interview ndi a shadrick namalomba

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 3 гру 2023

КОМЕНТАРІ • 138

  • @mayesojameskatete
    @mayesojameskatete 6 місяців тому +13

    Namalomba good enough to be a DPP spokesperson ❤❤❤

  • @joemlelemba6572
    @joemlelemba6572 6 місяців тому +5

    Achina dausi akufuna kuononga chipani ndi nankhumwa , I like this guy namalomba we are behind you

  • @hopeskafumbi2246
    @hopeskafumbi2246 6 місяців тому +4

    MR Namalomba zikomo kwambiri you are good spokesperson.

  • @nicholaskachingwe7143
    @nicholaskachingwe7143 6 місяців тому +3

    Journalist ofooka..sakudziwa bwinobwino chomwe akufuna kudziwa

  • @georgesmart3791
    @georgesmart3791 6 місяців тому +7

    Nambalomba more fire 🔥

  • @VictorBanda-tq5ob
    @VictorBanda-tq5ob 6 місяців тому +2

    Good job Leah keep it up osawopa

  • @user-tq6pg7bv9x
    @user-tq6pg7bv9x 2 місяці тому

    Namalomba more fire umakwana chibwana cha kwathu ichi chosamba ichi 😅😅😅😅 2025 bomaaaaaaaa I love you Namalomba ❤❤❤❤❤

  • @LysonMtalika-tb6fk
    @LysonMtalika-tb6fk 6 місяців тому +5

    I like the way honourable Namalomba present things, we are behind you and our beloved DPP 🔥🔥🔥🔥

  • @user-wd9yd1bg9n
    @user-wd9yd1bg9n 6 місяців тому +1

    Namalomba is a smart guy, nawo anankhumwa, dausi ndi geofry ndi makape osayambisa chipani chawo bwanji

  • @enerstmwakhundi4400
    @enerstmwakhundi4400 6 місяців тому

    mbambande Leah 👏Good questions

  • @kha6068
    @kha6068 6 місяців тому +2

    This guy is very smart 🎉

  • @user-xm2xy5oz7g
    @user-xm2xy5oz7g 6 місяців тому

    Namalomba more fire keep it up

  • @georgesmart3791
    @georgesmart3791 6 місяців тому +2

    More fire Nambalomba fire 🔥 🔥

  • @FelixChizanja
    @FelixChizanja 6 місяців тому

    Namalomba amatha,kuyakhula and akuziwa zomwe athuwoipa wofunakusokonez chipan, ambili achinasonda ndi azizawo alowa zipani zambilimbili and mbilizawo ndikusokoneza kenako athaweko, anamalomba ndi azanu achinasaka musalolele Anawo kusokoneza

  • @DICKSY-kz1qd
    @DICKSY-kz1qd 6 місяців тому +1

    Love you namalomba

  • @Chikulamayembe57
    @Chikulamayembe57 6 місяців тому +2

    This Journalist, Leah Malekano, just cuts it for me! 👏👏👏

  • @hendrinagama5325
    @hendrinagama5325 6 місяців тому +3

    Inutu chemwali mwadzitenga udyo akutumaniwo kuti mudzatola pakamwa

  • @user-ty7mc9mg1f
    @user-ty7mc9mg1f 6 місяців тому

    Komatu apa zikuoneka kuti,mtolankhani uyu sakumvetsa zomwe a Namalomba akukamba.

  • @isaaczuze
    @isaaczuze 6 місяців тому

    Mr namalomba ineyo ndikukulimbikisani kuti pitilizani bwana ndipo musagonje
    ....ineyo ndili mwanja mwa Peter mutharika ....nankhumwa ndichisilu akufuna ntchito yoti sangayikwanise ayi

  • @fraserluwemba6364
    @fraserluwemba6364 6 місяців тому +2

    Namalomba akunena chilungamo kuti mcp ndi yomwe ikusonkhedzera

  • @user-xq5ju2uo9h
    @user-xq5ju2uo9h 6 місяців тому +3

    Namalombe ndi mbuli uyu saziwa zamaundindo 🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣

    • @patrickmacheso5062
      @patrickmacheso5062 6 місяців тому +3

      Paja mbuli zilipo maguru angapo, Umbuli wa Namalomba uli better than wanuwo coz simungamufikile or pang'ono even mutatengana nonse ku family yanu.

  • @rashidsaid2232
    @rashidsaid2232 6 місяців тому

    Mr Namalomba good answers without hiding God bless u if u love DDP us we love it Chakwela must removed in 2025 akuononga too much our country

  • @patrickmacheso5062
    @patrickmacheso5062 6 місяців тому +4

    Namalomba is a very smart guy and he deserve to be the spokes person for APM and DPP, Nankhumwa, Dausi, G Jeffrey and other empty tins that there making noise including Ken Msonda are Just making Jealous for him.

  • @HappyMphande
    @HappyMphande 6 місяців тому

    One step at a time Leah 🎉

  • @AlexisKantondo
    @AlexisKantondo 6 місяців тому +1

    Ntchito ya utolikhani adona simayitanidwe anu

  • @JohnKamanga-tu2il
    @JohnKamanga-tu2il 6 місяців тому

    All the best mr

  • @brinokalemba4503
    @brinokalemba4503 6 місяців тому +1

    Leah ndiwe dolo🔥🔥🔥🔥🔥

  • @markhamdaddy
    @markhamdaddy 6 місяців тому

    Muthu wamkulu namalomba kuyakhula zamchere

  • @whitethamangar2950
    @whitethamangar2950 6 місяців тому +1

    😂😂😂😂Namalomba 🔥🔥🔥🔥🔥🔥

  • @clintonhodda9830
    @clintonhodda9830 6 місяців тому +1

    Nankhumwa, Dausi, Msonda komanso Jeffrey pls yambitsani chanu Chipani

  • @brianchimwaza
    @brianchimwaza 6 місяців тому +1

    Mbambande namalomba

  • @paulmakaula4937
    @paulmakaula4937 6 місяців тому +2

    This is the caliber of politician Malawi needs onwards wadzake wolemera, full of politics. He can thoroughly present Malawi before international bodies like IMF, World Bank, bilateral donors and ably convince on behalf of Malawians...actually bomali can tap his talents....DPP please let Nankhumwa and APM amicably solve this wrangle with few reputable clergy as moderators...Nankhumwa should not be underrated has support base pa ground...reach out possible new intellectual faces who should help clear image yomwe inaonongeka in the last reign...otherwise Malawians akufuna izizi squabbles zithe! However odana ndi Namalomba akudana ndi progressive minds, he's simply the best!

  • @edsonnyasulu5394
    @edsonnyasulu5394 5 місяців тому

    Namalomba naye akusaka ya deya kuti azikadya ndi Ana aka palibe cha zeru apa

  • @user-wt4hl4ps2k
    @user-wt4hl4ps2k 6 місяців тому +2

    Namalomba, a mere rift raff...Such position suit well level head persons.. always avoiding questions... deliver lacks substance... exposing the party gone to wayawaya wading in Chikangawa forest..Namalomba is the one brewing problems in the party...Unless replaced, party problems and confusion will never die until 2025 and the party will walk out again with tail tapped between the two legs...Namalomba amaopa Nankhumwa kwambiri...Analephera kumchotsa Nankhumwa as Leader of Opposition ku Parliament. Akuopa party convention...Is this not litmus to show Nankhumwa is powerful and threat to APM...Namalomba and gang are the ones forcing APM to stand stand...Zawo zaima...zosolola zija zatha..akufuna azizasololanso kumbuyo Kwa APM... These people are denting the image of APM... Shame..

  • @kingsleylabvulani5515
    @kingsleylabvulani5515 6 місяців тому

    😂😂😂😂😂 Namalomba ndi dolo

  • @user-kr1kg5hy9l
    @user-kr1kg5hy9l 6 місяців тому

    Bravo Namalomba.

  • @clintonhodda9830
    @clintonhodda9830 6 місяців тому +1

    Namalomba ndi machine onse otumidwa ndi Mcp ali madzi

  • @user-hr2cg3ku1l
    @user-hr2cg3ku1l 6 місяців тому

    Mbuzi ya munthu Namalomba

  • @user-tq6pg7bv9x
    @user-tq6pg7bv9x 2 місяці тому

    Mbambande Namalomba

  • @bichardmoises9685
    @bichardmoises9685 6 місяців тому

    Nthawi zina ndizofunika osamapitako uku

  • @GustavoBoloi-kz8js
    @GustavoBoloi-kz8js 6 місяців тому

    Osaopa lakhula

  • @greychizaka4088
    @greychizaka4088 6 місяців тому +1

    Genius shad

  • @user-rk4ch1ly3z
    @user-rk4ch1ly3z 6 місяців тому

    Namalomba iwe ndi katswiri palibeso chipani wachigwira bwino ,ife tili pambuyo pa APM dpp woyee!

  • @user-ty7mc9mg1f
    @user-ty7mc9mg1f 6 місяців тому

    Leya ,bwinobwino ee

  • @IsaacKachimanga
    @IsaacKachimanga Місяць тому

    Mukuchoka ku mangoch South west

  • @user-nw6ie3xx8b
    @user-nw6ie3xx8b 6 місяців тому

    Aaaaaa yai namalomba muli ndizifukwa ndi adaus, grizeda, ndi na nkhumwa

  • @levisonmoyo1306
    @levisonmoyo1306 6 місяців тому

    About time she realized she just being used these politicians for their little funny games

  • @JOHNSANGWALI-ox8mu
    @JOHNSANGWALI-ox8mu 6 місяців тому +1

    Live from Kimberley
    Km vuto palibe no sound

  • @user-gk6bf7xe9g
    @user-gk6bf7xe9g 6 місяців тому

    Anamalomba 🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣

  • @MisterBanda-pl8ct
    @MisterBanda-pl8ct 6 місяців тому

    Thank you

  • @brightngwira8170
    @brightngwira8170 6 місяців тому

    Mipandoyo tayikanipo ya bwino aaaaa nanga Professor Anthur adzakhalapo bwanji
    Pakhale mipando ya exuctives ..
    Wena adzakhala ataminula apa adzakhalapo bwanji🎉
    Pilizi sinthani furniture apa 😮

  • @JamalNgumba-pe6xo
    @JamalNgumba-pe6xo 6 місяців тому

    Grezeda,Nankhumwa ndi osokoneza

  • @user-kx5uk8vj1j
    @user-kx5uk8vj1j 6 місяців тому

    Namalomba kuchikamwa

  • @victorbanda9039
    @victorbanda9039 6 місяців тому

    Namalomba nthata yanjala yaku dpp ati afuna azakhale a minister of information koma maloto achumba gogo wakoyo sangawineso

  • @archraphnkhoma-lw6wx
    @archraphnkhoma-lw6wx 6 місяців тому +1

    Palibe za Dausi apa Adadi Basi

  • @user-kr1kg5hy9l
    @user-kr1kg5hy9l 6 місяців тому

    Nankhumwa ndi wakuba...akufuna kuba chipani mgwilenj.

  • @ndalamaandrew
    @ndalamaandrew 6 місяців тому

    Akuluwa ndi Solo kwambili 😂😂

  • @ChisomoMsiska-oi2vg
    @ChisomoMsiska-oi2vg 6 місяців тому

    Awa ndiwozikonda kwambiri ndichifukwa chake anzawo amathawako musonda ali ndi nzeru awa mmmm

  • @user-tq6pg7bv9x
    @user-tq6pg7bv9x 2 місяці тому

    Matchin Namalomba

  • @user-du9qs4tb6u
    @user-du9qs4tb6u 6 місяців тому +1

    Iwe leya ndiwe kape usamafuse mafuso oyambanitsa anthu chomwe ungadziwe panopa amalawi akuvutika pa moyo watsiku nditsiku tikufuna mafuso opindulila amalawi kodi iweyo leya makolo ako sakuvutika kumudziko ndipo iweyo usamakhale pamenepo ngati azichimwene ako sakuvutika kodi ndiwe wa mcp. Ngati ukufuna kumva zokhudza amuthalika upite ku page house ukawafuse maganizo awo.

  • @patassonelucaszovuta3431
    @patassonelucaszovuta3431 3 місяці тому

    Uyuyu ndi amene wagoneka Peter panopa madala aja ali ntulo akugona chifukwa uyuyu adawayika pa lo adzazindikila mochedwa chipani chitatha

  • @user-du9qs4tb6u
    @user-du9qs4tb6u 6 місяців тому +1

    Ndipo anthu amenewa akutumidwa ndi boma kuti azivuta ndicholinga aboma azapeze polowela do you think panopa tilindi a opposition nankhumwa

    • @user-pn7ek7wb7n
      @user-pn7ek7wb7n 6 місяців тому

      Iwe sudziwa kalikose time ndiye ya mcp

  • @user-uf1tz7bp5q
    @user-uf1tz7bp5q 6 місяців тому +1

    Kom ndiwambalumetu fira

  • @roberttungande7850
    @roberttungande7850 6 місяців тому

    Alandisa chipani😊

  • @user-mj3ms4jt3b
    @user-mj3ms4jt3b 6 місяців тому

    Namalomba sioyenela udindo umenewu anapatdidwila kukachipinda. Leya wangoiwala kuwafusa kuti Kodi 2018 ku convention ya DPP anthu anapikisana pa udindo wa spokesperson? Nanga ena anapikisana pa udindo wa publicity secretary? Nanga ngati anapikisana mumaudindo onsewa pa convention, iwowa anatenga udindo omwe unali wandani yemwe anasakhidwa pa convention yo?

  • @GreenFacksoncassim
    @GreenFacksoncassim 6 місяців тому

    Apm boma 💙💙💙💙2025

  • @martinkalaka2667
    @martinkalaka2667 6 місяців тому

    Eish pano tapumulako za kupha alubino nde wina mkumati ndiwabwino kusaganiza kapena chani namalomba nda zake adpp amkapha alubino sitinayiwaletu agalu inu mwava😮

  • @robsontyg3928
    @robsontyg3928 6 місяців тому +2

    Professor wa kumatako,

    • @lewisbonongwe8518
      @lewisbonongwe8518 6 місяців тому +1

      Wa carlolite sopano chomwe amadziwa ndi kutukwana basi
      Utaphoda😂

    • @robsontyg3928
      @robsontyg3928 6 місяців тому

      @@lewisbonongwe8518 pathako pa mayi ako wava, dzitsilu dza anthu dza alhomwe

    • @lewisbonongwe8518
      @lewisbonongwe8518 6 місяців тому

      Inu mulibe pathako Mr yelesa😂🤣

    • @robsontyg3928
      @robsontyg3928 6 місяців тому

      @@lewisbonongwe8518 ma refugees dzi anthu dza Mozambique 🇲🇿 msunu kanyoko palikundu penu

    • @randolphkazembe229
      @randolphkazembe229 6 місяців тому

      Umazola chani kod

  • @user-km8ni2yk2c
    @user-km8ni2yk2c 6 місяців тому

    Ndozitukumula chabe chilungamo mulibe umu

  • @user-ty7mc9mg1f
    @user-ty7mc9mg1f 6 місяців тому

    Akuti ,a spokesperson ndi amene amaitanitsa ,ma meeting,koma mopatsidwa mphamvu ,kapena kutumidwa ndi a President iiii siukumva pati?

  • @JohnKamanga-tu2il
    @JohnKamanga-tu2il 6 місяців тому

    Tell them

  • @fraserluwemba6364
    @fraserluwemba6364 6 місяців тому +2

    Leah udziwe kuti mcp singalamulire DPP and zodiac ndi station ya MCP

    • @hendrinagama5325
      @hendrinagama5325 6 місяців тому

      Zoona man ndkudabwa naye Mai yu

    • @martinkalaka2667
      @martinkalaka2667 6 місяців тому

      Palibe radio station yachipani kambani zina inu

    • @martinkalaka2667
      @martinkalaka2667 6 місяців тому

      Namalomba alibe fundo ayi akukanika kuyakha mafuso busy kukamba za mcp kupepela basi

  • @henryphiri6100
    @henryphiri6100 6 місяців тому

    Kukanganirana chipani agalu inu.mwini wake yemwe anapanga mbiri yabwino yachipaniyi.Nankhumwa akupanga chiani chanzeru pano tikuvutika ndi Chakwera ngati mtsogoleri wa opposition.Ndiye akufuna adzatsogolere ndani wakeyo.

  • @user-lw4hw9ce4w
    @user-lw4hw9ce4w 6 місяців тому

    Udindo umakukhalani kwambiri inuyo anamalomba dausi ndiye mwana ndani

  • @gilbertkumlinde-id9nc
    @gilbertkumlinde-id9nc 6 місяців тому

    Namalomba 0 pa 10

  • @reltonmbawala1329
    @reltonmbawala1329 6 місяців тому

    Namlomba agawanitsa chipani uyu, kodi anatulukila pati

  • @mervinchinga2342
    @mervinchinga2342 6 місяців тому +1

    Leah wakumana nazo amawonele ena aja🤣🤣🤣

    • @user-mv1vp4mf7r
      @user-mv1vp4mf7r 6 місяців тому

      Smart man namalomba , go-ahead amalawi akudikira boma lokoma la dpp

  • @jomochirwa
    @jomochirwa 6 місяців тому

    Namalomba mpakana kunena kuti ali ndi chuma kuposa a peter muthalika.pali za utsogoleli apa.izi ndichimodzimodzi ndi tonse ilipoyi

    • @user-frasernamaona14
      @user-frasernamaona14 6 місяців тому +1

      Mwamunvela bwino bwino koma? Wonelaninso sanati ali ndi chuma kuposa Mutharika wati mwinanso. Kodi mwina ndimawu oti ndi mumawasiyanisa bwanji?

  • @dominicmphepo-jk8lk
    @dominicmphepo-jk8lk 6 місяців тому

    Mwatikwana anthu inu just showing kuti you are not there to save but money hungry. Peter akagiver chipanichi chatha no one will save chipanichi.
    Anthu adyelanu mzanu anayiphula inu muli komweko now mukunva kuwawa mufuna muzabenso.
    Pano nthata za MCP zakhuta nanu munapopa zija zayamba zachepa don't worry.

  • @AllanBanda-hy3lh
    @AllanBanda-hy3lh 6 місяців тому +4

    Koma ndikadakonda DPP ikadatha kuthelatu psitiii mwina tiveko Zina zanzelu zamasomphenya kukhale zipani zawanthu oganizako mwawumunthu osati zitsilu zokhazokha ziliku DPP zogawana nyama musadaphe R I P Dr bingu ndimasomphenya awo in shot zabwino zose zidapita ndia bingu bas

    • @SheenahMwalabu-iz3pr
      @SheenahMwalabu-iz3pr 6 місяців тому

      Kugawanikanatu kochititsa manyazi, why mukungokhalira kusemphana ndemutatenga boma mudzaphanatu 😂😂

  • @henryphiri6100
    @henryphiri6100 6 місяців тому

    Komanso a Leah mudzipanga interview anthu oti afotokoza za nzeru.please anthu akuvutika.kuti tidzimva izi zamikanganozi ayiii it's an insults.zandalezo ayii chifukwa mwini chipani chimenechi ankakana kuti iyi siwandale ayi.ndiye please mudziyika zanzeru.mbuzi zimenezi tatopa nazo

  • @ireenkafatiya6568
    @ireenkafatiya6568 6 місяців тому +1

    Leah nde uti were is Brian, leah is trying to be somehow kkkkk zosabeba

  • @user-xx5dc5wl7g
    @user-xx5dc5wl7g 6 місяців тому

    DPP sikulowanso m Boma akuchita kuoneselatu kuti mbava zabodza zokhazokha

  • @wayneivanmacadam
    @wayneivanmacadam 6 місяців тому

    Adadi 2025

  • @ambrozonamazemba8986
    @ambrozonamazemba8986 6 місяців тому

    Didn't have time, to watch the whole interview kma ndangovera mmene wactra differentiate PRO and Spokesperson.bac kwina koseko ndagwirzana naye bac amenei

  • @wayneivanmacadam
    @wayneivanmacadam 6 місяців тому

    If APM dosnt stand as president DPP is finished to much childish politics nakhumwa and associates

  • @johnman4619
    @johnman4619 6 місяців тому

    Kodi chimene mukulepherera kuitaninitsa conversion ndichichiyani

  • @user-qb1ef1xw5d
    @user-qb1ef1xw5d 6 місяців тому

    Dpp vuto ndiloti sichinayambile pa ground chinachita kuba chipani cha udf

  • @JohnstoneNkhoma-jf7qe
    @JohnstoneNkhoma-jf7qe 6 місяців тому

    mawu tidaluza boma chfukwa cha nakhumwa ndi azakewo

  • @EmercianahKasiku-en6hl
    @EmercianahKasiku-en6hl 6 місяців тому

    Munthu uyu ndi inu nose mukuti Nankhumwa , Jeffrey,Dausi komaso Msonda ayambitse chipani chawo mulibe nzeru komaso ndinu ufunila zoipa chipanichi bcuz kuchoka kwa Chilima kunapangitsa kuti DPP iluze nde achokeso Nankhumwa nde 2025 yo muzalowa bwanji mu Bomamo?poti Nankhumwa pochoka azachokaso ndi gulu la Anthu ambiri,Chisale,Namalomba komaso Bright msaka ndi oba chimanga aja asiye kumulangiza komaso kukhala kufupi ndi president chipanichi chidzukaso kupanda apo chitha ngati UDF chizapeza mavote 250.000 basi😂😂😂😂tisaiwaleso kuti masankho ndi a 50+1 nde tichotse mamembers ena pali nzeru?

  • @DoYouKnow3838
    @DoYouKnow3838 6 місяців тому

    Ndi Brian Banda yekha angafuse Namalomba mafutso omveka bwino probably seconded by Joab Frank Chakhaza.

    • @viktornginde3720
      @viktornginde3720 6 місяців тому

      Mukadzamuchita analyze Brian Banda, n'pomwe mudzamudziwe bwino-bwino.

    • @SabitiChisawa-gm8ev
      @SabitiChisawa-gm8ev 6 місяців тому

      Joab akhale pa number 1 bwanji?

  • @BUY_YOUTUBE_VIEWS_d035
    @BUY_YOUTUBE_VIEWS_d035 6 місяців тому

    I wish there was a 'super like' option for this.

  • @chikondigondwe4669
    @chikondigondwe4669 6 місяців тому

    Koma

  • @SheenahMwalabu-iz3pr
    @SheenahMwalabu-iz3pr 6 місяців тому +1

    Who else notice kuti Namalombwa voice kufanana ndia Chilima 😊

  • @gladysbonongwe1038
    @gladysbonongwe1038 6 місяців тому

    Ntola nkhaniyo apite kumudzi akadzimvere yekha

  • @user-qi8xe7qh1e
    @user-qi8xe7qh1e 6 місяців тому

    Anamalomba zoti anthu akufuna zisankho 2024 zimenezo mukudziziwa? apa ndiye mudzitibhowa ndi 2025 mukukakamila 2025 bwanji uchitsiru kapena chani usadziwa malamulo kapena kodi bwanji a opposition nonse ndiopepela munadyetsedwa chani ndiye mukati 2025 mukuganiza kuti kwacha izakhala bwanji??

  • @SaidiMbawa-st6bj
    @SaidiMbawa-st6bj 6 місяців тому

    Kunena zoonadi anthu awa atitopesa ndi nkhani zawo zopusazo

  • @user-dp3fo7tl8c
    @user-dp3fo7tl8c 6 місяців тому +1

    Komatu sibwino kumapeleka interview kwa anthu osakhwima ngati ameneyi kodi Joab Chakhaza alikuti?

    • @SheenahMwalabu-iz3pr
      @SheenahMwalabu-iz3pr 6 місяців тому +1

      Mulinso phuma mwamayiwa, sadikila kuti munthu amalize kuyankhula. Inde ali ndika potential ndithu but shes not there, ofcourse bolako interview yaachisale ija anayesetsako mwinammwinamu koma iyiyi ndiena amafuna kutamika maybe koma sanafikepobe koma angokonza zimenezo ayi she will be great ❤

    • @LovemoreZondani-fj7hk
      @LovemoreZondani-fj7hk 6 місяців тому +1

      Awa ndi mavuto

  • @leonardwadi9148
    @leonardwadi9148 6 місяців тому

    Anamalomba mukuopa convention bwanji?inuyo ndi gulu lanu ndi amene mukuononga chipanichi

  • @alfredtanga8029
    @alfredtanga8029 6 місяців тому

    Anamalomba china chilichonse kukana inuyo NDE zandale ndikumbali

    • @whitethamangar2950
      @whitethamangar2950 6 місяців тому

      Kkkk ndiye mwanamatu munthu wandale samavomela oloko munthu atanena zoona