MEC and NRB please take note,U must learn from our neighbouring countries like Kenya,azabajan,Uganda, Mozambique just to mention a few,all these countries I mentioned here the cause of conflict is a machine called smartmatic so please please we don't want war here in Malawi
THIRD GUY TO YOUR RIGHT IN BLACK AFTER NAMIWA NCHEWA WENI-WENI AKUCHITA KUMVEKA. THE LADY CALLED ABITI CIDEDI MCHEWA WENIWENI VUTO MWACHULUKISA KUYAMBA KUSANKHA MITUNDU INEYO NDI MCHEWA WAKU DOWA WENIWENI WA NYOOOOOOO KOMA SINDINGAFELE ZIMENEZI DZIKO ILI LAFIKA PONYASA CHIFUKWA CHA DYERA LA ACHEWAFE .NANE NDIKUTI NDI MCHEWAAAAAAAA KOMA MOYO UKUWAWA BUSINESS SIZIKUYENDA AND MAWA NDILI NAWO KUMA DEMOKO
Akulu awa ndamene amaoneka ngat ndi omenyelad maufulu
❤❤❤❤❤❤❤ ndazikonda adindo athu awonjeza
Zingovuta Koma CDEDI yanu ikuyesesa Mr Namiwa,
Namiwa my best ❤
All the best guys eeeshiiii anthu tikufiniya dziko lathu lomwe
HAHAHAHAHAHAHAHHAHAHHA NSAPATO YA VP MWATI YATANI????????😂😂😂😂😂😂😂😂😂
Imeneyi yandidutsa patiiii
😂😂😂😅
Zoona chilungamo ndiye mukuyesetsa km pot ena anachiluka dyera akubisa chilungamo
That journey please Mr continue and make it successful
Ampingo alikuti?
Mulungu dalisani Malawi.🙌🏾✊🏾🙏🏿
Well come back Mr namiwa uremu wanu basi chakwera angochoka basi sitikumufuna achoke ndi chakwera basi
Zoona galu wa kupha Uyu chakwera kachatche😂
Smart Martic ikapita kalembera azchitikenso.Palibe chicken mwe wachita Anabel . Please shake this out.Namiwa you must hold our flag
Namiwa ndi Katundu😅😅😅😅😅
Zoona mr namiwa a chakwela arephera amakhara ngati ndi mubusa koma ndinjoka yoruma achoke basi
Big up guys we together
Tieni tieni, kwa chikondi cha dziko antuwa amati tola. Tiyenera kulankhula ngati amodzi.
Namiwa ndye akueseaa kbali yake 😊
Kodi ku state house mumayuza calendar yanj?
Tili konko mmawa,,viva CDEDI
Mulungu atetezere ni anamiwa
Powerful message
Ndipo chakwera saangamake!
Mr Namiwa Mulungu azikudalitsa pa ntchito yomwe mumagwira .Kuyimilira Ife anthu osauka
Go deeper our God sent Namiwa 🔥🔥
Thanks God for good job to you all
MEC and NRB please take note,U must learn from our neighbouring countries like Kenya,azabajan,Uganda, Mozambique just to mention a few,all these countries I mentioned here the cause of conflict is a machine called smartmatic so please please we don't want war here in Malawi
Ndipo ulamuliro umenewu siunawonekepo ndipo siuzawonekanso pansi pano.
Let's support this group
❤❤❤❤❤ a ailavu Yuu misila namiwa
MCP busy kuwononga ndalama zathu Manyi awo sakuziwa chilichonse
NDIPO NDE ZIKUONONGEDWA ZINGOTHERA MALISECHE A-ANA MMA AREA'MU
Kod iwe ukuti alomwe awa mkwiyo koma iwe ulindizelu koma akuvutika ndi alomwe okha zikuchitika muzikomuno iwe sukuwona
Mawa tili komweko but azikwanjewo mutithandiza bwanji
Mmmmmm mr. Namiwa mwatilankhulila zenizeni ndipo mukubaya peni peni. Chakwera ndi boma lake la MCP atikwana. Palibe chomwe akuchita.
Mawa kunkhala kugwetsa nyumba za a police onse aphuzile mwambo
Ulemuwanu team CDED
Well come Mr namiwa ❤❤❤I love you so much
Takhozekela popandanso galu winawake yemwe sanareredwe bwino ndi makolo awo
Good point guys
Tikufunira mademo abwino tili pambuyo panu
Koma akulu Awa bola agokhala president mongoyembekezela boma li
Namiwa May Allah protect you
Zoona akuna ngati ife zisilu mmalawi muno
nzika zamalawi zofunila umoyo wadziko lathu musaloleso nantakumba waboma aliyese alipheretseso mademowo ayi
MEC AND NRB AKWATILANA AFUNA ABELEKE MWANA YEMWE AMALAWI SITIKUMUFUNA😂😂😂
Muyambenso kuyimitsa kamba ka apolice busy😢
Chonde a zikwanje mukangozipha izi zikusokosera kwambiri muziko
Mtola nkhani wa capital ndiwe ofoira.
Ineyo ndiwa mcp kma mawa ndlinanu achoke bas
Ukapita wekha aise ,ine mmalo mokasaka ndalama ndikapite ku ma demo kkkkkkkkk iwetu unyaaaaaa
Waredzera mesa
Yellow man. Umakwana ase 😅😅😅😂
Arongosi tumani transpot tize ise wakum zimba
Ulemu wanu anamiwa
Ulemiu wanu cdedi pachiganizo mwachikomza tikulira kwambiri
👏🏾💪🏾👏🏾🇲🇼🖤❤️💚
Mawa tiyende mokonzeka
Ndipo anamiwa Kaya ndizakupaseni chiyani mwina muzangokwatiwa mwana wanga chifukwa ndinu munthu munthu oti muli ndi uzimu ochokela kwa mulungu
😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
namiwa ndi machine
Namiwa mulungu akhale nawe
Namiwa ndilowele ku in box nditumize thandizo lamayendedwe mmawa walankhula bwino kwambili
Alutaaaaaaa
😂😂Koma kutalikiraku nkwiyo ukumatulukira pa chipumi 😂😂😂😂
Apolice Kodi ndinu athu kapena ndinu abilimankhwe?
Ndipo inu mmmm
Vry gud vry gud
Alutaaaa🎉🎉
Mbambande Namiwa,,, osaopa osafooka osatopa 🔥
Umbuli wa azisogoleri
Tili pa live namiwa
Tiyeni tigwirane manja a Malawi onse okonda dziko lathu tituluke mawa tipite ku mademo mtendere osawononga chilichonse
Mawa tlikonko
Tiyetiyetiyeni
Mawa tikumana tatopa sitiopa sitifooka
Ndipo a Malawi sitikugona kuganizila komwe chakwera ndi MCP yake akutengela, eisha! Worst President ever in Malawi.
Pangani mademowo koma be assured kuti ife mavenda mukatipeza konko tikuteteza ma business athu....chibwana chimenecho mukapangire ku thoko konko
Alhomwe awa nkwiyo
Okay we understand
Bola asasokonezekeso
Tchito yabwino tetedzani zikolanthu Ku asogoleli oyipa
Tili palibe namiwa
Anawathamangitsa ku statehouse awa
Hahahahahahh koma naweso za nziii kanyere uko
Alomwe muli pachintchito koma simukwanisa chifukwa panthawi yanu munatizunza kwambiri sitilola kut mubwerereso boma
Choka iwe
A BON KALINDO OSAWAJOYINA ANZANUWA PA BRIEFING PA BWANJI.
🔥🔥🔥🔥
Ndipo mafuta avutad kwambil
Zamafuta akumva komakutiona kupusa
Boma LA anthu amatama
Komanso la anthu ozikonda
Omwewa anamiwawa 2019 anati chisankho chinayenda bwino yet khothi inati siziyende bwino just bcz anali ku statehouse
@@BlessingsKasiya zisiyeni izo koma pano dziko ravuta kwambili chakwera waononga dziko
@@stevenmwamadi3035WORDS! WORDS APAPA ZAONJEZA AM WITH YOU COMRADE STEVEN
Look onse akuchita phokosowa ndi alhomwe basi no yao on the front
Machende ako...ine ni mchewa Koma o chakwera alephera zed
THIRD GUY TO YOUR RIGHT IN BLACK AFTER NAMIWA NCHEWA WENI-WENI AKUCHITA KUMVEKA. THE LADY CALLED ABITI CIDEDI MCHEWA WENIWENI VUTO MWACHULUKISA KUYAMBA KUSANKHA MITUNDU
INEYO NDI MCHEWA WAKU DOWA WENIWENI WA NYOOOOOOO KOMA SINDINGAFELE ZIMENEZI DZIKO ILI LAFIKA PONYASA CHIFUKWA CHA DYERA LA ACHEWAFE .NANE NDIKUTI NDI MCHEWAAAAAAAA KOMA MOYO UKUWAWA BUSINESS SIZIKUYENDA AND MAWA NDILI NAWO KUMA DEMOKO
Mmmmmm mr. Namiwa mwatilankhulila zenizeni ndipo mukubaya peni peni. Chakwera ndi boma lake la MCP atikwana. Palibe chomwe akuchita.
Mumafuna kuti akupaseni chakudya akwanisa kukupadani nsima aliyese no sense
@@user-ii9ch7oz8naaaah inuuuuuu lilipo boma linayamba lapangako zimenezo? Kuyankhula kwa manyiii amako
Zoona akuna ngati ife zisilu mmalawi muno