Mn akupanga post ekha bakili muluzi tv km chifukwa chachikulu ndichoti bakili muluzi tv amakonda DPP ndie dalitso kabambe wakana kupanga alliance ndi chipani cha DPP
Ayi sibakili muluz TV ndi mahaka amene aja. Muivele bhobho ndi fake voice. Page imene ija yapangidwa haki ndi athu a boma ndiofina kuononga chipani cha utm. Ndiye choyamba akuyenera kuipisa mbili ya chilima. N mu audio imene ija muli zofooka zambili zimene zikupeleka chikhulupililo kut siwa bakili muluz TV
Olo zitakhala zoona, who cares about DK's private life? All I know he can run the economy way better than the current situation. Malawi is not looking for munthu yemwe sananyengepo. Tikufuna munthu woti atsogolere kukonza chumachi kuti wolimbikira azidya thukuta lake. Enafe we don't care kaya akhala Chakwera yemweyi, kaya Enock Chihana, kaya APM, kaya Atupele kaya DK, kaya wa Bakili Muluzi
Nkhani zonsezo a Malawi akudzidziwa, kaya chilimayo, kaya Kabambe a Malawi akuwadziwa. Nkhani za personal sizingasinthe chilichonse kwa a Malawi zotsatira UTM
Ndi kunena zoona Ana amasiku ano sakudziwa kuti Kodi Atsamunda amalamulira bwanji dziko lino. Chimene akudziwa ndi kulemba Nkhani ZOSOKONEZA A MALAWI pa SOCIAL MEDIA basi, komanso kuwapatsa Bomali popanda masankho sangathenso kulamulira dzikoli adzangokhala mavuto okhaokha basi.
Akung'alula ndithu😂😂😂 Best TV ever
🤣🤣🤣🤣🤣 Koma Ziliko liko komabe Utsogoleri usinthidwa.
Anyway I love BAKILI MULUZI TV, History is the best teacher ✍️✍️
Kutheka ndi yemweyu, pajatu chilungamo chimasakanikilana ndi mwana.l always proud with bmtv he is real the best teacher, now and forever.
Zachamba izi akufuna kuononga Zina la bakili muluzi TV koma akunama kwambili Ana achepa timamukonda ❤❤❤❤ kwambili bakili muluzi TV
Mn akupanga post ekha bakili muluzi tv km chifukwa chachikulu ndichoti bakili muluzi tv amakonda DPP ndie dalitso kabambe wakana kupanga alliance ndi chipani cha DPP
@@PromiseSaidinde moti a Kabambewo akuti ali nayo 50+1 yotchaira Chimwendo?
Bakili muluzi tv anayamba nkale kumung'alura chilima anangosiya apa atamwaliramu koma ndiyemweyu ndinthu BMT 😅😂
Ea ndima haka amene aja ineso ndavera nawo muli zofooka zambili zimene zikusonyeza kut siwa bakili muluz tv
iyi Nd bakli muluz TV yaa mcp
The ever best tv in mw we still love the people who are manengng this ❤❤❤
Kaya ndi yemweyu Kaya zopeka but never give up UTM my vote ❤❤❤
Ayi sibakili muluz TV ndi mahaka amene aja. Muivele bhobho ndi fake voice. Page imene ija yapangidwa haki ndi athu a boma ndiofina kuononga chipani cha utm. Ndiye choyamba akuyenera kuipisa mbili ya chilima. N mu audio imene ija muli zofooka zambili zimene zikupeleka chikhulupililo kut siwa bakili muluz TV
Ndipo ineyo chilima sindingamu bakile. He was indeed a bad guy with Lucius Banda.
Pamene page yomweyo ikawulutsa nkhani ya maliro a Chilima mumati ndiyabwino chifukwa akangofuna kukuthandizani kuti a UTM mumuziwe CHAKWERA pazomwe amapanga Chilima kufikira imfa yake.
Koma kunena chilungamo inenso ndinamuona kuti Chilima uja anali wamwano ndiponso anali chitsilu pa ndale. Kuzichotsa yekha kwa PETER kenako kudzalumikizana ndi Chakwera pamene paja anapusa pa ndale potengera mbiri ya MCP mbuyomu. Munthu amapanga mistake koma pokhapa ndimamukonda kuti ndiwadyera komanso ndiwamwano ndinso alibe nzeru zautsogoleri.
Mmene amamulankhulira BAKILI MULUZI purezideti wapuma uja ndinamuwona kuti tsogolo panalibepo mwa iye. Anali wa mwano kwa akuluakulu amayenera kumwalira basi
UTM sichipani chomasapota
Atupele Muluzi my Vote
Kunena zoona, Bakili Muluzi tv alibe mbali, amayamikila pamene pali bwino, komanso amadzudzula polakwikapo.
Zatembenuka, ng'ombe zayang'ana ku joko.
Yomweyo...
😆😆🤦🏽♂️❤️.
😅😅 tingodikira kut give zambili my vote to my chakwera is number one
Siwa bakili muluzi ameneyo anthunu musakhulupilire
Amene waja ndichi machine 😂🎉
Olo zitakhala zoona, who cares about DK's private life? All I know he can run the economy way better than the current situation. Malawi is not looking for munthu yemwe sananyengepo. Tikufuna munthu woti atsogolere kukonza chumachi kuti wolimbikira azidya thukuta lake. Enafe we don't care kaya akhala Chakwera yemweyi, kaya Enock Chihana, kaya APM, kaya Atupele kaya DK, kaya wa Bakili Muluzi
Chilima anasocheresa dzikoli😢😢😢😢😢
Nosense get lost bakili muluz zoputsatu izi
Ma pulopaganda a MCP awa ndipo BMT akangotukila musambulidwa🤣
Akubweletsa nkhanizi siwa bakili muluzi tv, ndiena mwa afisi achikangawa kufuna kuipisa ndikuononga mbili ya utm , komabe tinene mosapsyatila pano , chilima ndamene anationongesela malawi wathuyu , after all anangoti duuuuu ngati akumetedwa osafuna kususa nkhanza zomwe zilimdziko , nayenso chikangawa kukapha mzake pambuyo poti amabela limodzi y?, y dd u do dat chikangawa?
Zazii kumudetserela Kabambe akumuopa awa,,Zonse nchabe koma Chakwera walephera achoke basi
Aaa zazii uyu si wabakili muluxu tv
Ea ndima haka amene aja. Akayambileso. A mcp amaonatu ngat amalawi ngogona kwabasi kkkk
I don't think this is bakili muluzi , awa ndi mcp akufuna tisalankhule imfa yachilima .
This is the best station
Zimachitika koma bakili muluzi TV sayimila mbali ai palipose amang'alula bass
Ayi.izi akupanga ndi mayiko usi ngati simukuziwatu ndi manganya akupanga zosezi😊
Nkhani izi zokomera Kwa Anthu atambara wakuda.mcp
History is the best teacher 🎉🎉
😂😂😂😂 uyu nde ndakayika kut ndi Bakaili muludzi ukadusa wez history is the best teacher aa tabwali uyu
Amene uja si bakili muluz tv tikumudziwa ife ayi akusiyanilatu kwambili
Uyu si bakili muluzi tv
Who said ahhhh Like me here when listening
Dk my vote
Anthu woputsa inu asatana kupusa anachikangawa kufuna kutiwonongera utm yathu makape inu kupusa ndawononga bandle yanga panyo pani
Km yaaa ziliko kumalawi
History is the best teacher
Komano saknama bakili tvi 🎉❤
Uyuyu ndi munthu ong'alura basi
Sayendela kuti uyu ndi ndani
Ndiwe galu kwabasi sindiwe bakili muluzi TV mungofuna kungowononga mbiri zazipani zisiru inu
I like to listening BMTV 🔥
History is the best teacher
Uyu siwa Bakili tv...zaboza izii mwayitani.....Bm tv za chamba basi
😂😂😂😂😂😂😂 wakhaula uyu si wabakili muludzi tv
Kkķkkkk nane ndaivela so muli zofooka zambili
Agalu a MCP awa
Chilima anali opoila kwambiri
Uyu sibakili muluzi tv
Si wa Bakili Muluzi uyu mpang'ono pomwe. Olo mdani atakuchimwira chotani ndipo kwa nthawinso yoyamba, ungayankhulirenji zonsezi ngati kulibe mawa?
Mmmmmmmmm siwa bakili tv ameneyo ndi munthu wina
Akabambe akuchepa kwambiri kuyelekedza ndi Bakili Muluzi tv
Chimashini chija chayamba kugwira ntchito mukatero😂
Bakili muluzi guys wagudwa Inu simukudabwa ma videos ake for the past two weeks mmene akumvekela? Guys wake up everybody has price
Fake news
Munamiza ana kodi kkkk mwanya
Komabe sikudwisa big kuti ngati sanamuhaki😢
Let's gathering here
Iyiyi ndiye yeni yeni TV
Chilima anawononganawo dziko la Malawi, kupupuluma Chilima, that's why anamupha.
Mmmm kwesi koma B TV wadya chibanzi
Bakili Muluzi tv is not God cancel him in your mind be careful ndiye sitikavota if it is that
😂😂😂😂😂😂😂😂
Uyuu c bakili TV weniweni anthu a mcp awa muone kumapeto kwake akukakamila mau oti history is best teacher nonsese
Ubwino wake Chisale ndi wa kuba Kabambe mbava ya munthu
Nkhani zonsezo a Malawi akudzidziwa, kaya chilimayo, kaya Kabambe a Malawi akuwadziwa. Nkhani za personal sizingasinthe chilichonse kwa a Malawi zotsatira UTM
Machimo
I don't think that this is Bakili Muluzi TV kaya mwina
Bakili Muluzi ndi dolo ndamutayila kamtengo
Zosamveka izi mukuyakhulazi
Ai I hanger😂
Mwakhaula Uyutu si mtanyiwa ai oti tsiku ndi tsiku odzingolimbana ndi chakwela ai
Koditu chilima sanali munthu wabwino ayi ngakhale chakwera anamupha
murungu akunkhurukureni nthawi ndiyanu
Ndi bodza ili ndi propaganda ya mcp, uyu siwaBakili muluzi TV 😂😂😂😂😂 ndidzabodza ndi aganyu awa a mcp
Ku Chikangawa uku guys 😅😅😅
Sizona siiye
Ndiyomweyo kungot akangana bax kkk
Dars
Zaboza uyu
Doud Suleman ndi azizake kuyesera machine agula aja apa game mbola.
Inu uyu si wabakili muludzi tv kapolo wa mcp uyu
Kwamene akuvesesa sanganene kuti page yahakidwa koma vuto anthufe timafuna kuti munthu uja azikamba zambari imodzi
kabambe,wakuba
Yaaaaaah a mcp mwafika patali, koma mukunama naye wa bakiri muluzi simumukwanitsa ayi mwachepa dikilani akuyankhani nzanuyo akubwela ndithu chifukwa uyu si wathu wathu wa bakili muluzi ayi ine ndakana izi.
Sibakili tv ameney ndiwa mcp
nkhani izizi siza bakili muluzi tv
anjanjawidi angolowelelapo
Sibakili muluz ameneyo
Bakili muludzi TV imanena zoona ine ndimankhulupililad amankhala kut waziwona kale sogolo lake
Komatu TV imeneyi imakhwefura munthu kkkk achina kamajekete Ali ziiii
Aise ulemu wako umalongosola moveka bwino zaveka bwino kwambili
Chirima ineso sindingamuyikire kumbuyo
Sibakili muluzi TV imeneyo ndi propaganda
Si bakili muluzi ameneyo ndi zigawenga za chikangawa party mcp
MCP paja yakunga chiwembu kwa bakili muluzi TV this is plan ,,,,,
Ndale zaku Malawi ndi zosokoneza anthu
Ndi kunena zoona Ana amasiku ano sakudziwa kuti Kodi Atsamunda amalamulira bwanji dziko lino. Chimene akudziwa ndi kulemba Nkhani ZOSOKONEZA A MALAWI pa SOCIAL MEDIA basi, komanso kuwapatsa Bomali popanda masankho sangathenso kulamulira dzikoli adzangokhala mavuto okhaokha basi.
Zazi SI Bmtv uyu 😢😊
Lankhulani koma timuvoterabe
Ndi propaganda iyi zamkutu bas
Soi ndiye uyu wa BM Tv😂😂
Mkamalimbana ndi BMT mutha ngati makatani
Mmm ayi sizoona izi
Mayaz sibakili muluz tv uyu aaa timatha zimenezo kulemba pa page yamuthu
Kkkkk koma bakili muluzi alipo
Alipo tavera kale atulukira lero lino
Kulibe panopa. Wapangidwa haki
Ameneyo sibakili muluxi TV
Si wa Bmtv ameneyo
But you have to check because there are many bakili muluzi TVs...else you bakili muluzi never does this