god bless you the Dc mulibe mbali and ine ndi Dali osangalala ndi tanva zoti adapita ku CP anthu aku vutika kwambili company ime ija kuli khaza komaso unve kwambili mwati menyela khondo
Bwana Kalindo! Mukugwira ntchito yabwino......Koma amwenyewa akupanga izitu popanga copy zomwe amalawi tokhatokha tupangirana....... check working conditions of many civil servants,,, check their salaries.......ngat boma silusamala za ogwila ntchito awo ma foreigners wa atisamala bwanji
More fire the DC I gave you more respect brother ur the freedom fighter of the poor people kip it up iweyo chilungamo umachiiziwa Neba ine pakwathu ndipa khoviwa near fomo secondary school go on brother tili pambuyo pako
Ku Malawi katangale adachuluka, mpake anthu obwera amatizunza. Mmaiko mwao sasekerera obwera or mwayi waganyu sungaupeze chisawawa. Ma China ndi amwenye ofunika kukhala nawo serious. Ambiri saperekanso misonkho ya ma business awo
Koma iwe ndi chitsilu kwambili bon kalindo umamutsata walakwa chani pakachitika chabwino amayamikila paka chitika choipa ma dzudzula mutu wanu uzigwila ntchito man vevaaaa the DC 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Inde mwana wa satana iwe lankhula momwe uthere bola ukulandila koma zindikila kuti mulungu adzanena nawe mulandu wa zonsezi satana sapulunutsa koma yesu ndiye poti aliyense makonda makonda aaaa mtumikileni satanayo ndi mtima wanu wonse koma mulungu amadziwa kuti pa mpando wa u president pakhala uyu palibe amadziwa chotero boma ndi lomweri Michael usi ndi yomweyi sakusintha
Amadana ndi bon kalindo ndi mfiti amaunikila anthu mupitilize❤❤
Pamenepoo
Your Confidence is our treasure. We respect you the DC🔥🔥🔥🔥. God bless you forever
god bless you the Dc mulibe mbali and ine ndi Dali osangalala ndi tanva zoti adapita ku CP anthu aku vutika kwambili company ime ija kuli khaza komaso unve kwambili mwati menyela khondo
The DC ,God bless you and protect you always
Mukutiimilira , God blees you ❤❤❤
Zoonad zinthu zafika ponyasa kwambiri muzikomuno zoti muli president kaya
His excellency The DC The Freedom Fighter Be forever ❤❤❤❤❤ That is what we call a Leadership
THE DC
Bon
You are a true activist, keep on your good work, we dislike nepotism
Uyende mu ma company a amwenye! 😢😢😢
Anthu akuzunzidwa vitumbiko mumba please please ma company a amwenye please
Big up boss mumatiimilira!!!!
Keep it up our DC
Keep it up mr DC❤
Inuyo Mani mmakwana,The Deeeeceee keep it up🎉
Bwana Kalindo! Mukugwira ntchito yabwino......Koma amwenyewa akupanga izitu popanga copy zomwe amalawi tokhatokha tupangirana....... check working conditions of many civil servants,,, check their salaries.......ngat boma silusamala za ogwila ntchito awo ma foreigners wa atisamala bwanji
More fire the DC I gave you more respect brother ur the freedom fighter of the poor people kip it up iweyo chilungamo umachiiziwa Neba ine pakwathu ndipa khoviwa near fomo secondary school go on brother tili pambuyo pako
V Mumba sikuti ndi osauka ayi ndi chifukwa chake akupanga zimenezo
Chakwela ngati Ali ndi munthu oziwa chito ndi vitumbiko mumba osati kamajekete kukuyu Richard nkumba zen zen
Big up DC
Zonadi muthuyo waonesa chithu chatengo wapatali mafuno apitilize❤❤❤❤
Koma iyi inali massive Mr president
Keep it up,big man. We salute you comrade.
God bless you
The great Man
God bless you the DC
Katundu waboma mmakwana boss man
DC tikumudziwa kale, udzingo ika video yakeyo timumvele bas osayangula kwambili zimatikwana ok
Ndipo very true😂
Very good boss
Lovely lovely the DC
Love 💕 this
The d c timakunyadilani ❤❤❤❤❤❤
Ku Malawi katangale adachuluka, mpake anthu obwera amatizunza. Mmaiko mwao sasekerera obwera or mwayi waganyu sungaupeze chisawawa. Ma China ndi amwenye ofunika kukhala nawo serious. Ambiri saperekanso misonkho ya ma business awo
Bon ,you are more than an activist . Can't you contest as
independent president of Malawi on 16 Sept
this year ????
Continue to give us updates the DC
The DC Umakwana .Keep it up❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤
💪💪♥️♥️♥️♥️♥️
Continue on that DC💥💥
Mumba Ali bho
Keep it up
Pitilizani kutipanikiza ndi chilungamo the DC
Nde wati dzina lija ndi CHALAKWE?
More fire,,lyi yakuma company a tea yi mupitilize
The DC, Mwana woopsa kwambiri
Born kalindo mo fire 🔥
Amadana ndi born kalindo ndi galu wagalu born kalindio oooyeee
DC is the leader that's great
That's true ,go on
DC ndimafuna airtel money number yako
Mumatha abwana pitlizan Ife timadalila inu
Ku sanaso apite akayitseke anthu akuvutika ma bwana akuzunza anthu
Kuipamtima bass
Ya minda ya tea ndimaona ngat ndimaona ndekha kut ngat ziko situpindula nazo
The dc 🔥
Kkkkk kuti Zikhale Kunoko Zikhale Kunoko Zikhale Kunoko 😂😂😂 the DC
Auzitse V.Mumba ayendere monse MMA schools amwenye akuzuza anthu mmene MMA Islamic school malipiro osafika 100,000 mmene zinthu zaduliramu chonde ndunazi zitamayendera monse MMA N.G.O anthu akugwirabe ukapolo akadandaula akumawauza kuti ngati sukufunai ntchito siya
❤
The DC🎉
The DC ❤❤❤❤❤❤
The DC president of the voiceless
God bless you ❤
Ine pokavota kukapanda kupezapo Zina la DC sikavota kabwererapo 🇲🇼🇲🇼🇲🇼
Km Sheikh mwaganiza bwanji😂😂
Real activist.
💯 sure
🔥🔥🔥
Amwenye ndi anthu oipa dziko lina lililose anthu awa ndi ma racists that is why Idi Amin adazawathamangisa ku uganda
Zoona mophikiraso mabulendi ayendemoso amasekera anthu mukati .
❤❤❤❤❤❤
wathuwathu Bon Kalindo receive your flowers while u r alive
Yaku estate ndiye ndikuivotera
Sana ya ku blantyre amwenye akuzunza antchito
Galu iwe shatap
Patumbo pako pamako galu iwe
Chiii DC❤
Amwenye anthu oipa enaso ndi ma China ofukira kuwaona bwinobwino
The dc
Mwati Zikhale😂
Makosana plz improve your voice ok
I hate amwenye sapanga chitukuko mu ziko lino only corruption mu boma Kuba ndalama kuzunza a malawi omwe akuwagwilila nchito,ndalamazo kumatumiza kwao
Koma iwe ndi chitsilu kwambili bon kalindo umamutsata walakwa chani pakachitika chabwino amayamikila paka chitika choipa ma dzudzula mutu wanu uzigwila ntchito man vevaaaa the DC 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Anduna mupitenso ku chigumula ku HMS mukaone nyasi zikuchitika
The dc nkhata bey tea ikuwabelaso a malawi
The DC 🎉
Koma yaaa walasa
Mau aphamvu
ACHALAKWE KKKKK
Well spoken here, nepotism is still in Malawi because of useless activist thanks Bone
Kkkkkkkkk koma president musanisekese ine mutu ukuniphwe
Tiuzen za kudulidwa munthu kwa mzinayi ku mulanje konko ife zonamizidwa mayaz
Teka
At Estate Mandolo daily with nsima ya m,'gaiwa
Nyimboyo imaveka kwambiri
The DC
❤❤❤❤❤❤❤😂😂😂
Number one
Ndipo kunena chilungamo Mr Mumba angobwela mochedwa komano ndi dolo, next government please musazayendele chipani uyuyu zamupaseni udindo.
Kuyamba ayamba bwino Mr Mumba bola zisakhale za nthawi ino yokha the DC Boooon Kalindo 🔥🔥🔥🔥
More fire 🔥 ❤❤❤❤❤❤

The DC❤❤❤❤❤
❤
The DC