza675
    @patriciajangaza675 3 дні тому

    Akudziwa ndi mulungu

  • @HellenKanyemba
    @HellenKanyemba 4 дні тому

    Mulungu yekha ndiye odzuwa zonse

  • @KingDavedNkhata
    @KingDavedNkhata 2 дні тому

    Inu koma inu Satan uyu inu osamati prophet
    osamangofuna kutchuka kuti mumaulutsa nkhani palibe chanzeru apa

  • @ChimwemweMuhelliwah
    @ChimwemweMuhelliwah 4 дні тому

    Zopusa

  • @ElsaMalunga
    @ElsaMalunga 3 дні тому

    Watani munthuwu ndiolimbikira musiyine mukufuna kuziwa kumene anakatenga ndarama buzi nose musiyeni ndiolimbika