COMRADE NTANYIWA PA LIMPOPO FM - DISO NDI DISO NDI PATRICIA KALIAT

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 10 жов 2024

КОМЕНТАРІ • 227

  • @OssmanAbubaker-m5u
    @OssmanAbubaker-m5u День тому +19

    Tinalakwisa ku votera mcp .Mulungu atikhululukire ndipo tikupempha Mulungu kuti atichosele Mavuto alipowa

  • @AuphieBannet
    @AuphieBannet День тому +11

    MULUNGU adzikudalitsani ndikukutetezelani MR, COMRADE ❤

  • @SelinaNamagowa
    @SelinaNamagowa День тому +6

    Mulungu akati aike zobisika poyera eeeshiiiiish 🙌🙌

  • @DalitsoPhiri-sq5nl
    @DalitsoPhiri-sq5nl День тому +9

    Ineso so wandale komano nditha kumvomelezana ndi comrades cz Mr kabambe atalemba kalata kuwafunsa a vice president a usi kuti atenge uthenga kukapeleka kwa a presdent zokhudza commission of inquiry pa imfa yomwe inachitika ku chikangawa yet izi zinali zomwe rael utm fans komanso amalawi ambiri akufuna yet sanapangidwe support of which was very strange

  • @rabeccaphiri1333
    @rabeccaphiri1333 День тому +3

    Release the audio please we need tangible evidence

  • @Sherrie-b5s
    @Sherrie-b5s День тому +6

    Tikhulupirira tikamva ma Audio, Akweni omwewo 💯

  • @lyiemax
    @lyiemax День тому +8

    Ngati honourable Kaliyati agudwa, then who is going to rescue poor Malawians, this is bad

  • @MakabaBauleni-c2i
    @MakabaBauleni-c2i 2 дні тому +12

    Uyu mtanyiwa watumidzidwa ndi Mulungu kt atitsekure maso

  • @Andrewmwamadi
    @Andrewmwamadi День тому +16

    Comrade u hv started politics now kkkk this issue seems to b personal issue wit kaliati leave our utm alone pliz

    • @MartinKapito
      @MartinKapito День тому +6

      Anthu osadzindikira tayanganani dziko mmene likuyendera movuta anthu tikuva Koma sotivetsetsa tikuona Koma sitikuonetsetsa tikudzikira Koma sitikudzindirikitsitsa conco osamanyodza pamene Wina Ngati waonetsetsa chifukwa tikagwera kumphompho

    • @Mpungwe123
      @Mpungwe123  День тому +2

      U r right I feel the same❤❤❤

    • @emmanueljelemani4203
      @emmanueljelemani4203 День тому +7

      Hard to believe,. Mai Kaliati was one woman we trusted to stand firm for UTM party, but now tilowere kuti?

    • @Mpungwe123
      @Mpungwe123  День тому

      @@emmanueljelemani4203 koma zikukaikitsa izi

    • @GraceChiramb0
      @GraceChiramb0 День тому +2

      Ngabodza awaa, awa nga kabambe... Kaliati can't sell the party to MCP.....

  • @ShownMboma
    @ShownMboma 2 дні тому +8

    Palibe chobisika pasi pa thambo Lord have mercy to Malawi

  • @thulanimpphiri6873
    @thulanimpphiri6873 День тому +7

    Zoona ifa ya saulosi chilima mai kaliyati mupezerepo chuma anthu opusa kwabasi anthu nose mukulandila ndalama zakuba ku choketra ku chitipa to Nsanje nose ndinu agalu ndipo kaya ndiwandale kaya ndi mubusa kaya ndiomenyera ufulu nose mukulandira ndalama kuchokera kuboma ndinu zisiru makape mbumbuzi zisetekwete anthu opanda chifundo ndipo 2025 muziwa kuti kumwamba kuli Mulungu wamoyo. Ngati mukuganiza mcp idzawine 2025 muzawona zodabwisa zimene Mulungu wamoyo azachite

  • @simonpaul6567
    @simonpaul6567 День тому

    Comrade we really ❤❤❤ you please keep on showing us the secret of these evils

  • @KINGSLEYDINIWA
    @KINGSLEYDINIWA 2 дні тому +8

    Ndakhumudwa nawo Maiwa ndithu 😢

  • @MaxonKambazithe
    @MaxonKambazithe День тому +4

    Koma akaliati is fit to not be president of UTM she is fit SG BASI

  • @BasielBanda
    @BasielBanda 2 дні тому +18

    Atikhumudwitsa mai Patricia kaliati😢😢

  • @ShillahLawrence
    @ShillahLawrence 2 дні тому +5

    Ndiye kuti Patricia ndi Manganya akudziwapo za imfa ya a Chilima! Ine ndimadabwa kuti SKCthee VP ,MW kungoti ziii bwanji

  • @FredKanyerere
    @FredKanyerere 2 дні тому +8

    Please madam chilima tulukani UTM tengani udindo.

  • @SayidiMisessa-x6y
    @SayidiMisessa-x6y День тому +3

    Eish koma guys, zina ukanva, umadwala mutu waching'alang'a, mu tea umathira sabola, mundiwo nkuthira nchenga.😢😢 akaliyati chonde Amalawi musawasakanize manyi ndi mikozo
    Ife tikuvutika. Ndipo Akaliyati mukanvera oudio iyi mubwere poyera muzilongosole

  • @MarleyDKamphiripiri
    @MarleyDKamphiripiri День тому +8

    Mulungu apitilize kumugwilisa ntchito Mtanyiwa

  • @FredKanyerere
    @FredKanyerere 2 дні тому +7

    Mai kaliyati mwatinkhumudwitsa, 😢😢.

  • @OssmanAbubaker-m5u
    @OssmanAbubaker-m5u День тому +4

    Aaaaaaa Mr Ntanyiwa musamasowetu ifetu tikudalira inuyotu kumeneko

  • @PreciousHenderson-qc1hq
    @PreciousHenderson-qc1hq День тому +1

    Kaliat what's going on we had a great believe in you now you have turned the table

  • @FeliaNgunga
    @FeliaNgunga 2 години тому

    I love kaliyati, I think these people Ali ndi ma personal issues

  • @ArchangelBanda
    @ArchangelBanda День тому +2

    Za mai kaliati nde mwapalatu abwana.
    Kabambe mulendo ngati ameneyo mmm i've started luzing my trust in you comrade

    • @MillyKachepa
      @MillyKachepa День тому

      Kkkkk Ntanyiwa samanama

    • @RuthKaledzera
      @RuthKaledzera День тому

      Kwambiri ayamba bodzano ,Patricia kaliyati amaonekeratu kuti ndi mzimayi osatekeseka ,atumidwa awa

    • @SemteeTambala-rh2br
      @SemteeTambala-rh2br День тому

      Mfiti imakusekelera masana ikuzwa kuti ikupha usiku and amakhala bale wako​@@RuthKaledzera

  • @sparkdymon3429
    @sparkdymon3429 2 дні тому +6

    Eish koma abale tidalile ndani pa Malawi Pano azatisogolele mamaine

  • @DangerYaokingYaoking-m3c
    @DangerYaokingYaoking-m3c 2 дні тому +4

    Malawi zoti azakhalaso wabwino ndayamba kukaika coz izii zandizizilisa khongono😢

  • @Andrewmwamadi
    @Andrewmwamadi День тому +5

    Propaganda iyi don't be used by politicians ntanyiwa OK, muzionongera cv yanu ya bwino ija Jst bcz kaliäti wat ayima ku convention as president

    • @ChimwemweMuhelliwah
      @ChimwemweMuhelliwah День тому

      Inenso ndayamba kuwakaikira a Nthanyiwa .awawa akusiyana ndi wa Bakili Muluzi tv uja...

    • @OssmanAbubaker-m5u
      @OssmanAbubaker-m5u День тому

      Inu palibe chimene mukuziwa mukufuna muzitenge kuti ndinu ozindikila

    • @umalimaganga
      @umalimaganga День тому

      But you guys Ntanyiwa is saying akhoza kutulutsa ma audio omwe amayankhulana so if he is lying can he say that??

  • @susantembo2076
    @susantembo2076 День тому +2

    I hope it’s not a way of ousting Mrs Kaliati from the Convention so people don’t for her. Let’s get serious. If true It’s a sad development.

  • @Kachepamtsonga
    @Kachepamtsonga День тому +4

    This is controversial because kaliati is the one who expelled utm from tonse alliance and how come the same person kuti abwerereso😢 a mtanyiwa ndinu amisala ndye kuti mwalandila ndalama kuchokera kwa a kabambe kuti munyoze kaliati,

    • @OssmanAbubaker-m5u
      @OssmanAbubaker-m5u День тому

      Ukhulupilire zomwe akunena Ntanyiwazi ndipo ndipo uzimvere chisoni kuti dziko la Malawi 🇲🇼 likurowera kutiko

    • @ErnestChansa
      @ErnestChansa День тому

      Tanyuwa siwamisala ai ine ndikukhulupilila zomwe akunena tanyuwa sakunama ai anthuwa ndalama za pengesa

    • @HartleyMillion
      @HartleyMillion День тому

      Zikumveka ngati zoonaditu coz zikudabwisa kuti how come mai kaliati akukamukalipira kabambe coz wafunsa za commission of inquiry yet aliyense akufuna zomwezo?

  • @MiddayDeleza
    @MiddayDeleza День тому +8

    Mulungu ali mwa inu mtanyiwa long live comrade ntanyiwa zachisoni ndithu koma Mai kaliyat mzimu wa Chilima ndithu ukusowetsani mtendere, Mcp munapha Chilima ndicholinga choti mutenge chipani cha UTM koma choti mudziwe kunja kuno kuli mulungu la 40 likukwanilani

  • @DavidJackson-ox4xm
    @DavidJackson-ox4xm День тому +2

    Comrade Mtanyiwa Inspiring the nations

  • @thulanimpphiri6873
    @thulanimpphiri6873 2 дні тому +3

    Ngati mai kaliyati zimene akuyakhula mutanyiwa ndi true story ndiye mai inu ndinu opusa kwabasi ndipo ngti mai inu muzakhale pamozi ndi mcp ndiye ndiwe mai onunkha kwasi bola musayelekeze kuchita zomenezo ndalama zimakoma bwanji kudya azanu akuvutika muziko kuzipatala mankhwala kuli anthu atundu wanji wosalhala ndi Mulungu? Musiyeni Chakwera apite ku gehena ndi nduna zake zose

  • @LinlyMatheweKufakwina
    @LinlyMatheweKufakwina День тому +3

    Hmm koma Pena Mtanyiwa ukamayamkhula udzidziwa kuti kulu mulungu kunja kuno umaonjeza bodza

    • @MartinKapito
      @MartinKapito День тому +1

      Palibe bodza apa

    • @MathewsJanuary
      @MathewsJanuary День тому +2

      Chokapa iwe utiuze zoonadi iweyo ukoo.

    • @viennasamuel2976
      @viennasamuel2976 15 годин тому

      Inuyo onena zoona tamanenani ndipo mukhale ntanyiwayu inuyo

    • @viennasamuel2976
      @viennasamuel2976 15 годин тому

      Inuyo onena zoona tamanenani ndipo mukhale ntanyiwayu inuyo

  • @isaacchiwaula731
    @isaacchiwaula731 2 дні тому +3

    Kod mumanvera zitsiruzi? Awa ndi anthu oti mungamawanvere? Anayamba akambapo zinthu zabwino awawa? Zoti iwowa amakhala ndi ma person interest simudziwa? Muuze atulutse panopa ma audio-wo ngat akunena zoona? Zitsiru za anthu idzi kungofuna kugawanitsa anthu basi. Inu amalawi muli mdywooo kunvera zimenezizi zopusazi

    • @MzadziWanga
      @MzadziWanga День тому +3

      😂😂😂😂. Kmatu naweso uli dyooooo kuvera zomwezi ngt zili zokubhowa ukanangodusa osavela olo comment kma apapa zaoneseratu kt pg iyiyi umaisata😅

    • @samchibenene4458
      @samchibenene4458 День тому

      You are true these people are rubbish at all

    • @JeanKambala-gm1zr
      @JeanKambala-gm1zr День тому

      Chitsilu ndiiweyo wanvela kale bwanji ukuyika comment kkkkkkk chitsilu ndiiweyo wampatsa comlede ntanyiwa komenti 😂😂😂😂😂😂😂umbuli

    • @mianomaster4494
      @mianomaster4494 День тому +1

      Takuonani kale kuti ndinu anyamata ojiya

    • @PatricaTchuwa
      @PatricaTchuwa День тому

      Chilungamo ndimwano. Iwe umavera bwaa? Museyen Ntanyiwa ndi nthawi yake

  • @DaudBonomali
    @DaudBonomali День тому +2

    Ndiye ngati zili choncho atsogoleli nonse simakonda dziko lanu ndiye tidziti mwina dpp ndi aford bsitu

  • @mtenderemitembe3433
    @mtenderemitembe3433 День тому

    Never trust any politician.

  • @georgekesten3975
    @georgekesten3975 День тому +1

    Pali zinthu ziwili apa: mkutheka iweyo ndamene wapatsidwa ndalama from kabambe kapena amayiwa akufuna kugulitsadi chipanichi ngakhale zikukayikitsa.... kut tikukhulupilile tipatse ma audio akewo...coz wammodzi mwayinu watha apapa sazikondedwaso
    ndikhani imeneyi.

  • @AlgentChilanga
    @AlgentChilanga День тому +1

    Every hour ndimabwera kuyamba kutcheka ntanyiwa pa limpompo fm koma ndimapeza zakale zokhazokha ayi bwana msamasowe chonde muzibwerabwera even mtakhala ndika breaking News tatipasireni ife .ulemu wanu biggy

  • @LuciousChikopah
    @LuciousChikopah День тому

    Thanks for telling us the truth

  • @zelliachamboto5744
    @zelliachamboto5744 День тому +1

    Oh my goodness Why Kaliyati Kaliyati Kaliyati 😮 palibedi wa straight pa ndale hey

  • @BennettNjedza
    @BennettNjedza День тому +1

    Nice Job Bigman

  • @Iponga
    @Iponga 2 дні тому +3

    Tulusani ma audios tiwanvere ndichitsiluso ameneyu panyero pakeso mai chilima limbani mtima muimile

  • @JulietMunthali-g9b
    @JulietMunthali-g9b День тому

    Was wondering Kaliyati wangoti zii why eeeish koma ziliko kunjakuno abale wachilungamo palibe guys mmmmmm serious kaliyati

  • @ChimwemweMuhelliwah
    @ChimwemweMuhelliwah День тому +1

    Samalani may Kaliati ngati nkhaniyi ndi yowona..komanso mayankhulidwe awawa comrade xikuwoneka too personal issues....

  • @JeanMaganga-l3y
    @JeanMaganga-l3y День тому +2

    Comrade mulungu azikudalitsani mumatiimilila

  • @JasonMailos
    @JasonMailos 13 годин тому

    Tumiza ma audios Kuti tikhulupile, mwayambana mudzifukwa zanu osatinamize apa

  • @CharityMhone-uk9ym
    @CharityMhone-uk9ym День тому +1

    Ndi mayi ochenjeretsa kailati sangasiye kugulitsa chipan akuziwa kt sangawine paokha then amadana ndi Dpp paja msaiwale kt zipani zonse akalowa amamthamangitsa chifukwa Cha kuchuluka nzeru.. chilima yekha ndamene anamusunga chifukwa poti anali munthu wa chison😮😮😮😮ayisova

  • @MarleyDKamphiripiri
    @MarleyDKamphiripiri День тому +2

    A Mtanyiwa ching'ambeni chinsaru c tionemo nkatimo

  • @ChifundoZimba-jh7dh
    @ChifundoZimba-jh7dh День тому +1

    Marry chilima apite kuti osawuza mkazi wako bwanji leave Marry chilima alone

  • @alfredpower2334
    @alfredpower2334 День тому

    Kulapa pa zinthu zomwe ukuona kuti sudachite bwino ndipo ukupweteka anthu ochuluka sikulakwa, Comrade Ntanyiwa tangolapani pamodzi ndi inu UTM komanso DPP chifukwa mwayambapo kulumana nokhanokha. Lapani kuti mukhale mfulu

  • @kekeaufi9834
    @kekeaufi9834 День тому +1

    *Ngati zili zoona,,,,A Boni kalimdoo zinangovuta kuchoka ku UTM,,,,,Ndi munthu mmodzi akanamenyela nkhondo a malawi kuzela ku UTM kuima nao pa mphando*

  • @MiddayDeleza
    @MiddayDeleza День тому +1

    Ayi Mai chilima asaimilire UTM Mcp ndiya kupha, Koma ngati za Mai kaliyat zi zili Zowona nde kuti eishhhhhh zowopsa tu akukufuna kuyitengera UTM ku chipani cha mcp mmmm, nde ngati zili choncho anthu akutulukani Mai mupita nokha ku Mcp ko

  • @TelezaManyela
    @TelezaManyela День тому +2

    mai kaliati Malawi mukumuika pati?

  • @Blessings-b7h
    @Blessings-b7h День тому +1

    Kkkkk koma ndalama anapanga kwambiri.
    Munthu kulephera kulankhula chilungamo chifukwa cha ndalama.Chakwera akanakhala munthu wachilungamo sakaba ndalama komanso sakanapha vice wake.

  • @jixonromeo4111
    @jixonromeo4111 День тому +2

    Ayi shosha may kaliati

  • @HanneckManili
    @HanneckManili День тому +2

    😭😭😭, very disappointed 💔🤦

  • @stellamagomero
    @stellamagomero 15 годин тому

    Mwayamba bodza zinazi pitani ku box kwawo mukalalatilane komweko send vn here

  • @chimwemwenkute3839
    @chimwemwenkute3839 День тому +2

    Comred mwasowatu but you're welcome

  • @AlgentChilanga
    @AlgentChilanga День тому +1

    Welcome ntanyiwa pamenepo ipemerere Kariati wataniso nawe Kodi ???Kariati kariatiweeee chonde Siya zimenezo mmene udamukondera chilima iweyo Kariati naweso wangokhala ngati manganya .zoonadi wokudya naye ndi amene azakupereka shit Kariatwee

  • @MarcyKamaga
    @MarcyKamaga 2 дні тому +4

    koma ndarama ndiyopweteketsa kwambiri ndipo akariat mwankhumudwitsa anthu

    • @ChimwemweMuhelliwah
      @ChimwemweMuhelliwah День тому

      Sizowoana izi inu...this guy might be used by someone to destroy Kaliyati's image....wayamba zaukape ntanyiwa

    • @TemboHaswell
      @TemboHaswell День тому

      Bwanji tidikile mai kaliyati ngati angayankhe ndekuti ndizabodza km ngati akhale ziiii ntanyiwa moto kt buuuuuuuuuuh😂​@@ChimwemweMuhelliwah

    • @AlgentChilanga
      @AlgentChilanga День тому

      ​@@TemboHaswellzoona ayise let us wait and see kuti Kaliatinatichani

  • @mrperfectmw
    @mrperfectmw День тому +2

    Mulungu alinafe ndpo tituluka mavuto osewa

  • @MaryTchapo-py4hh
    @MaryTchapo-py4hh День тому +4

    Umat tivere ndani?

  • @jowiemhango5058
    @jowiemhango5058 День тому +1

    Komaso sakhala bwino convention isanachitike kut tidziwe mtima wa mayi ameneyu. Aaaah koma zoona mai?

  • @LeyvanSamuel-pe5tc
    @LeyvanSamuel-pe5tc День тому

    Anthu andalewa guys Mmmm ayi osakhulupilra 😢 kaliati ndnapasa 100% Koma mmm ayi dzikomo

  • @SoundmasterElectronics
    @SoundmasterElectronics День тому

    Mayi kaliyati pa chi phwi🫣🫣🫣🫣 kwinako nditukwana 😭😭😭😭😭😭😭

  • @OssmanAbubaker-m5u
    @OssmanAbubaker-m5u День тому +2

    Chakweratu wasalapang'ono kumwalira chaka Chino sichitha mukhulupilire

  • @stevenmwamadi3035
    @stevenmwamadi3035 День тому +1

    Kaliati ndi hure mbuzi yamuthu crocodile nayeso ndi nzake crocodiles wakeyo onse ndi mbuzi

  • @EliaSiska-n6r
    @EliaSiska-n6r День тому

    Inde musamasowe. We need information

  • @PatrickZinenanie
    @PatrickZinenanie День тому +1

    Mtanyiwa machende ako nthawi yonseyi unali kuti pita uko kagone shatap zako

  • @sautsoNguluwe-c1s
    @sautsoNguluwe-c1s День тому +1

    mtanyiwa God protect you

  • @PhiripChinkango-k5p
    @PhiripChinkango-k5p День тому

    Kkkkkk koma Limpopo FM, nkhanga zaona ndi comrade ntanyiwa umakwana iweyo ndakufila

  • @mollymasangano473
    @mollymasangano473 День тому +1

    Koma ku Malawi ntchito ilipo komatu a Malawi tilimbe nanzo pa galaundi .

  • @SheenahMwalabu-iz3pr
    @SheenahMwalabu-iz3pr День тому

    Is this mtanyiwa or chigoba? The way l know mai Kaliati sangapange chipongwe skc and Utm. If mukunenazo ndizoona ikani timvere zomwe ankakuuzanizo, akaliatiwo cz zinazi mukungopekapo and it doesn't sound real 😢

  • @samchibenene4458
    @samchibenene4458 День тому +2

    Iwe mutanyiwa uli mutesi chomene boza

  • @ChimwemweMaposa
    @ChimwemweMaposa День тому

    GOD save Malawians please 🙏😭

  • @CassimMbalaka
    @CassimMbalaka 2 дні тому +2

    Mulungu salakwitsa kalikose akuwoneni pomuyika aliyese wokhudxidwa pa ifa ya chilima

    • @jowiemhango5058
      @jowiemhango5058 День тому

      Ndipo zakhalaso bwino tadziwa convention isanachitike apa anakatidyetsa frass uyu

  • @stevenmwamadi3035
    @stevenmwamadi3035 День тому +1

    Koma Allah alipo mpaka chakwera atuluke mboma basi Allah atichosere crocodile mpaka a Malawi tiomboke mukaporo tili nawo pano ndi chakwera muthu otiyipa kwambili

  • @ChifundoZimba-jh7dh
    @ChifundoZimba-jh7dh День тому +1

    Iwe chikukuwawa ndichani iwe ndi wa UTM tamapanga za DPP leave kaliati alone

  • @eunicesaiti
    @eunicesaiti День тому +1

    Following up boss 🙏

  • @SilajZibelo-n4f
    @SilajZibelo-n4f 2 дні тому +3

    Tumizani ma audio

  • @augustMag
    @augustMag День тому

    Mr Mtanyiwa Limpopo FM 🔥🔥🔥🔥 koma sindikhulupilira kuti mama Kaliati angagulidwe ndikusiya chipani Cha UTM momwe amachikondera muja konse uko wayenda nacho chipanichi munthawi yonse yazovuta zija anaima ngati munthu wamamuna mmmmmhu zavuta ku Malawi

    • @MillyKachepa
      @MillyKachepa День тому

      Ambuye Yesu anapachikidwa chifukwa cha ndlama yomweyo kkkk nde mukanene Iwo angalamdred

  • @KondwaniLungu-x5l
    @KondwaniLungu-x5l День тому

    Ine ndi ndikudabwa nazo u and mr DC mukuti Merry chilima apitilize pamene mamuna wake analekezela. Kodi muli ndi omboni wanji kuti mai chilima ali ndi mphaso yausogoreli? Ine ndimaona kuti mai aja amangowathandizila pena ndi pena not 100% mwachidule ndingoti chipani cha utm pin code yake inapita ndi mwini wake chilima, maiyo musieni azipanga zake musamukakamize mufune musafune utm izakhala mbili basi.

  • @Moyo368
    @Moyo368 День тому +1

    Mai uyu anachenjeretsa ndipo okamuvoterawo asowa zochita

  • @JulietLizziePhiri
    @JulietLizziePhiri День тому +1

    Zomvetsa chisoni bwanji😢

  • @AlexKaunda-ny2eg
    @AlexKaunda-ny2eg День тому

    Antanyiwa mphindiso ya chani machende Ake kaliyati Samala wausilu iwe hule landare

  • @stevenmwamadi3035
    @stevenmwamadi3035 День тому

    Chingofa chikangawachob basi muthu oyipa kwambili ngati idya amin

  • @LoyceMhango
    @LoyceMhango 2 дні тому +2

    A kaliati ndiye ayinsotu.

  • @StoniaMoyo
    @StoniaMoyo День тому +1

    Ndizomvetsa chisoni 😢😢😢😢

  • @MarthaMbewe-uk5nn
    @MarthaMbewe-uk5nn 2 дні тому +1

    MAYI KALIYATI MWAGANIZA BWANJI KOMA?? KULIRA KONSE KUJA ZOONA??? MWATIKHUMUDWITSA KWAMBIRI

  • @PriscillaKhumbanyiwa-i1d
    @PriscillaKhumbanyiwa-i1d 10 годин тому

    Partilicia kaliyati ndi wosusuka ndi khalidwe lake sizachilendo

  • @OmegaChingamuka
    @OmegaChingamuka День тому +1

    Koma nde za ziiiiiiiiii zeni zeni ife timawakhulupiliratu

  • @Moses51
    @Moses51 2 дні тому +1

    Fire 🔥🔥

  • @HaleemaAllie
    @HaleemaAllie День тому +1

    OK my god mayi kaliyati mulungu akuyendeni muzina lam ulungu yooo

  • @S-rr1eu
    @S-rr1eu День тому

    Zimayi ameneyo ,,,,, asazitukwanise

  • @BerthiaChikopa
    @BerthiaChikopa 2 дні тому +2

    Heeeeeeee😂😂😂😂😂😂😂 ndiye yayisotu

  • @bosheenhakhomba
    @bosheenhakhomba День тому

    Comrade send ma vn kuti tidziwe zeni zeni koma Kaliati watikhumudwitsa

  • @Henry-vw2cz
    @Henry-vw2cz День тому +1

    😂😂😂😂😂😂kaliyati wayaluka

  • @MirajLaja
    @MirajLaja День тому +1

    Moti Mayi kaliati amakudziwa iweyoo!?

  • @GeshoMwakitwile
    @GeshoMwakitwile День тому

    Munkati Micheal usi relo mukut Mai kaliat antanyiwa panopa nanu ndi achitsiru chothelatu ,iwe ndiwe wa dpp chomwe ukufuna ndi nkhalamba yako ija kut yilamulilenso koma mwauponda

  • @alemaconstruction4329
    @alemaconstruction4329 День тому +1

    Mmmmh Ntanyiwa ngwaboza why????