TIMES EXCLUSIVE - 4 MAY 2019 WITH ARCHBISHOP THOMAS MSUSA

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 23 жов 2024

КОМЕНТАРІ • 19

  • @hassammaulana4529
    @hassammaulana4529 5 років тому +3

    Ndakunvesani abishop koma Mr brain Banda akupasani ulemu kwambiri umakwanira keep it up times

  • @innocentosmanjaffer9264
    @innocentosmanjaffer9264 5 років тому

    thanks alot bishop pa mawu anu oti ngati sanachite pa zaka zonsezo ndie apange lero

  • @kenfer7755
    @kenfer7755 5 років тому

    Brian.. the bishop is right, a visionary reader can change Malawi in few year.. Thomas Sankara proved it within 3 years he changed the country for the better

  • @mariumkuyerbarak3691
    @mariumkuyerbarak3691 5 років тому +1

    Nkani ndiyimeneyo Arcbishop kuyambira 42:25 mpaka 42:58 " Yawa zaka zonsezi anali chonchi lero ndiye asinthe" Tamva tichita zomwezo.

  • @goodsonmbewe8187
    @goodsonmbewe8187 5 років тому

    21 may is too close my dear Malawi ,pliz vote well and no violence let love peace and unity lead

  • @geraldmatchado8306
    @geraldmatchado8306 5 років тому

    Big up bishop

  • @jjphi7137
    @jjphi7137 5 років тому

    Ambuye ayankhula bwino. Ena akukana debtae, kupita ku PAC peace declaration. Ine Abusa awa ali clear.

  • @abdulrafiquekalembo469
    @abdulrafiquekalembo469 3 роки тому

    Ndi mwa mijomba amene analowa chi khitisitu chifukwa cha zolandiralandira.komanso ngati panalibe blessings ya Makolo ndinu opanda tsogolo pa uzimuwo.

    • @ussimasi2458
      @ussimasi2458 Рік тому

      Inu opepepalatu eti chisakho ndiwekha ngati anasakha kupita ku chikristu ndi sakho chawo

    • @ussimasi2458
      @ussimasi2458 Рік тому +1

      Kuchisilamuko sikukhala zolandila landila

    • @FelixMpinda
      @FelixMpinda 5 місяців тому

      Chipulumutso ndi cha iwe mwini sizikugwirizana ndi makolo, he made a good decision. Following Jesus Christ is the best option ever one should make in life

  • @josephmkweza6094
    @josephmkweza6094 5 років тому

    Akanatchula amene amakonda iwowa

  • @nathannbanda3345
    @nathannbanda3345 3 роки тому

    I see, nice

  • @emilymanjakaisi4693
    @emilymanjakaisi4693 5 років тому

    And ine ndidabwa kuti mipingo yonse azimbusa ambiri amakwatira koma a Catholic okha sakwatira koma amachita zanseri ndiye kuti akuchita bwino? no iwowa amazela Anthu koma akuiwaira ntchito imene akungwairayo akutumikira MULUNGU amene amayang'ana za zonse zapoyera ndi zanseri zomwe

  • @alexpeteribrameja1819
    @alexpeteribrameja1819 5 років тому

    Alex Fest1 always Takulandilani

  • @emilymanjakaisi4693
    @emilymanjakaisi4693 5 років тому

    Apa ine ndikuona kuti Archbishop apasanayakhe chilungamo akukhala ngati akumbakira ndithu Anscombe, koma masiku ano zikuonekera poyera kuti ansembe andi masisitere amanyenganadi and amapangaso abuse ana ang'ono ang'ono nchifukwa chake ansembe ndi masisitere ambiri amaiko ena ambiri anatuluka

    • @FelixMpinda
      @FelixMpinda 5 місяців тому

      Osamanena za ansembe okha ayi komanso inu mudziyang'ane kuti mulibe cholakwa

  • @chariekasokag6893
    @chariekasokag6893 5 років тому

    Nde mwampeza kuti wotukuka dziko lanuno ,abishop chilungamo mulibe zitukuko zose zayalidwazi simukuziwona?tisiye mmanja mwa mulungu kut amenyele complain chipani cha Dpp APM ndi munthu olemekeza wina aliyese choncho amaopa mulungu