Nafuneya pano wasinthadi,Unasiyadi miseche ija. Ndiye mwati chi Love chikumveka English,Masamu akukana?. A Maliro pezani Njira yabwino yothetsera mavuto anu ndi Duncan. Maliro be responsible Father osati za manja LENDE zakozo. Learn from Mr Kalanka, nthawi zonse amakhala ndi zochita za phundu kwa Iwo eni komanso ku Society. Dziko likufunika Anthu ngati achina Kalanka osati Anthu ngati achina Maliro omadikilira kukaba Cha Bwalo kwa Mfumukazi. One of my best MFUMUKAZI ndi iyiyi keep it up Guys. We love you all.
Mrs kalanka mayi odziwa kumukhazikisa mamuna mtima pansi, bambo afika kuwalandila bwino wow keep it up azikazi athu aphunzire nawo
Kkkkkk Nafuneya very nice cooling the temper of Mr kalanka we always learn through that
Koma iyi ndiye Madam Flora eeeeee this is outstanding nsaname, mumakwanira. Madam Nafuneya inuyo ndi match wa Tonde
😂😂😂😂😂 koma alongoawo a kalamka ndi number one ati alamu mwandichulutsamo,coca-cola wa Ali ndi June kkkkkkk😂😂😂😂😂😂
Ndi more tu
Nafuneya akunena mgamo koma nawonso mgapakamwa😂😂kalanka ndiumboni
Next week azaswanapo sure...mkazi Padera wakwiiratu
Iyiyi nde mwapha osat zibwana keep up the good work
I njoying this comedy keep it up guys you coming well
Mercy anadyetsa katundu ndithu... Nde zikapanga kuyenda zovuta.... I like the script
Mr Kalanka akundionekera ngati ndi a last born....zokwiyakwiya pafupipafupi..amazikonda kwabasi
Koma Danken ndi bambo ake maliro eshii 😂😂😂😂😂
Azimayi onse akanakhala ngati Nafuneya bwenzi mabanja akukoma, osati nkhalamo zamasiku anozi. Chikondi alibe koma ndalama basi
😂😂😂😂😂😂
inde atsikana masiku ndalama mbasi
I salute guys keep it up but we need Giring'ande n mfumukazi to in .💓💓
Che Flora ngusinanonyela
Kutandila pa ajilajila ja The last fishing boat ❤❤❤
Keep the fire burning Flora ,i enjoy watching fumukazi
Idyan muzinena maboza bwn😂😂😂😂😂
Ndipo inu😂😂😂
Sound yokhayo nde mumapeza yoyoyo tinyade
I love this,so educative, Mrs Kalanka please teach today's women to cool and love their husbands. So nice
Ndipo mai kalanga eeh
Maliro ndi danken ngati zamu film 😂😂😂😂
I watch this video from South Africa in Cape town .I proud with u .Nice comedy keep it up.
Akunkana maliro ndi momwe wavalira iwowo avalacho ncha usiku koma mpaka kukayenda nacho 😂😂😂😂
Yalelo ndiye siinabebe nsaname mopanda giling'ande or namoyo
I'm here 😅😅 mr first view and comment like
Am glad kt anafuneya is the one giving this type of advice
Wow so interesting keep it up 😂😂😂🤣🤣🤣proud of you guys , watching from Zambia.
Watching from Capetown. Guyz apa mwakwizinga heavy. Zikuchita kumveka mwamvemvemve
Very nce eeee achemwali awo akalanka eeee 🎉 "akut muli june mukakakola kkkkkk
Nafuneya you could kill alot of srs eee eeee kudziwa pomtobwanya kalanka😂
Kkkkkkkkk osat chagwa mbale ndindio 😂😂😂
Lululuuuuu chithumwa chayaluka m'mene zatoromo namoyo umbeta ndiosayamba
I like mayi padera amaliza nyazwaaaw❤❤❤
9:54 you always representing Us that's why this is My number one channel
😂😂😂😂 takumana 1 _1 kkkkk a malilo kuuza dankeni koma dankeni kkkkkk
Nafuneya pano wasinthadi,Unasiyadi miseche ija.
Ndiye mwati chi Love chikumveka English,Masamu akukana?.
A Maliro pezani Njira yabwino yothetsera mavuto anu ndi Duncan.
Maliro be responsible Father osati za manja LENDE zakozo.
Learn from Mr Kalanka, nthawi zonse amakhala ndi zochita za phundu kwa Iwo eni komanso ku Society.
Dziko likufunika Anthu ngati achina Kalanka osati Anthu ngati achina Maliro omadikilira kukaba Cha Bwalo kwa Mfumukazi.
One of my best MFUMUKAZI ndi iyiyi keep it up Guys.
We love you all.
Ya mfumukazi siituluka mphwemphwa
Ndipo kwa bas
Koma sister wake wa Kalanka ndi mbambande 😂😂🤣🤣🤣
Kodi akalamkawa ndi a last born nawo😂😂😂😂
Nafuneya anali mwala 🔥 keep it up guys
Kkkkk koma ine Ellen wandisekesa kukana kuti sanamuone Danken😂😂😂
Keep the fire 🔥 burning
Kkkk a farai ati mawu akulu amakoma akagonera. Nde akulu ake akanena inuyoye
Mlomwe amenei akukomesa (alongo a kalanka)
Well done nafuneya anakoza
Nafuneya wabwela amapolesa😂😂🤣🤣
first to watch
Nice keep it up waiting for next
Kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk,Nafuneya do the did tsopano!
Kwabhebha Ndikuno Motsooooo 🔥 🔥 Unandi Mai Padera
Koma kalanka anagwira mkazi wathanana Ali bho mamuna wa chiwala sachepa😂😂😂
Azimayi nkhani ndiyanu
nafuneya watinamizapo
Mumakwanisa bwanji kuugwira mukamvela kuti anali pakuti, malavu anu akuenda muchi English, alongo awo akalanka koma ndi Nyatwa, kaya Dzina lawo ndani.
Mulamu mwandichulusa kkkkkkkkk km inu
Ati nalibuluzi😅😅😅😅😅😅
Eeeee iyiyi ndeee mwavesa kukoma osanama
Koma alongo awo akalanka 😂😂😂😂😂 mpaka ayamba kuika June mu kokakoraaaaah
Mumakwana madolo nonse❤
Nafuneya ❤❤❤😂❤❤❤❤😂😂 keep it up
Falayi kupanda chinsisi kwabwanj uku 😂😂😂 Anafuneya ipatseni moto ya alamu anu nd a Maliro mwina akakwatira asiya kuthamangisana nd Danken 😂😂
😅😅😅😅 nafuneya ndi mulamwake zilibwino kwambiri
Kodi abale falayiyo ndi princes chitsilo eit🤗
Ayi ndi farai😅😅😅
Muziwelenga kumapeteko😊
😂😂😂😂😂mayi Padela tsopano
Malilo azamenyedwa one day
Mpaka kuika june mu cocacola kkkkkk bora ndadziwa
Ati zovala ngati nalibuluzi..kkkkk
Sopano alongo awo akalamka mwa Choka ku town ndi malaya ovalq pogonawo 😂😂😂😂😂😂😂😂 inuyo mumakwana guyz
Nafuneye eti pakana agututu ine 😂😂😂😂😂timakunyadirani guys , Se you again next week 🎉
Ma love anu akuyenda mu English 😂😂😂😂
Zili bwino 🔥😊😊
Me Mr Shoprite 😂
Apa anakoza abuyeo
Kakakola uyu... Heeeeey ..... Switihati Fa....🗣️
Nice ❤ June ndi coca cola emwe
Koma falai kkkkkk
Nafuneya 😂 June mukakakolaaa, momwenso athiramo suga nambara wanii😂😂😂
Dunken 😂😂😂😂
Good advise from Nafuneya
Koma pakamwa.....🤣🤣🤣
Kkkkk nafuneyaaa
Nafuneya malangizo kkkkkkkk
Kodi achina Gututu ndi Ching'ani ng'ani ali kutiko?
Kodi comedy ya 12 paribe? May because of the national mourning period we are in?
Mu kakakola muli June wambili ndi sugar number one 😂😂😂😂 alongo wao aKalanka ndi nkhani zina
Km danken ndi bambo ako ai ziikomo😂
Ati amandiziwa ine uyu
Next week kuchema osati masewela 🔥🔥
Koma mlomwe uyu😂😂
Falayi umakwana❤🎉🎉
Nafuneya umatha kuchengeta
Kkkkkk koma
Anafuneya mesa Amaliro mudawakana?nde mukupatsa azanu bwanji 😂😂
😂😂😂 ati maths akukana
Alongo akalanka kkkkkk ndi 1
Alongo awo a karanka eeeeh
Chemwali akalaka ND 1
Mr pangolini 😂
Nafuneya wallakhula zoona ndakulakhhlani sooth sfrica
Watching you guys from Zambia never disappoint.❤
Namoyo sing'anga anachindatu 😂😂😂
Nafuneya amayitha 😂😂
Koma Nafuneya umatha