Can we give mtebe and belita their flowers 😂😂😂 their scenes are always fire😂😂😂🔥🔥 ayi ine matemba ndimawakonda ndie ndimafuna ndizidya atleast Ka 6 pa week lachi 7 masamba😂😂😂 this got me😂... komanso hyphen timufufuze amudyetsa kenakake😂😂
Guys I came across this episode coz I didn't watch it all along actually have just started watching this usauver series koma ndaseka ( it's the way she articulated the mwaswera bwanji agogo) 😂😂😂😂 yoh! I was missing alot😂
😂😂😂with that smile Gani amvekere "now its my turn"...targetting Albert's wife 😂 cholinga mumulandenso,mukufuna mzanu achite kutani ngat wachita kusiya mowa.... Chenkope a.k.a ashado atibulidwa liti ndi aichocho awadyera ndalama ya nyumba ya ena aja??
Guys inuo mumandiwaza eeeeh❤ ati ati mungogogoda ngat kwanu😂😂😂ati mufuna muzabe muli mbulanda😅😅 eeeeh koma Sangie eeee🎉🎉🎉ai zikomo......😂😂 henewe love you guys ❤🌼🖤
This Usauver must be a TV Program we love this comedy
I support...the way we have mdyangu, mitekete, mfumukazi😅
Ndipo zoona brother
Ndipo straight pa TV ibwele
Sukunama bale anthuwa ali bho
Can we give mtebe and belita their flowers 😂😂😂 their scenes are always fire😂😂😂🔥🔥 ayi ine matemba ndimawakonda ndie ndimafuna ndizidya atleast Ka 6 pa week lachi 7 masamba😂😂😂 this got me😂... komanso hyphen timufufuze amudyetsa kenakake😂😂
,😂😂😂😂😂
'mungogogoda ngat kwanu' eeh but this guy also😂😂😂
M'busa yo mpatsen award 😂🔥🔥🔥 drama king
Berita+mtebe playing power couple 😂😂😂koma patricia ndika mlamu kakeko ntamwano 😂😂Albert>>>tchamani ngozo naweso ibhebhetse lavu kwa Patricia😂😂😂😂
Mwano wake wonyowa wa fresh
The true definition of a happy man is Albert the guy is happy now....big up guys❤
Akumpanilila udyo mpakatu chimzake ndi ngozo chitha 🙌
Ndipo he is happy
Albert ndi a former onse achinyengo.
Guys I came across this episode coz I didn't watch it all along actually have just started watching this usauver series koma ndaseka ( it's the way she articulated the mwaswera bwanji agogo) 😂😂😂😂 yoh! I was missing alot😂
Gani and Mtembe nde ndi fyaaaah ❤❤
Mtebede umandiwaza koopsa Ndiwe actor wa ma actor the whole Malawi ❤❤❤❤❤
Iyiy nde mwajambuladi yachita kukoma yafulumilanso kutha moto kuti booooooo tionana Friday 🙏🙏🙏🙏
😂😂😂😂 oh akuopa kuwakonda cifkwa ankhozaso kunathawa Kkkk.....nice
😂😂😂with that smile Gani amvekere "now its my turn"...targetting Albert's wife 😂 cholinga mumulandenso,mukufuna mzanu achite kutani ngat wachita kusiya mowa....
Chenkope a.k.a ashado atibulidwa liti ndi aichocho awadyera ndalama ya nyumba ya ena aja??
makolo akukadziwana 😂😂😂😂😂😂
eeeh eeh albert, kusintha sasintha choncho, mwasiya kucheza ndi ngozo
apa matambula a mowa abwezedwa,,,,,,,,kuyaka🤠🤠
Ofcorse this is comedy kma Dala nelson akhoza kupanga zamatemba. Anachenjelesa kkk
Mtebe just nailed it akut ndkuopa kukukonda kuopa kut uthawaso😂😂😂😂😂😂😂😂
Kod ngozo nd Patricia taberekani plz aaa 😂😂
Belita hane nakusowa umangoyakhulapo at chiseko choseka ndi mpando 😂😂😂😂
Gani ati now is my turn 😂🔥🔥🔥🔥
You guys mumupha Albert 😂😂
Albert Ali mchikondi
kusangalala kwadziko lonse lapansi kuli ndiiyeyo😂😂
Ya lero ndiyapa gate....koma ndaseka akuti ine ndi bambo awo amai ako😄😄😄😄😄
Guys inuo mumandiwaza eeeeh❤ ati ati mungogogoda ngat kwanu😂😂😂ati mufuna muzabe muli mbulanda😅😅 eeeeh koma Sangie eeee🎉🎉🎉ai zikomo......😂😂 henewe love you guys ❤🌼🖤
Ntebs ayayayay....akuti ampatse Belita ndalama akagule mankhwala amudyetse naye azimukonda hahahah Iyinso inali bho heavy. Eish guys mukutimvetsa kukoma heavy. Keep up the good work.
Ndufunisitsa nditazamva ulalikiwo😊
Tebe ufuna ukane kuti sigogo kkkkk proud of you gogo tebe❤
Ka sikisi pa week matemba,,, la seven masamba otendera 😂😂😂eeeemhu
Ati nduoneka ngati ndutamukapo pano😂🙌
Kwabwera ma tumbler awiri... cnt wait to hear what will these glasses bring😂😂😂
Belita wagwamo basi...
Deal ya nyumba ya njanja! Kuyaka motso!🔥🔥🔥
❤
Zokongola..pitilizan kutisangalatsa
Zoona
Mtebe + betita combo is🔥😂
Mtebe eeee mgogo 🤣🤣🤣🤣
Lero sikunakuchele eeee
Mtebede neva disappoint always 😂😂
😂😂😂😂🔥🔥🔥eeeeh😂ati agogo ambuyako ndikuoneka ngat nabeleka mayi ako🤣
Agogooooooo 😂😂😂😂😂😂
Ntebe wafa basi
Nchizungu bwanji .. Enafe chichewa sitikumva😢
Angozo mtendere amawupeza kunja 😂 Albert chenjera, Gani maso ali ku mpanda kwanu
Wow guys your the best🔥🔥🔥Bae eee ndati Berita kkkkk
Please don't quit to act this season is so hilarious 😂😂😂😂
Mai ngozo lemekezan bwana ozakugulani nyumba
Kkkkkkkkkkkkkk
Team usauver tili disappointed two weeks guys osaponya video plz achina piksy pakakhala vuto muzitiponyera our favorite videos atleast
Scene 1 kumapetoko voice recording device ndi camera zimasemphana
For sure.. Ikavuta azingobwereza yakale
Mwaswer bwanji agogo 😂😂😂😂❤
Albert ali mchikondi amwene🙌
Ati mtendere amati ndikusiyirani uja uli mwa albert🤣🤣
One of best series in Malawi
Mwaswera bwanji agogo🤗😅😅😅😅😅
😂😂😂😂😂😂😂 agogo mtebe eish this one........ akuti ambuyako😂😂😂😂😂 mtebe eish
Patricia umene uja mwano
😂😂 nyamata akukaonekela makolo adziwane😂😂....Agogo akukana😂😂ati ambuyako😅😅😅😅
Angauzo,,, musiyen nzanu ananale kaye osat zanuzo😅😅
😂😂😂😂😂😂 abusa ndi nyunsensi 🤣🤣🤣naye Berita mavuto owaputa awa
Banja la a mtebe nd🔥🔥🔥🔥
Albert immigration nokha man mwafikapo eeee Angozo kusilila.
Belita ndiye sukutopatu nkumanga manga tiakatundu Tako aaaaaaaah, angauzo pangani zotheka idzionetsedwa program yi
Agogo mulibwanji
Ine ndi amene ndinabeleka mai ako 😂😂😂😂😂😂😂 piksy umatotha 😂
Patricia kaya anadziwana kuti ndi mkulu uja...timva zambiri mma next episode 😅
Kkkkkk mwaswera bwanj agogo😂😂😂😂😂🎉
Iyiyi achina Pisky akuiponya patali nice
Kkkkkkk ntebe tambwali wamkulu Mpaka Matemba 6 deiz kkkkkkkkk. Nawe2 shadow akumbwandla
Tili munyengo Ya albert😂😂
Akuti ine matemba ndimakonda kkkkk amuna opanda kanthu ndichoncho ukundikumbusa ankolo anga ati ndiwo zilibe msuzi
Koma lero ndiye kwamwazidwa mwano 🤣🤣🤣🤣
Koma Albert wapeza moyo, eeh ndamusirira bwanji 😂❤
Albert umakhalana ndi nkazi wonenepa uja serious zimachita kubheba
Ati uzikangowerenga ine nzikalalikira😂😂mtebe umakwana
Akuti mulibwanji agogo😂😂😂😂 mwana wachipongwe
usauver ili bwino ndithu keep it up good work
Pano dziko Lili mmanja mwa alabati😂ngozo ndi Patricia nanu muchitepo kanthu kkkkkkkk
Albert ndi Ngoo mmm nd mabombaa okha okha 😂😂😂
Piksy instead of drinking Tea at his home he is just go around to disturbing others love 😍
🤣🤣
Hahahah agogo mwaswera Bwanji nabeleka amako ndine 🤣🤣🤣
Patricia mayi ngozo unava kuti kuti Anthu amaba bulanda .🤣🤣🤣🤣
Mtebe akuopa kunkonda Belita😂😂😂
🤣🤣🤣🤣 Ganizani Ada amandiwaza kkkkk ,
Ati mwaswela bwanj agogo iiiiiiiih 😂
Komano mtebe za serious sapanga nawo😂 zibwana too much😂😂😂
Mtebe ndi galu kwabasi 😂😂😂😂😂
Ambuye anamusiyila alabati mtendere wonse
Mtebe ndi Gan mbali inai Arbat ndi Ngozo mmasangalala fact mukakhala limoz🤣🍻🥂
Agogo😂😂 mtene🙌
Big up guys ilibho heve 🔥🔥🔥🔥 every episode is my favorite 🤗🤗🤗
Paja mamuna wako amakuphikira unathawa zomwezo😅😅.
Gani my guy 🔥🔥
Koma Patricia ndi wamwano eeeh😂, ati mukufuna muzabe mutavula Kaye 🤣
I Really want to have Usovar T-shirt I'm Big Fan where can i get it 😭😭😭
Inenso
Ku shop kwa Emmie behind immigration ntown mukayipeza that’s in Blantyre
In Lilongwe?
Keep the fire burning 🔥🔥🔥🔥
Ati mwaswera bwanji agogo 😂
Yili bho kwambiri koma masiku ano yayamba kuchedwa kutuluka timawona ngat mwasiya
Ati akazi ndizichita kuwayendera
Mwaswera bwanji agogo😅😅😅😅
Olo kukonda matembako mpaka ka 6 pa week😂😂😂😂
Albert ali mchikoooo😅😅😅
Gani will always be my favorite
Albat wadyesedwa 😅😅😅😅😅
I met Gani in town. Ngati ndikuwe kuti Ganiiii
Amandiwaza
Uyu palibenso
Albert's smile is giving😂😂😂
Sewero labwino ndithu koma vuto kuchedwa paka masabata awiri
Gani always be my favorite fan
chafikapo chikondi Albert kkkkkk mumakwana
Matemba aminga umodzi🤣🤣🤣🙌
Mpaka mubwere mbulanda😂😂
Nice .
Bring back the likes of Dan Lu and Mlelemba they perform
Guys koma nthawi, kakumafupika kwambiri,
Usauver is our best u kno
🤣🤣🤣 Mugwirizano wa alibati ndi gani umakwanila 🤣🤣
Mtebe ada😂😂😂
Uphika koma ndikagula🤣🤣