BRIAN BANDA KUWERENGA NKHANI ZA LERO PA 09 OCTOBER KUFOTOKOZA CHENICHENI CHIMENE CHACHITIKA LERO

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 8 жов 2024

КОМЕНТАРІ • 71

  • @FidesChandama
    @FidesChandama 41 хвилина тому +1

    Atimenyela nkhondo mulungu osati munthu ai

  • @PollyLysonLutepo
    @PollyLysonLutepo 2 години тому +10

    Kaya anthu achepe pa zionetselozo. Koma chachikulu ndi chakuti cholinga chaziwonetselozi chakwanilitsidwa. Madandawulo adziko apelekedwa.m'modzi Odandawula ndine.

  • @BrianAmbeswa
    @BrianAmbeswa 45 хвилин тому +1

    Kodi chamupha ndi chani simukunena mwatani kodi? Kugoti atisiya basi mzimu wa chilima wayamba kwaitna aziwona zagoyamba

    • @mcsellahntv6896
      @mcsellahntv6896 18 хвилин тому

      Anamwanso gonsolosi wina ndikukatenganso Elube ndiye mphamvu zinachuluka.

  • @Jacksonmuhackeya
    @Jacksonmuhackeya 3 години тому +11

    Anthu amene akuziona ngati ndi mulungu wa Malawi ayamba kufa mulungu wayamba kuyankha anthu osauka

  • @nhlakaniphoshabalala7337
    @nhlakaniphoshabalala7337 2 години тому +2

    Mawu ndi omwewo tatopa ndi chakwela Mr chilangawa 🐊🐊🐊🐊🐊🐊🐊🐊🐊🐊

  • @JohnMwafongo
    @JohnMwafongo 31 хвилина тому

    Times_so Nanu dzimene mwalemba nd izi different 😢

  • @MaryNgola
    @MaryNgola 2 години тому +3

    Nkhalamba ijatu sikufa mophweka akufa ndi mnyamata wanu wayamba kufa dziwaloyo,ngat sanafe km sagonerai

    • @hastingsbnyirongo
      @hastingsbnyirongo 2 години тому

      kkkkkkk kunena kwa ndithendithe. Aliyese adzafa ase usamathe mau ngati ndiwe wambewu

  • @JohnMakinah
    @JohnMakinah Годину тому

    Anali a mcp anthu onsewa kaya adya chimbazi kuchoka ku mboma

  • @MikecrmGamar
    @MikecrmGamar 57 хвилин тому

    Kod akuwerenga khanizi ndi brian Banda mulipa changutu

  • @RodgerChaula-r5z
    @RodgerChaula-r5z 42 хвилини тому

    Boma si M C P Boma ndi Malawi

  • @IvyChithyoka
    @IvyChithyoka 55 хвилин тому

    Bravo guys

  • @patrickkusailemp3769
    @patrickkusailemp3769 Годину тому +1

    Nanga thupi la Chakwera lifika liti m,dziko lathu lino? Akubanja mwawauza kale ? Nanga dziko ,mwaliuza zotani ? Auzeni anthu zoona . Maliro sabisa.

  • @MaryNgola
    @MaryNgola 2 години тому +2

    Amutsatiratu chilima chakwera

  • @IssahAluba
    @IssahAluba Годину тому

    Next year Kuli khondo osati masewera

  • @IvyChithyoka
    @IvyChithyoka 51 хвилина тому

    Nkhani ndi mfundo basi osati kuchiluka

  • @McDonaldMuyombe
    @McDonaldMuyombe 2 години тому +2

    Paja zirizonse mumati anthu agulidwa. Ndiye ku ma demo kunalibe amalawi aja mumawati akutumani.
    Amalawi akana ma demo, kodi lero mutiuza kuti anthu anyemeredwa ma billion angati

  • @giftpound-f6m
    @giftpound-f6m Годину тому

    za ziiiiii

  • @AbdulrazaqHussain
    @AbdulrazaqHussain 2 години тому +1

    Malamulo a mavotedwe, a dziko lathu tikuwadziwa, tisapondeleze anthu ena poti alibe chitupa cha unzika, be civil guys,

  • @shadrickmsungambeu962
    @shadrickmsungambeu962 2 години тому +1

    Where is brain Banda here?

  • @ishmaelbrighton9885
    @ishmaelbrighton9885 Годину тому

    Iwe uyu ndi brian Banda mboli yako osamalemba zithu zosiyana ndizomwe zili mu video ayi usiye zachikapezi

  • @user-ii9ch7oz8n
    @user-ii9ch7oz8n 2 години тому +1

    zaziii zioneserero zopanda mfundo

  • @daviekamanga1417
    @daviekamanga1417 Годину тому

    mutopa kkkkk mwamva kuwawa kunja kwa boma simunathe

  • @JoshuaMbewe-ff5mk
    @JoshuaMbewe-ff5mk 3 години тому +2

    Koma zoti ng'ona yafa nzoona?

    • @Alice-z7t4z
      @Alice-z7t4z 2 години тому

      😂😂😂😂😂😂😂 kaya

    • @Alice-z7t4z
      @Alice-z7t4z 2 години тому

      😂😂😂😂😂😂😂 kaya

  • @Amgwagwa
    @Amgwagwa 2 години тому +1

    Ndemwati akwataine???

  • @stevenmwamadi3035
    @stevenmwamadi3035 3 години тому +2

    Akapanga zimenezo ndiye mavoti Azavuta kuti athu azavote mumuuze crocodile wanuyo

    • @hastingsbnyirongo
      @hastingsbnyirongo 2 години тому

      Timuuza iweso bilimankhwe wakoyo umuuze

    • @stevenmwamadi3035
      @stevenmwamadi3035 2 години тому

      @@hastingsbnyirongo athu osapota crocodile Maoneka chikangawa team imeneyo

  • @frazereline
    @frazereline Годину тому

    Iii zilikotu ziliko..

  • @ShamimuBisani
    @ShamimuBisani 2 години тому

    Garu wafayo mukut mkulu wapolisiyo alibwino bwino ku mortuary koma unyolo unali kutiko panthawi yomwe amafayo inu

  • @ChiyembekezoPhiri-sv8nw
    @ChiyembekezoPhiri-sv8nw 3 години тому +2

    Ndiye mwati awelenga ndi Brian Banda eti

    • @jennyx6914
      @jennyx6914 3 години тому

      nawonso amatinamiza uyu mwina ndi brianda junior kkk

  • @HamanjaManyela
    @HamanjaManyela 2 години тому +1

    Ife sitimaziwa akadalengeza ma radio

  • @MaggieCement
    @MaggieCement 3 години тому +2

    Tikawapeza azikakodza Malo

  • @sharifujoe7633
    @sharifujoe7633 2 години тому

    Kupolice dothi lagwa lankhasa

  • @Brockbaby143
    @Brockbaby143 Годину тому

    Tiyenazoni

  • @Gorilla-k8e
    @Gorilla-k8e 2 години тому +1

    Mwanamatu boss uyu ndi E kamzikiti

  • @TimamuOwen
    @TimamuOwen 2 години тому

    Dziko lamalawi lafika paugalu tsapano

  • @daviechibwana3137
    @daviechibwana3137 2 години тому

    Boma ndilomweri Sitikusintha ai mpak 2030 wooooo

  • @Spaw-BTheGogoBoy
    @Spaw-BTheGogoBoy 2 години тому

    Makosana ma video anu amangojamajama bwanji

  • @OsmanYusuf-u1v
    @OsmanYusuf-u1v 2 години тому

    Timazifuna koma kuopa ku wire

  • @princedetbozsmallboy1749
    @princedetbozsmallboy1749 Годину тому

    kodi Brian ndiwophweka mwalemba kuti wowelenga ndi Brian banda kuwona wowelengayo ndi wina😂😂😂😂😂😂

  • @blessingbanda6206
    @blessingbanda6206 2 години тому

    Kodi bwanji mumakonda kudula dula nkhani .

  • @CharlesNamacha
    @CharlesNamacha 2 години тому

    That's true

  • @StainDandize
    @StainDandize 3 години тому

    Mau mzika iliyose ili ndiufulu ovota

  • @GeshoMwakitwile
    @GeshoMwakitwile 2 години тому +1

    Za chitipa zinayamba pa nthawi ya dpp ndipo unya uwona palibe kusintha boma boma ndilomweri

  • @MaxonKambazithe
    @MaxonKambazithe 3 години тому

    Mchiyambi chabe ichi ngati sizitheka zomwe tikufuna tizatuluka anthu ambiri

  • @YusufAbdulrashid
    @YusufAbdulrashid 2 години тому

    Koma Brian Banda uyu nde ndi uti?! Kkkkk

  • @shadrickmsungambeu962
    @shadrickmsungambeu962 2 години тому

    Nonsense

  • @RhodrickBanda
    @RhodrickBanda 2 години тому

    Iyambe kunfa nkhalamba yozikozera ija kaye

    • @RAFICKRAHIMUMUSSAH
      @RAFICKRAHIMUMUSSAH 2 години тому

      Koma ng ona afatu kumalawi tisangalale sopano

    • @JudithKatungwe
      @JudithKatungwe 2 години тому

      Ubwino wake mulungu amatenga yemwe wamufuna akule achepe,,,, osati zomwe mukufunazo

  • @JacquereenPereira
    @JacquereenPereira 2 години тому

    Akutelotu kuti ngona ya ngogwa itava kuti Ngona izake yafa nayoso Yangogwa tiziva

  • @FatsanTobiyas
    @FatsanTobiyas 2 години тому

    Zaziii

  • @PatrickMbenje
    @PatrickMbenje 2 години тому

    MuLungu ndi wachikondi ndipo sangalore kuti Ana ake akhale akulira mpaka kale 2025 MuLungu sangatisiye tokha...

  • @FlorenceDouglas-x5c
    @FlorenceDouglas-x5c Годину тому

    Nde mwati thupi la malemu chikangawa tiika liti ? 😂😂

  • @HappyMunthari
    @HappyMunthari 3 години тому

    Kd afa ndi chani ameneyo

  • @WedlardZandimwaya
    @WedlardZandimwaya 2 години тому

    Timayesa chakwela basi kayikeni nyamayo filijimo

  • @JohnMakinah
    @JohnMakinah Годину тому

    Anali a mcp anthu onsewa kaya adya chimbazi kuchoka ku mboma

  • @JohnMakinah
    @JohnMakinah Годину тому

    Anali a mcp anthu onsewa kaya adya chimbazi kuchoka ku mboma