COMRADE NTANYIWA - SATURDAY MR PRESIDENT AKUKASEWERA MASEWERO A GOLF

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 10 жов 2024

КОМЕНТАРІ • 43

  • @HamzahMiles
    @HamzahMiles 15 годин тому +2

    Pali anthu ena amene simumusata munthu yi, please ma post ake sananene kuti president wafa koma anati Ali ku chipatala cha Garden city hospital basi

  • @FatimanickisJaffer
    @FatimanickisJaffer 18 годин тому +1

    Mwat born kalindo akamamusak saoneka km ndasekatu 😂😂😂😂 man of God glory to God born kalindo pangolin my brother

  • @HalisonSolomon
    @HalisonSolomon 4 години тому

    COMLADE IFE SITINGATAYE NTHAWI KUPEMPHERERA CHIGAWENGA CHIMENECHI CHAZUNZA ANA A ISRAEL, CHIFE BASI TIKACHIIKE IYAAAA

  • @YusufJimmy-v1o
    @YusufJimmy-v1o 19 годин тому +2

    Ntanyiwa sananene kuti wamwalila...Tikumutsata bhobho...osamunamizila

  • @GideonKodimba
    @GideonKodimba 19 годин тому +3

    Kkkkk wabodza iwe umati chani uli ndi pakamwa

  • @HalisonSolomon
    @HalisonSolomon 4 години тому

    KAPE NDIWEYO WA CHIKANGAWA NGATI SIMUTSATA BWINO NTANYIWA UPANGE ZAKO, NTANYIWA MOOOOOOFIREEEEE , CHIKANGAWA WAFA AKAKUMANA NDI PRESIDENT WATHU SKC ,IYE AMAONA NGATI WA MUYAYA IYAAAAA

  • @NolityKondowe
    @NolityKondowe 10 годин тому

    Uyu koma zokamba zake.Timva ziti.Poyamba amati president wamwalira.pano akuti president akupita ku MUST ku Thyolo?

  • @Randy-er2xo
    @Randy-er2xo 19 годин тому +2

    Tidzaona mawalo kuti chakwera akusewera nawo masewero agolf

  • @JoelMwenegamba
    @JoelMwenegamba Годину тому

    Ife sitimu pemphelera reason tili ndi njala he take our money going to Unga for shopping.

  • @BrightLuciano
    @BrightLuciano 16 годин тому +1

    Ntanyiwa sananenepo kuti president wamwalila apo pokha musanamizle

  • @BerthaMlalama
    @BerthaMlalama 2 години тому

    Mmm sananenepo kuti wamwalira ayi ife tikuwasatira bwino bwino koma zikanachita bwino kuti Mr Chikamgawa akanafa iyaaa munthu wanji womva mavuto anthu ake

  • @LastonMmanga-r2u
    @LastonMmanga-r2u 19 годин тому +1

    Ntanyiwa sadaneneko kuti Chakwera wamwalira mukatelonso amene mukutelonu mukunama, ndatsatira bwino MA vn ake onse kuyambira dzuro atasowa kwa kanthawi koma zomwe ine ndinamva ndi zoti Ali ku chipatala cha Garden city ku south Africa, komanso musayiwale, 2018-2019-2020 mu nthawi ya Peter muthalika ambiri amakambanso nkhani ngati zomwezi president akasowa,nde monga ine sindikuwona cha chilendo choti mpaka Ena azimangidwa nazo, anthu akufuna Baba wa dziko atiwuze kuti wayenda bwanji ku UNGA koma kuli ziiiiiiiiii😢😢😢😢

  • @babranzima8120
    @babranzima8120 18 годин тому

    Chipita ndi chitembo ??

  • @IsaiasIsaias-yq7zg
    @IsaiasIsaias-yq7zg 16 годин тому +1

    Koma achakwelawo iwowo pamene akhala amangukhala ndidziwembubwanji osamasangalatsa amnthuawo akasakebonikalindo chifukwachiani bonikalindo safuna zopusa komaso iwowo adakamatopa ndikuganizakuti mdzikomuno amnthu adwachitedze ndipange bwanjikuti ndapulumutse kodi mesapaja adali abusapaja lelo mudziti mmatenda aaa kkkk kaya

  • @JamesChimera-hw1nv
    @JamesChimera-hw1nv 4 години тому

    Dzuro walengezamaliro lero ukulengeza matenda munthu yemweyemweyo? Iwe ulibe zogwirika ndiwekapekwabasi

  • @JamesChimera-hw1nv
    @JamesChimera-hw1nv 5 годин тому

    Akasewerabwanji golf munthu oti mwamupha? Mbavainu mungofuna udanitsa anthu inu mukudya masupageti kunjakwanuko zipanganizanuka bonikalindo asamalachani alimwanaoopsya ngati adzafa ndinu anthuodanitsa munthu opemphera nchisaleyo ufuna adanenaye

  • @BrightMbewe-fz5zf
    @BrightMbewe-fz5zf 20 годин тому +2

    Aaaaa mwachedwa nayo,

  • @LonexWataya
    @LonexWataya 17 годин тому +1

    Che macdonald kachala ndi iwe wa mcp eti

  • @ThivadoartistDyson
    @ThivadoartistDyson 15 годин тому

    Kunkuyu wachamba, panopa maiko usi akukozekela kunka ku state house, mkadakonda manganya akadantulitsa pasi udindo chimwendo kkkķkkk mimba njuu kulibe kusintha atsogoleleri kwa manu konko

  • @AmickKammalele
    @AmickKammalele 15 годин тому

    Golf akamenyela kuti muthu wamwalira kkkk tiyeni only 2days

  • @LameckNgwangwa
    @LameckNgwangwa 5 годин тому

    Machine

  • @isaihmagani5697
    @isaihmagani5697 19 годин тому

    Ntanyiwa umangidwatu iwe ndi bodza lako misleading Malawian ndi za bodza,ngati ulibe zolankhura kumakharako chete pena,ngati momwe amachitirako a Bon Kalindo amazakharako chete pene osati kubwetuka

  • @AnyuxyJulias
    @AnyuxyJulias 19 годин тому +1

    Aaa gofo sasewela nkono umoz

  • @GrecianWyson
    @GrecianWyson 19 годин тому +1

    Esh osamafaritsi khani ya ifa Koma arimoyo esh zopusa bwanji

  • @MagretDaniel-m8c
    @MagretDaniel-m8c 16 годин тому +1

    Musamunamizire ntanyiwa munthu wamulungu uyu

  • @FreserAaron
    @FreserAaron 15 годин тому +1

    👍

  • @MaxwellMalisawo
    @MaxwellMalisawo 17 годин тому +1

    Mumaitha a mtanyiwa

  • @EnriqueLemitton
    @EnriqueLemitton 15 годин тому

    Iwe ndi galu kwabasi..izi sizoona lumikiza a Malawi kuti tigwirizane

  • @alexandermeke6994
    @alexandermeke6994 13 годин тому

    Wabodza iwe wakhuta msima ya nyemba UDF woyeee

  • @AdamMakala
    @AdamMakala 3 хвилини тому

    Kkk

  • @NAUMIMiRACLE
    @NAUMIMiRACLE 5 годин тому

    Kulu uyu ngonama zulo watiuza zina apaso akutiuza izi mmmmmm

  • @MemoryMankhwazi
    @MemoryMankhwazi 17 годин тому

    Ntanyiwa mabodza usiye

  • @Felista-m4q
    @Felista-m4q 14 годин тому

    Azipita akapume

  • @TamalaKambanje
    @TamalaKambanje 18 годин тому

    Munthu wakulu nthanyiwa

  • @rodrickwiskes
    @rodrickwiskes 15 годин тому

    Pajatu boma ili silimanena chilungamo

  • @Desmond-q7r
    @Desmond-q7r 19 годин тому +4

    Antanyiwaso u misleading ppo nanuso mumati watisiya now u changing

    • @phindiswatshibo7101
      @phindiswatshibo7101 14 годин тому

      Abati Ali kuchipatala ku south Africa 😂😂

    • @fatsosmart4295
      @fatsosmart4295 11 годин тому

      Now u want to mislead us😂😂😂😂 he never said wafa plzzzzzz he said he is sick and has been taken to SA kuchipatala osati zokufazoyi eeeeeeeeeh eeeeee😂

  • @MacDonaldkachala-cm5gc
    @MacDonaldkachala-cm5gc 17 годин тому

    If you don't have news, you don't have it's not a crime, if you keep broadcasting false news, you will lose followers, that's my advice