Chakwera bravo to u . you really know where to fix the button .zinazo Zangovuta chabe but still little u will change the country for the better.Gud luck Mr Mumba
Congrats Hon. Mumba tiyeni tisiye ndale apo koma tinene zoonadi zenizeni ndi mwano yachita company yo potsekula pomwe inatsekedwa...abale athu akuzunzika kwambiritu omwe akugwira ntchito ku ma kampane
No need for dialogue with these people investors are supposed to employ malawians in all positions these chinese bring their own people make them supervisors and treat our young boys like slaves
Ndpo ngati akuchita iziii kamba ka zisankho nde wauponda chifukwa 90% ya amalawi si achikangawa koma Adad, koma ungopanga izi chifikwa chakukonda amalawi ..amalawiso azakukonda heavy..ndkukupatsa udindo umenewu titamuchotsa chikangawa nditi ana takee😮😮😮
Kutseka ndikutsekulaso ndi mwano wawukulu Ndipo ndikufuna kuyesana olo ndili ine nduna eeee sinkadakondwa nazo Ndipo anthu awawa Ali ndi ena Ake kumbuyo kwawo amene Adayamba nawo kale kupanga za usili amawapatsa ndalama kuti apitilize usilu wawowo mukumbukire nkhani ya ma thin papers imangothera mu mazilatu ndichifukwa chake sakufuna kulemekeza Malawi komaso malamulo Ake koma tsopano I think nthawi yakwana awone kusintha if we are to make Malawi very independent we must stop prays these guys and be brave because they take advantage on our cowered behaviour so Viva Mumba Viva son of Malawi.
What a nonsensical comment. Ralph Kasambara was so corrupt to the core and he is a northerner. In fact, 90% of the cash gate list of 2012-2013 if full of people from northern region. Stop it!
Amalawi ambiri Akhara job less ndie magwiridwe antchito ake amenewa ntchito amalawi azathu zitha,,,,kwa anthu Oona pafupi akhonza kuona kuti vitumbiko agwira bwino ntchito,,, But this will come up with bad result,,,,
Thanks alot Mr Mumba these people are abusing a malawi zikomo minister at last we got someone who can protect us malawians.awonetse mapepala okhalila ku Malawi.Malawi osamaionelera.i with all the best mulungu azikudalitsani amalawi aluzunzika mmakampani kunonso ku jon a Labour ali pa nseu daily
Damn this is long overdue. I mean why are we not protecting Malawians working in these foreign's companies, they don't treat Malawians well , poor working conditions. Makamaka amwenye eeh and the Chinese wtf. We need to clear this mess as soon as possible.
Ku chawezi quarry ogwra ntchto amagona limodz nd mabomba oswera quarry 😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢. Congrats and u shud wait for more tips and dont stop at nothng. Komaso misewu yambr inayambdwa pa kanthaw koma siikutha mutfufuzlekoso kt vuto nd chan ku cr20 ku. Eetu honorable minister. Osaphethra and osaopa 🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉
That's wow ndimadziwa kuti mmodzi yekha wa serious apezeka nanga mpaka mcp yonse basi uyu ndiye wawina mitima ya anthu or boma litasintha they'll still need this serious person usati kumangoti pitani mukaone mundiuza😢
Ypoooh inde Tamva amukonza Malawi komatu akhale ndikutholita athuo ndi ulemu osati like this AI sizoona ayamba ndimoto sizoona aiiii yoooo to this point mkazi wamwini kaya ndinene kuti chani or mlongowake azimulakhula kuchita kumata like that yoooo aiiii apple Moto walawilila tchito ikadalipo yoooooo akamatha 5month manga angati yoooo mwaunako manganya akufika apo mopanda ulemu aiiii aiiii sizoona
Koma I think maiwo eish mpaka amafuna atenge phone ya anduna m'manja mwawo? Eish ai sizinayendetu, apapa nzoona kuti andunawo athadi kukwiya...mesa bwenzi atapepesa?
Tikazasintha boma munthu uyu azagwirebe ntchito pa udindo womweo. This is great man ndakunyadirani man
Abwana inenso ndikuona chimodzimodzi
Ineso ndikuona kuti adzagwireso nthito imeyo this is great guy
Exactly
He is a businessman remember that he is just creating space for himself and his friends komabe this is good angochidwa dyera
Me too I do like him ,azagwile tchito ndi adadi next year this man good
Minister ndiyemweyu tingosintha Head of State
Man wonderful i agree with you💯
Limbikira tikutenga ku boma linalo phwanga. Mbuyanu amasekelera zopusa koma iwe suli chom'cho, very good very good😊😊😊😊😊😊😊😊😊
Great job Honorable Vitumbiko Mumba.....
His excellency that is what we call a Leadership vitumbiko ❤❤❤❤❤❤He has done this because he loves Malawi
Nanga atsogoleri anthu nzeru izi zinali kuti? Kunjaku ndimomwe amalawi timazionelatu. Sungaphyanye malamulo mu dziko la eni. Anthuwa akujaila kwambiri. Big up Vitumbiko 💪🏿💪🏿
😊
Iwo koma kunyenga bas
leader ship
Chikhala tinali ndi atsogoleri onga ngati awa 10 ndiye kut taiphula koma ma minister enawa zitsilu zen zen mumba more fire 🔥 🔥🔥
Bwezi palibeso akutiyankhula za nyama aaaa
May aimightly God bless you and protect you Mr Mumba you have done good and that good ministry
Exactly that's the caliber of ministers we need ❤
Bola Inu mumanvana nd ma ministry anu amakunvani koma kuno k Mozambique eeeeeeeeeeeeeee ataa zativuta bass
Minister ndiye mweyu tingozintha tate
Great job boss.keep it up.we are suffering out here coz of job condition ya Malawi..
Ndipo ku MCP kuja kukanakhala anthu adziwa ntchito ngati uyu bwenz Malawi Ali bwino heavy.
Am with u Vitu, great Job sir
Ndipo kwambiri bro
Thus great we need such people in all government position. Minister azigwira ntchito, osati kumangoganiza zakuba, kupha bas.
Great Job sir,keep it up ,anthu amenewa amatenga anthu akuda ngati akapolo
Mutumbuka wakuteta Yai , Always trueth keep up brother
Continue bwana.. Ma minister azikhala andalama zao kut tizipewa chinyengo. The guy has his own money sangatengeke ndika 10m
Bravo a minister.pitilizani muwasake anthu amenewo.mupitenso ma company mbali ya kukanengo uku.
Chakwera bravo to u . you really know where to fix the button .zinazo Zangovuta chabe but still little u will change the country for the better.Gud luck Mr Mumba
Aaaaa iwenso kt chakwera? Chakwera wakenso uti
Pamtumbo pako limodzi ndi Chakwera wako yemweyo
❤❤ tixamupasaso unduna ngati womweu or boma titasitha
Boma silisintha koma chipani
Very Good Honarable mumba continue
Excellent Minister that's why we need young powerful people to take over from old and retired people.
Pakayenda bwino tiziyamikira ndithu we are appreciate to u Mr Mumba well done anthu asalandire ndrama zonyenyeka yet they are working had
Uyuu Sagamudyetsa dollar Ali ndi cash yake yake
Great Job,well done Sir
Patriotic don't change ur mind coz of ur politics frnds malawian want people like u God bless u all the tym
These are the kind of leaders we need!!!
Big up minister.
Good job Mumba shame uli ku MCP iweyo ndi Kabambe can change this country
Congrats Hon. Mumba tiyeni tisiye ndale apo koma tinene zoonadi zenizeni ndi mwano yachita company yo potsekula pomwe inatsekedwa...abale athu akuzunzika kwambiritu omwe akugwira ntchito ku ma kampane
.... that's the kind of leaders we need nice move minister👍
Well done pliz continue yenderaninso ma compony a security ambiri akuzunzika ndithu
Zilibwino a Michael Usi aphunzitsa nduna kugwira ntchito moyenera.
Well done our minister, this is how we can change our beautiful Malawi.
Tingositha president nduna ndiyomweyi 🎉🎉🎉🎉🎉 I love you brother mwana wapakaya
Great job honorable 🔥
Well done job boss asakusokonezeni gwirani chito yanu
Sitikuti anthu asiye kusata malamulo ayi lamulo ndilofunika koma pakufunika ulemu pakuyankhula ndi anthu amene alakwa tisatenge kuti ndine nduna ndiye ndili ndizeru ayi kumeneko ndikupepera. Ziko lathu mwabweresa umphawi wadaladala ndiye mukapanda kuganiza ndikupupuluma ndi unduna muzapangisa anthu ene pamene amapeza muchere avutike
Lamulo liposa mphamvu, akuluakulu a company amayenera kumvera lamulo loti atseke company, koma iwo anazimva ndalama kwambiri nkusatseka ma office, ndye munthu asekelele zimenezo? Anduna pitilizani ntchito yanu, nchifukwa chakenso ma foreigner wa amatitola ife a Malawi.
Mutumbuka nthawi zose ndi 1😂😂😂❤❤❤ mwachita makola apo bwana mumba❤❤❤❤
Bwana ma minister onse akanamatero,even ziphuphu zikanatha,bwana you deserve to be congratulated
True
This is how ministers have to work. Osamangopanga ma plan okuba misonkho mma office mu. Great work Honourable Mumba
Remember these are investors in the country. Dialogue is the best solution and not arrests.
No need for dialogue with these people investors are supposed to employ malawians in all positions these chinese bring their own people make them supervisors and treat our young boys like slaves
❤❤❤ Mr vitumbiko pitilizan operation imeneyo coz athu ambili akuvutira dziko lokhala lathu lomwe amwenyewaso akupanga katundu emwe athu akusokoneza ukhondo wadziko ...mwachitsanzo Ku limbe kwajussab c kumaonekaso ngt nditown ai kwangolowa chipolowe
Mwamuona mzimayi ndimomwe zimakhalira kubosa chilungamo. Komaso kubisa chilungamo ama gwiridwe antchito ma company ama Chines kusiyana ndi ma lamulo aboma. Aminister pitilizani chito yanu ya bwino muku gwirayo Achakwera mukapeza munthu wokuthandizani weniweni Achakwera Boma ❤❤🎉
The grabbing of the lady though eeh.
It's a great initiative koma, especially it will improve working conditions.
Anakakhala mwenye sanakamugwila like that
@EmmanuelMatchado True. She even complained about it but was quickly shut down.
@@Zack-27 zilibe kanthu kuti he is minister...and anakayenela kudziwa kut nkaziyo atha kukhala kuti ali pa banja
Nice and recomandeble presentation, carry on
Yes. Tikufuna anthu okonda dziko kawo ngati a bwana Mumba. Bravo
That’s the to go Honourable minister continue doing that I salute you .
Well done mumba mwina ena atengerepo phunzilo mmakampanimu anthu amazunzika
He must be forever in that position
Thumb up minister
Koma abale Kodi zaka zonsezi munali kutiko anthu ambili mbili anataya miyoyo yawo kusowa owaimilila ngati inu iyayi tingoti mulungu akusogoleleni anduna kuti mupitilize mchito yomwe mwayiyambiyi ndiye poti amalawi timadana ndichilungamo basi ambuye yekha akudaliseni ❤❤❤
Amadikila zisankho ziyandikire kaye
Ndpo ngati akuchita iziii kamba ka zisankho nde wauponda chifukwa 90% ya amalawi si achikangawa koma Adad, koma ungopanga izi chifikwa chakukonda amalawi ..amalawiso azakukonda heavy..ndkukupatsa udindo umenewu titamuchotsa chikangawa nditi ana takee😮😮😮
Good work wolemekezeka, go ahead with the operation pls, amwenyewa ndi ma Chinese wa akutizunza kwambiri amalawife
I like this energy
Kutseka ndikutsekulaso ndi mwano wawukulu Ndipo ndikufuna kuyesana olo ndili ine nduna eeee sinkadakondwa nazo Ndipo anthu awawa Ali ndi ena Ake kumbuyo kwawo amene Adayamba nawo kale kupanga za usili amawapatsa ndalama kuti apitilize usilu wawowo mukumbukire nkhani ya ma thin papers imangothera mu mazilatu ndichifukwa chake sakufuna kulemekeza Malawi komaso malamulo Ake koma tsopano I think nthawi yakwana awone kusintha if we are to make Malawi very independent we must stop prays these guys and be brave because they take advantage on our cowered behaviour so Viva Mumba Viva son of Malawi.
Fantastic minister izitelo continue nice work
Good job mr mumba tathirani zipolopolo agalu akuuwawa hiyaaa we are citizens of Malawi 🇲🇼 ndie wina asatidzuze ai tili ndi njala ya chichele 😂😂😂
Mwano,kuderera or chani?
We need people like Mumba Vitumbiko in this country tikasintha Boma pa September pano this guy remains the same position ndanena ndanena
Minister of the moment he deserve an award
Viva Vitumbiko zinakati zizitelo bwezi Malawi ali patali
That is all I know about people from northern region
We don't need corruption. Keep on big man
What a nonsensical comment. Ralph Kasambara was so corrupt to the core and he is a northerner. In fact, 90% of the cash gate list of 2012-2013 if full of people from northern region. Stop it!
Amalawi ambiri Akhara job less ndie magwiridwe antchito ake amenewa ntchito amalawi azathu zitha,,,,kwa anthu Oona pafupi akhonza kuona kuti vitumbiko agwira bwino ntchito,,, But this will come up with bad result,,,,
Exactly,akanawapatsa timeline kuti akonze zinthu osangofikila kutseka apapa ogwira ntchito avutika
Chamba cha ku Jamaica chinja osazachiphwekesa bravo mr minister
Thanks alot Mr Mumba these people are abusing a malawi zikomo minister at last we got someone who can protect us malawians.awonetse mapepala okhalila ku Malawi.Malawi osamaionelera.i with all the best mulungu azikudalitsani amalawi aluzunzika mmakampani kunonso ku jon a Labour ali pa nseu daily
Uyu apweteka guru eeeeesh 🔥🔥😅😅
Thus good job akufunika atabwelaso komwe tikugwila ntchito ifeyo
Great job mr
Never give up! I will support you here in exile
Please can you visit LBL at njerwa
Mmm mwapeza sizilobwino nde amagotseka company mmesa muwapatse nthawi yokodza kenako akalephela nde kutseka..... Nanga ogwila ntchito azitani
Great job amalawi amatitola kwabas 😅😅😅
Good job i support it
Koma vitumbiko simunthu wamba ukundie kukonda zikolako vitu ♥️♥️♥️♥️
Good job sir ,,kwatsala amwenye
Uyu wabwera 💥💥💥 🔥🔥🔥🔥🔥
big up hon minster
Good start bwana Mumba,bola osatopa,osafooka
EYA TIKUFUNA ANTHU NGATI AWAWO...PATAKHALADI CABINET MINISTERS YAMPHAMVU YOTUKULA DZIKOLI NGATI M' MENE DZIKOLI LINKUFUNIKIRA. NDIPO TIYENI A MALAWI ...ALENDO ASATIPONDEREZE !! VIVA MALAWI 🇲🇼 VIVA DR LAZARUS CHAKWERA VIVA MCP 💕 🙏💺 ZACHIBYINGOZI ZIKUNYANYA MAKA NDI MAKAMOANI YA ACHILENDO..👍💪🙏
EYA Asazolowere Amalawi uyika KUMBUYO wotipondereza NGATI ma Company alendi NGATI AWAWO.. VIVA HON. VITUMBIKO AZ MUNBA... VIVA MCP 🇲🇼 VIVA MALAWI... VIVA A RIGHT PRESIDENT DR LAZARUS M CHAKWERA VIVA. MZOTIKUFUN.. ZAZIBWANAZO AYI... VZAKUTETE YAYEI... MWANA WAKWITHO !! 💺👍💪🙏 PRAYERS
That's great job..
Sir mumba pakanakhala maminister angapo onesa action osati kumangosewera pa what's app mumaoffece nd bwenzi ziko lili labwino
Mkazi Wavala za red kuderera chonchi bwanji?? Asa..... kuzimva sugar chonchi iyeyi bwanji??? Kuderera directive ya Minister ngati mamunache choncho?
Damn this is long overdue. I mean why are we not protecting Malawians working in these foreign's companies, they don't treat Malawians well , poor working conditions. Makamaka amwenye eeh and the Chinese wtf. We need to clear this mess as soon as possible.
Well done ndipo mupange check ma company onse country wide
Yaa that's good move komanso tikayiwonesetsa nkhaniyi nditha kupezapo zinthu ziwili mwina ma chines sakusonkha so let's wait and see
Ku chawezi quarry ogwra ntchto amagona limodz nd mabomba oswera quarry 😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢. Congrats and u shud wait for more tips and dont stop at nothng. Komaso misewu yambr inayambdwa pa kanthaw koma siikutha mutfufuzlekoso kt vuto nd chan ku cr20 ku. Eetu honorable minister. Osaphethra and osaopa 🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉
Wasaya Moto bwana minister😂😂😂😂🙌🔥great job
Good start Mr Minister
That's wow ndimadziwa kuti mmodzi yekha wa serious apezeka nanga mpaka mcp yonse basi uyu ndiye wawina mitima ya anthu or boma litasintha they'll still need this serious person usati kumangoti pitani mukaone mundiuza😢
You are great man
Ypoooh inde Tamva amukonza Malawi komatu akhale ndikutholita athuo ndi ulemu osati like this AI sizoona ayamba ndimoto sizoona aiiii yoooo to this point mkazi wamwini kaya ndinene kuti chani or mlongowake azimulakhula kuchita kumata like that yoooo aiiii apple Moto walawilila tchito ikadalipo yoooooo akamatha 5month manga angati yoooo mwaunako manganya akufika apo mopanda ulemu aiiii aiiii sizoona
Keep it up honorable mumba God bless you so much
Let evil not defest us but we need to defeat it
Romans 12:21
The best minister performer in MG now we need more of such ministers in this country
One of great men that the country need. Keep it up Minister, not these other greedy ministers
Zisiru zimenezi azichita bwino zimvekere ziko ndi wanu ndalama ndi zathu good job Mr mumba
Koma I think maiwo eish mpaka amafuna atenge phone ya anduna m'manja mwawo? Eish ai sizinayendetu, apapa nzoona kuti andunawo athadi kukwiya...mesa bwenzi atapepesa?
Fire moto 🔥 unandiiii mumba vtumbko!!!
Big up minister good work carry on
Kumeneko ndikupusa iye aku wona ngati ogwira ntchitowo akondwa?
Bwana vitu congrats .tikufuna ma minister achinyamata ajacup
Great job minister
Good job minster (koma osamagwira mabele akazi ayiniake )
Azimai awawa amanyegedwa ndima China omwewo
😂😂😂ndipo zoona
Amalawi alipo ambiri odziwa ntchito Mr president mwamuona Vitumbiko Mumba kuti mwasayina player wabwino? Ngati nkotheka timafuna former MEC chairman Chifundo Kachale akhalenso mu cabinet yanu (munthuyi amadziwa kugwira ntchito NO corruption)
Big up Mr Vitumbiko
Bravo minister ,am not mcp but this is not abt politics but reality
Under wise and dynamic leadership of Lazarus Mcarthy chakwera Boma ndilomweli