Nchifukwa Gwamba ali olemera kuposa oimba onse a Hip Hop Ku Malawi.

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 8 жов 2024
  • Program yakonzedwa ku 265entmag.live/ ndipo inapangidwa air live pa radio ya radio.265entma...

КОМЕНТАРІ • 16

  • @MwanaWachawuta
    @MwanaWachawuta 6 днів тому

    Grace chinga anaziwona kare izi awa ndi kumudima
    Opindura ndi kupeza dziko lapansi koma ataruza mzimu wa chowoonadi
    Galatians 6:7

  • @WalesAkazianyenga
    @WalesAkazianyenga 7 днів тому

    Nanga ndalama zopatsidwa ndi alamu awo zingafanane ndi zopanga okha

  • @johnyassin-je8rv
    @johnyassin-je8rv 13 днів тому +1

    satanic chisisi chaketu amafuna muthu olimbikipa cholinga azibisa mawanga eetu ndiye khaniyake

  • @zafarIqbal-p7h2k
    @zafarIqbal-p7h2k 14 днів тому +1

    this presentation is not cool enough much like NDAKATULO ....TRY TO CHANGE THE WAY OF PRESENTING OR COMMENTATING A PROGRAM ACCORDING TO THE NATURE OF IT

  • @LastonMlozi
    @LastonMlozi 15 днів тому

    Uyu ndi marketer weniweni great gwamba

  • @JuniorHala-vf9ov
    @JuniorHala-vf9ov 13 днів тому

    Paja ndi Mula wa bushili nde mukudabwilanji

  • @AbudulJohn
    @AbudulJohn 14 днів тому

    Fwamba ndi dolo komaso Gwamba samafuna kugwilisidwa ntchito ngati tishu kungosetela ndi kutaya ngati achina Dan lu ndi aziwo uyu ndi big

  • @rashidlamos3403
    @rashidlamos3403 14 днів тому

    Ndiye kut ndi olimbikira ma business komanso zoyimba eeetu nankha chan

  • @johnyassin-je8rv
    @johnyassin-je8rv 13 днів тому

    khani ndalama zimachokela kwa bushili musamapusitsike naye sinanga zimakhala zochokela kumidima ndichifukwa macampani amabwela muzidziwa zinazo amangobisalila eetu inu mukudziwa kale kuti gwambizo ndi wasatanic osamagona panyopakeso galu ameneyo

  • @HappyAbyssinianCat-xt2bm
    @HappyAbyssinianCat-xt2bm 13 днів тому

    Gwamba ndi wa satanic akuyenera kukhara ndi ndalama komaso ochuka paja akumidima amakhara ochuka

  • @johnyassin-je8rv
    @johnyassin-je8rv 13 днів тому

    anamwakale magazi ameneyo

  • @Johnybegood260
    @Johnybegood260 15 днів тому

    The thing is many us are busy concentrating on other peoples life instead of their own

  • @ChancyPolokela-bo2eq
    @ChancyPolokela-bo2eq 15 днів тому

    Chifukwa chake ndi satanic osat zanuzo

  • @goodwellnyirenda651
    @goodwellnyirenda651 15 днів тому

    Olemera salipila rent

  • @ChancyPolokela-bo2eq
    @ChancyPolokela-bo2eq 15 днів тому

    Chifukwa chake ndi satanic osat zanuzo