Greatly appreciated archbishop to may almighty God bless you & g e u More years of your life am really proud of your speech... Thus Indeed true thus good thoughts of a wisdom leader...🙏🙏🙏
I'm not a Catholic, I am an Adventist but I like what The Arch Bishop has said "Before we through stones at the bishops let us also look within ourselves". Truth and well spoke❤
My words goes to you Bosh, tengani mbali kuti anthu atukuke mumiyoyo yawo... osati muziwadyesa mawuokha ayi..... ambuye yesu anadyesa anthu nanuso adyeseni anthu.....
Ngati mudamverapo bwinobwino makalata aja si a andale wokha ayi. Mumakhala ma section osiyanasiyana mmakalata muja. So mumakhalanso mbali zina zodzudzula akhristu a Katolika komanso womwe sali akatolika. Mwachdule amalembera a Malawi as those who read them are not only Ctholics.
Kulankhula konveka bwino taphuzilaposo nafe tikuti zikomo abishop komaso a Banda. Pempho, potengela ndikumasuka kwanu pankhani ya ansembe anu, lolani kuti maganizo a anthu azipelekedwa koyenelela kuti mchitidweu utheletu chifukwa ndizinthu zonyazitsa mpingu. Kugula bank imene ija ndi effort ya akhristu eni ake ndiganiza choncho sikuti ndi bank ya ma bishop ayi koma ya ankhristu ndi anthu onse. Thanks for your openly kindness, you are just humble man.

Brave Archbishop Thomas Msusa
I'm not a Catholic, I am an Adventist but I like what The Arch Bishop has said "Before we through stones at the bishops let us also look within ourselves". Truth and well spoke❤
I like such an honest mind arc bishop! I also salute your brilliance in conducting interviews Brian!!!
My words goes to you Bosh, tengani mbali kuti anthu atukuke mumiyoyo yawo... osati muziwadyesa mawuokha ayi..... ambuye yesu anadyesa anthu nanuso adyeseni anthu.....
Bishop wa nzeru
Frankly speaking thank you ambuye
Muli bwino bwino kkkkkkkkkk wisdom 🔥🔥
Too much wisdom MOG
Zikomo ambuye arch bishop ,mulungu mulengi apitilile kukutsogolelani.
Father awa alibwino
Better
Father zikuchitika Maka ansembe akuthyolo Ku ana qkubadwa
NDANI ANATI SITIMAFUNA ZA MBIRI.....nafeso tufuna ma million....why not us
Ordinary Man and Men of the cloth can not be held to the same standards otherwise. Anyone can stand at the pulpit.
Kodi makalatwa mumalembera Atsogoleri andale okha kapena mumadzudzulana nokhanokha Akatolikanu?
Ngati mudamverapo bwinobwino makalata aja si a andale wokha ayi. Mumakhala ma section osiyanasiyana mmakalata muja. So mumakhalanso mbali zina zodzudzula akhristu a Katolika komanso womwe sali akatolika. Mwachdule amalembera a Malawi as those who read them are not only Ctholics.
Chipulumutso ndi chovuta Ngakhale ma bishope Anthu a m mabanja Naonso zimawavuta ku sunga chipangano
@@anthonynkhoma4265 njira ya bwino ndi yoti ngati ataona kuti nkhosa zawo zikusokonekera adzilemba ma kalata ndikuwerenga mmachalichi mwaomo. Koma ngati ndizokhudza boma adzilemberanso bomalo.
Anthu uyipa awa.they are nit very much into spiritual life,they pretend.Anthuwa are into worldly things and dominance.
Anthu oipa inu kwabasi, a khristu anu kumasauka inu mwagula bank
Kulankhula konveka bwino taphuzilaposo nafe tikuti zikomo abishop komaso a Banda. Pempho, potengela ndikumasuka kwanu pankhani ya ansembe anu, lolani kuti maganizo a anthu azipelekedwa koyenelela kuti mchitidweu utheletu chifukwa ndizinthu zonyazitsa mpingu. Kugula bank imene ija ndi effort ya akhristu eni ake ndiganiza choncho sikuti ndi bank ya ma bishop ayi koma ya ankhristu ndi anthu onse. Thanks for your openly kindness, you are just humble man.
Munayipangira campaign Tonse Alliance inu munatiponya mn'ganjo yamoto.mumalowelera za ndale kwambiri ini.bad people behind the bible
A khristu azikupasani ndalama chifukwa anthu munagura bank 😂