MPHUNO SALOTA BASI ~ AKUTITU CHAKWERA AKANAZIWA NDITHU CABINET IJA SANAIWONGA KWAMBIRI CHONCHI EEEH

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 19 січ 2025

КОМЕНТАРІ • 33

  • @HerlbertKaalis
    @HerlbertKaalis 17 днів тому +4

    APM ❤❤❤❤❤❤❤

  • @DONNEXKhama-bk1gy
    @DONNEXKhama-bk1gy 17 днів тому +3

    We love APM cool guy

  • @AdaMussah
    @AdaMussah 17 днів тому +1

    APM ❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤

  • @HashrouYassin
    @HashrouYassin 17 днів тому

    Chakwera ndi mbuli yomwe siziwa zomwe ikuchita,savage kwambir uyu Garu ameneyu achoke basi

  • @Mahamudu-q6b
    @Mahamudu-q6b 17 днів тому +1

    😭😭😭😭😭Mcp

  • @GiftMusorola-l2o
    @GiftMusorola-l2o 17 днів тому +2

    Palibe zomwe mungapange kulalataila wina singasinthe malawi

    • @WarriorKB-l3i
      @WarriorKB-l3i 17 днів тому

      Iwe ndi akwanu kavoteleni chikangawa koma ife wathu ndiyemweyi mufune, musafune dpp ikulowa boma chifukwa ndiyomwe tikukavotela iweo ndi zako chikangawayi ndichani chamzeru mwatichitira dxiko muno? Inu dzisilu kwambiri ngati mulibe dzolankhula mukhale chete anthu a satanic inu.

  • @JamesTeacher-b3o
    @JamesTeacher-b3o 17 днів тому +1

    Iweyo ulimgululo ononga dzikolino sindiweso wabwino ayi

  • @OfesiMakuwalo
    @OfesiMakuwalo 17 днів тому +2

    😂😂😂😂😂 koma nakhumwa eish 😅

  • @LawrenceMkweu-u2f
    @LawrenceMkweu-u2f 17 днів тому

    Mulungu atithandize chilichonse a president angapange ndichoipa KODI palibe zomwe iwo apanga mdziko muno? Nsanje ndi undani ndiwomwe wakula izi sizitithandiza a Malawi

  • @thomasbotha9790
    @thomasbotha9790 17 днів тому +1

    Kkkkkk dad vote ✔️
    Zinthu zakwera ndi chakwera Kkkkkk chakwera alephera kuyendesa dziko, Chilichonse chakwera mtengo ndi chakwera? 😮

  • @MussaAli-h4i
    @MussaAli-h4i 17 днів тому +1

  • @GiftMusorola-l2o
    @GiftMusorola-l2o 17 днів тому +3

    Anayamba Ndi muthalika pomwe anali M'boMA ndipo mavutawu sangasinthe olo Boma litasintha peter aziwe kuti zomwe akunenazo sizingasinthe

    • @FrankSaidi-vi8dn
      @FrankSaidi-vi8dn 17 днів тому

      @@GiftMusorola-l2o mbuyanga koma nanga zinthu zinafikapo apa

    • @WarriorKB-l3i
      @WarriorKB-l3i 17 днів тому

      Bvuto ndiloti mmene amalamulira peter unali usanabadwe, koma ife tagwilizana kuti APM wina afune, asafune ndiyemwe tikukamvotela iweo ndi anthu akwanu kavoteleni mufunazo koma ife wathu ndi APM ndi Dpp 💙💙💙💙💙💙💙💙 boma!

    • @petrokagona1708
      @petrokagona1708 17 днів тому

      Kodi mukati adayamba ndi Peter muntharika kuchita zimenezo: Are you serious kuti ife tidaika tonse alliance kuti idzapange zomwe amkapanga Peter? If so why did you vote Peter out of gvt? Kususuka kukuphetsani. Dziwani kuti ngakhale mukuyankhula motumbwa chifukwa cha ndalama zakuba koma anthu akuvutika ku Malawi kuno zomwe sizidawonekepo?

    • @BrendaJailosi
      @BrendaJailosi 17 днів тому

      Vuto tinamudukitsira panjira km iye uja kwacha sinagwepo chonchi sikuti tikukana zinthu zimavuta km pano it's too much sugar anafika pa 3000 ai pena tiyeni tizionanso zambuyo osangoti popeza ali kutsogoro wo nda achibale ai ngati ine ndilibe m'bale ku boma km mavutowa tikwaona ndithu km kusowa chilungamo

    • @ElizabethMajiga
      @ElizabethMajiga 17 днів тому

      Ndikuyakhe ife ndi pita timadya ndikumakhuta feteleza anali patengo wabwino,,Rand timasitha R1 pa K40 to K50 simakwela simasika koma amunanu achakwelawo lero R1 tikusitha pa K170

  • @WarriorKB-l3i
    @WarriorKB-l3i 17 днів тому

    Mmutu mwa chakwera mulibe chilichonse mamina okha okha dziko lili pa mavuto akulu iye akukweza chiwelengelo ca nduna zitithandiza chani? Nyau zimenezi caka cino zidzipita ku kasiya sitikudzifunanso palibe akuchita. APM ndiyemwe tikuvotela wina afune,asafune a malawi program yathu ili choncho.

  • @LimzeySande-b9n
    @LimzeySande-b9n 17 днів тому +1

    Chirungamo ichi

  • @LawrenceNdala
    @LawrenceNdala 17 днів тому

    Inetu ndimayesa chimanga chakwera chifukwa cha low production against more maize demand emanating from 4 poor
    consecutive Seasons.....
    School me, please.

  • @MaxChidothi-n3y
    @MaxChidothi-n3y 17 днів тому

    Andale ash

  • @InacioCement-t7n
    @InacioCement-t7n 17 днів тому +1

    Tabvutika kale basi

  • @FrankSaidi-vi8dn
    @FrankSaidi-vi8dn 17 днів тому +1

    ai zilibwino pajatu munthu sanong'oneza bondo popanda zammbuyo

  • @daviechannel8603
    @daviechannel8603 17 днів тому

    Panyopawo

  • @JustinKondowe
    @JustinKondowe 16 днів тому

    APM our Trump 2025

  • @DicksonEvance-h6g
    @DicksonEvance-h6g 17 днів тому

    APM machine