Dan Lu Waona Zosaona

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 18 жов 2024

КОМЕНТАРІ • 303

  • @MalikopoKho
    @MalikopoKho 24 дні тому +21

    Olo ayimbe sangayimbe momwe anayimbila dpp akunama

  • @BrownMaseko-f2h
    @BrownMaseko-f2h 24 дні тому +5

    Kodi Dan lu school yao anapita naye patali? Cfk munyamata ngat uja sangasapote boma ili mcp m'mene tikuvutikila Dan lu chisilu chamunthu

  • @FarookYahaya
    @FarookYahaya 25 днів тому +12

    Am from mangochi 😢 but l will leave bro dan lu ..my vote dpp

  • @MalidadJaffalie
    @MalidadJaffalie 21 день тому +2

    Adan mwaganiza bwanji kufuna kutchuka kapena bwanji km ndiye muli pa topic osati patop MN Malawi wakudan🤣🤣

  • @ManaleDavieson
    @ManaleDavieson 24 дні тому +18

    Ine kuchokera Ku Lilongwe Dan Lu ndikape ndipo ineso ndamutsika

  • @charlesmapulasi7230
    @charlesmapulasi7230 24 дні тому +2

    Nthawi sidikira munthu umafuna azituwa ndi maluzi mdzina loti ali loyal kwa APM? Iweyo usachedwe ndikumapanga follow moyo wa munthu wina kuti zimuthera bwanji, he is full grown man he knows what he is doing

  • @MMADICHANDE
    @MMADICHANDE 24 дні тому +10

    Dan lu ndamutuluka akhoza kundphesa ngat chilima

  • @SjohnHassan
    @SjohnHassan 20 днів тому +1

    Saziziwa ndale ameneyu, komanso ndichisakho chake

  • @BensonMajigaweston
    @BensonMajigaweston 24 дні тому +7

    Even me am from Ty ndamutuluka dan

  • @Zaiducassim
    @Zaiducassim 23 дні тому +2

    Dan lu is full with mad and he don't know what he is doing he still young

  • @FranciscoChipeso
    @FranciscoChipeso 24 дні тому

    Nde zimene mukupangazi mupindula chani😂😂😂😂 a Malawi tamaonan nkhani yojama pezan zina zochita

  • @KingDavedNkhata
    @KingDavedNkhata 24 дні тому +6

    Dan Lu ndi kape kwambiri
    Osalikonda dziko lake mwachidule kungoti ndi wa dyera

  • @NosiphoMazibuko-e9z
    @NosiphoMazibuko-e9z 24 дні тому +3

    Km guys tizaname chakwera anthu atopa naye kabasi km ndikudziwa kugwa kwandalama kumalawi zamanyasi ndalama daily kugwa ai zamukanika chakwera economic yamukani dziko zithu zikufuta kumalawi ndeno wina kubwela kumayamikila za mcp zikufutani chifukwa anthu kumalawi adazindikila zoyiopa amata kuzoona zabwino amayamikila km khuluyu zamukanika chakwera

  • @HappyAbyssinianCat-xt2bm
    @HappyAbyssinianCat-xt2bm 24 дні тому +6

    Dan lufani ndi kachisiru chakwera walephera kulamulira malawi waoneka kut ndi mburi sanalowe nkalasi zikuchita kuonetsa umbuli sizinthu

  • @Joel-o3k
    @Joel-o3k 22 дні тому

    Dpp my vote, Dan Lu saganiza my boh

  • @OmegaChingamuka
    @OmegaChingamuka 24 дні тому +8

    Wamisala ameneyo kukonda ndalama

  • @LacksonLombwa-b6x
    @LacksonLombwa-b6x 21 день тому

    Musiyeni Dan, iyeyo Ali ngati civil servant, amagwira ntchito ndi Boma lolamura.

  • @LeviImani-w3d
    @LeviImani-w3d 24 дні тому +2

    I salute the Senas from. Chikwawa. they don't waste time in talking or singing they act ask chakwera nkasi for referance

  • @PeterMhon-n6c
    @PeterMhon-n6c 24 дні тому

    Ndasiya kumupanga follow Dan Lu apite uko

  • @JonesGolomoti
    @JonesGolomoti 24 дні тому +3

    Ndamu Tsika Da Lu

  • @leahkasiwa5033
    @leahkasiwa5033 23 дні тому

    Dan lu sakudziwa komwe akulowera akungoyendela mwabi uja oti chagwa mumbale ndi ndiwo 😮

  • @EltonMbepula
    @EltonMbepula 22 дні тому

    Chilungamo ndichimene chimavuta iyeye kumbali yake zilibho mukutaya nthawi ndinthu musiyeni Dun lu ndichisakho chake 😂😂😂

  • @JamesChiphwanya-m4v
    @JamesChiphwanya-m4v 23 дні тому

    Chenjezo kwa anthu oyimba zandale muononga nazo nyimbo zanu khutilani ndi momwe mukupezera zandalezi pena zosaykisaso

  • @JemaxChibwanazulu
    @JemaxChibwanazulu 22 дні тому

    Ndayesera kutuzura maso anga kut ndionesese ma comment a anthu amene ali mbali ya MCP, kma ndaona modz yekha bas amene wakomenta kut MCP my vote. Ma comment onsewa munthu modzi bas ndili ine mkanangokhala chete ndthu😂

  • @JoshuaNgosi
    @JoshuaNgosi 24 дні тому +2

    Saziwa chomwe akuchita, akukwera chipani Cha ng'ona zoonadi😂😂😂

  • @FulaKampoza
    @FulaKampoza 21 день тому

    Mbuzi iyo amupanga follow nde abale Ake basi

  • @JohnMankhwala
    @JohnMankhwala 22 дні тому

    Muthu akamafuna kufa amayamba kufa mmakutu kumuuza osamva, zabwino zimene akuyamikila pamenepa ndiziti? amenewa akuvuta kuwamvesesa, komano ndalama sizimatha tinazipeza ndipo tizazisiyaso zomwe tilinazo muthawiyo MULUNGU amapeleka muthawi.

  • @MikeMoris-zp6yg
    @MikeMoris-zp6yg 24 дні тому

    Ngakhale mumusike kma ife tili nga! To follow him

  • @Idrissa-r2h
    @Idrissa-r2h 24 дні тому +7

    Muzipanga trening Kae kuyankhula ko mukuzilumaluma bwanji apa aaaaa

    • @VincentMaluwankhata
      @VincentMaluwankhata 23 дні тому

      Uli mbari iti nyan iweso? Ige kuno kumangochi zikutiwawa musiye sam mavita

  • @HastingsStoneck
    @HastingsStoneck 22 дні тому

    Zafika poti aliyese emwe dzina lake likumayambira ndi dan ndikumamupanga unfollow ndikuona ngat zawo ndizimozi agalu amenewa🙄

  • @thomasmtonga4056
    @thomasmtonga4056 24 дні тому

    Hustling ngati mmene iweyo ukumanenera za iye Dan Lu amene

  • @MoosaKaunga-w5w
    @MoosaKaunga-w5w 23 дні тому

    Sindingamvelenso nyimbo zake ndi kape ameneyo

  • @Amirkhan-nn6pz
    @Amirkhan-nn6pz 19 днів тому

    That’s the truth 😊

  • @isaacimmantambala5294
    @isaacimmantambala5294 24 дні тому +2

    kod ndingampange unfollow bwanji mthila kuwili amenei 🤣🤣🤣🤣

  • @bestonlamson213
    @bestonlamson213 23 дні тому

    Dan lu ndi chidzete sakudziwa pomwe Ali ai ndipo ndamutulukanso iyah

  • @CatherineDesire
    @CatherineDesire 23 дні тому

    Ka mutu ka kadzungulira (mtima wake wazungulira mutu👉♥️wazungulira👉😇)tsakudziwa chimene akuchita

  • @DavidPhiri-o6w
    @DavidPhiri-o6w 23 дні тому

    Kulibe Ali ndi udindo kusankha chofuna ndi anthu angati atuluka ku DPP, kabambe, Kondwani ambiri Dan lu alakwa chani leave him I and others will love him

  • @FernandoRaimundoMalefula
    @FernandoRaimundoMalefula 22 дні тому

    Adani Lu akumudwisa Malawi ayenera ku sika mapoete nhamata zimamuyera ku Dpp a ayenera ku kala ku Dpp ngati zili ndalama ha mavuto wokawoka

  • @ShukuraniChitanganya
    @ShukuraniChitanganya 23 дні тому

    Anali ndani wanga mkale wangowonjezera udani

  • @lungisanishezi1023
    @lungisanishezi1023 23 дні тому +2

    Malawi yomse sindinaone munthu opusa ngati Dan lu😂😂😂

  • @MusaGeorge-o8r
    @MusaGeorge-o8r 23 дні тому

    Dan lu ndayamba kukuda aise pazomwe wapang wayamba kundi nyasa ndi zikuda

  • @LawrenceNdala
    @LawrenceNdala 21 день тому

    Nkhani ndi malamulidwe ,achimwene, inuyo zilipo zina simukudziwa yanu ndi ya You tube yomweyo. Tisiyeni ife womwe tikuganiza mozama kwambiri. Muzakhulupirira tsiku lina maganizidwe anu akakhwima.

  • @GraceLimani-zw7dx
    @GraceLimani-zw7dx 24 дні тому +1

    Angowoneka ngati nyau akavala za mcp zakezo

    • @SliviaJosephy
      @SliviaJosephy 22 дні тому

      Waswala pangono kufa siyeni akafere komweko

  • @DEXSTALLONEKAWAMA-s4g
    @DEXSTALLONEKAWAMA-s4g 24 дні тому +3

    Titi agone ndi njala zanuizo mumutukwana mutopa ife tetitimutsike ndithudi azichimwene anga ndi chisankho chake zikomo

  • @BlessingsMasakala
    @BlessingsMasakala 24 дні тому +2

    Ngakhale ineyo kupita kukamuchezera nzanga ndy kumupeza akumvera nyimbo ya dan lu nditha kubwerera kunyumba sindingachezenso ndioipa kwambl dan lufan crc

  • @FUTUREALEX-b7k
    @FUTUREALEX-b7k 20 днів тому

    Mpeni wakuthwa mbali zonse umapha atipha Dan Lu tichenjele

  • @NdaonaSandifolo
    @NdaonaSandifolo 13 днів тому

    Pezani zina zoti muzilankhula chifukwa dan lu zake zikutheka chakwera kumenya kugwetsa

  • @SgoraNgubane
    @SgoraNgubane 23 дні тому

    Gulu ameneyo komaso zochita zake ndichimodzi modzi ndi hule wakubala

  • @EddiePhiri-w2d
    @EddiePhiri-w2d 23 дні тому

    Kape uyu Dan ndipo ndi kamwana kosakula panchombo

  • @GerladThole
    @GerladThole 23 дні тому

    Koma ma representer muzipangako proved before musanabwere ndi programs

  • @BwanaGD
    @BwanaGD 23 дні тому

    Masatanic asiyeni azipanga zawo izi ndizomwe anagwilizana kumidima kwawoko asativetse mutu ife

  • @HappyMwale-qy6up
    @HappyMwale-qy6up 24 дні тому +2

    Iweyo sam imila mpando wa u president tiwone ngati unga kwanitse.

  • @DavidPhiri-o6w
    @DavidPhiri-o6w 23 дні тому

    Uchitsiru leave Dan lu alone he has Rights

  • @KALOLINIKASIMU
    @KALOLINIKASIMU 22 дні тому

    Dan lu wandinyasa ndipo ndikangokumana nawo Kwake kwatha

  • @HamzahTwaib
    @HamzahTwaib 24 дні тому +6

    Iyeyo ndi mbamva

  • @lastongomebanda3621
    @lastongomebanda3621 14 днів тому

    Dan Lu ndidolo 🎉 mbambande

  • @YUSUFPILIRANIMKUWA
    @YUSUFPILIRANIMKUWA 23 дні тому

    Dan lu wapanga apa zosayenda Alibe mbali yeniyeni ali ngati lezara,amdala yatesiye wee pela ayao itunyalayisye ngawa twasisile iyayi

  • @PaulNtaibu-w9d
    @PaulNtaibu-w9d 23 дні тому

    Ineyo ndikudziwa kuti iyeyo akungofuna ndalama, dyera yakula pa iyeyo mwina waona kuti watsala pang'ono kodi siMutharika yemwe ampulumutsa pakati pompa, ndiye bola amusunge bwino

  • @DalitsoPhiri-sq5nl
    @DalitsoPhiri-sq5nl 23 дні тому

    Inetu zinthuzi ndazikonda kwambiri achinyamata sanadane ndi Dan komano akudana ndi ulamuliro omwe Dan akusatila now pempho ndiloti tiyeni achinyamata 2025 tikapange zomwe zamuonekera Dan zikakhaleso chimodzi modzi ndi pothana ndi ulamulilowu

  • @VincentMaluwankhata
    @VincentMaluwankhata 23 дні тому +1

    Iam from lilongwe but Dan Lu ndimkamusata but now ndamutuluka and iwill never back gain wapanga unve

  • @HaleemaAllie
    @HaleemaAllie 24 дні тому +1

    Dani lu mwangodya zimenezo voti yanga ndi apetar mutalika ❤❤❤

  • @RaffiqMahmoud
    @RaffiqMahmoud 24 дні тому

    So ma followers amagula Ufa kunyumba kwa dan lu ,zitsilu za mu social media 😊

  • @JosephMalunga-hp6fm
    @JosephMalunga-hp6fm 23 дні тому

    Dan lu ndikape akuopa kufa
    Koma ine vote yanga ili pa dpp

  • @KanthuSankalah
    @KanthuSankalah 23 дні тому

    Mbuzi imeneyi sizaidera bas

  • @AlexNjanje
    @AlexNjanje 22 дні тому

    Dan luu adzafa osauka dyera too ubwino wake amakwera zipani zakufa amagwersa zipani mwachinsinsi

  • @AusmanYusuf
    @AusmanYusuf 22 дні тому

    Musamaneneso kuti ndi kaswili
    Muzinena kuti galu alikumbuyoyu.

  • @SammieDickson-ln2hp
    @SammieDickson-ln2hp 24 дні тому +1

    Dan lu machende ako ndipo ndakutuluka namapwala iwe umaimba bwino km pa zimene wapangazi tchende lako ndipo nyimbo zako zonse mdachosa muphone mapwala ako

  • @MosesPinto
    @MosesPinto 21 день тому

    Kuno ku nsanje dan lu ndimamukonda koma ndamutulu alibe nzelu ndi opusa

  • @Samson-ve5rs
    @Samson-ve5rs 24 дні тому

    Koma muzakonzeke mukazamabweranso of course Dan Lu ndi kape kwambiri wapanga iye

  • @JumahKphiri
    @JumahKphiri 24 дні тому +3

    Siyani ndale achimwene please

  • @ChimwemweRajab
    @ChimwemweRajab 24 дні тому

    Kukana kukaimba ku conversation ya DPP kunamizira kudwala galu ameneyi

  • @kayceesamuels
    @kayceesamuels 23 дні тому

    Yense akubakira dan lufani mgalu kwabasi

  • @Echohorseman
    @Echohorseman 24 дні тому +2

    Nsanje ndi nkhani imodzi yomwe pa national anthem ikukambidwa momvekabwino.

  • @ChikumbutsoMaluwa
    @ChikumbutsoMaluwa 24 дні тому

    Inu osapanga zanu bwannj

  • @InnocentMtafya
    @InnocentMtafya 21 день тому

    Mwasowa chochita eti,mmalawi analozedwa ndithu brain ndindani anazichosa kuti tizingomvera zopusa zilizonse nkumamvera umbuli Ndi nsanje.

  • @Pamela-lu7vi
    @Pamela-lu7vi 24 дні тому +1

    Danlu walowa usataniki gayez chonde Dpp ndiye vot yanthu

  • @yowasschitsosa5348
    @yowasschitsosa5348 13 днів тому

    Kodi dan lu aziendela maganizo anu alibe chisankho ngat munthu ? Kkkkkkk anthu mulibe manyazi kkkkkkkk

  • @actuarialscience2283
    @actuarialscience2283 24 дні тому

    1) Atupele Muluzi, Danu Lu akhale chitsanzo chako. Atapanga ubale ndi MCPoop(=MCManyi) anthu amutuluka.
    2) Chitsanzo ikhale UDF ya abambo ako. A John Tembo ananenetsa kuti iwowo sanapangepo ubale ndi UDF polimbana ndi DPP ya Bingu👈Uzikumbukira izi.
    3) Chitsanzo chowawa ndi UTM. A MCPoop anakanitsitsa kuti iwowo sanapangepo ubale osayinirana ndi UTM. Kenako anapha Chilima.
    Anga ndi malangizo. Ubale sitipanga ndi Nyau.

  • @SliviaJosephy
    @SliviaJosephy 22 дні тому

    Asiyeni oyimba onse apite ku MCP we don't care about that what we need is freedom, peace in malawi,,,boma liti lomwe anagulitsapo fetereza 100,000 kufuna kupha apwawi

  • @AishaMaduka
    @AishaMaduka 23 дні тому

    Nthata ya njala mbuzi Dan lu

  • @HardwickKaunda-o7j
    @HardwickKaunda-o7j 23 дні тому

    Mavitha ndi wa DPP wayambaso ndale?????

  • @thomphalavi5027
    @thomphalavi5027 24 дні тому

    Nyimbo siku koma..... Inuyo guys izi simbali yanu pangani Zina mutitaisa thawi nonse awiri😂😅😂

  • @AshraffZuliyani
    @AshraffZuliyani 24 дні тому

    Tilibe naye ntchito kachitsiru gag

  • @RichardChalemera
    @RichardChalemera 24 дні тому +1

    Dan Lu ndi Munthu woganiza kwambiri ndipo

  • @ClearKondowe-m3j
    @ClearKondowe-m3j 17 днів тому

    Anthu wotengeka ndi ndarama hmmm sidzimuthandiza izi. Koma or manyazi ndithu

  • @GiftSteven-ur4ju
    @GiftSteven-ur4ju 24 дні тому

    Tazingo jamani yanu guyz mukuchedwatu iye wavaya basi😂😂😂😂😂😂

  • @osaukaonjoya
    @osaukaonjoya 24 дні тому +2

    Lebo la wachiyao wangalusya asiye asa.agwiritseso ntchito

  • @kasimmussa-c5v
    @kasimmussa-c5v 24 дні тому

    Dun lu wawonesa kupusa kwake pa a chinyamata that's y achinyamata amutuluka am one of them

  • @DEXSTALLONEKAWAMA-s4g
    @DEXSTALLONEKAWAMA-s4g 24 дні тому +1

    Palibe zimene mukukamba inu munthuyu sadya kwanu ndichisankho chake kodi wakupwetekani kwambiri inu adpp ayiayi musiyeni nzanu ndi M'malawi dan lufann pezani artist wina or Gibo piyason atha kumayimbira chipani cha dpp komanso amayimba kale mukufuna chiyani kwa dan

  • @OsmanMsini-xo1wh
    @OsmanMsini-xo1wh 19 днів тому

    Akunama Dan _lu ndichisilu

  • @LuciusMowa
    @LuciusMowa 24 дні тому

    Guys asatichedwetse D Lulu apapa waonekeratu kuti wadya ndalama ameneyo osazamuvotela ngati akufuna kuimilira U MP ndi munthu osathandiza

  • @seerchidothi8254
    @seerchidothi8254 23 дні тому

    Ndinkayesa munthu

  • @ThandiMwase
    @ThandiMwase 21 день тому

    Dan Lu dyela basi kufuna ndalama

  • @Alexchikweza
    @Alexchikweza 24 дні тому

    Dan lu samakhala ndi moyo chifukwa chama followers tisaiwaleso zimenez.

  • @BulianKandulu
    @BulianKandulu 23 дні тому

    Am also muyao but this did I left him

  • @MarkoMayuni
    @MarkoMayuni 10 днів тому

    Kodi dpp yapwetekedwa kwambiri lu ku joina mcp simunati

  • @EmmanuelGordon-q9s
    @EmmanuelGordon-q9s 21 день тому

    Mukuyesesa man

  • @AwaliShaibu-n6e
    @AwaliShaibu-n6e 22 дні тому

    Dan Lu ndi mthira kuwili

  • @ishmaelmaluwa5901
    @ishmaelmaluwa5901 24 дні тому +3

    Mbuzi yamuntu

  • @inessmsiyambiri8517
    @inessmsiyambiri8517 22 дні тому

    Anatsikidwa kalekale kapeyi