Life is a mockery to many civil servants not forgetting the likes mentioned in this song.....How I miss musicians that raise a staccato of real life issues.......Go further Joseph🇿🇲🇿🇲🇿🇲🇿🇲🙏
Nkasa your the best singer in Malawi because you're always transpire the truth you're really Phungu indeed. All of your songs got powerful massage and you don't care who gonna hate you but truth Must be open, God may bless you more your number 1.
Uyu ndioyimba waluso loopsa zedi yemwe oimba aliyense Ku Malawiko alibe, Ali ndiluso laganiza koopsa kupeka nyimbo size Ku Malawi imakana alibeyi zake n amaima ndikudzudzula osaopa aliyense Koma bola amenenye nkhondo Ndipo uthengawo Kuboma ukafike Kaya Adana nawo. Uyu ndi phungu wa Amphawidi zedi mmmmm
ndipo kudzakhala zivomezi zazikulu, ndi njala ndi miliri m'malo akutiakuti, ndipo kudzakhala zoopsa ndi zizindikiro zazikulu zakumwamba. LUKA 21:11 Ndipo pomwepo ambiri adzakhumudwa, nadzaperekana wina ndi mnzake, nadzadana wina ndi mnzake. Ndipo aneneri onama ambiri adzauka, nadzasokeretsa anthu ambiri. Ndipo chifukwa cha kuchuluka kwa kusaweruzika, chikondano cha anthu aunyinji chidzazilala. Koma iye wakulimbika chilimbikire kufikira kuchimaliziro, yemweyo adzapulumuka. Ndipo Uthenga uwu Wabwino wa Ufumu udzalalikidwa padziko lonse lapansi, ukhale mboni kwa anthu a mitundu yonse; ndipo pomwepo chidzafika chimaliziro. pakuti pomwepo padzakhala masauko aakulu, monga sipadakhale otero kuyambira chiyambi cha dziko, kufikira tsopano, inde ndipo sipadzakhalanso. Ndipo akadaleka kufupikitsidwa masiku awo, sakadapulumuka munthu aliyense: koma chifukwa cha osankhidwawo masiku awo adzafupikitsidwa. Pomwepo munthu akanena kwa inu, Onani, Khristu ali kuno, kapena uko musamvomereze; chifukwa Akhristu onama adzauka, ndi aneneri onama nadzaonetsa zizindikiro zazikulu ndi zozizwa: kotero kuti akanyenge, ngati nkotheka, osankhidwa omwe. Onani ndakuuziranitu pasadafike. Onani, Iye ali m'chipululu; musamukeko. Onani, ali m'zipinda; musavomereze. Pakuti monga mphezi idzera kum'mawa, nionekera kufikira kumadzulo; kotero kudzakhalanso kufika kwake kwa Mwana wa Munthu . Koma pomwepo, atapita masauko a masiku awo, dzuwa lidzadetsedwa, ndi mwezi sudzaonetsa kuwala kwake, ndi nyenyezi zidzagwa kuchokera kumwamba, ndi mphamvu za kumwamba zidzagwedezeka: ndipo pomwepo padzaoneka m'thambo chizindikiro cha Mwana wa Munthu; ndipo mitundu yonse ya padziko lapansi idzadziguguda pachifuwa, nidzapenya Mwana wa Munthu alinkudza pa mitambo ya kumwamba, ndi mphamvu ndi ulemerero waukulu. Ndipo Iye adzatumiza angelo ake ndi kulira kwakukulu kwa lipenga, ndipo iwo adzasonkhanitsa osankhidwa ake kumphepo zinai, kuyambira malekezero a thambo kufikira malekezero ake ena. Thambo ndi dziko lapansi zidzachoka, koma mau anga sadzachoka ai. Koma za tsiku ili ndi nthawi yake saidziwa munthu aliyense, angakhale angelo a Kumwamba, kapena Mwana, koma Atate yekha. Ndipo monga masiku a Nowa, kotero kudzakhala kufika kwake kwa Mwana wa Munthu. Pakuti monga m'masiku aja, chisanafike chigumula, anthu analinkudya ndi kumwa, analikukwatira ndi kukwatiwa, kufikira tsiku limene Nowa analowa m'chingalawa, ndipo iwo sanadziwe kanthu, kufikira kumene chigumula chinadza, chinapululutsa iwo onse, kotero kudzakhala kufika kwake kwa Mwana wa Munthu. MATEYU 24:10-14, 21-24, 26-27, 29-31, 35-39
Phungu Where were u befor to sing this nice song... The same things is happening here in Capetown thus why police are after people always so they may find there needs.. Thanks for u song hope our country will do something good for Police now.. Help Malawian teachers now with another song.. Ndine John From Tukombo Nkhata-Bay... but im not there.....
8 years down and I'm still on it. Sending some Flowers to Joseph in 2024
Ndipo amakamba chilungamo ndithu, ulemu wanu Mr Joseph Nkasa
Nyimbo imandisangalatsa ndimaonera Kuti ndione Mene anamangira tie bambo Nkasa ndimene a police amatichitira mu video iyiyi. Uthenga top notch 😉
😂😂😂
Nkasa is so creative and very talented. His music is always educative and life's real issue. Nkasa is doing what he was born for
He is a mature and intelligent man🎉❤
Sakukondwe mpaka lero good mwawanenela ndithu
Life is a mockery to many civil servants not forgetting the likes mentioned in this song.....How I miss musicians that raise a staccato of real life issues.......Go further Joseph🇿🇲🇿🇲🇿🇲🇿🇲🙏
Nyimbo iyi imakhudza mtima wanga❤
Big Man timakunyadirani kwambiri, nyimbo zanu nkhani zake zimakhala zothinana bwino Inu Ndi 1 pakusanja Mfundo
The man is just great, a song with nothing but just peaceful pure advocating message for men in uniform
Nkasa, billy, really enterterned us in our childhood. Legends
Who is here 2024❤❤❤
What great you are Joseph pointing the fresh not at the bone.Much love from Zambia 2021
🎉❤ truth ward s though Joseph voice respect to you dadah
The song just match to many countries it’s not only malawi well spoken big
wow woooooooooooooooo, Nyimbo adaimba bwinooooo iyi................. big up Mr. Joseph Mkasa
Yeah man he really did a good job.
2023 still enjoying the song,from Zowo the Northern part of Malawi.Mwana wapajiya, kip the fire burning 🔥🔥🔥 umatifilisa Mkasa 👍
This massage covers the plight of most African country's police force and public servants in general. Great song.
Nkasa your the best singer in Malawi because you're always transpire the truth you're really Phungu indeed. All of your songs got powerful massage and you don't care who gonna hate you but truth Must be open, God may bless you more your number 1.
Nkasa
apolice amuyamikire phungu.wawamenyera nkhondo.
Joseph! You are a 'Phungu' for real. Good song with a very powerful message
Uyu ndioyimba waluso loopsa zedi yemwe oimba aliyense Ku Malawiko alibe, Ali ndiluso laganiza koopsa kupeka nyimbo size Ku Malawi imakana alibeyi zake n amaima ndikudzudzula osaopa aliyense Koma bola amenenye nkhondo Ndipo uthengawo Kuboma ukafike Kaya Adana nawo. Uyu ndi phungu wa Amphawidi zedi mmmmm
I listened to this song 1000 *
Zoona alipilidwe, mkwana lm Dominic Mwaphashi
This man is very creative 🤩
Big up Mkasa Anenere its true song from zika ya ku Malawi
mmmmmmmmhhhhhh.......nikabwino aka kanyimbo nditu...iyayi pitilizani a josefe.
Kkkkk is a best musician in malawi kk
The fighter of development, ,many thanks to you big
ndipo kudzakhala zivomezi zazikulu, ndi njala ndi miliri m'malo akutiakuti, ndipo kudzakhala zoopsa ndi zizindikiro zazikulu zakumwamba.
LUKA 21:11 Ndipo pomwepo ambiri adzakhumudwa, nadzaperekana wina ndi mnzake, nadzadana wina ndi mnzake. Ndipo aneneri onama ambiri adzauka, nadzasokeretsa anthu ambiri. Ndipo chifukwa cha kuchuluka kwa kusaweruzika, chikondano cha anthu aunyinji chidzazilala. Koma iye wakulimbika chilimbikire kufikira kuchimaliziro, yemweyo adzapulumuka. Ndipo Uthenga uwu Wabwino wa Ufumu udzalalikidwa padziko lonse lapansi, ukhale mboni kwa anthu a mitundu yonse; ndipo pomwepo chidzafika chimaliziro. pakuti pomwepo padzakhala masauko aakulu, monga sipadakhale otero kuyambira chiyambi cha dziko, kufikira tsopano, inde ndipo sipadzakhalanso. Ndipo akadaleka kufupikitsidwa masiku awo, sakadapulumuka munthu aliyense: koma chifukwa cha osankhidwawo masiku awo adzafupikitsidwa. Pomwepo munthu akanena kwa inu, Onani, Khristu ali kuno, kapena uko musamvomereze; chifukwa Akhristu onama adzauka, ndi aneneri onama nadzaonetsa zizindikiro zazikulu ndi zozizwa: kotero kuti akanyenge, ngati nkotheka, osankhidwa omwe. Onani ndakuuziranitu pasadafike. Onani, Iye ali m'chipululu; musamukeko. Onani, ali m'zipinda; musavomereze. Pakuti monga mphezi idzera kum'mawa, nionekera kufikira kumadzulo; kotero kudzakhalanso kufika kwake kwa Mwana wa Munthu . Koma pomwepo, atapita masauko a masiku awo, dzuwa lidzadetsedwa, ndi mwezi sudzaonetsa kuwala kwake, ndi nyenyezi zidzagwa kuchokera kumwamba, ndi mphamvu za kumwamba zidzagwedezeka: ndipo pomwepo padzaoneka m'thambo chizindikiro cha Mwana wa Munthu; ndipo mitundu yonse ya padziko lapansi idzadziguguda pachifuwa, nidzapenya Mwana wa Munthu alinkudza pa mitambo ya kumwamba, ndi mphamvu ndi ulemerero waukulu. Ndipo Iye adzatumiza angelo ake ndi kulira kwakukulu kwa lipenga, ndipo iwo adzasonkhanitsa osankhidwa ake kumphepo zinai, kuyambira malekezero a thambo kufikira malekezero ake ena. Thambo ndi dziko lapansi zidzachoka, koma mau anga sadzachoka ai. Koma za tsiku ili ndi nthawi yake saidziwa munthu aliyense, angakhale angelo a Kumwamba, kapena Mwana, koma Atate yekha. Ndipo monga masiku a Nowa, kotero kudzakhala kufika kwake kwa Mwana wa Munthu. Pakuti monga m'masiku aja, chisanafike chigumula, anthu analinkudya ndi kumwa, analikukwatira ndi kukwatiwa, kufikira tsiku limene Nowa analowa m'chingalawa, ndipo iwo sanadziwe kanthu, kufikira kumene chigumula chinadza, chinapululutsa iwo onse, kotero kudzakhala kufika kwake kwa Mwana wa Munthu.
MATEYU 24:10-14, 21-24, 26-27, 29-31, 35-39
Phungu Where were u befor to sing this nice song... The same things is happening here in Capetown thus why police are after people always so they may find there needs.. Thanks for u song hope our country will do something good for Police now.. Help Malawian teachers now with another song.. Ndine John From Tukombo Nkhata-Bay... but im not there.....
inu ndi amuna onena zoona koma kwinaku kupanga ndalama ine ndinakupasani ulemu pamene mkakumbusa galimoto lanu kumbuyoko aaaa nice songs bwana
Much love from Zambia 2021
The sad part of it, the Polise have failed to appreciate the efforts by the citizens. We end up to be victims of Polise attrocities
Mkasa you nailed
Apolice anthu omwe ukuvitika koopsa pa Malawi ilike this song trues God
Legend ♥️
Joseph nkasa na amuna kwabasi akukana ndi muntu
zoona,sakukondwadi koma kuti ayankhule Amati ndie kuti aukila boma kkkkk nice song Fumwe!hamunaname anta!
Perfectly said and it's true l
NICE songs and we get nice ideas
Lol koma Phungo sudzathekaxo maka manyumba mmm akananganizilako
Nice song zoona
Very good zoona zokhazokha idzi 😢😢😢😢
2024 still apolisi sakukondwa koma kugwiritsidwa ntchito pomanga odananawo, imagine till now apolisi kumavala jombo yobowoka and old uniform 😢
If this song was in English! Forsure nkhasa could be praysed by most police officers
Totally true Sister ndipo he was going to make more money through the viewers + well wishers
MKASA UMATHAAAAAAAAAAA KOMA UNANGOLAKWA KUKAKAMIRA ZANDALE,PANYIMBO ZOMWE UMAYIMBA M'MBUYOMU NDIZOMWE ZIMANDIGWIRA MTIMA KUSIYANA NDIZATSOPONOZI.
Kkkkk Kkkk koma nkasa kuvinako nde umandisangalatsa, nice one! !
Ndipo amavina za smart
Nakuno ku Zambia you spoke on behalf of them.
Remember we are 1 people, when I see zambian people l always feel happy knowing we are brothers and sisters.
Praise to you phungu teach us
God bless you. Real issues. Zambia
Mumalawi wolikondadi ziko lake.🔥🔥
Good message and well delivered..
Mafumu enieni🔥🔥🔥🔥
Phungu ndi katundu weniweni,welll well Phungu
Nyimbo zayadidi
mwalakhulatu chilungamo bwana nkasa (phungu)
Nice song kp it up phungu
This man has powerful lyrics. His trademark
You are the heroes and the warrior Mr nkasa
uphungu wanu pitilizani,nice song
Nkasa is a legend,and he deserves flowers b4 he dies
Bravo nkasa
Nkasa ndi dolo keep it up
Powerful msg
Many thanks to you Mkasa
Nkasa yaaaaa. Good
Machine ❤
Most of the houses our police live in were built by the British rule long time ago since that time there's no government that can all these structures
True
This song is so touching,am a son of a Malawian man stays in zambia
Mudayesetsa kuwanenera
mmm komandiye eh apadi payenera kukozedwa
Long life mkasa
Sangakondwere nayo
By only this song wow😅😅😅😅😅
Great song full of real issues
Nyimbo sinkhani koma kuvina ayi
Best nkasa
Glory to God. Zoona
do u have the maloto nkasa song
Number one
Joseph nkasa landira ulemu wako
Wow so nyc music
Robert a
Anthu osamuuzako kuti akonze neck tieyo bwa?
Kkkkkkk
One nkasa
That's true NYC songs
Joseph nkasa wise music
Fantastic song
Phungu aziwoneka kumenya nkhodo ya anthu ena
Wanena zoona
zoonadi Mr mkasa
Zowona mkasa!
ndakaika
hahajaja I miss Malawi!!!
typical of him, always fighting for the truth .
chilungamo nd I chabwino
Fact
Mkasa
nyc vd
Zimbabwe
❤❤❤❤
cholungamo big
Nice song
Bhoo