MILANDU YA NORMAN CHISALE YAONJEZELEKA KU KHOTHI AKUTI ANABASO SATIFIKETI YA FORM 2

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 4 лют 2025

КОМЕНТАРІ • 6

  • @HappyAbyssinianCat-xt2bm
    @HappyAbyssinianCat-xt2bm 9 днів тому +1

    Mcp ilibe nzeru ndpo chitukuko Chao ndi chomwecho agalu amenewa kd muja ayambira kumusaka zisiru za anthu

  • @IsaqueFernandoAntônioAntônio
    @IsaqueFernandoAntônioAntônio 9 днів тому

    Zaziiiii,mbuzi za mcp mbuzi.

  • @VaidaSidreck
    @VaidaSidreck 8 днів тому

    Angomupekela amamusakasaka

  • @AfricanChina-im1op
    @AfricanChina-im1op 8 днів тому

    Tsono mwina wake certificate nthawi yonsei analikut nanga mcp nthawi yonsei anali kut afune asafune mcp ikuchoka bas ikachoka boma onse a mpc kuwamanga chakwera ndi abale ake onse mbava izi zalephera kulamula boma apakire nsanga nthawi yawathera bas mene mene tekelo farasi umfumu wao watha bas apakire nsanga ku state house ko

  • @PempheroMoleni
    @PempheroMoleni 8 днів тому

    Kkkkkk fundo alibe

  • @AfricanChina-im1op
    @AfricanChina-im1op 8 днів тому

    Moti athandize anthu akuvutika ndi njala angolimbana ndi kumanga anthu zaziiiii mbuzi izi