Bon Kalindo Pa Face The Nation Rainbow TV Kusankhula Zakulephera Kwa Tonse Alliance Muzaka Ziwilizi

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 16 жов 2024

КОМЕНТАРІ • 94

  • @benjaminkampiyon1130
    @benjaminkampiyon1130 2 роки тому +8

    Exactly!!!! Born kalindo atazakhala president zinthu zizasintha uyu kungoima tizamupatsa ma vote ,this guy is so special I’ve never seen courageous man in Malawi like Bon Kalindo (take care wherever you go coz maybe thy may plan to deal with you so please take care Bon kalindo we will stand wth you at least your giving hope?🙏🏼🙏🏼

    • @masaukolikomo5548
      @masaukolikomo5548 2 роки тому

      Zikho la malawi pazentenga thawi kuti lithukukhe Oze Andale Aku malawi ofuthikha ndiye akhalowa boma amafuna Kuti alemele pazentenga thawi Zaka Zaka Kuti malawi izayimire payekha .azepheseke president olikhonda zikho ngat johi makufuli

  • @noordeenali7463
    @noordeenali7463 2 роки тому +5

    We need people like this to talk what is wrong in the country...no fear Mr ... tel them the truth

  • @williammhoni5729
    @williammhoni5729 2 роки тому +4

    Apa ngati kuli anthu otukwana bon kalindo ndekuti munthu ameneyo ndiwontheratu zeru winiko wanyamula unthenga wabwino kwambili

  • @chiccojelly9287
    @chiccojelly9287 2 роки тому

    And exactly mr born kalindo you're right, tonse alliance government is failed to ruling county of republic of malawi, you need to shout them powerful maybe they can change, malawi aonengeka I supporting you mr don't give up.

  • @kudakwashechindima967
    @kudakwashechindima967 2 роки тому

    This is a true leader with people at heart not money may you keep on doing this good job Mr for the people of Malawi.Salute

  • @yakissah3287
    @yakissah3287 2 роки тому +2

    Clap hand's for him ur my hero

  • @kingstonmazulu8547
    @kingstonmazulu8547 2 роки тому +2

    Shaaàa
    Mkuluyi koma akunena zoonatu

  • @pusparaz8438
    @pusparaz8438 2 роки тому

    Tikanapezeka anthu angapo angati Kalindo dziko likadasintha pitiliza Bon tilipambuyo pako(Shadreck Matenje fromRSA)

  • @ConfusedBabyTurtles-gi4hb
    @ConfusedBabyTurtles-gi4hb 3 місяці тому

    Kunena Chilungamo Bon Kalindo is the patriotic citizen. It may be true kuti mwna he is frustrated for not being given the minesterial position koma ngakhale akanakhala Nduna mkulu ameneyi akadalisusabe boma momwe lisakuyenda bwino. Kwa Maguys amene tikumu hater Bon Kalindo , let us think critically, nkuluyi if he was do it kt yekha apeze kenakake From Kuboma im telling you he would have been bribed by government as how other activists did. Mr Kalindo amaganizila anthu osauka kuposa mmene amaziganizilila okha. Mmene wakhala akumangidwila mkuluyi , he would have surrendered and began kumapanga ma business ake oti iye ndi banja lake kumasangalala koma iye amayesesa kuwayankhulila amalawi amene sangathe kuyankhula. BON KALINDO , kaya amapangira motive yanji koma Mulungu azikhala naye nkulu ameneyi

  • @mikemakamo6617
    @mikemakamo6617 2 роки тому

    I hear you mr born kalinda your issues very sweet and truth go deeper, pakhani ya feteleza, passport, madzi,magesi and E.t.c zikolathu la malawi lalowa mbola akumuzi afanjala. I lke your speech winiko

  • @geraldfdickson6069
    @geraldfdickson6069 2 роки тому

    Mr born Kalindo Pa mfunso zanu zili bwino kwambili 😘 😘 ndiposo zikulimbikitsa kwambili Komaso zikupeleka tsogolo La bwino. Pano A 🇲🇼 ambili tikuvutika kamba koti tinkakhala busy kuvotel zolakwikwa

  • @WilliamKamwendo-f4j
    @WilliamKamwendo-f4j Рік тому

    Am at the back to B kalindo 🔥🔥

  • @angelicajoseph3080
    @angelicajoseph3080 2 роки тому +1

    Kkkkkkkkkk was waiting for this video upload! 🙏

    • @tichezeamalawi9691
      @tichezeamalawi9691  2 роки тому

      Thanks for commenting we will keep on updating on what is happening in our country

    • @angelicajoseph3080
      @angelicajoseph3080 2 роки тому

      @@tichezeamalawi9691 Yeah it had already gone viral even before uploading..

  • @peterbanda5425
    @peterbanda5425 2 роки тому +1

    Moto kuti bhoooo winiko amayenda ndi machesi

  • @fynessambiri997
    @fynessambiri997 2 роки тому

    Bon kalindo ur no 1 timenyereni khondo anthu comwe akucita sakucidziwa amaombera manja zosayennera koombera manja , anthu tikuvutika akumdzi soap,mafuta, mcere mmmm ili ndi boma lamwazi

  • @ausbonchimgolo9984
    @ausbonchimgolo9984 2 роки тому

    Akamuna awa and my Uncle ipatseni moto basi

  • @bensonmanda235
    @bensonmanda235 2 роки тому

    Tikufuna anthu olimba mtima ngati amenewa komanso oima pachilungamo.
    Lets support him.

  • @samuzymkwanya8490
    @samuzymkwanya8490 2 роки тому +1

    Kma pachilungamo kalindo ndilimbali yanu zomalemekeza asogoleli zikuwononga ziko

  • @blysontytus2146
    @blysontytus2146 2 роки тому

    Boni kalindo ine naona ngati akusuta chamba kapena mkapime nzelu Kaye
    Zinthu zadula mtengo ziko lonse lapansi
    Iiwe ndi mbuzi yeni yeni

  • @williammhoni5729
    @williammhoni5729 2 роки тому

    Winiko amandivesa kukoma ngati kumalawi kulimunthu amene akunena zoona palibeso oposa bon kalindo. MALEMA WAKUMALAWI

  • @basiliojeremias6200
    @basiliojeremias6200 2 роки тому

    Akunama iyeso azachita zomwezo akunama uphawi amalawi wakuphetekani munthu wa zisunzo akhale president Winiko phawi ngati imeneyi

  • @fanuelmanuelcipriano2605
    @fanuelmanuelcipriano2605 2 роки тому

    Amene akunyoza winiko Ndiye Kuti ameneyo akumabanawo ndalama

  • @luciascharles4345
    @luciascharles4345 2 роки тому

    We are together Mr kalindo

  • @BeckhamDavid-v6c
    @BeckhamDavid-v6c 2 місяці тому

    Munthuyu ndiwazelu kwambiri mutagwila naye ntchito bwino dziko lamalawi lingasithe

  • @johnajassi3677
    @johnajassi3677 2 роки тому

    God bless you

  • @andrewmphande3677
    @andrewmphande3677 2 роки тому

    Very few can speak and stand on the truth

  • @charitychikadya8363
    @charitychikadya8363 2 роки тому

    Iyeyu anali mp muja anapanga chiani?

  • @ismailkhuneya3346
    @ismailkhuneya3346 2 роки тому

    Very strong en wise politician

  • @brendadumisan2526
    @brendadumisan2526 2 роки тому

    Mwamasukatu akalindo koma nanu munali a mp Ku DPP mungatiuze chimene munapanga

  • @samsonnyirongo6469
    @samsonnyirongo6469 2 роки тому

    Freedom of expression on the stearing..... Change must come...viva malawi

    • @yakiwemarko6694
      @yakiwemarko6694 2 роки тому

      Wininko kodi ndi boma liti lina chitako bwino mutanena chifikwa izizi mulakhula panozi muziona kuchokela boma liri limodzi mpaka pano chomwe mukuwona kusitha ndichoti palibe chositha mungovutika kunali anthu alikuti tangokhalani bas

    • @yakiwemarko6694
      @yakiwemarko6694 2 роки тому

      Kapena mwina mukufuna udindo chifukwa mwina achilima ada kunamizani zaudindo?

  • @AndrewMdala
    @AndrewMdala 5 місяців тому

    Ndikumamvelabe mpaka pano
    Kalindo alibe matha

  • @wisemanchilangwe947
    @wisemanchilangwe947 2 роки тому

    Truth should be taught.

  • @henrypondani6832
    @henrypondani6832 2 роки тому

    Mukufuna udindo komano sizitheka remember mawu omwe udayankhula pa zodiak pa 08 may 2018 akulu akalindo ndinu opusa zedi

    • @clivendecha8554
      @clivendecha8554 2 роки тому

      opusa ndi iweyo

    • @tichezeamalawi9691
      @tichezeamalawi9691  2 роки тому

      @@clivendecha8554 Zimene akukamba Winiko mmalawi weniweni oganiza komanso kutengera ndi momwe ulili pa Malawi akukamba zoona Zokha Zokha ma business athu agwa Palibe chikuyenda

  • @daudmatola9649
    @daudmatola9649 2 роки тому

    🙏🙏

  • @peterbanda5425
    @peterbanda5425 2 роки тому

    Kkkkk koma inu dzikoli khaya ndichani amadya matembatu muchi njinga chija koma lelo sangakayendensotu ha ha ha kaya nyumba imeneyija khaya muli satana wanji khaya kkkkkkkkkkkkkkkkkk

  • @wysonmpatama4393
    @wysonmpatama4393 2 роки тому

    Kalindo amwenyele nkhongo anthu akumudzi

  • @williamkalilangwe8275
    @williamkalilangwe8275 2 роки тому

    Anthu wa amkafuna kukonza za mimba Yao aiwala za ovotafe so day ya ma demo yo please dziwitsen nili ni kagulu kanga kodzwa kuyatsa bwno matayala asatinyanye aguduwa malaw niyathu iyi

  • @leonardwadi9148
    @leonardwadi9148 2 роки тому

    Akalindo kukwela kwazithu ndi dziko lililonse kusogolokuno ziyenda,vuto mwasauka mukulilila udindo takuonani kare,nde mwajijilika nazo

    • @abduljafari6577
      @abduljafari6577 2 роки тому

      Iwe uzinva anayamba kuzuzula ali nboma la bpp osamango ombela nmanja zopusa

  • @happynjikho8718
    @happynjikho8718 2 роки тому

    Fact💥💥💥

  • @williammhoni5729
    @williammhoni5729 2 роки тому

    WINIKO AKANANKHALA NGATI NDI WADZIKO LA SOUTH AFRICA BWEZI ALI NDI SAPOTI YOWOPHA KWAMBILI

  • @rawiisamade8016
    @rawiisamade8016 2 роки тому

    Achikulire adanena kuti mutipaty ndi nkhondo lero ndi izi,

  • @worldnewschannel973
    @worldnewschannel973 2 роки тому

    dziko asamalitenge ngati munda wao a china tonse alliance wo, komaliza mkomweka next election sutuwafunanso

  • @kassimumar6421
    @kassimumar6421 2 роки тому

    Bon Kalindo tiri pa mbuyo panupo
    People think you're acting

  • @ibrahimmeemzy9754
    @ibrahimmeemzy9754 2 роки тому

    Muma nthiyimilila kalindo

  • @brendadumisan2526
    @brendadumisan2526 2 роки тому

    Uchisilu fodya wankulu wakuzunguzani inu akalindo ugaru wanu

  • @charitychikadya8363
    @charitychikadya8363 2 роки тому

    Zimakomatu poyankhula

  • @fanuelmanuelcipriano2605
    @fanuelmanuelcipriano2605 2 роки тому

    Winiko ndakunyadila Kwambili chifukwa umatha

  • @nkosinathimarcus4826
    @nkosinathimarcus4826 2 роки тому

    Ino sindawi ya kamuzu mukutengela kamuzu anthuluke akanika yaka ziko

  • @nkosinathimarcus4826
    @nkosinathimarcus4826 2 роки тому

    Komaso ndalama sa kolona sikuteka mukunama kuti sakuyimisani kofiti bosa mutiononga mukupa ziko tiusani

  • @paulnkhama3621
    @paulnkhama3621 2 роки тому

    Amatitenga Ngati zisilu one day wina azadulidwa machende

  • @rawiisamade8016
    @rawiisamade8016 2 роки тому

    Awuze tikuthawira mayiko ayeni chifukwa cha ulamuriro wa chakwera

  • @fynessambiri997
    @fynessambiri997 2 роки тому

    Kuno kuthekerani mmmmmtikuvutika cipani cosintha zinthu cija

  • @nkosinathimarcus4826
    @nkosinathimarcus4826 2 роки тому

    Utukwana chiyani ndinu sizilu akupasani ndalama machende ako pano sitiopa

    • @ommyomario3154
      @ommyomario3154 2 роки тому

      Yes tell them bro there is another flooring man that his tonking zopanda mutu

    • @Littlefair7
      @Littlefair7 2 роки тому

      Koma zotukwana on a public platform like this ndi usaveji, kusutsana ndi ufulu koma kutukwana ndi kusowa khalidwe.

  • @yakiwemarko6694
    @yakiwemarko6694 2 роки тому

    Ngati mupita kusewu mugwilitse tchito malamulo chifukwa muka phonya mudzapeza vuto

  • @joycenkosi420
    @joycenkosi420 2 роки тому

    Good one madala ndikubwela kuzakuthandizani

  • @peterbanda5425
    @peterbanda5425 2 роки тому

    Alowe ndi anzelu uyu nde anakonza

  • @paulnkhama3621
    @paulnkhama3621 2 роки тому

    Waboza abisala

  • @robsontyg3928
    @robsontyg3928 2 роки тому

    Misala kupenga uchitsilu nguluwe fisi, mademo amenewo mudzipangila kwanu konko ku lilongwe kuno tikukhapani khapani

    • @tichezeamalawi9691
      @tichezeamalawi9691  2 роки тому

      Monga Winiko akunama moyo uli pabwino pa Malawi pano? Zoti zinthu zikudula daily, ma business athu akugwa akunama? Let's love our country

    • @robsontyg3928
      @robsontyg3928 2 роки тому

      Ase ine panopa ndikukhala ku Singapore zinthu zakudula dziko lonse la pasi not ku Malawi kokha, anthu ambiri achotsedwa ntchito ma company ochuluka atsekedwa ndiye dziko lathu lodalila ma Donna's muti zinthu zitchipe munamanga ma factory muli ndi ma company?

    • @tichezeamalawi9691
      @tichezeamalawi9691  2 роки тому

      Ife sitikunena za Singapore, Tonse Alliance inalonjeza zambili zomwe amati aziona kuti ndizotheka, Lero mmalo mwake zinthu zikusintha from bad to worse, Zoti ku Singapore zinthu zikuvuta muzinamiza anthu ena pano maiko ambili akuchita recover after Covid-19 kuwasokoneza zinthu zikuyenda, Koma ku Malawi Palibe chikuyenda ma business athu agwa agwa, ndalama ikukwera daily, vuto uli kunja ubwere uzaone momwe zilili PA Malawi Lero, iweyo ukukamba zimenezo chifukwa uli kunja Kwa Malawi, munthu kugula galimoto 4 million kulipila duty 3 million, misonkho angokweza mosayang'ana economy yathu Toll gate kuchita kudula kuposa RSA dziko lolemera

    • @robsontyg3928
      @robsontyg3928 2 роки тому

      @@tichezeamalawi9691 ase gwila ntchito kuti upeze zosowa zako usayembekezele kuti boma likupatsa zinthu zaulele wauponda

    • @hendrixchimalizeni750
      @hendrixchimalizeni750 2 роки тому

      Sukudzowa zomwe ukuyankhula zinthu zikudula konse yes koma kumalawi it’s too much

  • @worldnewschannel973
    @worldnewschannel973 2 роки тому

    Mr kalindo sakuyankhula izi kuti akufuna udindo limeneli ndi bodza, nkhani yayikulu ndiyoti tiwone zomwe akuyankhula bon kalindo kuti ndi zoona kapena ayi? yankho ndi loti akunena zoona chifukwa kalindo izizi adayamba kuyankhula motere ngakhale ali MP ndiye omwe mukuti sadampatse udindo mukulakwitsa

  • @robsontyg3928
    @robsontyg3928 2 роки тому

    Iwe kalindo usatinyase wava

    • @clivendecha8554
      @clivendecha8554 2 роки тому +1

      Mboli yako iwe kadet wa mcp

    • @robsontyg3928
      @robsontyg3928 2 роки тому

      @@clivendecha8554 I'm very proud kukhala wa MCP, iwe ndi cadet wa DPP, atsogoleli anu onse ku DPP munachokela ku Mozambique, Peter munthalika, Nankhumwa, Mwanavekha, Kabambe, Mchacha, Leston muli, nose munachokela ku Mozambique amalawi tatopa ndi kulamulidwa ndi ma Portuguese

    • @robsontyg3928
      @robsontyg3928 2 роки тому

      @@clivendecha8554 ine wa MCP panopa ndili ku Singapore ndumwa mkaka ndili phee

    • @clivendecha8554
      @clivendecha8554 2 роки тому +1

      @@robsontyg3928 thats right... you and me , we are not in Malawi so you can not say Mr kalindo asakunyase as if you are feeling the pain.... nothing wrong to support MCP but if there is wrong doing,akuyenela kuzuzulidwa . its right for everyone

    • @clivendecha8554
      @clivendecha8554 2 роки тому +1

      @@robsontyg3928 i dont support dpp and i will support mcp either, not any political party..... i only support any govervement that run the country well..... people like you that is why malawi is poor..... mumangoimbila mmanja zilizonse