The DC mwana owopya kwambiri 4rm mj kkkk umakwana. Gyz ine ndikufuna tsiku la mademolo yolamu akakhaleko osati zisilu akumadzitumazi, ndikufuna zikhale komanso uyu wanyenga mkazi wa dan lu.Anthu atatuwa ndimafuna akabweleko ku mademoku tikadziwane mitima cifukwa akuona ngati malawi ndi wa amawo.
Iwenso nde umavutikatu iwe,kodi umalipilidwa zingati??aaaaaaaaaaa, daily kutulutsa audio kukhala ngati ndi Bible kt likupindulira aaaaaa, unatikwa a ife iwe
Ndifunse nawo lero funso Lopita kwa Bon kalindo; ndicifukwa cani every day mumakhala ndicoyankhula?? Kodi kampeni ikatha muzakhalanso ndicoyankhula motere??? Muli UCI wanji kodi kumbaliku??? Every day simusowa nkhani,olo mwana kulakwako nde mmmm every day kulakwa???
Ndiponso ndichitsilu kwabas iwe boon kalindo amamenyela ufulu wa amalwi iwe dziko lino likuyenda bwino boon kalindo sangayankhule kalikonse ndiwe upusa bwanji Iwe ukuona ngat dziko lino likayenda bwino anthu angayankhule chilichonse ndiwe chitsilu pat we love bon kalindo any way
OC,ABWANJA!! FROM MANGOCHI T/A JALASI.Auzeni zoona ndipo ife tatopa nazo izii
Sumalakwisa Born ing'alure bas
mumakwana inuyo , ❤❤❤❤❤❤❤
Born Kalindo you are a strong man 😂😂😂
The DC mwana owopya kwambiri 4rm mj kkkk umakwana. Gyz ine ndikufuna tsiku la mademolo yolamu akakhaleko osati zisilu akumadzitumazi, ndikufuna zikhale komanso uyu wanyenga mkazi wa dan lu.Anthu atatuwa ndimafuna akabweleko ku mademoku tikadziwane mitima cifukwa akuona ngati malawi ndi wa amawo.
DPP moto moto ,Bon kalindo ❤ powerful
Dpp inapangapo condemn ndizilwanje nthawi yawo? Kalimdo just get water and bath please
Long leave the DC✊
The DC man of the moment Munthu owoopsa kwambili
The DC ang'alulen agalu amenewa
mmm a bon kalindo amene amalanditsa ndalama ndi a dpp kuno zimenezi ziliko amatengaso anthu kuti azikalembetsa ndikuwaptsa ndalama nde zichani zimenezo ine singavote chifukw Mwatiputsitsa kokwanila
The DC Boooon Kalindo akatero wamaliza kuying'alura 🔥🔥🔥🔥
Osamaiwala zomwe ena anachita mmbuyomu bwana Kalindo
Bwana kalindo mmandidabwisa kwambiri...last time mumkati mmalawi simunthu omufela ndyeno pano bwanji mukumabwela ndi mfundo ngati zofuna kufela amalawi omwewo????
Nanu munali kut mene amayankha zimenezi?bush
Plessident wamanyi zamuvuta kape ameneyu
More Fire 🔥...The DC.....Osaopa..osafooka ...❤❤❤❤❤❤❤❤
Dzilimbikirani zanu athu awa amadziwana amadyera limodzi mudzangovurara zaeni ose awa ali bwato limodzi asakupusitseni malawi mzanga look forward keep eyrs open vula mesho yakoh fwethuu😂😂😂😂😂😂😂😂😂
Sir zikomo mumatiimirira Malawi's
You are number one DC this is Manyaka President
We love Mr boon kalindo we are on your side chifukwa mmatiimilila ife amalawi
Koma police yamalawi chito yawo ndiyo manga Amalawi first???? Tsoka kwainu apolice
Mba en mbe😅😅
iwe kalindo tamaganiza
sitisitha boma imfe timangositha munthu l love you boooooooo kalindo kulimbana ndi zithu zosatheka kalindo ndimamukonda kwambili musamataye thawi kulimbana naye tiye ukoo
Mbebaka
More fire 🔥🔥🔥 born
Aborn karindo more fire 💯
Popita kumademoko osaiwala zikwanje kuti ikakhale 50:50 ,uku zikwanje,kwinakonso zikwanje
Umakwana boss wanga
Inu bwana Mulungu anakudalisani kwambiri,, chifukwa mukuyakhura chulungamo ,, Mulungu akudalitseni ❤
Mofaya❤❤❤❤
Umakwana DC,,,,,
Km kalindo umalimba ntima ndichani apele kuwauza kt kuwanyudza nchoncho xool yamuvutadi pamenepo chulungamo chimawawa
😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂❤Koma ichi ine
Bodza DPP inachita condn ndani Peter Mutharika atapha malubino?
Facts
The DC 💥🗡️💥🔥🔥🔥🔥
Go aherd bon kalindo thats him
Osawopa 🔥🔥🔥
Kkkkk😂😂😂😂😂😂 koma The DC simunthu wamba
💪💪💪💪💪🔥🔥🔥🔥🔥💯
Chomwe mungadziwe ndi ichi boma sitisitha koma timasitha chipani
Bon kalindo ❤❤❤❤❤
Wamisala wamkulu
❤
Boma ndi lomweli boma lake liti taonatu maboma ife mmalawi muno ili ndi boma lomwe lalephereratu
Kukhapana kukhapana game ndi zikwanje
Amandawala!😅
Koma ng" oma yolira kwambiri sichedwa kung'ambika, dikirani zimene zichitike
We are of the same view the DC.
Dr Kabambe omwewooooo
Osauka ngat iwe angapange zaiwe ndani
Iweyo ndolemera???
koma iwe tili limodzi awa akufuna ndalama
Kkkkkk koma iwe
Kulibe police kumalawi kuno
Koma ichiso kkkkkkkkk
Iwenso nde umavutikatu iwe,kodi umalipilidwa zingati??aaaaaaaaaaa, daily kutulutsa audio kukhala ngati ndi Bible kt likupindulira aaaaaa, unatikwa a ife iwe
You can skip his videos or audios,nobody akukukakamiza
Ndifunse nawo lero funso Lopita kwa Bon kalindo; ndicifukwa cani every day mumakhala ndicoyankhula?? Kodi kampeni ikatha muzakhalanso ndicoyankhula motere??? Muli UCI wanji kodi kumbaliku??? Every day simusowa nkhani,olo mwana kulakwako nde mmmm every day kulakwa???
Iwe ndi galu ngati watumidwa ukawauze akutumawo kuti alephera
Ndie wat akawauze kt pachan pawo
Funso lopusa limenero ndipo nzeru ulibe chitsiru chamunthu ur nt malawi iweyo unakakhala mmalawi sungafunse funso lopusalo wamva mbunzi yamunthu iwe
Ndiponso ndichitsilu kwabas iwe boon kalindo amamenyela ufulu wa amalwi iwe dziko lino likuyenda bwino boon kalindo sangayankhule kalikonse ndiwe upusa bwanji
Iwe ukuona ngat dziko lino likayenda bwino anthu angayankhule chilichonse ndiwe chitsilu pat we love bon kalindo any way
Mapwala akonso patiiii pamodzi ndi chimwendo wakoyo
koma Malawi police
The DC!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!! fire 🔥 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Kkkkkkkk km kalindo anakonza
😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
Kkkkkkkk ❤
Bon kalindo ndiwamisara sipaja amavara blauz wamisara uyo
Ichi ndi nkhani zina 😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂 Sewero + Chilungamo + kulimba mtima 🙄🙄🙄🙄🙄🙄🙄🙄🙄🙄🙄🙄🙄🙄🙄🙄
Ukunenazo kulibe iweee kkkkkkk BOMA NDI LOMWERI kulibe kusintha 🔥🔥🔥🔥🔥 motooooo 2025
Chest pain