Розмір відео: 1280 X 720853 X 480640 X 360
Показувати елементи керування програвачем
Автоматичне відтворення
Автоповтор
Honestly I ❤ ngozo & Patricia's part.... Can't wait to watch more of this... otherwise big up to u guys. U deserve a bunch of 🎉
If Ur here for sangie let's gather here😅😅😅
Chete kudikilira🤣🤣🤣
am here for everyone
Anyanyalatu mango aja😂😂😂
Makina ndi Gan
Ine pano
I miss this so long,, thanks for coming back
kafungo ka tala kaja kamazafunikira mtsogolo muno 🤣🤣
If u here for Ganizan, let's gather here😅
Ganizani ndi nbr One.eeee!!
We are here team gan
Che mkope ngat ili misala😂😂😂😂😂🙌🏼🙌🏼....angozo mwagweseratu congratulations 😂😂😂😂😂😂
Kkkkk ma battery akulu akulu😂😂😂 mwabwela bhoo guys watching from joz
❤❤❤Chibwenz chake sichimaphelapo chimankhala ngat nsuzi wamaofozi 😂😂😂😂
😂😂😂😂Che mkopee nde mwatiiii chikuuluka koopsaaa ngwengwee😂😂🙌
A Sangie mwaimatu nanga Masau bwemba😂😂😂
Che Mkope ndi dolo kwambiri 😂😂😂😂
Ndimasowa oyamika apa, guys, you are doing great all of you're
This Che Mkope guy is underrated 🔥
Komaso Belita akanatulukila..ndamusowa😂😂😂
@@Tina-db1mf alitu ku Israel abwela koma mochedwa
@@zawardmakawa6196 anapitadi Ku Israelko
Ati chibwenzi changa sichitherapo chili ngt msuzi wamaofozi😂😂😂😂
Kugula bwemba nde kuchita manyazi kma kukhala kuno osachita manyazi😂😂😂😂😂
Kkkkk komatu yafika udyo mpaka bwembwa, masawu & mango 😂😂
Ati kutapako tala ngat wamisila... Gani ndiwe galu😂😂😂
Kkkkk mimba yafika udyooo 😂😂😂😂😂😂😂😂😂 Abusa ali ndi mabatile ang'ono okha
Kudya mango ndi tsabola nthawi yomweyo sweet koma ayi dzuwa😂😂😂 kwavuta
Gan eeeehh ndidolo kwambiri,... at Congratulations 🎊🎉🎉🎉🎉🎉🎉
Eti muli ndima Battery akulu akulu🤣🤣🤣🤣🤣🤣 kufusa kwanji uku
Mbambande quality. Big up. I can’t wait to see Ngozo jnr bolanso asakhale Patricia akungofuna kumuchotsa dolla Ngozo.
I love this serie for sure❤
Keep 🔥🔥 burning sangie♥️😍
A shadow ati akupanga presidential dairy 😂🙌 koma guyz mumatha!
Takondwa ndichibwez chake😂😂😂😂
😂😂😂 supu wa maofozi..Ayi zikomo 😂😂
Series's simply the best.
Ndadikila nthawi yayitali mumandivetsa kukoma m'mene ndikuwoneramu angauzo apalamulatu apa
Pangani tizikuonelaniko pa tv kaya times kaya chani koma pa tv chonde🤣🔥
I love this show too much talent guys
Quality pictures & production is top notch🔥
Ashado ndichi drink bottle 😂😂😂
Ati pamenepo dziko likundikana mumandipatsa hope hahahahaha
madhala gani atsimikiza kuti pachitika za mimba mimba eeeh😂😂😂😂
Nice one, the waiting is over❤❤❤❤🔥🔥🔥🔥Chenkope ndiwabodza koma 😂😂😂😂
Muli ndi ma batile akuluakulu😂😂😂😂😂
Albert mkazi wabanja sanampeze😂😂😂😂😂😂
Kkkkk 😂😂😂 km Gani Sali bwino ndithu ATI muzitenga Tala uja Pena mkumuyika galimoto adzafunika tsogolomu
This is top notch acting 🙌❤️... Keep on
Ati zayambika chaka cha arsenal ....😂😂😂😂😂
Man Gani .... Ati yabwera hard
Ndege ikuthamanga kwambiri, achinyamata akulepher kudya
Gani mene yawambira mula, mula aaaa congratulations aaaa kuceza kwa bwnj
Mtebede waibadwatu kkkkkkkk fuso ridamukulila ❤
🤣🤣🤣🤣 honourable shadow MP🙌🙌🤣🤣
Akut ndkumfuna ndkupititse kuxul😂😂😂kt naweso ukadzwe momwe ndichira🙌
Chikuuluka kwambir chigwela mu chikangawatu 😂
Kodi Congratulations wapeleka GanizaniTiziti Sangie alindi mimba??😂😂Tikudabwa ndi Angozo tikuyaka penapake
I like the way Ganizani perform
Koma Gani kkkk ai ndithu iweyo unabwera ati kutapa Tala kusunga amazathandiza😂😂😂 ati congrats 🤣🤣🤣
Eti muli ndima Battery akulu akulu😂😂😂
Ine mnabwra kudzamalizisa nkhan Yama batile yomweyo kkkkk
Gan akuti Tala uja amadzafunika 😂 @ mafuta kumagulako mu chigubu😂😂😂
We Awu ready, Angawuzo
Mango odyera sweet, sweet yodyera mango😂 Hayi congratulations 🎉
Finally, after waiting for a long time 🎉🎉🎉❤❤❤❤❤
Chibwenzi sichizantha kkkkkk,,,,,,sangie litima ndimango 😅😅😅😅😅😅 dziko layakadi😅😅😅
We waited for so long welcome back guys waiting to see the investment 😅😅😅
Vasectomy ndi aviator zikugwilizana bwanji koma a shadow amwene🤣🤣🤣
More fills angawozo😊
tadikila thawi yayitali kma eeh kungofikika kufuna mango sangie😂😂😂🙌
Zayamba bwino🔥🔥🔥❤️
Nkhan nd ma batire akulu akulu 😂😂
But when do you post the next episode😢😂😂I've been coming here every day for the past week to check
Akonza🥳🥳🥳🥳big up guys
Nkhan ndi aviator mwina chemkope atimenyela nkhondo akawina😢
Usauver crew inuyo you deserve respect madaulo keep hard working guys
This series 😂 Eeee makes my dull days😅🙌
Yabwera hard😂😂😂😂 yes Gani iweee
Gani mpaka yabwera hard 😂😂😂😂
Ashadow nkhani ya aviator mukuyendetsa bwanji 🤣🤣🤣🤣 18:56
Wozaaaaa, Ganizani ati chani ulendo uno
Kkkk iiiii ayi zikomo et ma battery akuluakulu 😂😂😂
Km ganizan nd mulam wak kkkkk power
Gani simwana okhala naye nyumba,mmene wayambila congrats mula wamkulu ameneyi mumtimamo akusilira kui ...
Komanso nawo Abusa mpaka ndili Ma battery ang'ono okhaokha
Hahahaha nkhani ndi mabatile akulu akulu basi 😂😂😂
Ngozo wafailamo😂😂😂
Munthu akufuna ma battery a wailesi, kodi bwanji Mtebede😂😂😂
Apa tikudikira usauver junior 😂😂🎉
Congratulations in Ganizani voice😂😂😂
Well Ngozo, 😂 a Ganizani akt mwapereka pha
Che mkope ndale zake zolepherekatu aaaaa😂😂😂😂😂😂
Koma Ganizani🤣🤣🤣 ati congrats
Mango awawa amanjela Mcheleosakhala sabhola mngoso mukutam😂😂😂 🔥🔥🔥
😂😂😂 mula congrats Ma batile akulu akulu😂😂
Sangie wayima😂😂😂ndakusowa aise ndi gani moni kwa ngauzo ndi ena nonse
Mtebede my actor 😂😂😂😂😂 Mabatire akulu akulu
Ku airport komweko😂😂,
Ganizani has always been my favourite
Ati youth people😂😂😂😂
Opemphela kwambir kowopsa😂
Takondwa girl yoooooo🎉🎉
😂😂😂😂😂Best episode
Tonse tinavomeleza kuti Usauve inapanga replace tikufelanji❤❤❤❤
Mtebede Ali ndi ma battery ang'ono ang'ono,,, akulu akulu alibe😂😂
Naye Takondwa😂
Kugula bwemba kukuchititsani manyazi koma kukhala pano nde osachita manyazi 😂😂😂😂
Eeti mulindi ndi mabatile akulu akulu😂😂🙌
mbambande HD, keep the fire burning
Honestly I ❤ ngozo & Patricia's part....
Can't wait to watch more of this... otherwise big up to u guys. U deserve a bunch of 🎉
If Ur here for sangie let's gather here😅😅😅
Chete kudikilira🤣🤣🤣
am here for everyone
Anyanyalatu mango aja😂😂😂
Makina ndi Gan
Ine pano
I miss this so long,, thanks for coming back
kafungo ka tala kaja kamazafunikira mtsogolo muno 🤣🤣
If u here for Ganizan, let's gather here😅
Ganizani ndi nbr One.eeee!!
We are here team gan
Che mkope ngat ili misala😂😂😂😂😂🙌🏼🙌🏼....angozo mwagweseratu congratulations 😂😂😂😂😂😂
Kkkkk ma battery akulu akulu😂😂😂 mwabwela bhoo guys watching from joz
❤❤❤
Chibwenz chake sichimaphelapo chimankhala ngat nsuzi wamaofozi 😂😂😂😂
😂😂😂😂Che mkopee nde mwatiiii chikuuluka koopsaaa ngwengwee😂😂🙌
A Sangie mwaimatu nanga Masau bwemba😂😂😂
Che Mkope ndi dolo kwambiri 😂😂😂😂
Ndimasowa oyamika apa, guys, you are doing great all of you're
This Che Mkope guy is underrated 🔥
Komaso Belita akanatulukila..ndamusowa😂😂😂
@@Tina-db1mf alitu ku Israel abwela koma mochedwa
@@zawardmakawa6196 anapitadi Ku Israelko
Ati chibwenzi changa sichitherapo chili ngt msuzi wamaofozi😂😂😂😂
Kugula bwemba nde kuchita manyazi kma kukhala kuno osachita manyazi😂😂😂😂😂
Kkkkk komatu yafika udyo mpaka bwembwa, masawu & mango 😂😂
Ati kutapako tala ngat wamisila... Gani ndiwe galu😂😂😂
Kkkkk mimba yafika udyooo 😂😂😂😂😂😂😂😂😂 Abusa ali ndi mabatile ang'ono okha
Kudya mango ndi tsabola nthawi yomweyo sweet koma ayi dzuwa😂😂😂 kwavuta
Gan eeeehh ndidolo kwambiri,... at Congratulations 🎊🎉🎉🎉🎉🎉🎉
Eti muli ndima Battery akulu akulu🤣🤣🤣🤣🤣🤣 kufusa kwanji uku
Mbambande quality. Big up. I can’t wait to see Ngozo jnr bolanso asakhale Patricia akungofuna kumuchotsa dolla Ngozo.
I love this serie for sure❤
Keep 🔥🔥 burning sangie♥️😍
A shadow ati akupanga presidential dairy 😂🙌 koma guyz mumatha!
Takondwa ndichibwez chake😂😂😂😂
😂😂😂 supu wa maofozi..
Ayi zikomo 😂😂
Series's simply the best.
Ndadikila nthawi yayitali mumandivetsa kukoma m'mene ndikuwoneramu angauzo apalamulatu apa
Pangani tizikuonelaniko pa tv kaya times kaya chani koma pa tv chonde🤣🔥
I love this show too much talent guys
Quality pictures & production is top notch🔥
Ashado ndichi drink bottle 😂😂😂
Ati pamenepo dziko likundikana mumandipatsa hope hahahahaha
madhala gani atsimikiza kuti pachitika za mimba mimba eeeh😂😂😂😂
Nice one, the waiting is over❤❤❤❤🔥🔥🔥🔥
Chenkope ndiwabodza koma 😂😂😂😂
Muli ndi ma batile akuluakulu😂😂😂😂😂
Albert mkazi wabanja sanampeze😂😂😂😂😂😂
Kkkkk 😂😂😂 km Gani Sali bwino ndithu ATI muzitenga Tala uja Pena mkumuyika galimoto adzafunika tsogolomu
This is top notch acting 🙌❤️... Keep on
Ati zayambika chaka cha arsenal ....😂😂😂😂😂
Man Gani .... Ati yabwera hard
Ndege ikuthamanga kwambiri, achinyamata akulepher kudya
Gani mene yawambira mula, mula aaaa congratulations aaaa kuceza kwa bwnj
Mtebede waibadwatu kkkkkkkk fuso ridamukulila ❤
🤣🤣🤣🤣 honourable shadow MP🙌🙌🤣🤣
Akut ndkumfuna ndkupititse kuxul😂😂😂kt naweso ukadzwe momwe ndichira🙌
Chikuuluka kwambir chigwela mu chikangawatu 😂
Kodi Congratulations wapeleka Ganizani
Tiziti Sangie alindi mimba??😂😂
Tikudabwa ndi Angozo tikuyaka penapake
I like the way Ganizani perform
Koma Gani kkkk ai ndithu iweyo unabwera ati kutapa Tala kusunga amazathandiza😂😂😂 ati congrats 🤣🤣🤣
Eti muli ndima Battery akulu akulu😂😂😂
Ine mnabwra kudzamalizisa nkhan Yama batile yomweyo kkkkk
Gan akuti Tala uja amadzafunika 😂 @ mafuta kumagulako mu chigubu😂😂😂
We Awu ready, Angawuzo
Mango odyera sweet, sweet yodyera mango😂
Hayi congratulations 🎉
Finally, after waiting for a long time 🎉🎉🎉❤❤❤❤❤
Chibwenzi sichizantha kkkkkk,,,,,,sangie litima ndimango 😅😅😅😅😅😅 dziko layakadi😅😅😅
We waited for so long welcome back guys waiting to see the investment 😅😅😅
Vasectomy ndi aviator zikugwilizana bwanji koma a shadow amwene🤣🤣🤣
More fills angawozo😊
tadikila thawi yayitali kma eeh kungofikika kufuna mango sangie😂😂😂🙌
Zayamba bwino🔥🔥🔥❤️
Nkhan nd ma batire akulu akulu 😂😂
But when do you post the next episode😢😂😂I've been coming here every day for the past week to check
Akonza🥳🥳🥳🥳big up guys
Nkhan ndi aviator mwina chemkope atimenyela nkhondo akawina😢
Usauver crew inuyo you deserve respect madaulo keep hard working guys
This series 😂 Eeee makes my dull days😅🙌
Yabwera hard😂😂😂😂 yes Gani iweee
Gani mpaka yabwera hard 😂😂😂😂
Ashadow nkhani ya aviator mukuyendetsa bwanji 🤣🤣🤣🤣 18:56
Wozaaaaa, Ganizani ati chani ulendo uno
Kkkk iiiii ayi zikomo et ma battery akuluakulu 😂😂😂
Km ganizan nd mulam wak kkkkk power
Gani simwana okhala naye nyumba,mmene wayambila congrats mula wamkulu ameneyi mumtimamo akusilira kui ...
Komanso nawo Abusa mpaka ndili Ma battery ang'ono okhaokha
Hahahaha nkhani ndi mabatile akulu akulu basi 😂😂😂
Ngozo wafailamo😂😂😂
Munthu akufuna ma battery a wailesi, kodi bwanji Mtebede😂😂😂
Apa tikudikira usauver junior 😂😂🎉
Congratulations in Ganizani voice😂😂😂
Well Ngozo, 😂 a Ganizani akt mwapereka pha
Che mkope ndale zake zolepherekatu aaaaa😂😂😂😂😂😂
Koma Ganizani🤣🤣🤣 ati congrats
Mango awawa amanjela Mchele
osakhala sabhola mngoso mukutam
😂😂😂 🔥🔥🔥
😂😂😂 mula congrats
Ma batile akulu akulu😂😂