WAING'ALULA BON KALINDO LERO PA 16 July 2024

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 22 сер 2024

КОМЕНТАРІ • 22

  • @dondamissonchdziwe3958
    @dondamissonchdziwe3958 Місяць тому +3

    Viva kalindo, ALuta continua não pode ter medo você cidadão dá verdade, still goes on to speak justice, Iwo amamupha Chilima amaona ngati wabisala Osaziwa Kuti Wanthu ama tsiku wa Lero Ndi openya,taimani muone kusogoloku,awona zosawona, Manganya Ndi Munthu woipa kwambiri Ndi amene waphesa Chilima, nkhope yake yonyansa ngati mbira

  • @angelicajoseph3080
    @angelicajoseph3080 Місяць тому

    Fredo resembles Chilima, Fredo's voice resembles Chilima's

  • @MadalitsoChilinjala-pt3hx
    @MadalitsoChilinjala-pt3hx Місяць тому

    Bon kalindo katundu omanga mawaya

  • @charleshenderson70
    @charleshenderson70 Місяць тому +1

    Nkhani yavuta apa ndikuchoka kwa Kabambe ku DPP kkkk

  • @MarginJullius
    @MarginJullius Місяць тому

    Ati ngt mukufuna kundimanga kuzela mwa pepe kale😅😅😅

  • @yassinn5634
    @yassinn5634 Місяць тому +1

    Zomati muzachita involve akubanja nchifukwa chake zipani m Malawi muno zimakhala zakubanja chifukwa chakuganiza mombwambwana ngati mmene akuchitira akuluwamu. Muziona zipani zinazi maina ake ndiomwe omwewo chiyambire chipani akuti amuyaya azisithana okhaokha mpaka malire imfa ndiye zidzalowe zidzukulu kapena Ana. Nanga kumangomva Muthalika,Muluzi, Chihana kuti ena alibe nzeru koma mabanja atutu okha basi.Mary Chilima sanali wandale ayi koma mauna wake.

    • @TroubleMuthala
      @TroubleMuthala Місяць тому +1

      Kkkkk Chichewa chikuchita kukuvuta, sorry kabambe ndiye akutsogolela mdipiti umeneu

    • @charleshenderson70
      @charleshenderson70 Місяць тому

      @@TroubleMuthala muuuze aixe kalindo watumidwa izi kkkk nkhani yavuta apa ndikuchoka kwa Kabambe

  • @RamadanShafisha
    @RamadanShafisha Місяць тому

    Mulibe fundo inu muchita manyazi kkkkk

  • @KamangaEdlebert
    @KamangaEdlebert Місяць тому +1

    Akulakhura zaiye

  • @MaxWell-d7o
    @MaxWell-d7o Місяць тому

    Bambo anyooo😂

  • @AliWadi-f2r
    @AliWadi-f2r Місяць тому

    Auze

  • @KondwaniNdobvie-f4v
    @KondwaniNdobvie-f4v Місяць тому

    Mbambande

  • @JamesMunthali-r6l
    @JamesMunthali-r6l Місяць тому

    Booooon kalindoooooo

  • @ChikupizgaKajawaMkandawire
    @ChikupizgaKajawaMkandawire Місяць тому

    Awa akazatopa azatiuza

  • @AndrewMumba-yu5gn
    @AndrewMumba-yu5gn Місяць тому

    Palimpopoo!!😆😆

  • @user-hh4wn4vf9e
    @user-hh4wn4vf9e Місяць тому

    ❤❤ DC

  • @LoveNcity-h8t
    @LoveNcity-h8t Місяць тому

    Zoona

  • @user-ml2vw1dc9c
    @user-ml2vw1dc9c Місяць тому

    Wamisala uyu