KWAKOMA NDI KU UTM CONVENTION NDIPO KWACHEMERATU TAONANI ZOMWE ZIKUCHITIKA PAMENE AYAMBA KUVOTA

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 16 лис 2024

КОМЕНТАРІ • 85

  • @Mom-pw3wr
    @Mom-pw3wr 5 годин тому +18

    Kungoti kaliati ndi m'zimayi koma anayenela kuwina iyeyu bas chifukwa mayi kaliat ndiolimba m'tima kwambiri mama ulem wanu ❤

    • @PeterTimkeje
      @PeterTimkeje 5 годин тому

      That's true

    • @RuthKaledzera
      @RuthKaledzera 5 годин тому

      Zoona Zake

    • @KeithSamata
      @KeithSamata 5 годин тому +2

      Komaso ndamene anawonesa chikond kwachilima alipo ndamene akuyiziwa bwino UTM

    • @VeronicaChirwa-ct4os
      @VeronicaChirwa-ct4os 14 хвилин тому

      @@Mom-pw3wr Komanso ku Malawi kuno ambiri samavomerezabe kuti Mzimayi angatsogolere dziko.

  • @KamozaMlunda
    @KamozaMlunda 2 години тому +2

    Wishing kaliat to be the president ❤🎉😢

  • @elizabethbalalasdp721
    @elizabethbalalasdp721 4 години тому +1

    I love so much Mama Kaliati, she is so loving, so strong hearted so caring, so, so so, Soo! however, I would wish her to maintain the SG position due to my some other valuable reasons which I cannot just air them out anyhow. Therefore, if DK wins, it will be so much of great importance! Praying for you all who are there on our behalf!

  • @haneefmuyaya7472
    @haneefmuyaya7472 Годину тому

    Akweni for for President,
    if not
    DK must Lead
    that's my prediction

  • @jameskananji4884
    @jameskananji4884 Годину тому

    I wish DK for presidency

  • @SheenahMwalabu-iz3pr
    @SheenahMwalabu-iz3pr Годину тому

    Dalitso Kabambe ❤❤ Mama Kaliati l love you but l wish mukanakhala pau VP or pau SG pompaja komabe am wishing her the best ❤❤ continue RIP Saulos Chilima

  • @doreenkaliati3166
    @doreenkaliati3166 4 години тому +2

    Awine maiwe ndithu chifukwa eeeee ai alimbana nako kulimbana kwabwino aona zophinja awa ndipo mai wa ndi opilira kwambiri iiiiihh❤❤❤❤❤❤

    • @VeronicaChirwa-ct4os
      @VeronicaChirwa-ct4os 50 хвилин тому +1

      Ndi zoonadi Mama P. Kaliati ndi opilira kwambiri madeligate akanaganizapo pamenepo

  • @AlumakioChingalu
    @AlumakioChingalu 3 години тому +2

    The woman is too emotoonal komanso woyankhula mwachipongwe

  • @ColbyNkhambala
    @ColbyNkhambala 35 хвилин тому

    I as a UTM fan aliyense owinayo

  • @xrissymapwesera787
    @xrissymapwesera787 33 хвилини тому

    God intervine to mama kaliati

  • @OustinLysani
    @OustinLysani 51 хвилина тому

    Nice❤❤❤ 🎉🎉❤❤❤

  • @KondwaniHara-i2v
    @KondwaniHara-i2v Годину тому +1

    Ndimafunisisa kuti kaliyati awine ambuye muve pephero ranga

  • @AnnieMaxwellphiri
    @AnnieMaxwellphiri 5 годин тому +4

    Ine akawina Kabambe ndizabvotera U.T.M

  • @ArnoldBanda-b9q
    @ArnoldBanda-b9q Годину тому

    Nice my UTm

  • @ronaldordinga6537
    @ronaldordinga6537 Годину тому

    Dr Mathews mtumbuka 🎉🎉🎉❤

  • @gracemandala-xf4kt
    @gracemandala-xf4kt Годину тому

    Kaliyati my vote

  • @bensonchiumia2667
    @bensonchiumia2667 5 годин тому +2

    Personally I would love if there was that possibility yoti apange contest pa mapositions awiri which is general secretary and president so that is she looses one position atengeko one position. Because she deserves to get one big position in the party. Atiyimirira nthawi yayitali mayiwathuyu. 25:11

    • @HassanChibwana-m8j
      @HassanChibwana-m8j 5 годин тому

      Yes you are right,but to be honest in presidential position Mmmm am not sure

  • @BelucLucas
    @BelucLucas 37 хвилин тому

    Kaliat🔥🔥🔥🔥

  • @InnocentEdasi
    @InnocentEdasi 2 години тому +1

    Mai Kaliat 🔥🔥🔥🔥🔥

  • @GeorgeMarizani
    @GeorgeMarizani 4 години тому +2

    Patricia Kariati for President

  • @NiyondikoChadrack
    @NiyondikoChadrack 5 годин тому +6

    Kabambe awina masankho

  • @AustinMhone-r3s
    @AustinMhone-r3s 5 годин тому +1

    Who ever can win as UTM president is good for the party it will be good preparation for general election.

  • @abgi.doctor.august
    @abgi.doctor.august 2 години тому

    ❤❤ vote ipite Kwa Mai Kaliati pls

  • @mphatsombewe-hj4nf
    @mphatsombewe-hj4nf Годину тому

    Muli nd Tsoka potaya Dr Usi. Kaliati wasintha zipani zingati iwe, munthu oipa and u can't win this convention

  • @mackalfred-s3i
    @mackalfred-s3i 5 годин тому +2

    Utm oyeeeeeeeeee moto kt buuuuuuuuuuuuu🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🤣

  • @Paul-q2p
    @Paul-q2p 4 години тому +2

    Akawina kabambe kaliat atha kutsangalala chifukwa akumumenyela nkhondo kaliat kuti kabambe awine zovota ndi mwambo chabe

  • @madalitsophiri2373
    @madalitsophiri2373 5 годин тому +2

    Kaliyati ndi muthu olimba mtima atawina better

  • @OsmanYusuf-u1v
    @OsmanYusuf-u1v Хвилина тому

    Akanawina kaliat nkanakondwa cause ku utm kulibe olimba ntima kuposa kaliat and ndiyemwe angasunge chipanichi

  • @JacksonKaitano
    @JacksonKaitano 2 години тому

    Love it

  • @JoiceNkhoma-s1m
    @JoiceNkhoma-s1m 4 години тому +1

    Mayi kaliati disserve to win for now we can't trust kabambe though he seem so interigent

  • @kelvinchola739
    @kelvinchola739 4 години тому +3

    Kuchokela ku Zambia 🇿🇲🇿🇲🙏 ndingoti chonde Mai Kaliati akhale mtsogoleli wa dziko la Malawi ❤

  • @mariahmatto8182
    @mariahmatto8182 4 години тому +1

    Patrice kaliati ayenela undindowu chonde

  • @SakinaLoveness-r3o
    @SakinaLoveness-r3o 3 години тому

    Simene kulili uku ❤

  • @ellensambo6323
    @ellensambo6323 2 години тому

    More ❤

  • @MwaiSambo
    @MwaiSambo 2 години тому

    The problem is that in this world people did not choose the right thing, always they are going for wrong things, kabambe is dangerous person people wakeup you will cry than today's cry

  • @DamaliceWamalanguluko
    @DamaliceWamalanguluko 4 години тому +1

    Akweni atenge udindowo ndi mzimai wolimba mtima ku dziko lathu la malawi

  • @FrancisOrbet
    @FrancisOrbet 13 хвилин тому

    Akweni womweobasi

  • @juliusmateyu
    @juliusmateyu 3 години тому +2

    Chipani chokondedwa

  • @evansjohn7766
    @evansjohn7766 Годину тому

    Komatu nkhope zinzi troops 😂😂😂😂

  • @FladielMwase
    @FladielMwase 5 годин тому +1

    Kaliati moto❤❤

  • @GETRUDEEDWARD-q7q
    @GETRUDEEDWARD-q7q 4 години тому +1

    Bola amayi athu awine apa ndawona kale wowina akaliat

  • @dicksonkalinga6747
    @dicksonkalinga6747 5 годин тому +3

    ❤🎉🎉🎉🎉🎉

  • @GertrudeKumwenda-wz5fs
    @GertrudeKumwenda-wz5fs 4 години тому

    Kaliyati atenge udindowu serious ndiwolimba mtima ngati mwamuna

  • @ChammundaMary
    @ChammundaMary 4 години тому

    Mai kaliati 🔥🔥🔥

  • @EmiryMsowoya
    @EmiryMsowoya Годину тому

    Zabwino zonse ku convention

  • @WiltonSingini
    @WiltonSingini 4 години тому

    Akweni 🔥🔥

  • @MoyendaChileka
    @MoyendaChileka 4 години тому

    Akweni❤

  • @AmonKaonga
    @AmonKaonga 4 години тому

    Wawina ndani

  • @JessieMbewe
    @JessieMbewe 4 години тому

    Moto ku woooye go koko

  • @PeterPhiri-nd6op
    @PeterPhiri-nd6op 4 години тому

    Ine ndikufuna kariyati awine achoka kutari inawa akufuna mupando

  • @BENGAJ-z5x
    @BENGAJ-z5x 5 годин тому +1

    Kaliat awine amachikonda kwambiri chipanichi

  • @Elizabethmanda-es7se
    @Elizabethmanda-es7se 4 години тому +2

    BIYENI mukuona uko muliko

  • @MoltonZgambo-z4i
    @MoltonZgambo-z4i 4 години тому

    Vote vote azanga

  • @DANIELSimwaba-f5p
    @DANIELSimwaba-f5p 4 години тому

    Sangawine kaliat inu

  • @WilliamNyilongo
    @WilliamNyilongo 5 годин тому

    ❤❤🎉💪💯

  • @DoliccahChilinda
    @DoliccahChilinda 5 годин тому

    Moto unandi kaliat

  • @EsnartGirivin
    @EsnartGirivin 4 години тому

    Mbuzi yamunthu davil you're a liar 😂😂😂😂😂😂

  • @SalatielMathews
    @SalatielMathews 2 години тому

    Kaliyati moto kt buuu!!!!!!!

  • @EdwardBanda-j7e
    @EdwardBanda-j7e 5 годин тому +3

    Utm sidzalamulirapo dziko

  • @KondwaniHara-i2v
    @KondwaniHara-i2v Годину тому

    Ndimafunisisa kuti kaliyati awine ambuye muve pephero ranga

  • @RauryneBishop
    @RauryneBishop 2 години тому

    Akweni ❤