It's so nice Guys, but one thing; Piksy, Sangie and Hyphen must not be Actors, how come enawo mukuwatchula maina apa msonkho koma inuyo mukumazitchula ma funky names mu Serious business ngati iyi? Separate Music and this thing please. We appreciate but make sure to think about it.
Mama bwelani mama mukomokatu😂😂😂
It’s always ganizani 😭🤣🤣🤣 wayamba kudziwa mankhwala liti 😭
Eeeh ma guys inuyo wisdom yabwanji iyi kkkk
so nice
Mukumadya Ndiwo nyumba muno. .. Koma Jengeeeee🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Koma chibwezi Cha Mtebe ndi machine pa acting eeeeh
Thank you dear
Koma Patricia 😂🤣🤣the way she said inu akukanganatu panjapa😂🤣
Ati I'm afraid of heights 😂😂🙌🙌
❤ the new guy..... Mind smartness
Koma ngozo, zoona anzako dazi lawo ndi Ganda?
kanyimboko kaliboh tipatseni link ti downloade ...kaya nkugula tigula 💪😍😍
I'm in love with the song as well ❤️
Title ndi chani kodi
It's the way ganizan n Ngozo chill for me😅😅 ati mlamu zikumasukira😅😅😅
Angozo ali ndi mwano😂😂😂
Komanso azimai ndi nsapato za amuna awo😂😂🙌🏼🙌🏼
Am inlove with the song, whats the title
Ati olo chidacho chitasulidwa ku ndilande sichingapambane😂😂😂😂😂😂😂😂😂
😂😂😂😂was about to say that
It's so nice Guys, but one thing; Piksy, Sangie and Hyphen must not be Actors, how come enawo mukuwatchula maina apa msonkho koma inuyo mukumazitchula ma funky names mu Serious business ngati iyi? Separate Music and this thing please. We appreciate but make sure to think about it.
Mrs Ngozo maboza eeh mpaka kusemphanitsa sando 😂😂
Muthu mwasiya banja bwinobwino nde chozembelelaso mchani 😂😂 in sangie voice
Sangie,,, mabodzaa eeeh😅😅ukufuna uzimuphunzitsa Ngauzo
😂😂😂😂😂😂😂 sangie mabodza mpakana mwasephanisa shoes ai zikomo😂😂😂😂😂😂😂.....ganizani naye😂😂😂😂😂😂🙌🏼🙌🏼🙌🏼🙌🏼
We done guys keep the fire burning
Big up guys zili bho even picture ili good.
😂😂tebe kulota akulota what a creativity... Guys mumatha
Iweyo ndiwe Mr Ginty pabalaza 🍾🍾🍾🍾🍾
Ha ha ha koma Belita mpaka kusemphanitsa slipas😂😂😂😂😂😂
Patricia what a friend🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣 Belita sopano,ati ndiwe ozungulira mutu etiii
Pothamangira waleche u wear chomwe chakuyandikira. I can relate to Patricia's behaviour 🤣🤣🤣🤣, team kukonda zinthu 😅😂😅😂
Koma Patricia ndi kamagung'a ndithu iiiii mpaka slippers zosemphana zoti sizakeso😂😂😂😂
Nyimboyo ituluke nthawi yabwino ilimushe🔥🔥🔥🔥🔥
😂😂😂at mukumatha ndiwo😂😂😂bambo waumbombo
Am in love with the wig 😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
Ati umajamburaa😂😂😂😂zoti amadana aiwara😂😂😂😂
😂😂😂😂😂 koma akoko Ako ka ng'ono kake kangozoko muli wano eeh muthamangiseni
Continue doing good work
Komaso gani eti🤣🤣🤣Aaaa anyway... Usauver anakoza
Gan ndimunthu wamkulu, amayankhula pang'ono pang'ono ngati zanzeru
A shadow ndi representation of anyamataolubwalubwa
Etii mama mukomoka bwererani 😂😂😂😂sangie suli straight
Ganizani ayambe kuchosa dazi lake Kaye 😅😅😅😅😅
Whats the title of the song at the end, or is it unreleased
😂😂😂😂😂 ati analota miyendo yake itatakika ngati ya piksy ati amapanga chizungulile koma mwano wake kkkkkk😅😅😅
Nice one, love the soundtrack
Iiii Patricia phuma mpaka slippers zotyana😂😂😂😂 kma iyi ya full chicken iyi aisowad mtebede akuoneka kt nd linya uyu
Piksy white white ngati kakowa🤣🤣😄😄😄🤣🤣
Sengie mpaka kuvara slipers zosemphana kuthamangira mabodza kkkkk
Berita ati Husband and Wife 🤣🤣🤣🤣🤣 wife wake odya ndiwotu 🤣🤣🤣🤣
Akut kmaso muli ndi vuto mukumadya ndiwo nyumba muno😂😂😂😂
Koma mmene banja la Ngozo ndi Patricia likubhebhera zikundiwaza😂😂😂😂
Ati ndiwo zake matembawo🔥🔥
The song ❤ is so nice what’s the title
Patricia kukonda nkhani mpaka kubwla slippers zosiyana eeeeee🙌🙌🙌😄😄😄😄
Gani will remain my favourite 🔥🔥🔥
Mavalidweo Kaya ndi phepo, koma kuli zithu. #ndimakufilani madolo
Apapa nde yafikapo 🔥🔥😊
Love the soundtrack 😍🔥
the soundtrack👌
Eeeeh eeeh kuthamangila content kwabwanji uku Patricia!😂😂😂😂🙌
Matemba omwewa kkk
Kukonda zinthu sangie mpaka kumvala ma slippers osiyana 😂😂
Ganizani maloto kkkk shaa koma ngozo pls tipezeseni tshirt ya usauver naoooso
Koma Patricia 🤣🤣🤣🤣 kuchita kusemphanitsa malipha,,
Belita mukuzembera amuna anu
Ganizani dazi mphepo simudwala liwombo😅😅
Ati ngozo amapanga chizungulire akaima Hahaha Ganizani wayamba mwano
Ati umajambula? Tamajambula 😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
Ati or chitasulidwala ku ndirande😂
😁😁😁😁 phuma Patricia mpaka kusemphanisa nsapato 😁😁😁😁
Ati m'mutumo si skin so iyoyo Ndi Ganda basi😂😂😂
Kkkk chizungulire chifukwa choti miyendo nduyayitali
Koa usauver 😂🙌 its always Patricia with something to laugh about😂
Ganizani one day uzafera manja mwa anthu iwe 🤣😂🤣
Kkkkkkkk koma patricha kkk asandikomore kkkkkk iiiii anakhoza
Koma gan ,ATI musauze sisters 😂😂😂😂😂😂
Patricia awe sure ma slippers, I like it
Love it always turent
Akufuna kutumiza latest 😂😂😂😂✊✊✊ upole moto sangie 🤸🏾🫡
😂😂😂😂😂😂
Mtebe ndi 1
Ka nyimbo kali kumapteko guys..tittle ndichan
Ntebe akudusa mu nyengo zowawa😂😂😂
Kkkkkk aguni mpaka makhwala ochotsa dazi
Title ya “Sound track” yo ndi chani???
Ndipo am looking for that very same song. Ndi Nyimbo kawawa simasewera. Please whoever knows the song, let us know.
Mankhwala a danzi obweletsa danzi ??? Kapena ochotsa danzi?? Ine I’m dead
Kkkkkk gani ukufuna ukhale sangoma eti
Akuti chida olo chitasulidwila Ku ndilande sichingapambane Kwa Ntebe
Psychological torture ijah kuno yayamba kubala zipatso😂😂😂😂😅
😂😂😂😂😂 psychological torture yabala zipatso
😃😃😃😃😃 kubanja osachokako isaa mithulo yakeo aisova
Mtebede afa ndi mtima 😂😂😂
Or chidacho chitasulidwira ku headquarters ya ma Ghetto (ku Ndirande)...Pa Jedediah sichingapindule..😂😂
Mumakwana
Kod mwina vuto ndi phone yangayi?? koma iweyo Ngozo ndinkazakoyo mumavekela pasi kwambili ka,,,
😂😂😂😂 koma ntebede ukufa ndithu kkkkkkkkk
Gani iweyo siwamasewera😂😂😂
Kkkkkk eshii Km adha ai. Ma slippers ofuna content nu, maloto Mpaka ma teraz nd revenge kkkkkkkkk zachabeee. Camera man next time polish up
Gani the goat 🤣🔥
Nakaliza kkkk chizake ukupanga chachinyengo sure
Kma berita zipewa zonsezo😅😅
🤣 ati olo chida cho chitasulidwila ku ndirande
It's always Sangie's sarcasm for me😅😅
Koma abusa mulimba😅
Koma sangie ndi Chi vibe amwene🤣🤣🤣
Km ayi ngati ajambula dzulo angozo ineyo pano daily basis paka kumaliza ndithu
Belita🤣🤣🤣phee ku banja
Sangie slippers yo chonde😅😅😅😅
😂😂 koma ma gwaladi amenewo Sangie ndi Ako? 🤣🤣🤣
Eish koma Patricia eeeeh 🙌🙌🙌