Deputy Speaker wakalipa! Muziyankhula chizungu tioneseni kuti Mumatha chizungu

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 1 лис 2024

КОМЕНТАРІ • 78

  • @AbudulJohn
    @AbudulJohn 2 місяці тому +12

    Kodi opita ku school siawo akulephela kuyendesa dzikowo iyeyo sakuwawona school ndi kuganiza ziwili zosiyana munthu atha kukhala kuti sanapite ku school koma ndi wa mzelu kuposaso anapita ku school wo

    • @actuarialscience2283
      @actuarialscience2283 2 місяці тому

      Chakwera siophunzira. Munthu wa theology ndi osaphunzira. Ali ngati khoma la tcharitchi. Khoma la tcharitchi limamva baibulo likuwerengedwa daily koma losaphunzira.

    • @actuarialscience2283
      @actuarialscience2283 2 місяці тому

      Peter anali ophunzira ndipo amayendetsa bwino. Bingu ophunzira amayendetsa bwino. Koma Bakili/Chakwera/Joice anali osaphunzira ndipo dziko linawacheka.

  • @SolomonNjolomole
    @SolomonNjolomole 2 місяці тому +6

    Chikhala kuti kulankhula chingelezi kuli ndi phindu bwezi malawi atalemera ndi achakwera km ndi 0/10 matama thoo nzeru mayazi.

  • @JustineKhoviwa
    @JustineKhoviwa 2 місяці тому

    Iyeyo ndiye achitha chingerezicho. Kumangoti a speaker achani usavi

  • @PatrickMangochi
    @PatrickMangochi 2 місяці тому

    English is a must in Parliament because we depend on donors so they have to hear what they are discussing.if not then allow anyone to contest as Mp regardless of his/her education background.the truth is that a number of our Mps cannot speak English,I have a good example our former Mp Bon Kalindo

  • @SammyPhiri-r9r
    @SammyPhiri-r9r 2 місяці тому

    The speaker was right to emphasize on that point, members shld speak English not chichewa.

  • @junaidibrahimishaaq
    @junaidibrahimishaaq 2 місяці тому +5

    Ku Parliament ya ku Tanzania amalankhula Swahili, osati zozigwira ukapolozi

  • @giftnyirongo-ey3qy
    @giftnyirongo-ey3qy 2 місяці тому +4

    Qualification ya Member of Parliament ndi MSCE

    • @yusuflifa2923
      @yusuflifa2923 2 місяці тому

      Starting from PSLCE, JCE going above

  • @FrancisChiwayabanda
    @FrancisChiwayabanda 2 місяці тому +1

    Ma guys chaka cha mawachi ine ndikangotenga mpando wa u mp dela la kwathu ndikasitha zimenezo ndipo nyumbayi iyiyo iyi ya malamuloyi izizalankhula chichewa fine ine monga francis chiwaya mp ndikathesa mwano umenewo ndipo dj nyimbo ikhale dani lu lozani zanu ndili paselipa

  • @tracybennie7783
    @tracybennie7783 Місяць тому

    Agalu. Awa. Kuno. Kumalawi. Timayakhula. Chichewa. Kumalawi. Awa. Chilipo. Akubisa. Chilima. Anamutani

  • @GiftNkhoma-n2w
    @GiftNkhoma-n2w 2 місяці тому

    Nkhan ndi yakuti kufuna kumatinamiza kwambir ka amadziwa kuti timva ambir zopusa zawozo 😅

  • @isaihmagani5697
    @isaihmagani5697 2 місяці тому

    Kkkkkki ena choncho odolo onse kutheratu, kuonesa udolo pa chichewa pokha achina Namalomba choncho kikkkkkki

  • @ChristopherKhili
    @ChristopherKhili 2 місяці тому

    Uyundiwopepera adyazambiri

  • @hanifahmponda8711
    @hanifahmponda8711 2 місяці тому

    Aaa uyu wa MCP nde ukudziwa kuti amalawi ambili olo apite ku school koma kuyankhula English kumamvuta nde iyi ndinjila yoti kwapasa puma ma MP koma olo ku south Africa amaphatikidza ndichiyankhulo chawo akafuna palibe mulandu ayi nde muwone ma MP ena amatha dzaka 5 otsadzuka kunenapo kuwopa chidzungu awa MCP dzikuwanvuta kuyendetsa dziko la malawi nde apedzelapo pata oti akhadzike chete ma MP akafuna kuyankhula zofuna dzawo adziwopa English koma po vote nyumbayi awafuna kkkk

  • @imranhopewell-yv4zc
    @imranhopewell-yv4zc Місяць тому

    Kodi maiko azathu sayankhula ziyankhulo zao kunyumba ya malamulo a speaker muzitenge bwinotu mwasala ndi myenzi khumi ndi umodzi muchokamo menemo

  • @hackwellkagolo6614
    @hackwellkagolo6614 2 місяці тому

    English ku parliament ili ndi phindu lanji popeza ifeyo aMalawi tafunaso chiyakhulo chathu kuti wina aliyense aziva zomwe Aphungu anthu akuyakhula ku parliament.

  • @McleanChawinga
    @McleanChawinga 2 місяці тому

    Langweji is a midiya ovu communication. Pulizi let us displin it

  • @PATRICKTHlMZY
    @PATRICKTHlMZY 2 місяці тому

    Ndi galu ameneyo osenda a malawi ndiye anthu azichita kufinyika

  • @AlexArmandomasswaganheMasswang
    @AlexArmandomasswaganheMasswang 2 місяці тому

    koma amalaw ndiye tinalozedwa kwabazi this is malawi not USA musakakamize athu kuti ayangure chizungu chimene tikufuna ndi chilungamo atsogo

  • @PabroKadams-q7y
    @PabroKadams-q7y 13 днів тому

    Chakwera mbuzi anthu ake mbuzi,mbuzi mbuzi mbuzi

  • @jameskachulu8141
    @jameskachulu8141 2 місяці тому

    Mayiko ena amayakhula zimene wa funa munthu kuyankhula za kamuzu zimenezo

  • @LenoMvula
    @LenoMvula 2 місяці тому +1

    Akuyesa kt afka kumeneko sazacokako
    Km tsiku ndli mozi likubwera

  • @IBRAHIMCHIPASULA
    @IBRAHIMCHIPASULA 2 місяці тому +2

    Kkkkkkkkk nambo kweleko😂😂😂😂😂

  • @actuarialscience2283
    @actuarialscience2283 2 місяці тому +1

    Awa ndi zitsiru. Malawians ayenera kumva zomwe mbuzi za ku parliament.

  • @KhadijaMsosa-d7z
    @KhadijaMsosa-d7z 2 місяці тому

    Aaa za ziii kumangoyankhula poti ayasama chizungucho chimatipindulira chani

  • @MathewKalinkhu
    @MathewKalinkhu 2 місяці тому

    Si ku Europe kuno, ndiku Africa, ndiye si vuto kulankhula chilankhulo chathu. Ophunzila ndi awa akulephera kuyendetsa dziko.

  • @AbdulsharifulKalipinde-m6u
    @AbdulsharifulKalipinde-m6u 2 місяці тому

    Ndiamene amakakwera njinga ku njawo

  • @RiteRoderick
    @RiteRoderick 2 місяці тому +1

    Awansp ndi Achitsiru bwanji, English ndikuyendesa Dziko zikugwirizana? Bwanji mukulephera kuliyendesa dzikoli anthu chonsecho mukut munapita ku school? Enafetu pa English simungaimepoyi Ndipo simungafikire mutha kuyaluka so osamangoziputayi

  • @blandinabonaventure
    @blandinabonaventure 2 місяці тому +1

    Matama ku malawi kulephera kunyadira chiyakhulo chanu 😅😅

  • @PreviousStanley
    @PreviousStanley 2 місяці тому

    Eya ili ndi phindu chifukwatu olo ena samayankhula Chichewa chomveka ndiye English ndi communication yosavuta tiyeni tivome speaker akunena zoona ndinthu komaso aphunguwo anavomereza onkha Kuti aziyankhula English

  • @Extratremendouszeus
    @Extratremendouszeus 2 місяці тому

    Malawians are not from England....chichewa basi...remember...English is from England

  • @DivineMercy-df2pu
    @DivineMercy-df2pu 2 місяці тому

    Akagwero uko does English put food on the table.

  • @juliussamson6212
    @juliussamson6212 Місяць тому

    MUXIKAYANKHULILA MUKAMAKABA NDALAMA KWA ZUNGU ENGLISH YANUYO

  • @HaroonKampepule
    @HaroonKampepule 2 місяці тому

    Olo chizungu akulankhula a deputy speaker chopoila heavy .zikuchita kuonekelatu chimizimizi too much

  • @UncleBusy-c6l
    @UncleBusy-c6l 2 місяці тому

    Panonso tikufuna chizungu chithe kunyumbayi chifukwa simumalankhulilako azungu kumeneko mumalankhulila ife amalawi tikufuna chilankhulo chathu kunyumbayi Kuti aliyese azimva ndinunomwe amene mukutiwonongela dzikoli ndichizungu chanucho

  • @SydneyMwale-u9w
    @SydneyMwale-u9w Місяць тому

    Eya afunika kutero ku yankhula chizungu

  • @robenallie6985
    @robenallie6985 2 місяці тому

    Malawi aziyakhula chichewa akafuna chizungu aayakhule home language is the best

  • @zumahmedison9672
    @zumahmedison9672 2 місяці тому

    Mhhj ayi olo kuno ku china amalankhula
    Chi china

  • @HaroonKampepule
    @HaroonKampepule 2 місяці тому

    Muziti chitsamunda . Kodi kuyankhula chizungu sikuphunzila ndi chida chophunzilira .Mupita ku china saziwa chizungu komatu as as amaphuzira kupanga machine osiyanasiyana . Kaganizidwe kubwelera mbuyo akaka kozimva kupelewela a Malawi tizinyadila chikhalidwe chathu

  • @IshmaelMusa-p5z
    @IshmaelMusa-p5z 2 місяці тому

    Kodi amwene zakulacha zikuti bwanji

  • @ThokohPrescotKalonga
    @ThokohPrescotKalonga 2 місяці тому

    Kodi adayambitsa ndani, zogwilitsa tchito chilankhulo chimenechi mu parliament yathu. We need to speak our language chichewa not za English zanuzo ayi.

  • @AshimayeGama
    @AshimayeGama Місяць тому

    I know hou to speak English Bat I didn't go to school u to Mr speak sir u speak English that English language is not for us use malawi letters tock chichewa my flaws malawi

  • @cassimyusuf6683
    @cassimyusuf6683 2 місяці тому

    Kape ameneyu, bwanji abwana ake oziwa English akukanika kutsogolera ziko kom kuba

  • @ClementinoAnerio
    @ClementinoAnerio Місяць тому

    Chizungu chilibe ntchito Lima chitukuko

  • @StevenFombe
    @StevenFombe 2 місяці тому

    Hesnt thete for ever. Check constitution of malawi

  • @wisdomchilanga723
    @wisdomchilanga723 2 місяці тому

    Zachizunguzo akutaya nazo nthawi chabe ,tikuwaona Ena akuyankhula zizungu zawo koma dziko likuwakanika kusogolera what's that? Tangoyankhulani your on language kumeneko ku parliament kulibe ma white people

  • @paulpaseli6310
    @paulpaseli6310 2 місяці тому

    Zamanyazi chakwela amayakhula English. Koma athu osauka tikupindula chan mu English yachikangawa

  • @gmxplayboy6559
    @gmxplayboy6559 2 місяці тому

    Aaaaaaa mmayiko anzathu mu nyumba ya malamulo amalankhula zilankhulo zawo. Even muzochitika zambiri amalankhula chilankhulo chawo, ndimadabwa kwathu kuno timakakamira chingerezi ngati kuti chingerezicho mchilankhulo chathu. Ndimadabwa ngakhale mmipingo ya mbiri kwathu kuno muwona kuti muli anthu akuda okho okha koma akulalikira mu chingerezi

  • @lastonmasoatenganji-bs5gf
    @lastonmasoatenganji-bs5gf 2 місяці тому

    Ufulu odzilamulira ulipati ngati tidzingolimbikira kuyankhula chinenero choti ngakhale ambilife sitimamva. Kodi mmesa amakakambirana za ife?

  • @JonesMuyaba
    @JonesMuyaba 2 місяці тому

    Zikomo aku parliament uko (deputy) English does not mean kuti ndiye kuti munthu unapitako ku school or kuti uli ndi maphunziro apamwamba ayiii...!!!
    Monga m'mene mukulankhuyo ikusonyeza si english yoti munapita patali ndi school,, even your grammar shows kuti nanunso simunafike patali nayo,, only that mwayi unangokugwerani...
    Pali maiko ena, ma members of parliament ndi ophunzira kwambiri, koma dzikolo akakhala mu parliament amangolankhula chilankhulo chawo cha m'dzikolo...
    For example; pali Tanzania, Mozambique, or even Zambia, etc...
    Ma nabouring countries amachita bwino ndipo ndi otukuka koma mu ma parliament awo salankhula zizungu monga ngat zimene mukutukumuka nazozo ayiiiii...!!
    Musamakhale ngati mukupanga za umbuli wotherathu.... Ndi anthu ngati inu mumalepheresa dziko kupita patsolo...

  • @tiyachisale9075
    @tiyachisale9075 Місяць тому

    Mwasowa chokamba kumeneko et

  • @GoalPhyoka-g7r
    @GoalPhyoka-g7r 2 місяці тому

    Debate stand up? Nkumati show us your grammar.

  • @AboudujanahMawulidi
    @AboudujanahMawulidi 2 місяці тому

    Awanso ndi achisilu kwabasi achina malema kunoko amakwapuka chipeli kapena suthu English ndichani??

  • @SaidiMbawa-st6bj
    @SaidiMbawa-st6bj 2 місяці тому

    😂😂😂😂 Achita bwino kwambiri dziko lathu ndilovesa chisoni mwana wa school form 4 English samatha kulakhula kupita ku South Africa kulephela kulumikizana ndi Amzungu bolaso azathu akumangochi amayesera

  • @endmwambene2766
    @endmwambene2766 2 місяці тому

    Azungu anatipepeletsa we African

  • @NosiphoMazibuko-e9z
    @NosiphoMazibuko-e9z 2 місяці тому

    Kd yemwe akufuna anthu asilangula English iyeyo mwiniwache sakutha kuwona kuti ndimbuli chisungu chomatuluka motere akachape lilime lake Kaye achotse chichiwa kamwa mwake alibe chisungu chabwino namulemba ntchito ndindani?

  • @DivineMercy-df2pu
    @DivineMercy-df2pu 2 місяці тому

    Chakwera amayakhula English ya sirwi rwii akupanga chani ku MW KUNO?

  • @edsonnyasulu5394
    @edsonnyasulu5394 2 місяці тому

    Apa zikuwonekelatu kuti nkhalamba za Ku malawi sizingathandize malawi saziwa kuti English chiyankhulo cha maiko ena monga ine ndimaziwa chichewa chifukwa ndakhala kwambiri ndi achewa pamene makola anga anali alimi mu ma farm a anthu ena speaker uyo ndi mbuli ya chabe chabe English si sukulu ayi koma ukayenda umatha kuyankhula ine English ndaziwila pano pa jon

  • @MalitaKapesi
    @MalitaKapesi 2 місяці тому

    Amalawi ndiife mitundu yathu ndiya chewa, romwe, yao,tumbuka, ngonde,tonga,sena komaso zilankhulo zina ngati ndaiwalapo; ndizachisoni iyeyo wachiwili nyumba yamalamuloyu agogo ake amamva chizungu, bwanji osakhala ngati anzathu kudziko la South Africa amakwanitsa bwanji kulowa nyumba yamalamulo aliyense ndichilankhulo chake bwanji?

  • @TestReznov
    @TestReznov 2 місяці тому

    Paliamenti nja kumalawi. Chichewa or English bola understanding ya mfundo yomanga dziko basi.

  • @IsmaelBilal-lh1pi
    @IsmaelBilal-lh1pi Місяць тому

    Ukapolo dziko mwatu momwe mmmmmm

  • @francismphande7181
    @francismphande7181 Місяць тому

    Malawi Parliament house is not for azungu. Here shows speaker ndi mbuli,sadziwa tanthauzo la Nyumba ya Malamulo. You are there to bring development to the people who elected you,not show off ya English. Maiko ena amayankhula their local languages and chituko dziko likunka chitsogolo.
    English si kanthu amwene!!!!

  • @TsalaniponDan
    @TsalaniponDan 2 місяці тому

    Apo nde zoonad ationetse nafeso

  • @FrancisStima-sc7zs
    @FrancisStima-sc7zs 2 місяці тому

    Ooooo apondiye zoonadi kkkkkk ationese basi

  • @ChemandandacassimMilanz
    @ChemandandacassimMilanz 2 місяці тому

    😂😂😂

  • @MadaalaYare
    @MadaalaYare 2 місяці тому

    Kkkkkkkk kwavuta 😂😂😂😂😂😂😂

  • @MaryNgola
    @MaryNgola 2 місяці тому

    😂😂😂😂😂😂😂