zomwe zachitisa kut Tamia amangidwe

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 18 жов 2024

КОМЕНТАРІ • 207

  • @johnbanda-v8x
    @johnbanda-v8x 27 днів тому +4

    Ndiwakuba nanga anapitiranji Ku south Africa ngt ndalamayo sanatengedi ndi iyeyo

  • @afoso-hy1hc
    @afoso-hy1hc 7 місяців тому +3

    umenewo ndimoyo wakuba ndichifukwa amalawi tikuvutika ndiumphawi tidazolowela zaulele

  • @T0R1N0.
    @T0R1N0. 7 місяців тому

    ,,,😂😂😂same Story life goes on with straggle....sapasa pamanja guys amene anyambisa mawu awo analakwisa *(SAPASA PAMANJA)*

  • @joycemhango4353
    @joycemhango4353 7 місяців тому +2

    Otumiza tiyeni tizionesesa, osamayikana mmayesero Malawi wavuta uyu tonse tikudziwa chonde!!😊

  • @Doreen-r3w
    @Doreen-r3w 7 місяців тому +3

    Tamia ndi wakuba kumene akufuna kukolora pamene asanalime mmmm ntsikana iwe umuziwe yesu ndi ophunzira ake 12

  • @AbdulIssah-l1e
    @AbdulIssah-l1e Місяць тому +2

    Waba abweze zonse .apange back to sender kwa mwini wake wa ndalama .nkhani inthepo .ngati iyeo akufuna ndalama akagwire tchito kujoni kweko it's fine.

  • @EuniseMasuku
    @EuniseMasuku 22 дні тому +2

    Yakwiya ndi mizimu😂😂😂😂😂

  • @YamikaniHardwick
    @YamikaniHardwick День тому

    Ndiwakuba ameneyi sanakantawa

  • @sparksLupia
    @sparksLupia 14 днів тому

    Ameneyo sanabe cos zinagoneka iyeyo kukana

  • @HamidMalisawah
    @HamidMalisawah 23 дні тому

    Sanarakwise

  • @YassinHayatu
    @YassinHayatu 22 дні тому

    Mr. Sam Mavitha share me the underground song. Please please. " Undiphunzitse"

  • @ChrisBanda-f5d
    @ChrisBanda-f5d 22 дні тому

    Oky tamia alakwitsa ku samutsa ndalama zoti sizake pa umunthu guys

  • @SamuelMoyenda-p6k
    @SamuelMoyenda-p6k 7 місяців тому +2

    Mbava imeneyo boss😂😅😂

  • @AllanNkolimbo
    @AllanNkolimbo 12 днів тому

    Chimene chimamupangitsa kusintha account yake nkubwela pomamukananso nzakeyo kuti sanaziond ndalama,nde kubako kumeneko

  • @QUAVOMANANA-zy8ey
    @QUAVOMANANA-zy8ey 3 години тому

    Mwina amaona Ngat ndi mwayi wake

  • @MelassiKamanga
    @MelassiKamanga 7 місяців тому

    Kodi nanga mesa pamatsamba a zodiak ndi enawo akuti koma zoti walandira ndalama anavomera?komanso 8million yo anaipanga transfer online pakamodzi Kodi sikhala ndi limit patsiku?

  • @ElizabethKazambwe
    @ElizabethKazambwe 7 місяців тому +1

    Tamia ja siwakuba,ndipo sikutiso walakwitsa ai ameneo ndi manner😅😅

  • @LotiesMadula
    @LotiesMadula 16 днів тому

    Siwakuba amusye

  • @TIMECLEMENT
    @TIMECLEMENT 12 днів тому

    Kusamutsa ndalama kokhako ndkubakumeneko

  • @RobertNKhoma-i6j
    @RobertNKhoma-i6j 22 дні тому

    Koma ngati police sagwira ntchito moyenerera ndie kuti ali mbali yake

  • @PatrickMedson-c2i
    @PatrickMedson-c2i 12 днів тому

    SApatsa pa manja unali mwai wake

  • @MaggieChingamba
    @MaggieChingamba 12 днів тому

    Ndikuba kumeneko amagwidwe

  • @EdinaChimkwita
    @EdinaChimkwita Місяць тому

    Yes kumeneko ndikuba. Chifukwa mwiniwake anadziwika komaso kupta ku joni kunali kusowa mtendele ndi tchimo

  • @TemwahChavula
    @TemwahChavula 22 дні тому

    Akanakhala wakuba sakanabwelako ku south

  • @FebbieNjewa-g3k
    @FebbieNjewa-g3k 22 дні тому

    Anacenjeretsa ndipo ndidolo mbava

  • @BillySaukani
    @BillySaukani 7 місяців тому

    Munthu sungatenge ndalama zoti sizako , kumeneko ndi kuba , amupani apolice kuti apereke ndalamazo.

  • @SimonCovane
    @SimonCovane 29 днів тому +1

    Ndikuba kumeneko Amangidwe ameneyo

  • @patrickkalivea6879
    @patrickkalivea6879 7 місяців тому

    Ngati Pali umboni kuti ndalama zinalowa mu account yake iye akanawona kuti watuma ndalamayo ndindani then amufunse kuti zakhala bwanji ?,kutenga ndalama zisali zako ndi kuba kumeneko

  • @ChisomoGanizan
    @ChisomoGanizan 3 місяці тому

    mbuz imanya pomwe ayimanga kkkkk wakhoza

  • @MakiyiBanda
    @MakiyiBanda 6 днів тому

    Eya analakwitsa ndi moyo wakuba

  • @MccollingsPmtambo-v4u
    @MccollingsPmtambo-v4u Місяць тому

    Anaba akufunika abweze ndalama zamwini

  • @Freedomchennl47
    @Freedomchennl47 7 місяців тому

    Eya Tamia analakwinsa chifukwa munthuyo anatumiza by mistake mwanchidule kumeneko ndkuba

  • @YasintaChiphamba
    @YasintaChiphamba 7 місяців тому +1

    Zalowa zokha 😅 amujata bwa

  • @MagretNgunga
    @MagretNgunga Місяць тому

    Ndiwakuba ameneyo.Akanazibweza ndalamazo

  • @RabbiMacheso
    @RabbiMacheso Місяць тому

    She was supposed to return money to the owner because she became aware of who accidentally sent that amount of money. Transferring money from one account to another signalled an element of theft in her.

  • @DaudAjusu-y3x
    @DaudAjusu-y3x 12 днів тому

    Zinangochitika koma iyey siwachoncho mumadziwa ukaona ndalama satanas amakulo iyey ndimunthuy angokambilan zandendele

  • @DavideWilliam-x8s
    @DavideWilliam-x8s 7 місяців тому

    Kkkkkk eeee kma zavuta mayeselo awa

  • @KidoJames-y9u
    @KidoJames-y9u 7 місяців тому

    Koma ameneyi wayaluka chaka chino nkhani chake chachuluka uhule ulimomo apaso akuba kkkk zachisoni

  • @denissegabriel2752
    @denissegabriel2752 7 місяців тому

    Sanabe koman zangochitik alanakhal iwow akanatan😥😥😥😥

  • @ImranIshmael-j7v
    @ImranIshmael-j7v 7 місяців тому

    😂😂😂😂sizochtanso kufunsa ndkuba kowonekera kwaumbuliii

  • @NelsonPhakira
    @NelsonPhakira 7 місяців тому

    Siwakuba wapereka yekha wachola kunyumba kwake?

  • @ActonSamkachingwe
    @ActonSamkachingwe 14 днів тому

    Kkk

  • @xinalungu9616
    @xinalungu9616 7 місяців тому

    Kamtima kakuba Ali nako.
    MY OWN WXPERIENCE:
    I wanted her to advertize for me on an awareness campaign, and she insisted that I should just send the money without meeting or signing a thing.
    Ndinaona ngati ndalama zanga zipita.
    I withdrew

  • @Mercybanda-m3d
    @Mercybanda-m3d 24 дні тому

    Tamia ndi mbava chifukwa amamufusa iye amakana

  • @WatsonChimphine
    @WatsonChimphine 7 місяців тому

    Siwakuba Tamia apopo apolice aziona Kaye information yankhani ndi mene nkhani inachitikila mtulutseni Tamia izo ndi chisomo chamulungu kuvomela anamuuza mkului kuti unditumizile ndalama wa shaut mulandi ine watson kuno Ku Durban SA

  • @HenryChitenga-j4r
    @HenryChitenga-j4r 6 місяців тому

    Kudziko lapansi kulibe yemwe samaba kungoti timangosiyana mabedwe.Tamia asayankhulidwe chipongwe Chifukwa cake zaoneka lero

  • @LesterGamula
    @LesterGamula 23 дні тому

    kuba kumenekoo

  • @EdwardZuze-r7w
    @EdwardZuze-r7w 24 дні тому

    uku ndi kuba basi

  • @nathanvanderberg6558
    @nathanvanderberg6558 7 місяців тому

    Eya ndiwakuba ammeneyo ndipi wazionongeka cv

  • @RichMavoko-nx8cn
    @RichMavoko-nx8cn 7 місяців тому

    Timvele nawo brother zimenezi 😂😂😂😂😂😂

  • @HawaPearson
    @HawaPearson 6 місяців тому

    Ndikuba anakana bwanj atamutumizila?

  • @Rajabuhassani-nu9cd
    @Rajabuhassani-nu9cd 6 місяців тому

    Chakuba chimenecho ayse

  • @esthermalixani2244
    @esthermalixani2244 7 місяців тому

    Ea ndiwakuba coz nga munthuyo anamuuza kt warakwisa number anayenera kuvomereza ndikubweza ndaramazo

  • @JaytrixMalawi
    @JaytrixMalawi 3 місяці тому +1

    Wakuba bas

  • @patienceThomJannah-xy8uw
    @patienceThomJannah-xy8uw 7 місяців тому

    Or ndili ine ngatenge😂😂😂😂

  • @HenryHarrison-d2n
    @HenryHarrison-d2n 13 днів тому

    Ndiokuba anapitilanji kunja

  • @EduardoTipa-pb2bc
    @EduardoTipa-pb2bc 7 місяців тому

    Mabigi ameneyu sanabei mutakhala inu mungatani amalawiso umbuli udakula inu mungatani

  • @FrankGoodwill
    @FrankGoodwill 6 місяців тому

    Ndikumba kumeneko ikhale kuti ndiyake sakanasitha account

  • @MathewsEnamu
    @MathewsEnamu 7 місяців тому

    Sangalakwitse Mulungu sapereka pa manja aaaa

  • @MankhauleErnest-i3v
    @MankhauleErnest-i3v Місяць тому

    Kumeneko ndi kuba umaona ngat zalowa Za manja lende Za sefukila masikwanozi

  • @mphatsomonjeza4371
    @mphatsomonjeza4371 7 місяців тому

    Zaziii kungo funapo ma comment athu ku UA-cam

  • @MankhauleErnest-i3v
    @MankhauleErnest-i3v Місяць тому

    Kumeneko ndi kuba analakwisa

  • @JamesChiphwanya-m4v
    @JamesChiphwanya-m4v 7 місяців тому

    Akanakhala kt siwakuba akanabweza ndalama kwa mwini wake koma ngati sanabweze ndiwakuba

  • @MavutoSandfor
    @MavutoSandfor 7 місяців тому

    Siwakuba ai km muthuyo amamuyesa

  • @George-yi2iz
    @George-yi2iz 7 місяців тому

    Kkkkk zonsayenda bwanjik apa 🤔🤔

  • @LloydPund
    @LloydPund Місяць тому

    Mmmm PA easy zimachitika

  • @JoabCharly
    @JoabCharly 13 днів тому

    Ndiwakuba

  • @SaraiKambata
    @SaraiKambata 7 місяців тому

    Kumeneko ndikuba abweze ndaramayo

  • @JimmyBanda-fi3pw
    @JimmyBanda-fi3pw 6 місяців тому

    😂😂 km yooo

  • @TheresahChilinjala
    @TheresahChilinjala 7 місяців тому

    Ayitu analakwisa akangovomela ndikumubwenzera mwiniwake yo if zili zoonadi

  • @LukeTsakalalo
    @LukeTsakalalo Місяць тому

    Anapanga umbav

  • @LovenessBanda-s7o
    @LovenessBanda-s7o 7 місяців тому

    Akanabweza ndalama zaeni ake bas

  • @VaidaNkhana
    @VaidaNkhana 7 місяців тому

    Pena chilungamo chimafunika ndithu uku ndikuyaluka choncho munthu ndiwachichepere mbiri yako yikuonongeka eish zandikhuza bwanji bola abwenze aona kuti apanga bwanji chamwini ndichamwini basi tamia uzivere chisoni
    komwe uliko

  • @AustinKanjoka
    @AustinKanjoka 7 місяців тому

    Amayenela kubweza ndalamayo kwa miniwake chako ndi chako chamwini ndi chamwini basi

  • @RedsonChabwera
    @RedsonChabwera 7 місяців тому

    Chilungamo ndichakut Tamia analakwitsa kwa kukulu Mistake ngt imeneyo mix kwa munthu otiso akuchita naye malonda sanayenera kupanga zimenezo Apo nkhan ndi kubweza ndalamazo bas.

  • @PiriraniMaganga
    @PiriraniMaganga Місяць тому

    Ndiokuba ameneo

  • @lusolawo73
    @lusolawo73 7 місяців тому

    Kkkkkk km khani zake 😊

  • @MaxwellNjanji
    @MaxwellNjanji 2 місяці тому

    Ndi wakuba ameneyo😮😮

  • @CassimAssam
    @CassimAssam 24 дні тому

    Mbava imeneyo

  • @BrianLucas-me4sg
    @BrianLucas-me4sg 6 місяців тому

    Ndiwakuba ameneyo

  • @ShafineLouis
    @ShafineLouis 7 місяців тому

    Ndiwakuba basi khani ikuzikamba yokha big

  • @frankkassim1254
    @frankkassim1254 7 місяців тому +1

    Kumeneko ndikuba sakazisakusa ndalamazo

  • @ChikondiKajawo-tm1ud
    @ChikondiKajawo-tm1ud 6 місяців тому

    Ea niwakuba iyeyo anakavomela

  • @MuhammadJuma-h7w
    @MuhammadJuma-h7w 7 місяців тому

    Ndiwakuba ndi chifukwa chan anasintha acount

  • @PUTOJOAQUIMUPILARE
    @PUTOJOAQUIMUPILARE 7 місяців тому

    Kumanena chilungamo Tamia ja ndi wakuba

  • @OmakiMataya
    @OmakiMataya 7 місяців тому

    Ameneyo.ndiwakuba
    Kwambiri.akufuna
    Nzake.angwire
    Ntchito.yopanda
    Malipiro

  • @HappyFlamingo-dz1uo
    @HappyFlamingo-dz1uo 6 місяців тому

    Oimba wakuba mbala?😂

  • @AdelaZabibu
    @AdelaZabibu 7 місяців тому

    Ndiwakuba kunonso zinachitika chimozimozi ndipo anagamulidwa kukaseva 2yrs chifukwa three qts yandalama anayipeza

  • @Cobra.D-t3z
    @Cobra.D-t3z 6 місяців тому

    Ndye yake Tamia mistake siyako
    Mulungu amapatsa mosiyana osalora munthu kulanda zomwe Allah wapelereka mu mwezi wa Ramadan uno

  • @AustinYusuf
    @AustinYusuf 6 місяців тому

    Ndiwakuba basi aaaa

  • @franciskhomela
    @franciskhomela Місяць тому

    ngati otumiza ndalama yo inali mistake iye ndi kukana ndiwakuba

  • @JackMaster-m1y
    @JackMaster-m1y 6 місяців тому

    Siokuba km anachita kumungayila

  • @AMWENEJomba
    @AMWENEJomba 7 місяців тому

    Ndiwakuba ameneyo 😂😂😂

  • @MichaelBanda-q7w
    @MichaelBanda-q7w 9 днів тому

    4 y

  • @sanniebwanali4643
    @sanniebwanali4643 Місяць тому

    😂😂😂ndiwokubaameneyo

  • @HaroonMaundala-e4z
    @HaroonMaundala-e4z 7 місяців тому

    Ndiwokuba basi

  • @MavutoSandfor
    @MavutoSandfor 7 місяців тому

    Sanalakwitse

  • @marypatriciamakuru226
    @marypatriciamakuru226 7 місяців тому

    Mmmm ndiwakuba

  • @fraiserkapito-yb2ob
    @fraiserkapito-yb2ob 7 місяців тому

    Pamenepo analakwitsa anaba, chifukwa analandira ndalama yoga khala yake komanso anaziwitsidwa kuti siyake koma iye ndikupanga chitsankho choyisintha account

  • @GibsonTembo-e9m
    @GibsonTembo-e9m 7 місяців тому

    Sana chite bwino

    • @HassanTaibu-w4d
      @HassanTaibu-w4d Місяць тому

      akanakhara kt siwakuba akanabweza ndaramazo