Mwamva uyu za kundale mpaka ma bra 😂😂😂 bwanji simuitanitseko ka g string 🏃♂️🏃♂️ odi nchoke kuma comment akugenda miyala uku 😂😂 kodi a dan lu muliko 😂😂😂 beans nyemba khobwe mbwanda inuyo musankha ziti pamenepo 🏃♂️🏃♂️🏃♂️
Can't wait for the next episode😅 I watch this for all the actors and actresses in this series kkkk osanama guys mmandiwaza. I can't pick a favourite......you are all too good😅
Guys iyi nde yathela m'mwamba tu aaaa.... nde idzibwera twice per week... Coz iziz sizoona ayi...we can't wait till next week.. Ma scene achina shado asamatalike kwambiri akutitayitsa nthawi ka😂😂😂
Patricia, Patilishaaaa 😂😂😂😂😂. I like you😂😂, Ngozo nde sizikumukhuza olo. A Ntebe Belita uja mumamufunabenso kodi Komanso kwa Albert kukhala drama eeeeh
Sangie is a natural beauty
And she has positive energy
Not only sangie but both of them
Patricia plz kkkkkkkkk
Aaah 😂
Louder
Aaaaah Patricia Nyimbo Yanji Imeneyo 😂😂Kumangosekelela Mpaka Kumapeto This is Dop🔥🔥🙌
😂😂ngozo is just used to his wife 😂😂
He’s no longer bothered at all by her😂
Kikikikik
Anangozolowera😂
Sanjie wandisiya m'malele😂😂😂😂
Anatopa nazo😂😂😂😂
Koma chi Abati nchokongola abale😂😂😂😂😂
Uku nde kufuna kusokoneza 😂😂
Wamufila
Ndipotu kwambiri
Mbambande 😂
In Izeki voice, "mukati ndi okongola mukufananiza ndi ndani?" 😅
Ma scene achina shado asamatalike azitalika ndi achina Sangie ndi banja lake ndi Hyphen ndi banja lake 🎉
Ndipo live
Mwamva uyu za kundale mpaka ma bra 😂😂😂 bwanji simuitanitseko ka g string 🏃♂️🏃♂️ odi nchoke kuma comment akugenda miyala uku 😂😂 kodi a dan lu muliko 😂😂😂 beans nyemba khobwe mbwanda inuyo musankha ziti pamenepo 🏃♂️🏃♂️🏃♂️
Sukunama
Ashado kubhowa aaah ...koma Sangie mpka kubhebhesa nyimbo choncho kkkk
Ashado n ntebe r my favourites 😂,,,,,asamasowemo
I hope we're all voting for these guys for the maso awards best series/drama😊🔥#usauver
Vuto amachedwesa😊
Usakaike
Coming from Usauver Facebook page👍
Albert mayesero a beans amupeza mnyumba mwake
Wathira diso munthu wam'bambo
😂
Patricia wamuputa Ngozo😂😂 can't wait for next episode
Sangie is the best 😅
Effortlessly funny 😂
Kutchula modzi modzi kulakwitsa koma, ndingoti ma gyz mwadza ngati coming keep it lit!!!
Kuzangoona Ka notification khaaaa!! Ndati eyaaah tionele basi❤🔥
Koma arabati ndi Mnyamata ooneka bwino😊😊tsono sangie uli ndi mtopola😂😂😂😂
Koma sangie adah 😂 receive your flowers 🌷 umatha acting
Atonde amandimvetsa chisoni kaya bwanji kaya 😂😂😂😂😂😂😂😂
Suli wekha 😂😂😂
Kikikik but he is a good actor😅
😂😂😂😂😂
Ngamadando
Komatu brother wawo ndi othamanga thamanga😂
Can't wait for the next episode😅 I watch this for all the actors and actresses in this series kkkk osanama guys mmandiwaza. I can't pick a favourite......you are all too good😅
Ndipo fact😂😂 recruitment yawo ndiyabho
@chikondiphiri7077 heavy mmmmmh
Hyphen waidabwa, kuti mlendo wabwera kuzakhala kwa 2 years 😂🙌
Ati angosamuka akhalemo yekha😂😂
Nice one sangie ndipo ndiwe favourite wami❤️🎉
😂😂😂 Anali hule bamboo mwachisomo anasintha😂😂 sangie umatha🙌
Let's all gather here for ganizani guys 😂😂😂😂🎉🎉
Ganizani ndichi actor ase 😂😂😂
Hyphen,albert kukongola ngt madzi akumwa 😮sangie shes a vibe😂😂
Wobhebha ngati baula 😂😂
Koma patilisha nyimbo ya mtopola ngat iyoo😂😂😂
China nchina eeeeeh Hyphen ndi handsome 🥺😍🥳
Guys iyi nde yathela m'mwamba tu aaaa....
nde idzibwera twice per week... Coz iziz sizoona ayi...we can't wait till next week..
Ma scene achina shado asamatalike kwambiri akutitayitsa nthawi ka😂😂😂
Ashado akumachedwesa zinthu zabwino
Kkkkkk akut anali hule ngozo mwazisomo ndinamusitha❤❤❤😂😂😂😂😂
Ati adzasamuka alendo adzakhalemo okha😂😂😂
Eti mpaka 2 yrs
🤣🤣🤣🤣
Koma sangie😂🙌nyimbo zake zimenezi koma banja likhalapo😂😂
Aaaaah muchulukisa zochitikatu ,,, awo akagula ma bla wo zutanthawuza Chani sopano ,,,,, kumapetoko kma a sangie makwana inuyo❤
Mesa ndi shadow MP nde he's buying for campaign.
Zosabeba ,,, Nanga awo akut wina onukha mkamwa this and that palibe chomwe ndaonapo ine aaah
@@ChisomoPhweyaMwayamba kuonera liti?😂
@@PriscaAtupeleNyirendapanenepo…????😂😂😂👍🏾👍🏾👍🏾👍🏾
@@johanahseven4520 chifukwa oyisata sangafuse izi ndi alendo awa😂😂😂😂
Sangie my favorite 😅😅ndwe chi vibe mamie❤️🔥
Patricia iiiiiii kukhala ngati wasuta chamba kkkkkkkk koma ndaseka upole moto komaso awa amabulawa ine sindimava amen
Anthunu mumabhebhesa ❤ lovely inenso ndilowe nawo
Koma ngat nyimbo zake zikhale iziz album situluka sure 😂😂😂😂
Ndipo yalephereka kale album 😂😂😂😂
@gracekachali4505 😂😂😂
🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣
🎉🎉🎉sangie she have pure acting and don't forget Ganizani
Patricia ama komesa koma 🤣🤣🤣🤣🤣 🔥🔥
Koma sangie you have made my day ❤❤❤
Sangie ndiwamtopola eeeeeee😂😂😂😂😂😂😂😂💔💔💔Wakhala hule litiro ngozo
ATI Chabwino imbani jojojo tigosekelela😂😂😂😂😂
😂achokera kutali onsewo
@gracekachali4505 awawa banja atopa nalo😂😂😂😂💔💔
@alexmaulana7378 akut ndimomwe amachezera 😂😂😂😂😂💔💔
😂😂😂😂
😂 Ndifuna kunena....
Zamoyo wake.......
Sangie nso Pena 😂
Hyphen, hyphen, hyphen 😂 Mwayamba kudzuka 3 am eti okheee 😂
Ndipo 3AM Sakumapita ku Bedroom Kwa Alamu koma??😂😂😂😂
Koma pati... kumuyamba ngozo kumeneko 😂😂😂😂😂 more fire 🔥 guy's ❤❤❤❤
Camera very nice🔥🔥🔥🔥🔥
Chimbale chamtundu wabwanj uwu Patricia 😂😂😂😂😂
Achado chenkope ndiosokoneza mablaa ndi campaign zikhuzana bwanji eesh yah neh kkkk
Patricia, Patilishaaaa 😂😂😂😂😂. I like you😂😂, Ngozo nde sizikumukhuza olo.
A Ntebe Belita uja mumamufunabenso kodi
Komanso kwa Albert kukhala drama eeeeh
Nyimbo zake zoopsa. Iyiyi iyambitsa world War 3
Hahaha! Ati tingotsekela ndi njonjonjoo! 😂
I think this one is short 😢😢 can't get enough of Usauver 1:13
😂😂😂 a manzy😅
@TawongaGondwe-e1v paja nanuso mumapezeka kuno 🤣🤣🤣🤣
I love you guys,🔥🔥🔥🔥🔥❤️❤️❤️❤️ mumandi vesa Ku koma
Its Sangie for me😂😂😂
Sangie umatha
This drama has a perfect cast. aliyense zuchita kumkhala malinga ndi role yake. Keep it up maguyz
This was too short
😂😂😂😂😂 koma Patricia 😂😂ayayaaaaa ine ndikomoka guys😂😂😂😂😂😂
Campaign mpaka ma brah 😂
Ndipo inuu😂😂😂😂
😂😂😂 oh yes Patricia kung'alula za moyo wa ngozo pamaso pachibale😅🙌
Nkope usandikomole😂😂😂😂😂, khamisolo mpaka campain
Koma sangie a.k.a patricia,,mtopola wa bwanji uwu😂😂😂🙌
Ati tizasamuka azakhala yekha... 😂
Hyphen ada... 😂 😂
Nkhamusolo wazonse ndimalaya omwe pomwepo 😂😂😂😂😂koma Ashadow kkkkkkk😂😂umakwana Shadow wamankhamisolo kkkkkkk
Bwana Ganii tsopano ndi mnzake Mtebe, kukaniza mpunga wakuchibwenzi kkkk
Nice one 🔥🔥 koma che nkope kamisolo ku campaign 😂😂😂 Sangie mwatisiya mmàlere
Sangie kunkhala opanda mtopola sangankhale🤣🤣🤣🤣nyimboyo yatunduwanji🤣🤣
Kkkkkkkkk koma pati ngozo umamuyamba dala,nawo a gani akuti utijoina tikamasula fasting yet mwadya kale🤣🤣🤣🤣🤣🤣ayi zikomo,next kom plz
Eeeee Patricia iweyo umatha😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂 nyimbo ikhale a repeat
Emwe amalemba ma script wa ndi dolo 🤣🤣🔥🔥🔥🔥🔥
😂😂😂😂😂😂😂nyimbo ya bwanj iyi Patricia iiih 😂😂😂😂😂
Shadow uyuyu wa ma khamisoloyu akutitayitsa nthawi heavy.. Isamatalike ndithu
Nice one, 🎉🎉 Sangie 🔥🔥
Sangie ndi fire guy's, I really like it😂😂
Koma Patricia 😂😂😂😂😂 njonjonjo wathela pa njira😂😂😂😂
Koma pena pake Patricia uzikhala serious😂😂😂😂😂😂🤣🙌aaaaah mhu
Munthu wavala akuti ndikavale kaye 😂😂😂😂😂😂
Azimayi amadziwa ndithu kuti kwinaku sikuvala koma amapangabe zomwezo
At kanakandifera nthovu kukamwa kkkk mwina zinangolowa oversize nanga ntchani🔥🔥
🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣 Ngozo kubanja kuja akupilirako ndithu 😂😂😂😂😂 Sangie eeeh ndaseka
Sangie umakwana 😂😂 Kuma umangofuna kunyoza muthu iwe osati zoyimba
😂😂😂😂 kom pa nyimbo pokhapo eish ndagomanapo eeee 👏👏
Atchado mpaka kuyesa mabraa😂😂😂😂
😅😅😅😅Berita anaimba akuti She is in love 😂😂 mtebe ndi one.
Ati anali Hule mayi mayi mayi 😂😂😂😂uwu ndimtopola sure
😂😂😂😂😂koma ndaseka AAA kumuimba ngouzo koma Patricia sazatheka 😂
My favourite artist anankabango,mfumu hyphen 🎉
Ikhale njonjoyo koma 😂
Ganizani koma ine azandipha ndi phwete
😂😂😂
Kma patricia wandiseketsa😂😂😂😂😂 za uhule wa angozo kma ndinamusintha😂😂😂😂
Komano Albert n Ngozo ndi amuna opilira😅😅😅😅Jabulosi welcome to our family
😂😂😂😂😂😂koma ndaseka😂😂sangie banja watopa nalo serious😂😂😂😂
tso'no macheza anji awa Patricia🤣🤣🤣🤣
Ati wina kamwana kanafuna kumufela😅😅😅😂😂
Usauver 😂🔥🔥Tengan award bas
Kali bho ka Ngozoko .....mwachisomo anasintha
Khamisolo akuyetsa kuti sha adow
Now I want Sangie to record and release her version of Ndifuna kunena
Sangie can sing for the whole world 😂🌎nanga nyimbo yanji iyi😂😂
Hyphen is so gentle n I like this Man
Patricia kundipatsa mutu waching'alang'ala chifukwa chiseka 😂🤣🤣🤣🤣🤣🤣
🎉🎉 madolo kwambiri
Ntebede ndi gani amuwonesa mbutumwa tonde kikikikikikikikikiki!! 😂😂 koma gani umakhala serious ase eishii kikikikikikikikikiki
Albert akuoneka kuti malangizo a Edoh aja anawamva😂😂😂
Ndipo straight 😂😂😂
Ati mpaka 2 years tingosamuka ndifeyo azikhalamo ndiyeyo 😂
Sangie kumuputa ngozo kumeneko 😂
Madala Gani mumandikomesela 💪💪💪
Kma Namkalizi ndee wati nyimboyo Amati Chan 😂 😂😂😂 ......mpaka uhule wangozo😂😂😂😂
Ndufuna kunena nzamoyo wangayu nenanena😂😂😂😂 Patricia anakonza
😂😂😂😂koma chenkope mpaka kuyesa bra
😂😂😂😂 kma ya lero ndi fire 🔥 ♥️ 👌
Albert the handsome guy,waidabwilatu Ali kukhala mlendo 2 yrs 🤣🤣🤣🤣 tidzasamuka ifeyo , where's angauzo koma
Km ine sangie ndimasowa pomuika ndi2😂😂🙌